MAFUNSO AMTOPORA OMWE ATOLANKHANI ANAFUNSA KU PRESS BRIEFING YA DPP LERO ZOKHUNZA CONVENTION

  Рет қаралды 23,440

Makosana

Makosana

Күн бұрын

Пікірлер: 157
@gkay-striker
@gkay-striker 2 ай бұрын
DPP MY VOTE
@PreciousBandah-l2r
@PreciousBandah-l2r 2 ай бұрын
Yako ife bro mcp back amalize kukoza dzko
@DickensChirwa-by5jt
@DickensChirwa-by5jt 2 ай бұрын
Fact​@@PreciousBandah-l2r
@BenjaminKamanga-p8w
@BenjaminKamanga-p8w 2 ай бұрын
​@@PreciousBandah-l2ryimalize kupha anthu kkkkk
@NancyNyirenda-v9o
@NancyNyirenda-v9o 2 ай бұрын
@@BenjaminKamanga-p8w eya paja idayamba kare kukuphela amayi ako ndi bambo ako🤣
@BenjaminKamanga-p8w
@BenjaminKamanga-p8w 2 ай бұрын
@@NancyNyirenda-v9o chikangawa
@Abdullah-u6z9s
@Abdullah-u6z9s 2 ай бұрын
Congratulations APM
@elizasingano
@elizasingano 2 ай бұрын
My vote
@RABSONSIKELO
@RABSONSIKELO 2 ай бұрын
Tangotchulan total budget
@CosmasChikwindi
@CosmasChikwindi 2 ай бұрын
I can see Dr Nankhumwa akukhala VP wachakwera 2025 ndipo azawina chifukwa DPP inatikwana🎉🎉🎉🎉🎉🎉❤❤❤❤❤❤❤
@MaritaBanda-p4z
@MaritaBanda-p4z 2 ай бұрын
siyani kulota akulu
@EllahChikwatu
@EllahChikwatu 2 ай бұрын
Akulotadi
@BenjaminKamanga-p8w
@BenjaminKamanga-p8w 2 ай бұрын
Chamba chokukuta sadya aan😂😂😂😂
@KondwaniNguleti-x1q
@KondwaniNguleti-x1q 2 ай бұрын
APM ndi dolo ndipo akudzalowanso m'boma mufune musafune agwape a Mcp inu
@NancyNyirenda-v9o
@NancyNyirenda-v9o 2 ай бұрын
@@KondwaniNguleti-x1q tiyeni tidikile nanuso mwina mufaso simufika nthawi yama vote aaaaa
@BenjaminKamanga-p8w
@BenjaminKamanga-p8w 2 ай бұрын
​@@NancyNyirenda-v9okomabe APM ndi dolobe
@NancyNyirenda-v9o
@NancyNyirenda-v9o 2 ай бұрын
@@BenjaminKamanga-p8w dolo kuti apa kuzolowela za manja lende basi kumalimbikila pena nsima yokha izipezeka
@kingsleyhopematchaya5184
@kingsleyhopematchaya5184 2 ай бұрын
​@@NancyNyirenda-v9okomatu aliyese alindi pokomera pale koma eine ngati mlimi WA fodya aaa ma no sale sindifunaso dpp pano alimi tikuva kukoma
@NancyNyirenda-v9o
@NancyNyirenda-v9o 2 ай бұрын
@@kingsleyhopematchaya5184 eti bwaaa ndiye wina aziti agwape pazokonda zathu
@WachiyawoWangalusa
@WachiyawoWangalusa 2 ай бұрын
Nankumwa.ndi.wa.mcp.
@VictorBanda-tq5ob
@VictorBanda-tq5ob 2 ай бұрын
Muthu akuknik kulankhula akufunika kumuzi azikaweluz milandu niadzukul awa
@MosesDzonzi-em5px
@MosesDzonzi-em5px 2 ай бұрын
Aaa zaaziii mukuchita kukanika kuyakhula, khalamba inu, mkamwa mwadzadza malovu ngati mwa a APM ine siningakuvotereni.
@NikolasNanawe
@NikolasNanawe 2 ай бұрын
mmmmmmm my vote MCP ❤❤❤❤
@Fanzo-h2l
@Fanzo-h2l 2 ай бұрын
Munthu atopa ndi congress yakupha anapha chilima pamodzi ndi anthu 8 aja chipañi chakupha ife ai APM 2025 boma mufune musafune nyau Inu mubwelera kudabwe 2025
@adamashrafi5875
@adamashrafi5875 2 ай бұрын
Unorganised party Zogwetsa ulesi mmene akuyankhira mafuso 😂
@FrancisChisuse-dc9ok
@FrancisChisuse-dc9ok 2 ай бұрын
So APM ,mix Chaponda nkhalamba zokhazokha DPP must be serious Zee generation singalole zimenezo
@mabvutochimbalame
@mabvutochimbalame 2 ай бұрын
Ukunamiza ndani miseu inamunyela unamize alomwewo
@PreciousChlima
@PreciousChlima 2 ай бұрын
APM my vote
@KennedyPhiri-h9h
@KennedyPhiri-h9h 2 ай бұрын
💙💙 DPP boma basi afune asafune ikutenga and inu atola nkhani amalawi akufuna report ya chilima
@Fanzo-h2l
@Fanzo-h2l 2 ай бұрын
Anthu Inu amene mukusapota Malawi chikangawa party MCP mukhaula komanso awuzeni achitsiru anuwo atulutse report la chilima munya gede 2025
@thomasky2084
@thomasky2084 2 ай бұрын
Chairperson of convesion is also contesting as a vp. Is it going to be fair?
@VeraVermaak
@VeraVermaak 2 ай бұрын
Koma APM akalimba osagona ngati mzawo wa aMCP kkkll😂😂😂 Dpp
@PulayaKalaka
@PulayaKalaka 2 ай бұрын
Kupha albino Peter muthalika a Galu inu
@EmmanuelMoyo-hy5ni
@EmmanuelMoyo-hy5ni 2 ай бұрын
Ife tikufuna kumva zomwe akuyankhula zo,,beat ikumveka pansi ikusokoneza..
@PiliraniDanielDaniel
@PiliraniDanielDaniel 2 ай бұрын
Mukunama inu anthu atsankho simudzawinaso
@OscarKathumba
@OscarKathumba 2 ай бұрын
Kkkkkk sangawine anthu adatinzunza kwambir agulu amenewa
@JustinLipipa
@JustinLipipa 2 ай бұрын
Kkkkk a Congress inu simukumvetsetsa pati? Anthu ngati mwakhapana nokhanokha ku Convention nde muziti mcp ndiyabwino? ​@@OscarKathumba
@MarthaBango
@MarthaBango 2 ай бұрын
Takwera yanuyi chikangawa ai
@NchebeMilliyano
@NchebeMilliyano 2 ай бұрын
MCP mbolo yanu watsankho ndi chikangawa chija
@VeraVermaak
@VeraVermaak 2 ай бұрын
Let's wait and see
@JoshuaNyirongo
@JoshuaNyirongo 2 ай бұрын
Vilombo vayamba kale kuonda
@MuhammadBAKILI-kl2mj
@MuhammadBAKILI-kl2mj 2 ай бұрын
Ku ZBS kuli atolokhani kopusa komanso antopola
@EdwirnMatewele
@EdwirnMatewele 2 ай бұрын
Galu kwabasi miseu ndi ya muthalika bwanji osakapanga masakho anuwo bwanji miseu ndi ya malawi kutsogozedwa ndi DR chakwela osaba kkkkkk muthalikayo
@TamUs-u2h
@TamUs-u2h 2 ай бұрын
Kkkkk ma cadets akuiwopa MCP
@PreciousBandah-l2r
@PreciousBandah-l2r 2 ай бұрын
Kkk mcp ilowanso osaopa
@MaritaBanda-p4z
@MaritaBanda-p4z 2 ай бұрын
mcp yake iti yolowa boma chifukw cha zipani zina ndiy zipan zomwe zinakuthandizan kut mulowe boma zakuthawan ndiy muyaluka
@edsonnyasulu5394
@edsonnyasulu5394 2 ай бұрын
Ndalama a dpp anaba kale zokwanila
@NchebeMilliyano
@NchebeMilliyano 2 ай бұрын
Ndiye tidat kuti atsogoleriwo achinyamatawa adzipha chilima? Mr chikangawa wadya manyi kapena chani Galu iwe
@RaphiqueYusuf
@RaphiqueYusuf 2 ай бұрын
Bambo Chaponda mwakula tasiyilani achinyamata ayendetse ntchiyi,kodi inu akulu akulu -akulunu simungapume kwasiyila achinyamatawa kodi ophunzira ndinu nokha nzikomuno?
@AlexMphalasa
@AlexMphalasa 2 ай бұрын
Dpp motoooooo😂😂❤
@PreciousBandah-l2r
@PreciousBandah-l2r 2 ай бұрын
Kwanu2 not kumalaw kuno
@JoshTech-h4r
@JoshTech-h4r 2 ай бұрын
😂😂😂 aah ​@@PreciousBandah-l2r
@henryhenry6632
@henryhenry6632 2 ай бұрын
FRELIMO, albino run for your life 😅
@gladwellnyirenda-u9s
@gladwellnyirenda-u9s 2 ай бұрын
be organized enough otherwise you remain in exile
@OscarKathumba
@OscarKathumba 2 ай бұрын
Munadakali ku opposition mpaka 2030
@chikuchimbatata3169
@chikuchimbatata3169 2 ай бұрын
mesa munamuthamangitsa munthu yemwe amafuna kupikisana nawo... komatu DPP mmatitola amalawi zowona lero mukatiuze kuti thawi yanu zinthu sizimakwera komaso inu simumaba aaah
@JosephNambazo
@JosephNambazo 2 ай бұрын
Boma lililonse anthu amaphedwa momvesa chisoni kwambiri koma ili lanyanya kwambiri Kodi anthu simukuo a nokha ozawina 2025 akudziwa ndi Mulungu yekha basi
@Littlefair7
@Littlefair7 2 ай бұрын
Atolankhani aku malawi ndi mbola zokha zokha, amafunsa mafunso ngati akupanga malumbilo a ubatizo. Ndinaonera atolankhani atamupanikiza president ku Kenya kumufunsa mafunso okhwima osati izi, za ziiii. Mafunso opusa ngati awa even mwana wa kindergarten akhoza kuyankha.
@Chancykwalingana
@Chancykwalingana 2 ай бұрын
atopa kale campaign asanayambe kma magogo party 😂😂😂😂😀😀😀😀😀😀
@edsonnyasulu5394
@edsonnyasulu5394 2 ай бұрын
Anthu a nzeru onse mwawathamangisa kale asalako ndi anthu A dyela
@PaulineSakala-q8z
@PaulineSakala-q8z 2 ай бұрын
Mmmmmm zina ndizabodza chilungamo ndichofunika
@CosmasChikwindi
@CosmasChikwindi 2 ай бұрын
Muthalika alibe nsewu miseu ndiya Amalawi ndalama za Amalawi.... Anthu akubainu.
@VeronicaChirwa-ct4os
@VeronicaChirwa-ct4os 2 ай бұрын
Amafuna azingotinamiza ngati sitikudziwa kanthu
@HumphreyWillima
@HumphreyWillima 2 ай бұрын
Padzana mudaononga ndinu... apa tikuona zotsatira zakuonongako... Zimene awononga a Tonse zidzaoneka akadzachoka .. ngati angachoke.
@edsonnyasulu5394
@edsonnyasulu5394 2 ай бұрын
Koma anthu ena alibe nzeru zoona munganene kuti Peter athandiza dziko pomwe analephela kale komaso mukufuna azafere pa mupando ngati ku malawi kulibe anthu A nzeru zachamba basi
@KondwaniGumba
@KondwaniGumba 2 ай бұрын
Muuponda ife agogowo ndi anu ife ai, .
@MrAhmidu
@MrAhmidu 2 ай бұрын
So you mean that when in government you have corrupt ways to raise funds and since you are in opposition and those means aren't there, you decided to just do with the non-lucrative means you have? Iyayi, tamva nawo.
@dumbokadaluka5759
@dumbokadaluka5759 2 ай бұрын
I felt that was stupidest answer as a response to a qn
@yasitafuphiri-nw2he
@yasitafuphiri-nw2he 2 ай бұрын
Budget yonse ikalowa zingati ,yankhani funso osadzilumaluma lilime apo
@GanduBondu
@GanduBondu 2 ай бұрын
Guys trying to put youth to be reader please people is tried where is young youth of Malawi to give power 😢guys one day we gonna done with government like Kenya Nigeria bec kind of reader who done long Malawi future we can't allow them to take advantage with our country no to them same people who kill our Malawi bt we still gives long time dream no matter what let's say no this people again again take Malawi give power to our young youth team to build Malawi
@DoYouKnow3838
@DoYouKnow3838 2 ай бұрын
English yabwanji iyi 👆😂😂😂❓❓❓
@PiliraniDanielDaniel
@PiliraniDanielDaniel 2 ай бұрын
Sitikufuna mgogo ife kulamulilaso Malawi
@MaritaBanda-p4z
@MaritaBanda-p4z 2 ай бұрын
choka malawi muno ifes sitikufuna kulamulilidwa ndi chakwera
@charleskayamba-s7c
@charleskayamba-s7c 2 ай бұрын
kodi inu nkhalambaiyi yuti chani taniuzn gays
@JamesSaidi-rw6ek
@JamesSaidi-rw6ek 2 ай бұрын
Dziko lawonongeka ndi chikangawa party
@PeterRabson-z3w
@PeterRabson-z3w 2 ай бұрын
Mbambande namalomba APM woyeeee
@VeraVermaak
@VeraVermaak 2 ай бұрын
First president of Dpp wos Dr Bingu wamutharika and second president of Dpp Professor Peter mutharika it's family property not National zawo zakubanja
@MarthaBango
@MarthaBango 2 ай бұрын
Inde asiyeni azanu Chala cha mulungu chinaloza iwe,chakwera inuyo ndi akubanja kwanu anthu akuvoteleni
@PatrickMangochi
@PatrickMangochi 2 ай бұрын
Madala team😂😂😂 Koma anthu mulibe manyazi,a Chaponda akulephera kuyankhula apa chifukwa cha ukalamba
@charleskayamba-s7c
@charleskayamba-s7c 2 ай бұрын
palibe uwina ninkhalamba yakoyo
@EliSMpuka
@EliSMpuka 2 ай бұрын
Komatu Zinazi asiyileni achinyamata
@JoelKacheche-x6i
@JoelKacheche-x6i 2 ай бұрын
MCP Yatengaso boma mosa Kanyika,Dpp yasogoza okalamba,chibwana chachikuru ku voteraso peter mutarika azizango gona mbava zikutenga misonkho ya A malawi.
@JamesSaidi-rw6ek
@JamesSaidi-rw6ek 2 ай бұрын
Ife tikwera dpp mcp ikagwere
@ChifundoZimba-jh7dh
@ChifundoZimba-jh7dh 2 ай бұрын
Namalomba kape
@yasitafuphiri-nw2he
@yasitafuphiri-nw2he 2 ай бұрын
Chaponda mweya unatha 😢
@hassammaulana4529
@hassammaulana4529 2 ай бұрын
Ai koma sindlama zake koma za amalawi osati zakuyumba kwake
@PulayaKalaka
@PulayaKalaka 2 ай бұрын
Ndi mbuzi izi inu
@yasitafuphiri-nw2he
@yasitafuphiri-nw2he 2 ай бұрын
Chaponda vomerani mwakula zitayeni zandale kazidyani pension 😂
@RobertCosmas-bo1uo
@RobertCosmas-bo1uo 2 ай бұрын
Greedy ndimpando waupule zaka 90
@amosnyirenda-pl1ss
@amosnyirenda-pl1ss 2 ай бұрын
zisili za dpp chidala icho si tikuchifuna ziko chinaononga kale
@MjombaMjuba
@MjombaMjuba 2 ай бұрын
We don't want Chaponda tikumudziwa kale ndi mbabva imeneyi, tsinzina mtole
@donmoyo5592
@donmoyo5592 2 ай бұрын
Komatu zolinga zowaitanila azipani zina sizinanenedwe
@anthonynkhoma4265
@anthonynkhoma4265 2 ай бұрын
Kodi George Chaponda mchimangayu mwamutenga ku museum?
@LawrenSonga
@LawrenSonga 2 ай бұрын
Zinakuvutani kare inu mthawi yanu inamtha basi
@EllemiaChaduka
@EllemiaChaduka 2 ай бұрын
Mwabwita kale inu a Dpp convention ya chipani chanu mukathana a zipani zina kkkkkk anamalomba kanganizani popanga zinthu
@TamUs-u2h
@TamUs-u2h 2 ай бұрын
Namalomba kuchikamwa
@MaritaBanda-p4z
@MaritaBanda-p4z 2 ай бұрын
iwey ndiye uli ndikuchani
@anthonynkhoma4265
@anthonynkhoma4265 2 ай бұрын
Anthu womwe ankafuna kupikisana ndi agogo ndi womwe munawathamangitsa aja. Za misewu musatinamize. Iwo aja anangokumba pa area 18 round about paja basi. Ma 6 lane roads musatinamize. Mufuna kunamiza anthu. Komanso za agogonndi mombera University yomwe aphunzitsi ake ndi achina Dan lu. Kkkkkk cementgate simukutchula bwanji?
@JuvenileDebwe-bv8ow
@JuvenileDebwe-bv8ow 2 ай бұрын
Atsogoleri osaba Kodi?
@NancyNyirenda-v9o
@NancyNyirenda-v9o 2 ай бұрын
Inu munali muboma momo bwanji osakoza zinthu or ndimanyazi omwe mulibe tuuuu 😅😅😅😅😅😅
@VeronicaChirwa-ct4os
@VeronicaChirwa-ct4os 2 ай бұрын
Ndipo inu a ndale wa mmmmmm mabodza basi
@yotamumahomed1313
@yotamumahomed1313 2 ай бұрын
Palibe ukudziwa nde plz 😊
@elizasingano
@elizasingano 2 ай бұрын
Iweyo nthaw ya Dpp suger unagulapo 4000
@NancyNyirenda-v9o
@NancyNyirenda-v9o 2 ай бұрын
@@elizasingano iweyo ukuwona or gogo wakoyo abwerere ukuwona ngati zinthu zizabwelelaso kumbuyo khulupililani chabe kuti ndinthawi zakumapeto ubwino wake mu bible zinalembedwa zamasiko omalidza ndipo tikudziwona chikondi chidzasowa pakati pathu si izi mukungotukwana daily koma osapindula nazo
@JonathanBwezi
@JonathanBwezi 2 ай бұрын
😅😅
@RobertKaiteni
@RobertKaiteni 2 ай бұрын
Ngt mudakanik kukoza zithu mulimbima pano ndiye mungaokoz?
@AchalumeKunsanama
@AchalumeKunsanama 2 ай бұрын
UDf wooooyeeeee
@JimmyMpinda
@JimmyMpinda 2 ай бұрын
Inu a mcp mwapangapo chani mukuzicha achinyamata kuba komweko ndikupha chilima ndicho chanyaudira zisiru inu
@MchachaGoodson
@MchachaGoodson 2 ай бұрын
Atsogoleli wabwino Boma losapa osati minzukwa ilipoyi
@isaihmagani5697
@isaihmagani5697 2 ай бұрын
Chaponda akulephera kuyankha mafunso
@VeronicaChirwa-ct4os
@VeronicaChirwa-ct4os 2 ай бұрын
Anthuwa akalamba inu kulephera kuyankha mafunso moyenerako ndikukalamba. Dzikoli likufunika anthu a nzeru za tsopano koma anyamata. Amene akutha kuyenda ndi dziko osati nkhalambazi ayi.
@MuhammadBAKILI-kl2mj
@MuhammadBAKILI-kl2mj 2 ай бұрын
Chimanga chikugulidwa 45pin not 35pin
@WachiyawoWangalusa
@WachiyawoWangalusa 2 ай бұрын
Chikangawa.sangawine.ndiwakupha.
@EagerChicken-qj6xu
@EagerChicken-qj6xu 2 ай бұрын
Izi ndizopandanso demokarase ndi chimodzi modzi nthawi yakamuzu,
@WinerdShadreck
@WinerdShadreck 2 ай бұрын
Muzingoika nyimbozo
@WachiyawoWangalusa
@WachiyawoWangalusa 2 ай бұрын
Imfa.yachilima.ndiimene.imugwese.chakwela.
@ChrisyMbewe
@ChrisyMbewe 2 ай бұрын
DPP..yomweyo
@johnkambala692
@johnkambala692 2 ай бұрын
Bodza lankhkhuniza. Muona the next five years.
@CosmasChikwindi
@CosmasChikwindi 2 ай бұрын
PDP woooooooyeeee❤❤❤❤
@EllahChikwatu
@EllahChikwatu 2 ай бұрын
Kkkkkkkkkk kom ndaseka
@FunnyKalimwayi
@FunnyKalimwayi 2 ай бұрын
chikangawa sawina
@RafnikMaida
@RafnikMaida 2 ай бұрын
❤😮😅
@JACKSONHULUWA-j2n
@JACKSONHULUWA-j2n 2 ай бұрын
Opposition woyee, mcp ichoke basi
@MjombaMjuba
@MjombaMjuba 2 ай бұрын
Munya muwona, mudzakomoka, dikilani
@WachiyawoWangalusa
@WachiyawoWangalusa 2 ай бұрын
Chakwela.sakumuziwa.mmalawi
@BlessingsSimbi-s2d
@BlessingsSimbi-s2d 2 ай бұрын
Dpp my vote tikuchedwa kovota adadi omwewo🎉
@DanielPeterson-k5o
@DanielPeterson-k5o 2 ай бұрын
Sindingabetse vote yanga ine kupatsanso peter bola akanayimira wina koma chakwera ndi peter dzikalima adyera nonkhanonkha
@MLWPhiri
@MLWPhiri 2 ай бұрын
Nde voti yako ife tisegule nayo mmimba kagwele uko
@DanielPeterson-k5o
@DanielPeterson-k5o 2 ай бұрын
@@MLWPhiri khalambanso la lero? Shame on you bro look at chaponda kkkkk koma guys ndizoona tikufuna kusitha koma team yankhalamayi ikagwere
@MLWPhiri
@MLWPhiri 2 ай бұрын
@@DanielPeterson-k5o shame on you too by the way am not your bro mwina iweyo umatamba nkuona chilichonse chili bwino bwino kma ukanakhala wanzelu sukanatengela Za kukula Kwa Munthu kma kuganizila amalawi
@DanielPeterson-k5o
@DanielPeterson-k5o 2 ай бұрын
@@MLWPhiri iwe chisankho changa sichako panga chisankho chako but for me l will follow my heart ndipo sindingavotere peter ineyo anthu ambiri apanga macomment why target yako ilipaine?Peter akanapatsa wina ku ddp ndikanawapatsa vote yanga chifukwa l need charge koma peter himself bolanso chakwera emweyu
@MLWPhiri
@MLWPhiri 2 ай бұрын
@@DanielPeterson-k5o khala nayo vote yakoyo ngat ukuziwa Kut siwe sapota wa APM ukanangodusa osapanga comment yako yofoirayo
@ChifundoZimba-jh7dh
@ChifundoZimba-jh7dh 2 ай бұрын
wadya chamba namalomba
@MjombaMjuba
@MjombaMjuba 2 ай бұрын
Chaponda, kkkk talking about transparent, wonders shall never end in Malawi. What about maize gate? Mbabva zikulu zikulu za chi Llomwe.
@CosmasChikwindi
@CosmasChikwindi 2 ай бұрын
Mukufuna nkhalambayo cholinga muzizaba iye akugona😂😂
@NancyNyirenda-v9o
@NancyNyirenda-v9o 2 ай бұрын
😅😅😅😅😅
@MarcosDjussa
@MarcosDjussa 2 ай бұрын
Iwe chakweo sakuba??
@WinerdShadreck
@WinerdShadreck 2 ай бұрын
Zako zimenezo
@VeronicaChirwa-ct4os
@VeronicaChirwa-ct4os 2 ай бұрын
Mau akufuna azidzalamulira iwo osati Peter Muthalika. Dzikoli likufunika munthu wa changamu.
@georgechinangwa3454
@georgechinangwa3454 2 ай бұрын
Akufuna azimubela bwino awa
@ConfusedCheetah-ok9ui
@ConfusedCheetah-ok9ui 2 ай бұрын
Kodi a chaponda, mkamwamo mwaikamo phalala la mtandasya Komanso mukudikira boma lilakwitse ndiye ikhale kampeni yanu Nanga boma likanakhala kuti sirikulakwitsa zinthu zawo inu kampeni yanu bwezi mukuti bwanji.... AAA munachotsa munthu ofunikira nonse mwatsala kumeneko ndiinu odambana mkamwa.....
@adamashrafi5875
@adamashrafi5875 2 ай бұрын
😂😂
@chesterphiri7523
@chesterphiri7523 2 ай бұрын
Ayi Peter Mutharika anamuwopa Nankhumwa not that people
НИКИТА ПОДСТАВИЛ ДЖОНИ 😡
01:00
HOOOTDOGS
Рет қаралды 2,9 МЛН
버블티로 부자 구별하는법4
00:11
진영민yeongmin
Рет қаралды 25 МЛН
Wait for the last one 🤣🤣 #shorts #minecraft
00:28
Cosmo Guy
Рет қаралды 13 МЛН
WATCH | Floyd Shivambu dumps EFF for MK Party
2:44
News24
Рет қаралды 378 М.
НИКИТА ПОДСТАВИЛ ДЖОНИ 😡
01:00
HOOOTDOGS
Рет қаралды 2,9 МЛН