And the surprising thing is that most private universities are only offering liberal arts. Kuopa to offer Engineering, Medicine and Applied sciences. Aliyese now wants to teach Political Sciences, HRM and Law.
@mutafireАй бұрын
exactly...!
@MGSE4663Ай бұрын
After my secondary education… I went straight to Nasawa Technical College… and I'm a welder now… yes 👍 ndikuthamangisa zingini apapa
@SamuelNandolo-s5wАй бұрын
Am a tailor now kudya ndalama kkkkkk😂😊
@lonjezompaso9512Ай бұрын
@@SamuelNandolo-s5w good move
@mtsitsaАй бұрын
Chilungamo chenicheni. University education should be intended for those who are academically inclined and should be geared towards producing high-quality research output to foster innovation. Only the best academic minds (i.e., academically gifted) should go through the university track. Sizaaliyense! We need more people in the trades (i.e., vocational skills). Anthu ambiri ali ndi maluso osiyanasiyana ndipo ntchito zamanja zikhoza kuwapindulira komanso kupindulira dziko.
@PhiriJohn-b9yАй бұрын
After finishing my secondary, I became a hustler.... Zama degrees is a wast of the time
@mutafireАй бұрын
@@PhiriJohn-b9y it's not... munthu wa Master's simungafanane naye ...koma sionse akuyenera kukhala ndi Master's
@PhiriJohn-b9yАй бұрын
@@mutafire Long ago it was true to say "Education is the key to Success" but now it's the different story Man...
@blessingsbandulophiri769Ай бұрын
Very true
@peterthawiАй бұрын
😂😂😂😂😂😂😂 wagwaza,aise
@kolwanigondwe9868Ай бұрын
It's not a weste of time bro, the problem is that we want to get educated to end poverty. School enriches us with knowledge that benefits humanity
@mornalisamkwezalamba1259Ай бұрын
Thanks Morton👏👏👏
@Dee-h7cАй бұрын
Cheers 🍻 🎉🎉
@goldenselenje686Ай бұрын
You are right, in fact in USA they fund PhD based on benefits to be realized from that PhD research area. And they fund that be via assistanceship or fellowship and it's the University and not govt
@HopesonChembekezoАй бұрын
Umandiwaza aisy siname umakwanila
@andrewchalimbanakanyinji5434Ай бұрын
You are so damn right
@innocentchikwakwa6277Ай бұрын
Morton ise tinjilire kochi sono aaah,nase takhumbanga degree
@richardkamwezi9297Ай бұрын
What camera are you using?
@mutafireАй бұрын
go pro her 10 black
@MlengaChituteАй бұрын
Ine vep singagwireso pano kuthamangise zingin bas zopusisana ayi
@kondwanimoseschirwa7804Ай бұрын
Nowadays these public universities alowa business. Thus why akupikitsana intakes other than quality and relavance to the world economy
@GeorgeChiwandaАй бұрын
O Kuona ma tv programs apa Malawi zazii zenizeni mmalo moonesa zinthu zutulula dziko koma kuipo akuti gospel yaanthu amayamba komaso akuti zachilhalidwe zakusimba basi. Maiko azathu ngati Japan amacheza ndi anthu azaulomi momwe akupangira o ma engineering new developments kapena ma foundations azinthu zaluso o agriculterkoma kumo mmm. Mibawayo akuti sapota kusowa nkhani zoikapo. Koma akangova kt Malawi yawina ka game eeee kutopesa kuzivera. Pomwe azathu sazitengerapaka 10 hourskuikapo ai😊😂
@PriscaAtupeleNyirendaАй бұрын
MBC amachita kulawilira kuika news za ku Japan ndi 11:am zachani?😂😂
@Mazizi26Ай бұрын
Umwa chani aise
@stanfordmuyilaАй бұрын
Iwe degree Yuko ndi field tanning.?
@jeremiahmemmanuel9988Ай бұрын
Nde zomwe zikufunika Morton apapa tiyeni tiwathamangitse akulu akulu wa abwere achinyamata basi 😂
@GeorgeChiwandaАй бұрын
Zomwe ukiganizazo kuzizila iwe sukudziwa kt akhale ambili ndiene anali ndi basic knowledge kaso ngati Malawi anachitako bwino ndiakale. Koma maboma ama yooh ndiamene akupisitsa anthu. Chilichonse chaluso kutengera momwe tinayambila tikanapitiliza bwino pano tili pabwino. Nkikumbuka kale kuno kumapangodwa assemble magalimoto ku pew tomato zonse inali ndi Chevrolet engine zomwe tinapitiliza pano zina zikuumbidwa konkuno lero kulibe lasanduka dziko lokhala ndi ma degree koma opanda ntchito bola ine ndinapanga yanga chifukwa nachitilaimboni kt nzotheka kupanga even engine koma Malawi walero akufunaukhale wa dpp kaoena ngati ili yolamula mcp ukhale wavhipami ndie akuthandiza enafe tili nzambili. Koma siyanha,anidwa ai. Black is blind and blank brains
@peterthawiАй бұрын
umakwana Morton
@VetaerhPhiriАй бұрын
Umakwana Morton
@handsomenkonde2552Ай бұрын
Ma degree a Chamba Kkkkkkk
@GomanHumphreyАй бұрын
Komato 😅 Moro kumene ukuendako haaa
@brianmangulenje660Ай бұрын
Facts 🤝
@HuaSDORRAWUАй бұрын
Ine school ndilibe nawo ntchito uyu akunena zoona iya
@luciamwanza-mf3fdАй бұрын
Koma ndaseka😂😂😂😂
@chancymzama7478Ай бұрын
ati HIV management
@imranjihad1528Ай бұрын
Wayamba kuoneka ngat nchina😅
@mutafireАй бұрын
ah ah...akulu akulu
@Prescort-kk2jwАй бұрын
😂😂😂😂😂
@lonjezompaso9512Ай бұрын
painful truth
@samuelsamirawjohns2671Ай бұрын
Muli kachilungamo koma muuthengawu
@AlexKaunda-ny2egАй бұрын
Kodi ukudyaso achule kumeneko wanenepatu
@NelsonMd-x5hАй бұрын
Painful truth
@SamuelNandolo-s5wАй бұрын
Koma chi baghya chinabweratu
@MrMagomboАй бұрын
Achimwene a Unima akuba ku bomamu ndi mma company a boma. Sukulu yo I differ ndi inu anthu apatseni aphunzilo ambiri, akhale ozindikila. Chimene chafuta ku malawi ndi kuba kwa anthu aku CHANCO. LAWYER NDI JUDGE NDI WOKUBA ANAPITA SCHOOL IMODZI. AMANGANA BWANJI? NDIPO ENAWO AMAYENDA LIMODZI KU COLLEGE
@IndianaderickАй бұрын
Only reality
@josephsilungwe6893Ай бұрын
Now you can agree with jb how can you waste too much time studying politics doc?