HOT CURRENT YA LERO NDIYOSAONA NKHOPE ANG'ALURA ALIYENSE MOSANYENGELERA KOMA AWAWA NDOLIMBA MTIMA

  Рет қаралды 34,324

Makosana

Makosana

Күн бұрын

Пікірлер: 96
@daviskamonde4882
@daviskamonde4882 Ай бұрын
This has been my best to listen to.
@BakhePaliso-h8h
@BakhePaliso-h8h Ай бұрын
Kwamene kumuzikwanu kulibe njala ayi avotelen achakwela koma mene ine kwathu anthu akuvutikila kut apeze chakudya sindingachite kumvotela amenewa mpaka mulungu atandilanga ndithu
@wellssimbili2750
@wellssimbili2750 Ай бұрын
Thank you guys I wish your rhetoric should reach the people in every corner of Malawi ,the electorate to be enlightened so as to vote wisely,Your discourse is really on point.Tapangani to mashot videos of your podcasts tapasile anthu kuwhatsapp.
@joegibsonzulu2599
@joegibsonzulu2599 Ай бұрын
Iyi program ndimayikonda kwambiri ndipo for me, sunday evening is never complete if I don't watch this informative program.Gentlemen pitirizani kutipatsira program yozamayi.
@DavidPhiri-o6w
@DavidPhiri-o6w Ай бұрын
Mwatokota zonse dzazeru, thanks so much wamakuto wava
@Haka-tb8ih
@Haka-tb8ih Ай бұрын
Komanso Mai Chilima apanga bwino kuyankhula, ayankhulira anamalira anzawo omwe alibe voice Ku dziko
@DigleDafter
@DigleDafter Ай бұрын
Maguys awa chilungamo alinacho ndipo tikanakhara ndi athu awa bwez mw 🇲🇼 aribwino ❤
@LoveNgona
@LoveNgona Ай бұрын
Ndpo zoona
@MaxwellChiwaya-i8q
@MaxwellChiwaya-i8q Ай бұрын
TV iyiyi ndi number 1 chifukwa sikamba zambali imodzi ndipo sikondera ngati kwina kuja big up maguyz
@TiongeChilongo-j4f
@TiongeChilongo-j4f Ай бұрын
MCP siidzasintha ataaaaa ndipo ipite sitikuyifunanso
@SedoMissi-m3c
@SedoMissi-m3c Ай бұрын
Radio iyi ndiyawanthudi ndiyaife a Malawi
@AbdullahAllie-k9l
@AbdullahAllie-k9l Ай бұрын
Kd Pali zogwetsa boma apa? Guys kd bwanji pazoona mumaikapo ndare adevu zamwai sakufuna upuretu ndipo satumidwa km zomawawa.
@geofreydzinyemba6107
@geofreydzinyemba6107 Ай бұрын
Kukamba kosayang'ana mbali keep it up
@MaxwellChiwaya-i8q
@MaxwellChiwaya-i8q Ай бұрын
This is the only tv we love most
@MuhammadSamson-yz1kl
@MuhammadSamson-yz1kl Ай бұрын
Congratulations anyamata
@TonyMzindiko
@TonyMzindiko Ай бұрын
guys keep it up program imeneyi eeee amatiimilila ndithu
@user-ux3ed3ni1p
@user-ux3ed3ni1p Ай бұрын
Ndikupemphera Amalawi onse azi alankhula truth to power. kumphamvu ngati njondazi. True Warriors of our time patriots ✊🏾💪🏾🇲🇼
@WillyNyirenda-l7h
@WillyNyirenda-l7h Ай бұрын
Ng'alulani makosana, andale ndianthu osamva. They act to protect their status.
@AbelBlack-f9q
@AbelBlack-f9q Ай бұрын
Lero mwayankhula zogwira mtima ndipo ali ndi makutu amve ❤
@GloriaChinkanda
@GloriaChinkanda Ай бұрын
Chilungamo chokha chokha klkkl😅
@JimmyMaster-l1x
@JimmyMaster-l1x Ай бұрын
Chilungamo chimapweteka big up Gays chakwera akutipwetekesa uyu wayalika basi Boma ndilomweli koma chipani tikusintha😂😂😂😂😂😂😂😂
@MzombeDaniel
@MzombeDaniel Ай бұрын
Anthu manjalende sakufuna kuziyimilila pawonkha Kodi anthuni panokha mwachitapo chani
@sulagrey
@sulagrey Ай бұрын
kodiiiii akuchedwa kukhazikitsaaaa commission chifukwaaa chan ine kuno kumzuzu ndikidikira chilungamo
@BlessatuecBwikaloz
@BlessatuecBwikaloz Ай бұрын
Guys mumatha
@charlesmbale7739
@charlesmbale7739 Ай бұрын
Amakanika ma reform Eni Eni kutulutsa report... ndiye za Commission of Inquiry mmmmmm
@FortunePhiri-kl7oe
@FortunePhiri-kl7oe Ай бұрын
Kkk ndizonama iziii
@RaphaelMaunde
@RaphaelMaunde Ай бұрын
Mcp will never ever change
@JamilaJafali
@JamilaJafali Ай бұрын
❤❤❤
@chesterphiri7523
@chesterphiri7523 Ай бұрын
Yes we need commercial farmers guys
@laston-rj2qs
@laston-rj2qs Ай бұрын
God is watching
@WillyNyirenda-l7h
@WillyNyirenda-l7h Ай бұрын
Maganizo awo ndioti kuliso ndani. Mtima ndioti nditchuke ndine. Akuiwala kuti Malawi sikuchipinda kwa munthu.
@HolmanDazah
@HolmanDazah Ай бұрын
No, wonder,Bayana, pamkuku,am one of morners, Chakwera knows kuti he assassinated our icon in our family and entire Ntcheu. Thus why, Mary is greatly shocked and Chakwera together with his companions, they killed our people since 1983 our people were killed masacadly, and this is their nature. Ndiye, our entire morners family we're pleading to our the well wishers and majority as well as NGOs may intervene to call up commission of inquiry mwachangu kuti chakwera ndi his murderer as he is Malawian Macbeth.
@asahelmachila3026
@asahelmachila3026 Ай бұрын
Indeed Chakwera and his girlfriend Kabwira wanted to sell that island. There is no smoke without fire.
@jameshend9453
@jameshend9453 Ай бұрын
I caught kafungo koipa😮
@JohnJohn-og8rt
@JohnJohn-og8rt Ай бұрын
Zoona big man nosenu ulemu wanuso🎉
@sulagrey
@sulagrey Ай бұрын
likomaaaa yapita kareee agulisaaa bassaaass
@DanMhone-iw6xg
@DanMhone-iw6xg Ай бұрын
Zapamwamba Mr mapha ng'ombe
@YusufJimmy-v1o
@YusufJimmy-v1o Ай бұрын
Mafilu❤
@edsonkamba3170
@edsonkamba3170 Ай бұрын
From your program and the three case studies the beneficiaries of the so called farm inputs loans are from kasungu, jenda and dowa what about southern region districts? Show us the beneficiaries of the so called farm inputs loans from anyone from the southern region to balance up your story.
@RabeccaGama-f7m
@RabeccaGama-f7m Ай бұрын
Kodi zimakhala bwanji ineso ndimafuna ngongolezo malima ku Neno
@KennyThindwa
@KennyThindwa Ай бұрын
Politics has destroyed agriculture sector. AIP for politics.
@EliaSiska-n6r
@EliaSiska-n6r Ай бұрын
Neef is not honest. It should be scrapped. What is said is not what is done
@EthelKudah
@EthelKudah Ай бұрын
Zili bwino mukuperek, kwa anthu a ndalama kare ngongore, zanuz ndi amene akakuvotereni
@jagudanicolas5436
@jagudanicolas5436 Ай бұрын
More fire azibambo or atule pasi undindo anthu oipa kwa mbiri a MCP
@AustinDawood-qc3uz
@AustinDawood-qc3uz Ай бұрын
Anthu inuyo Mulungu alinanu zimene mukunenadzi nde zoona zokhazokha
@FlorryVugy-g4f
@FlorryVugy-g4f Ай бұрын
😂😂😂 boma ndilomweli koma tizasintha atsogoleli
@ClearKondowe-m3j
@ClearKondowe-m3j Ай бұрын
Ine izi zandilimbikitsa kwambiri
@chitanibenito1109
@chitanibenito1109 Ай бұрын
Mcp ndi agalu okha okha!!!
@robertMangochi
@robertMangochi Ай бұрын
Tingachite bwanji kuti tizikhala ndi chakudya chokwana 4de hall 12month thats the question to ask our self not chakwera. Hunger is the pandemic that attack African continent nt only malawi in the continent. For how long we will brem the politicians instead of get the solutionz asblief mensa
@WakuMalawi
@WakuMalawi Ай бұрын
Anhu athu a ndale sakufuna zitukuko.
@AlidihGanie
@AlidihGanie Ай бұрын
✊️✊️✊️
@WillyNyirenda-l7h
@WillyNyirenda-l7h Ай бұрын
Tikutseguka kumaso ndipo pitilizani kulankhula mosaona nkhope. Ma A I P awa ndingozi.
@Dan44-x5b
@Dan44-x5b Ай бұрын
Kodiak a Chakwera iwo Eni are adapitako kamala komwe anagwera a Chilimakooo?
@KingDavedNkhata
@KingDavedNkhata Ай бұрын
Inu siyanitsani alimi ang'o ang'o akumudzi ndi zitsanzo mukuperekazi
@ChembeWaimba
@ChembeWaimba Ай бұрын
Koma anthu inu muzalowa pansi 2025 Chakwera akazakutumulani tizawone zimene muzakambe paka program Kanuka, kazathera pompo.
@sulagrey
@sulagrey Ай бұрын
komaaaaa mtsukuluziiiiii wayitambasulaaaaa eeeeeee next week aBandaaa akharepo kuti andevuuu azitambasulaaa chifukwa andevuuu saopaaa kung'ambaaaaa
@robertnambazo9936
@robertnambazo9936 Ай бұрын
Nthawi zina anthu amangofika potopa basi amaphang'ombe ndi ampakuku 😂😂😂
@bamusitwaibu
@bamusitwaibu Ай бұрын
Hy
@ChembeWaimba
@ChembeWaimba Ай бұрын
Koma Times kulimbikira mtunda opanda madzi, BOMA ndi Lomweli la MCP.. basi mwauponda.
@TonyMzindiko
@TonyMzindiko Ай бұрын
samakhala ndi mbali ngati mumawatsata bwino bwino, mungoti ma guyswa samaopa komanso sanyengelela
@ChembeWaimba
@ChembeWaimba Ай бұрын
Kugwesa BOMA sizitheka, Chakwera sizikumukhuza izi aaaaaah.
@FortunePhiri-kl7oe
@FortunePhiri-kl7oe Ай бұрын
Waziwa bwanj iweyo
@HumphreysFunsani
@HumphreysFunsani Ай бұрын
Akhaula sitisiya kulira unkol
@SelinaGamaliyere-q8v
@SelinaGamaliyere-q8v Ай бұрын
Anthu oyipa a mcp achoke bas
@PrinceKamundi-h4y
@PrinceKamundi-h4y Ай бұрын
Achakwela akuwakayila kale ndiye mwati awathandize ndi aboma omwewo kkkkkk mitu yanu ilibwinobwino kkkkkk
@FortunePhiri-kl7oe
@FortunePhiri-kl7oe Ай бұрын
Welcome guyz
@FrancisDominic-w1s
@FrancisDominic-w1s Ай бұрын
Fisi wakana nsasi
@WillyNyirenda-l7h
@WillyNyirenda-l7h Ай бұрын
Boma zidodo nkuona anthu tikuliganizila anakonza chiwembu ndiowo. Kuli zili! Mmati mai anganene chaini?
@veronicagullo9373
@veronicagullo9373 Ай бұрын
Ndipo nde mwauponda kooopsa
@0wenNkhambule
@0wenNkhambule Ай бұрын
MCP ndiyakupha guys
@KennedyMvula-js7uk
@KennedyMvula-js7uk Ай бұрын
Mabala akupwetekabe.
@BairdThomas-c2k
@BairdThomas-c2k Ай бұрын
yalelo ndi imeneyi mache anu
@FrancisDominic-w1s
@FrancisDominic-w1s Ай бұрын
Mumakwa Guys
@GeraldGomati
@GeraldGomati Ай бұрын
First to comment
@ChembeWaimba
@ChembeWaimba Ай бұрын
Koma anthu inu misonkhano ya MCP yakuwopyani, mukupara bwanji.
@JohnJohn-og8rt
@JohnJohn-og8rt Ай бұрын
Kkkkkk Eya taikanadi zoona mcp ayisovasayandikileso
@AllieKaisi-je6rm
@AllieKaisi-je6rm Ай бұрын
Mwayankhula nanunso chifukwa mulibe chipani chilichose koma mutakhala andale nanunso mzisilu zenizen aaaa
@user-gp10.10
@user-gp10.10 Ай бұрын
Wonder you are mad😂😂😂 mpaka English amachita kugulira bundle!😂😂😂
@ThungaLivuza-p7j
@ThungaLivuza-p7j Ай бұрын
Aboma ndilomweli sangayankhule
@ChembeWaimba
@ChembeWaimba Ай бұрын
Program iyi yaluza direction, becoming useless
@Chikwawa
@Chikwawa Ай бұрын
kwa iweyo
@ChembeWaimba
@ChembeWaimba Ай бұрын
Apa ndale zimenezo zizitheka, mwauponda, chovuta chinali chani kumuwuza Chakwera munjila yolongosoka. Akuyankhula payekha or wapopedwa ndi ena pepani zizitheka, achite clear mutamtukwana nthawi yonseyi you think ndinu wochenjera.
@RoyKambalame
@RoyKambalame Ай бұрын
Mwapanikizikatu
@Chikwawa
@Chikwawa Ай бұрын
Satan wathawa mkachisi kukakhetsa mwazi wa a Chilima ndi ena.
@lungsTug
@lungsTug Ай бұрын
Anthu onse 9 ndiwofunikira zofufuzidwe ....chifukwa pali mafunso.....apakuku ndi amnzanu mukulongosola
@ChembeWaimba
@ChembeWaimba Ай бұрын
Zokamba zanu ngati muganiza kuti mumpanga de campaign Chakwera mwauponda.
@JohnmarkNazombe-hi9xd
@JohnmarkNazombe-hi9xd Ай бұрын
Chakwera de campaign himself....
@ChembeWaimba
@ChembeWaimba Ай бұрын
Mulungu aliko kumwamba ngati mukuganiza kuti mugwesa BOMA ndi izi mwauponda.
@ShamimFailosi
@ShamimFailosi Ай бұрын
Satan get lost
@NthawiKatanga
@NthawiKatanga Ай бұрын
Chipani Cha MCP ndichokupha kuyambila kale koma 2025 mufune musafune yambañi kupakila mwagwa basi
@geofreydzinyemba6107
@geofreydzinyemba6107 Ай бұрын
Mukakhala pa bwino, muzithanso kuganizila anthu ena osangowona pomwe Inu muli please
@TiongeChilongo-j4f
@TiongeChilongo-j4f Ай бұрын
Mulungu wake uti nanu akalore MCP kupitiliza kupha wanthu
@sulagrey
@sulagrey Ай бұрын
iweeeeee
How Much Tape To Stop A Lamborghini?
00:15
MrBeast
Рет қаралды 198 МЛН
Ice Cream or Surprise Trip Around the World?
00:31
Hungry FAM
Рет қаралды 17 МЛН
小丑揭穿坏人的阴谋 #小丑 #天使 #shorts
00:35
好人小丑
Рет қаралды 54 МЛН
PRANK😂 rate Mark’s kick 1-10 🤕
00:14
Diana Belitskay
Рет қаралды 11 МЛН
BON KALINDO   "THE DC"  WANG'ALURA AREA 30 YONSE KUPHATIKIZAPO IG MAI YOLAMU
11:30
How Much Tape To Stop A Lamborghini?
00:15
MrBeast
Рет қаралды 198 МЛН