Nonsenu amene mutukwana Abishop pachifukwa choti ayankhurapo za imfa yachilima mlungu akulangani kumapereka ulemu ndi bwino
@KestherMkandawire10 сағат бұрын
Ulemu ukuyenera kupta kwa Mulungu osati bishop yemwe akupanga zandale chifukwa cha ndalama.
@KunjeFarouk4 сағат бұрын
Ndipo inu
@MaryJamali-w7t6 сағат бұрын
Alibe dzeru amene akutukwanayo
@MarySinjirani12 сағат бұрын
Ma bishop musaope, musafooke, musatope ndipo musakhumudwe imani pa chilungamo chanu komatu chakwela chakwela chakwela ambuye chonde imvani kulira kwa Malawi 😭😭😭😭😭
@TriciaMalikebu13 сағат бұрын
Thank God for our bishops, the church needs to stand on the truth & proclaim it. We rejoice when persecuted because of proclaiming the truth of the gospel 🙏🏽
@YamikaniMituka6 сағат бұрын
Ma bishop sakuwadziwa amenewo ,,,akalemba kalata dziko lonse limadziwa ,,,ndipo kamuzu anachoka chifukwa cha ma bishop akatolika atalemba kalata ,,ndipo kamuzu anali oopsa kwambili koma analimbana naye mkumufoola aaaaa Mulungu atichitile chisoni ndthu
Yakwiya ndi mizimu,,akusowa mtendele anthuwa ,,nde mukulimbana nawowo amaima pachoona Ukalimbane ndi ma bishop akatolika kkk akusewela ndthu ,,,
@WisikiBlack-gj4gu5 сағат бұрын
Bishop Susa allah akudalitseni,allah salephela, ndipo satana alibe mphamvu yoposa ya allah ,alihamudulilah allah wachifundo , allah mutetezeni bishop uyu ndipo chilungamo chiende ngati madzi,,zili poela allah kuti chilima anachita kuphedwa ndi chakwera, allah phulumutsani malawi 🇲🇼
@GraceShaibu-i9d10 сағат бұрын
Iwe chakwela kumkuyu chimwendo zikhale mukamati boma ndilomweli mukuzina miza kwambili chakwela sakulamulila dziko la malaw pazitsongoleli wose president olempela okanika osanganizila za ife 🇲🇼💪💪
@henryphiri61008 сағат бұрын
Akunama utsogoleri okanidwa ndi mulungu.tiyichotsa ngati mu 1994 musadandaule ikuchoka iyi. Muona kunali Young Poineer ndi Youth League. Analephera.pachipanda ma bishop bwenzi pamenepo.auze Ana a 2000
Mndani amachita advise MCP as a party. Ali ndi alangizi opusa mission yopha Chilima sinayende bwino, pano akutuma gulu kutukwana ma bishop nso. Asaiwale kuti Chilima anali ndi 1.4 million and ma bishop nso Ali ndi anthu omwe amawakonda ngati anthu ndipo kupanga chipongwe anthu amenewa ndi kulakwitsa. Ndalama sizigula mavoti. Atengere phunziro pa momwe analuzira Zikhale atepereka ndalama zankhani nkhani. MCP find better advisers
@chimwemwemuwalo242614 сағат бұрын
MCP MCP!!!! Iyi ipalapatika sure padziko lapansi pano
@PriscaMussah10 сағат бұрын
Nde mumafuna ma bishop wo azingovomeleza zonamqzo??
@GeoffreyGondwe-pk6sy13 сағат бұрын
Chipani cha mcp chidzathetsedwe chikadzatuluka mboma
@SydneyNkoma13 сағат бұрын
Atumiki amulungu amaima pa chilungamo basi mutukwane momwe mungathele koma nkhani ndiyakuti alipo wina mpaka pano alimoyo ndipo anaona zose zomwe zinachitika ku chikangawa patalike pafupike anthu adzadziwa choonadi
@IreenMwachande8 сағат бұрын
Ndithu akupasani 90 days kuti mutule pansi udindo ma bishop ake siameneyo samalani pofuna kuyakha kwa ma bishop akatolika afunseni anzanu mbuyomu kuti zinali bwanji mukasitsa volume inu amcp
@Randy-er2xo12 сағат бұрын
Akulimbana ndi mabishop akatolika akunamatu ndipo chakwera adikire kalata samaopa ai mitunda iyi
@DavieLester7 сағат бұрын
Chakwera watipha basi
@feliciajohn604111 сағат бұрын
Chakwela ndifit
@RexMatchado10 сағат бұрын
Aliyense ameme wayankha zonyoza ma bishop Mulungu awapasa chilango chomwe ana amanyoza eliya anawina.period.
Anthu omwe akupanga breifing ndi akuba adya ndalama agalu achabe achabe ati concerned faith leaders akuti?? Zachamba basi.
@REMIGIUSKANONGWA-r7i13 сағат бұрын
It reminds me about the "myth of the cave".
@WysonChilonga13 сағат бұрын
Titukwaneni akatolikafe, September ndi pompano mutifuna
@EvansKachulu13 сағат бұрын
Vuti la anthu amadana ndi munthu kapena mipingo kapena azibusa achilungamo amafuna onseee adye chibanzi then aphese anthu ochuluka Koma timaenela kuasapota mabishop ngat amenewa awapase Moyo wautali ndiochepa amabwera poela Chikangawa ndiabale Ako muziona tukwanani Mene mungathele
@paulbanda963813 сағат бұрын
Ngakhale nthawi ya Dr,H Banda ma bishop atatumiza chikalata ananenedwa, I'm sorry, a kamplepo kuluwa ananena fisi ndi, chakwera wakuba anawabela amalawi kugwilisa ntchito mau oti tikhululukireni ndine mu busa,
@augustinechibbalazi889712 сағат бұрын
The problem is that even religious leaders are divided: Some are democratic while others are kleptocratic and money- minded leaders.
@IsabelLuka-i8f12 сағат бұрын
Ndale nzachabechabe eish!!!!!!😢
@henryphiri61008 сағат бұрын
@@augustinechibbalazi8897Chilima anapha, bottom line
@henryphiri61008 сағат бұрын
@@IsabelLuka-i8fzabwino koma Chakwera wationjeza
@WarriorKB-l3i13 сағат бұрын
Ndimanena nthawi zonse kuti mcp ili ndi msanje ndi dpp simwaona? Nkhani njakuti akudziwa kuti APM akhala ndi molalo yochuluka kuposa chikangawayo ndicifukwa anamulesa. Cifukwa panopa a malawi tikufuna APM osati chikangawa ai.Ndipo mcp ili ndi tsoka, yasekeka mmakutu mabishop akunena chilungamo awa koma iwo akuti ai imeneo nde mphamvu ya satanic yo. Lipoti limeneli lija mulibe ciliconse camzeru.Black box ibwele apa itiuze za kucikangawa, adad osadanda inu pa low palibe cingatisinthe maganizo ife 2025 APM ndiyemwe tikukamvotera.Dziko lathu panopa mulungu wakwiya nalo kwambiri chifukwa ca ulamuliro wa chikangawa.💙💙💙💙💙💙💙💙💙.
@DalitsoZabata12 сағат бұрын
Mau amene nd m'ganene nd zikomo ambuye
@LanjesMallick13 сағат бұрын
Thanks Mr 🙏
@LuckiaIbrahim7 сағат бұрын
❤ Mofire Mr bishop akunama
@Mirriumkamwendo13 сағат бұрын
Anthu ku Malawi mmadana ndi chilingamo ,munthu akuyankhula chilungamo koma kunyozera
@CosterMustafa-m6h14 сағат бұрын
Ndipo inu😢
@LivaneMsyamboza13 сағат бұрын
Osadandaula mulungu wathu ndiwamoyo ndipo yense yemwe akunyoza ma bishop mulungu awalanga ekha ndipo awonekera ng'amba ndipo tinakafinya ma kolona
@elhananmwenda36868 сағат бұрын
koma yeah 😰
@GrecianMaganga11 сағат бұрын
Mbusa km iwe ulemu wanu kukhuzika km uku
@REMIGIUSKANONGWA-r7i13 сағат бұрын
Ndi pamene timadziwa kuti boma likugwa.
@BillyBentryMunthali6 сағат бұрын
Ukumva kupwetekadi nanga si ulikudzuwa
@CostasNyirenda12 сағат бұрын
Keep on
@IbrahimUseni-p8f10 сағат бұрын
Akutukwana ndindani
@AnishaMoosa-ej7yr14 сағат бұрын
ashh life is hard
@RaphaelWinford-t7u2 сағат бұрын
Zitsilu za atsogoreli a mcp asatanic afalisi ....
@EsnartGirivin10 сағат бұрын
Nkhondotu izi zimayamba ndi azibusa
@andiwochishadreck375314 сағат бұрын
Ngati ali ma dolo atukwane pop
@Randy-er2xo12 сағат бұрын
Mmanja mwako game charger ukunena zoonadi ziuze zitsiruzi
@0wenNkhambule5 сағат бұрын
Zoonad auze
@AlexanderTraffick13 сағат бұрын
Apapa tingoupanga Ulendo waku state house.Asogoreri achipembedzo Cha chisilam ma bishop ndi Akuru Akuru ena amipingo yosiyana siyana. Tatiyeni tigwirane manja tonse polipurumutsa dzikoli.Tatiyeni tisitike miyoyo yathu popita ku state house konko
Anawapusisa chifukwa cha makhwala nyanga zithumwa akulu amenewa
@FrancisNyayi14 сағат бұрын
Apapa tudikira akubanja basi chete
@chirwaellace10939 сағат бұрын
Tsiku lizakwana
@HalisonSolomon11 сағат бұрын
TATIUZENI INU A MIDIA MUMAPANGA BWANJI KUTI UTHENGA USIFIKA PAMENEPA MUNTHU AKAYANKHULA TIUZENI NAFE TATOPA NDI BOMA ILI TIKUFUNA KULIUZA CHIRUNGAMO
@GiftBello-v1i13 сағат бұрын
Chilungamo ndi chowawa ,
@REMIGIUSKANONGWA-r7i13 сағат бұрын
A sign of the fall.
@TanazioBanda-i9y13 сағат бұрын
Ana ena ananyoza mtumiki wa Mulungu nthawi yomweyo Mikango inawadya, DIKLAN 2025 Mulungu achita monga mwa mphamvu zake........ munthu wa Mulungu, sanyozeka!!!
@MolesBrown13 сағат бұрын
Atumiki amulungu sakhala pati ndidziko ayi awa ndi atumiki amafano amapembedza mafano Mau amati musakonde dziko lapasi kapena zadziko lapasi awa si atuumiki amakhala bize ndi zadziko
@WysonChilonga13 сағат бұрын
aaaa zinalembedwa pati m'bible,chikondi cha dziko lapansi achionetsa pati??,paja mdima umadana ndi kuwala eti?, chanzeru chomwe chiri mu report mliti😢😢😢
@WisikiBlack-gj4gu5 сағат бұрын
Baibulo liti limenelo, bishop susa is number 1 mumalawi muno ,ndinu nokha bishop wachilungamo phulumutsani 🇲🇼