JESSIE KABWIRA WAYANKHURA PANSOKHANO LERO KUTI NGAKHALE KAMBA ATADIKURA DPP SIMUZALAWANSO BOMA

  Рет қаралды 28,047

Makosana

Makosana

Күн бұрын

Пікірлер: 415
@MedarMw
@MedarMw 26 күн бұрын
Dpp my vote
@AvideOfficial
@AvideOfficial 26 күн бұрын
Tikuferanji nde yalowa mu mcp😂😂😂😂 nde muona kuti mutani!! Inetu chomwe ndikuona apa ndisewero basi😢😢😢
@eliffagondewe8214
@eliffagondewe8214 26 күн бұрын
Wina akukana kwera njinga, wina kukadya msima ku restaurant koma tiona zinthu..
@SamboRuphan
@SamboRuphan 26 күн бұрын
Amayi mukutaya nthawi 😂😂😂DPP boma
@user-tk6wf2eg4z
@user-tk6wf2eg4z 26 күн бұрын
Dikilani muzaone action kt malawi ndiotani
@FranciscoEduwado
@FranciscoEduwado 26 күн бұрын
A MCP mukuthela kuchikangawanso mukuwona ngati tikunva kukoma ndi chilima😢😢😢😢😢
@IvyMkhura
@IvyMkhura 26 күн бұрын
Ikakwana 2025 uiona MCP kumene itakathere, mutha ngati makatani
@wisdom20mkango49
@wisdom20mkango49 26 күн бұрын
😂😂😂😂😂 iwe aise forget dpp will never win...all of u mukuti iwina you will not even vote
@STEVENMPONDA-o6r
@STEVENMPONDA-o6r 26 күн бұрын
Mpoo lived
@ShabaniKuswere
@ShabaniKuswere 26 күн бұрын
Simunati mulira kuteroku mukuona Ngati onsewa abwerera Kuti akudzapanga support MCP?😂😂😂 DPP 2025 Boma ndipo mukolopa nyanja sikutalitu nthawi mkachitsiru,inu mukati mzanuyi sakavota mumupha Kuti asakavote? Pajatu mumatchuka ndikupha, kumeneko mwapitako musaiwale Kuti munawaphera Sidik miya​@@wisdom20mkango49
@ShabaniKuswere
@ShabaniKuswere 26 күн бұрын
Simunati mulira kuteroku mukuona Ngati onsewa abwerera Kuti akudzapanga support MCP?😂😂😂 DPP 2025 Boma ndipo mukolopa nyanja sikutalitu nthawi mkachitsiru,inu mukati mzanuyi sakavota mumupha Kuti asakavote? Pajatu mumatchuka ndikupha, kumeneko mwapitako musaiwale Kuti munawaphera Sidik miya​@@wisdom20mkango49
@JohnsonMaulana
@JohnsonMaulana 26 күн бұрын
​@@wisdom20mkango49 akulu mwamwa ambuye mtengen et Mpaka kuchemelera chikangawa 😂
@ShillaShamil-v2y
@ShillaShamil-v2y 26 күн бұрын
DPP Boma
@Marymahendra
@Marymahendra 26 күн бұрын
She doesn’t know what she’s doing
@RelaxCool-dp9jn
@RelaxCool-dp9jn 26 күн бұрын
Yes
@KennedyPaipi
@KennedyPaipi 26 күн бұрын
Ovota ndife mai ndipo umphawi tikuona ndifeyo iweyo ngati ukudya bwino zako zimenezo
@RelaxCool-dp9jn
@RelaxCool-dp9jn 26 күн бұрын
Awuze
@ElizabethMulinde
@ElizabethMulinde 26 күн бұрын
Anthu akupha inu mutibwexele kaye chilima ndi 8 others
@RiteRoderick
@RiteRoderick 26 күн бұрын
DPP ndimakina ndipo ifeyo tikuivotera zedi, mukhaula agaru a MCP inu. Kwanu kwatha
@PatrickMtira
@PatrickMtira 26 күн бұрын
Mtsongoleli wanu wasanduka chidore Cha azungu 😢 amupatsa njinga kuti adziseweletsa
@EllahChikwatu
@EllahChikwatu 26 күн бұрын
Kkkkkkkkk kom sambi
@FrancisDay-br7xb
@FrancisDay-br7xb 26 күн бұрын
​@@EllahChikwatu onelerani chakwera galu ukwera njinga pakati pazungu chidole
@user-ww9rj2wx8d
@user-ww9rj2wx8d 26 күн бұрын
😅😅😅😅😅 chakwela ndi chisilu
@RuthBandula
@RuthBandula 26 күн бұрын
Kkkkkk eyadi Mr Aviator akweladi njinga kkk azungu akujambula
@BrightZionga
@BrightZionga 25 күн бұрын
Kkkkkk akumuphunzitsa kukwela njinga
@ElizabethMulinde
@ElizabethMulinde 26 күн бұрын
Ubwino wake ovota ndifeyo zowinazo Nde musazipusitse ife achewa aku Lilongwe nchezi sitikukufunan
@RiteRoderick
@RiteRoderick 26 күн бұрын
Thanks boss mumatha zedi, anthu okupha awaaa agaru achabechabe atidzuza koopsa mmmmm
@kingsleyChisenga-i8g
@kingsleyChisenga-i8g 26 күн бұрын
Maganizo saletsana mungodziwa kt siose alimbaliyanuyo
@AgnesMatola
@AgnesMatola 26 күн бұрын
Kodi akuyanjhulawo ndi a Bambo😂
@blandinabonaventure
@blandinabonaventure 25 күн бұрын
Mayi osaganiza bwino awa zizawapha ndale
@Blessings-b7h
@Blessings-b7h 26 күн бұрын
Kkkkkk uku kunali kulankhula kwa anamalira kulira udindo omwe ukupita ku dpp iwe yankhula zoti ndalama zako zilowe mthumba mwako.
@apostledavismsosa
@apostledavismsosa 26 күн бұрын
Kkkkk munthubkamafa amaitanisa botolo la fanta akuziwa kuti samwa akufa
@user-wl4nd7ic1s
@user-wl4nd7ic1s 26 күн бұрын
Mai uyuu ndichisiluuu
@WistarChauya
@WistarChauya 26 күн бұрын
DPP my vote
@GiftBonomali
@GiftBonomali 26 күн бұрын
APM my vote
@STEVENSOKO-kq2kx
@STEVENSOKO-kq2kx 26 күн бұрын
APM 2025 boma💥 mukuxinamixa
@JonesChingaya-yf4gg
@JonesChingaya-yf4gg 26 күн бұрын
Chilima ndiamene anakuikani M'boma, mzimu wa Chilima yemweyo ukuchosani m'boma.
@mollymasangano473
@mollymasangano473 21 күн бұрын
The words without aparch ❤🎉❤
@beinhardkausiwa7107
@beinhardkausiwa7107 26 күн бұрын
A....P....M my vote!!!!
@FletcherGuzani
@FletcherGuzani 26 күн бұрын
Koma a Jesse kabwila ngati kuli kulodzedwa mudzathawa pakhomo panu pomwe nthawi ikufika
@SimenyeSimkondachirwa
@SimenyeSimkondachirwa 26 күн бұрын
Usavutike muziyi mau ako athera pachabe dpp my vote
@AdamAhamad-k2i
@AdamAhamad-k2i 26 күн бұрын
Anthu akuchikwawa ndizitsiru MCP inakuphelani sadick miya lero mukuwawombera m'manja
@DIMZYRECORDS
@DIMZYRECORDS 26 күн бұрын
Ndpo even one useless of mcp anabwera kumaliro azathu Mia chikwawa pple are stupid
@eliffagondewe8214
@eliffagondewe8214 26 күн бұрын
Mposo inu
@graceeneya9893
@graceeneya9893 26 күн бұрын
Muchedwatu a Jessy kabwira, nthawi nkachitsiru
@EstherZintambira-sq3yy
@EstherZintambira-sq3yy 26 күн бұрын
Mai osowa zocita
@BalipoChilongo
@BalipoChilongo 26 күн бұрын
Chikangawa party
@IshmaelZakazaka
@IshmaelZakazaka 26 күн бұрын
Kumangotaya nthawi Dpp boma😂😂😂😂😂
@mayesojameskatete
@mayesojameskatete 26 күн бұрын
APM uja osazaphwekesa
@CassimMbalaka
@CassimMbalaka 26 күн бұрын
Palibe angavotere chikangawa zaziiiii athu woyipa munampha chilima
@JOHNSANGWALI-r6x
@JOHNSANGWALI-r6x 26 күн бұрын
Maiii ameneyuu amulozaaa komaso zikumveka ngatii there's no mchere
@apostledavismsosa
@apostledavismsosa 26 күн бұрын
Chikangawa party muno ayi takana
@EllenChimera
@EllenChimera 26 күн бұрын
Amayi kanyereni Kaye zomwe muyankhurazo zilibe mutu😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂
@FebbyPhiri-n7j
@FebbyPhiri-n7j 26 күн бұрын
Ndichifukwa munapha Biyeni ndiolotse mpaka kupha munthu😭😭😭😭
@JohnsonMaulana
@JohnsonMaulana 26 күн бұрын
Ngankhale Sadik Mia anamuphanso anthu awa osawapasa mpata atimaliza😢
@MeniyaMikaya
@MeniyaMikaya 25 күн бұрын
🎉🎉🎉🎉🎉🎉🎉🎉❤❤❤ APM akalamulila kundata 2030 woooooo ndipo a DPP munyela
@PatriciaAlomwe-oz8wc
@PatriciaAlomwe-oz8wc 25 күн бұрын
Mulimbana ndi omwe nkhondo semenya okha omenya nkhondo sangonjedwepo APM my vote
@JohnsonMaulana
@JohnsonMaulana 26 күн бұрын
Mukunamatu ife sitikukufunan muzipakila nd chikangawa wanuyo😅
@LuwisKaigwaze-gr6cg
@LuwisKaigwaze-gr6cg 26 күн бұрын
Aaaah nde mukuona ngati mukagaea zinthu zanuzi tivotera inu zamanyi
@isaaczuze
@isaaczuze 24 күн бұрын
My vote is for Apm in any way.....mcp the party of darkness
@RichardKuden
@RichardKuden 26 күн бұрын
Chakwela my vote 😂😂😂
@augustMag
@augustMag 26 күн бұрын
Musegula naye mmimba APM 2025 Booooomaaaa ❤❤❤❤❤
@tasmania527
@tasmania527 26 күн бұрын
APM ngoluzaluza iwe khala chete
@augustMag
@augustMag 26 күн бұрын
@@tasmania527 Sindikhala chete mpaka anthu a MCP Bpp yanu itakwera mu 2025 Chifukwa Cha kuluza kumene muluze Our APM akunyada ulendo okalowa ku state house kuziona inuyo muzizinamiza kuti mupitirira kulamulla mpaka 2030 Mulungu wake utiyo kuti akatitaye mkumangomphulabe njerwa Zamoto? Siwa Abraham ayi
@tasmania527
@tasmania527 26 күн бұрын
@augustMag Kkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkk. If wishes were horses, beggers would ride. Do you think pamene munampinda JB in 2014 then zikhalaso choncho ndi Dr. Laz? Mwauponda.
@Alexkalonga-t9s
@Alexkalonga-t9s 26 күн бұрын
Uzilakhula zoti akutame km amalawi apanga chiganizo mbuzi iwe
@JulietKapata
@JulietKapata 24 күн бұрын
Dpp boma ❤❤❤
@JoyceShaibb
@JoyceShaibb 26 күн бұрын
Pitani mudzikapakila inu akabwira musachedwe mkulongolola hiiiimmyaaaa
@RahimLuemba
@RahimLuemba 26 күн бұрын
Mai onyasa mau ngat amneyu,
@emmanueljelemani4203
@emmanueljelemani4203 26 күн бұрын
Kicks of a dying hose....
@JohnmarkNazombe-hi9xd
@JohnmarkNazombe-hi9xd 25 күн бұрын
This is nonsense mama!!!!!
@PrinceBlessings-bv5bs
@PrinceBlessings-bv5bs 26 күн бұрын
So bad party... Tinkangova mbiri koma mmmm . Akoma akagonera ndithu 😂😂
@PollyLysonLutepo
@PollyLysonLutepo 26 күн бұрын
Nyimbo yimeneyo ndagwilizana nanu. Chakachinotu mcp siyonyengelera apha aliyense odzudzula chakwera ndi mcp. Kuyamba m'nayamba kale. Kwatsala kutsiliza.
@DominicNantowa-t4d
@DominicNantowa-t4d 26 күн бұрын
Kukwela ndege ulendo wakunja kumakakwela njinga yakapalasa 😢😢😢nsonkho wanga I eee!!!
@anthonysawa2039
@anthonysawa2039 26 күн бұрын
Bundle yanga ine mayooo!
@HevenChiwaya
@HevenChiwaya 25 күн бұрын
Ukulila ndi mtima iwe zimenezo ngati ukufuna kusangalasa a president Malo mowauza chilungamo momwe dziko likuyendela
@YoweliChipapaChipapa
@YoweliChipapaChipapa 26 күн бұрын
Akabwila mulimba pá 50+1 Mulimba 2025
@John-qm8qx
@John-qm8qx 25 күн бұрын
DPP❤
@jamesgama5489
@jamesgama5489 26 күн бұрын
Ayi wayiyamba bwino office, kamba akamayika machine kumalo sayang'ana koma akafuna kuswa ana inuuu.
@JackMvura-ik2td
@JackMvura-ik2td 24 күн бұрын
A DPP Moyo kuwawa vuto DPP kupha malubino kwambili chimenecho sidzalowanso boma
@MosesTangwe
@MosesTangwe 21 күн бұрын
Akanadziwa chikuwavuta ndiya DPP sangazavotere agalu inu
@DavieKumbanga
@DavieKumbanga 26 күн бұрын
😂😂😂😂😂😂😂😂 Akabwila ndimakukondani koma na MCP yanui ndi mbola Tatulutsani report la SKC plz anuzo ai
@MussaLenard-k4l
@MussaLenard-k4l 26 күн бұрын
😂😂😂😂 kulankhula kozililirauku....APM my vote
@JohnTimbenao
@JohnTimbenao 26 күн бұрын
M'malo moti munene zomwe mukufuna kuwachitira anthu koma kulimbana ndi DPP basi. Mukusowa chowanamiza anthu. Nanga sikwacha. Paja ukanama sikuchedwa kuchatu.
@user-ww9rj2wx8d
@user-ww9rj2wx8d 26 күн бұрын
Chisilu iwe Peter sadaphe munthu ali ndi mtendele ogona chakwela amangowosa chilima plus anthu 8
@MisheckAselo
@MisheckAselo 26 күн бұрын
Kkkk apule ali ku Germany kukakwakwera njinga😂😂😂
@BLESSINGSSTOLO-lt9di
@BLESSINGSSTOLO-lt9di 26 күн бұрын
Nzimai amenei ndichisilu zed ndipo M'mutu mwake simukugwira aii , imanei l think wapenga.
@GospelSoldiers-sr7np
@GospelSoldiers-sr7np 22 күн бұрын
Zikuchita kuwonesa kuti DPP mukumva nayo kutentha kkkkkk mukulephera kugona 😅😅😅
@StarchJonas
@StarchJonas 23 күн бұрын
Ambwiyako akuseweretsa njinga ku Germany ati kopempha koma awapatsako njinga kuti azikwera kkkkkk
@MussahBamusi
@MussahBamusi 26 күн бұрын
Kabwira azikamba zamcp nanyongo yake asakambe zadpp
@AnnaPhiri-b8t
@AnnaPhiri-b8t 26 күн бұрын
Ahule awa
@AgnessJonas-zt9wp
@AgnessJonas-zt9wp 26 күн бұрын
Vote ndimutima omwe alipompowo enaso ndi azipani zina angofuna kudya nawo,nthawi yodyeka ndino
@lawrencemsopa9769
@lawrencemsopa9769 24 күн бұрын
Vote yanga DPP yatengakale kkkkkkk mwachedwa
@BillyChunga
@BillyChunga 26 күн бұрын
Mcp yalulani kwanu kwatha simungawine ovota ndifeyo
@MajiduMakiyi
@MajiduMakiyi 26 күн бұрын
Angabwele ndani kwa Inu akupha
@rahimmand4130
@rahimmand4130 26 күн бұрын
Kodi Jessie iwe mcp inayamba yawina zisankho ? Kuyankhula kopanda nzeru uku
@Mainje-jr4pl
@Mainje-jr4pl 21 күн бұрын
Mahule amaterotu..lero atukwane chakwera, mawa akutamanda laz
@aubreymaonga4266
@aubreymaonga4266 26 күн бұрын
Politics entertainment 😂
@ChristopherKazembe-c8t
@ChristopherKazembe-c8t 25 күн бұрын
Ukunamatu jessie kuli chikangawatu paja otsamaiwala
@user-zc1mg5lj7p
@user-zc1mg5lj7p 26 күн бұрын
Nyimbo mwaiyambayo simunyengerera muziona Hule wa chabe iwe uziona
@PreciousMauka
@PreciousMauka 25 күн бұрын
Time will tell
@MussaZakeyu
@MussaZakeyu 26 күн бұрын
😂😂😂😂 mantha amenewo musadadaule kulila kumeneko iweyo Jess chilungamo mukuchiziwa kt adadi akukugayani nose chagada 2025 A P M ikulowa boma
@SandrahPretty
@SandrahPretty 26 күн бұрын
Ambuye akathenii anthuwa
@blessingsnyalo-rp9ko
@blessingsnyalo-rp9ko 26 күн бұрын
Kulira kwanu amayi inu simulira bwino zizakubwereserani Mavuto ndithu
@LozaniSiginala-e8n
@LozaniSiginala-e8n 26 күн бұрын
Mmmmmmm zikuyakhulidwa apapa anthuwa a kuopa Peter basi malo motulusa fundo akulimbana ndi kuti Peter sanakhare nawo PA convention za ziiiiiiiii
@HendersonNambera
@HendersonNambera 26 күн бұрын
Ndy ona comment ngati pali mcp yakoy😂😂😂 APM my vote wamv galu iwe
@JoelMwenegamba
@JoelMwenegamba 26 күн бұрын
Koma anthu muwanamiza awo adya???????? God is watching you mana.
@Mustapher-fb4qp
@Mustapher-fb4qp 24 күн бұрын
Amarawi honani má komenti kuyambila muntunda kufukira komenti ❤dpp yawina di mavoti 95 MCP 5 dpp moto moto
@ChikumbutsoChomali
@ChikumbutsoChomali 26 күн бұрын
Inu musatinyanse apa mai munawina chifukwa cha chilima inu muyambe kutenga masaza anu muzipita mmakwanu ndi chakwera wanuyo Peter sanaluzepo dpp ndiyomwe imaziwa kutsogolela ndikudziwa kuchengeta wanthu sizanuzo mbalame za anthu
@shadreckjumah
@shadreckjumah 26 күн бұрын
Mayi mbuzi yamunthu uchisilu pa mwamba pa uchisilu
@DalitsoMatope
@DalitsoMatope 26 күн бұрын
Kodi ngati mulungu sakusangalala nawo utsogoleri wako mulungu amakutumizira matenda,cyclone ndi ifa njala chifukwa cha utsogoleri opusa nde zomwe zina bwera zinja ndi chifukwa choti mulungu sakusangalala ndi ufumu wanu
@GiftMathewe-fr3kn
@GiftMathewe-fr3kn 26 күн бұрын
Mukulankhur zaboza
@dagaphiri1867
@dagaphiri1867 26 күн бұрын
Ayi muwina nanga simunapha mumamuopa. Komabe mukutuluka basi. Anthu anabwera kudzaona anthu akupha.
@lawrencemsopa9769
@lawrencemsopa9769 24 күн бұрын
Kuli2 mavoti mcp musazinamize
@WisikiBlack-gj4gu
@WisikiBlack-gj4gu 26 күн бұрын
Kkkkkk muzanamiza athuwo mukupita inu, chimanga tilandila , tileni tizidya ifeyo, zachamba
@ClaudinaAugustoAugusto
@ClaudinaAugustoAugusto 25 күн бұрын
Mwakula mwatha muziona nthawi yatsala pang ono tikuonani mcp muchita manyazi
@ChisomoLester-h7x
@ChisomoLester-h7x 26 күн бұрын
Umakwana kabwila okunva wanva, kudziwa kutenga anthu opanga kampeni osati nkhalamba zija
@MikeChimpeni
@MikeChimpeni 25 күн бұрын
@JoaquimElidioChiwisse
@JoaquimElidioChiwisse 25 күн бұрын
Ngati kuli pavuto ndiye ndikulower shire ndiye ikuti chani galu iwe
@RahimLuemba
@RahimLuemba 26 күн бұрын
Aaaaa bola akanakhal chatsika , cyclone fled munabweretsa nokha agalu inu
@imranhopewell-yv4zc
@imranhopewell-yv4zc 26 күн бұрын
Iwe ukanakhala unabadwa mwa munthu sukanayankhula motelomu
@TamikaKaponya
@TamikaKaponya 26 күн бұрын
Ndipo kwambiri
@paulnyondo7572
@paulnyondo7572 26 күн бұрын
Koma vuto chipanichi ndichagazi chinatiphera chilima.njala ndiyosayamba anthu awa ndiaboza amalawi osawakhulupiliranso.mcp ndimagazi okhaokha.thumba lachimanga mpaka 50000 koma mcp chipani chosamvera chisoni amalawi .
@FelixTsabolaNamaya
@FelixTsabolaNamaya 26 күн бұрын
Mcp singawinenso, its time for DPP ikonze za vuto lomwe labwera chifukwa cha MCP
@GraceZumazuma
@GraceZumazuma 26 күн бұрын
Ofzavota ndi anthu amene akuona mavuto Dpp kaya ukukonda kabwira kaya ai koma sikulowaso m'boma akupha inu chilima anakuikani m'boma uja alikuti
@EmmaculateWasiya
@EmmaculateWasiya 26 күн бұрын
Koma jessey upite ku mental mwina misala yayamba kupatula iwe wekha koma amalawi onse DPP 2025 BOMA fertilizer ndi 120000 don't forget!!
@EdwardMatewelex
@EdwardMatewelex 26 күн бұрын
Simungawineso ayi , ine sindimavota kunena chilungamo .
@KennedyPaipi
@KennedyPaipi 26 күн бұрын
Palibe chomwe akunena awa
Пришёл к другу на ночёвку 😂
01:00
Cadrol&Fatich
Рет қаралды 9 МЛН
HON.DAUSI kufotokoza bwino mbiri ya KAMUZU BANDA pa @MibawaStudios
29:12
Mpungwe-Pungwe mw
Рет қаралды 18 М.
Chisomo Nyamalikiti Nthiwatiwa Mdala - Barabas
6:30
Joab Frank Chakhaza
Рет қаралды 46 М.
Пришёл к другу на ночёвку 😂
01:00
Cadrol&Fatich
Рет қаралды 9 МЛН