Ku Malawi konse nyimbo iyi Ili pa number 1 . Azimayi akuwoneka achilengedwe ndipo ndi 100% mmene tikuyenela kuwoneka munthu wokhulupilira. Ambuye akudalitseni mochuluka azimayi
@AlphonsinaLupiya2 ай бұрын
I'm always encouraged each time I listen to this song 🙏🙏🙏 I'm humbled, from Zambia
Nyimbo iyi imandikumbutsa nthawi imene ndinaluza azibale anga 5 pakamodzi ndipo moyo unali owawa koma nyimbo iyi imasisimura ndikulimbitsa moyo wanga 😭