Ndale za Chipani chopsyodza Mafinya Za Uchitsiru. Mukubwera ndi imeneyo mukuona ngati muyiwalisa za Anthu munawapha Ku Chikangawa? Ayitu palibe kuyiwala apa. Munapha Anthu Osalakwa ana a Njoka inu 🐊🐊
Vuto la DPP limafulumila kulankhula koma samapanga kanthu pamene MCP mmangozindikila zikwanje zatuluka
@ChifundoZimba-jh7dhСағат бұрын
Mene anabwera chisale central region tinamusiya kupanga sokhano ku central region sikuti iyeyo ndiwochenjela koma democracy si nkhondo that's why tikulora kuti zitero
Mukuyankhulazi Ngati ndizanzeru lero. Koma Kodi zikwanje Zanu munazionetsera ku Lilongwe KO kwa anzanu muyetsa kuti a Malawife sitiludziwa za inu. Dpp iyi mwina yangonena mau amene akuwawani koma inuyo mudazichita idzi ku Lilongwe anthu anaopyedzedwa inu boma Muli konko Y?? Malawi tiyeni tikondane. Chidzadziwe nchipande powomola nsima and This is through voting. Though tikumva zambiri Zama leakages. Tionetsetsa tisanafike povota kuti Kalembelayu wayenda bwanji situlufuna ma vote obera ayi.Malawi ndi wanthu uyu tisazunzike mdziko lanthu lomwe. No nono.
@GoodsonLevison-r1rСағат бұрын
Panyopanu amcp ndimahule anuwo kod zikwanje mukupanga zja mwaiwala kod kangat mukupanga chipongwe adpp ?? Munaphwanya magalimoto kuvulaza wanthu ayi dekhani muona kusogoloku ,,,, coz mwaziyamba dala
Zoti ndi mwana wa JOHN TEMBO nzopeka,kod anthu anagendedwa kubowe kuphwanyidwa magalimoto a Dpp sumaziona
@ChiyembekezoNjolinjo2 сағат бұрын
Mul ndi chibwana inu a mcp, km mutulukabe m'boma, km mukatuluka m'bomamo simuzalowaso m'boma, mesa a police-wo ndi anu, mudandaura chani pot dzikori ndilanu
@GodfreyMitiyaniСағат бұрын
Muuzane anthu onse sakukufunani ku Malawi kuno. Eya kuphatu mumagumuladi
@DanielJuwawo-s5n5 сағат бұрын
Komatu DPP yavutitsa kwambiri mwaiwara kt ndinu nomwe munapha achina chilima ndi achipan chanji kodi adatenga chikwanje aja
@WillyNyirenda-l7hСағат бұрын
MCP ndi DPP zanu mdizimozi. Zikwanje ndi zanu anthuwa sakumangidwa. Osanamiza anthu.
@ChifundoZimba-jh7dhСағат бұрын
Chilima koma DPP munya muwona zachilima zadziwika kuti inali ngozi
Bwanji simunadzudzule za ku mbowe zija because it was more serious than this one by hon musowa
@ChristopherJumuСағат бұрын
Patumbo PANO nonse a MCP. Kod mmesa zomenya anthu munayamba ndinu?? Lero mukufuna ntendele chifukwa chot DPP yayamba kubweza?? Tikuswa kumene agalu okupha Inu. Maka Maka iwe okula mutu iwe chimwendo banda ulipila magazi a anthu aja unawapha kuchikangawa aja
@WILFREDBANDA-o3r4 сағат бұрын
DPP ili desperate ndi utsogoleri koma sizitheka. MCP m'paka 2030
The last time I checked, MCP was in the streets demonstrating for the then MEC chair to step down. Have you known the process for appointing the chair just now? Jane Ansah munangodana naye eti?🤔
Lilongwe ndiyi 1900000 rular 315000 Lilongwe urban totals Lilongwe 2215000 koma wina alira basi
@JusticeChasweka3 сағат бұрын
Mary Chilima akudandaula ndi mabanja nine aja afiti inu a MCP Mr and Miss Chikangawa
@FunnyNyirenda-m5k5 сағат бұрын
Zosatheka DPP kuwina inalephera kale asakhare ngati abwino lero
@JamesJonkha-y7t35 минут бұрын
Zisilu
@AnsaAsante11 сағат бұрын
Ine ndawona chomwe a kumva kuphweteka nachimutuyu sonkhano wakamajekete uja siunazaze anthu ngati mene anazazila ku DPP kamajekete siuja amachita kugawa ma 10,0000 kuti ayankhe kuti kwacha 😂😂😂 lelo a kulila poyela ndiposo guys mongokumbusana a mcp sinawinile man to man inawinila pasewu monthandizidwa ndi chilima lelo kulibe tiyeni nazoni