MPAKA A NEWTOWN KAMBALA KUULURA ZONSEZI LIVE PA TV? ANTHU ASIYA KUBISILANA CHICHEWA KU UTM AVULAZANA

  Рет қаралды 19,645

Makosana

Makosana

Күн бұрын

Пікірлер: 63
@mcfarlenmatope4138
@mcfarlenmatope4138 2 күн бұрын
the way i used to see this man ... now i have got a different perspective... Newton is intelligent.
@hastingskalambo8502
@hastingskalambo8502 Күн бұрын
Am perceiving alot of lies in his truthful statement of how the UTM party started.
@supa4dupa
@supa4dupa 2 күн бұрын
Awa ndiye Atsogoleli ofunika kusintha Malawi,a gentleman,a engineer okhonza zinthu,zikomo Honourable Kambala,all the best🎉🎉
@billybanda7280
@billybanda7280 Күн бұрын
Kambala he's a true leader and can be a right person to lead UTM for next year elections
@Owen-n1v
@Owen-n1v 2 күн бұрын
Leah, I know you don't know me, but I would like to let you know that you're a true journalist. You know how to ask questions. We miss you, welcome back.
@NikolasNanawe
@NikolasNanawe 2 күн бұрын
zoonandi km guys kunena chilungamo dzisisi sotse za chilima akuziwa nda usi bas palibe winaso ai enawa ndale bas ❤❤
@innocentkhumbanyiwa4780
@innocentkhumbanyiwa4780 2 күн бұрын
Kambala is an intelligent person
@OscarNamaya-x1u
@OscarNamaya-x1u 2 күн бұрын
Lea tinakusowatu umaziwa tchito your number one 💪💪
@alfredpatel3984
@alfredpatel3984 2 күн бұрын
This is my first time to hear Kambala speaking. The man is composed and seems organised. The mistakes made by Chilima in identifying Usi as vice president. Kambala has vast knowledge of the UTM other than Usi. Manganya couldn't stand against people like Kambala no wonder Manganya saw defeat. Manganya is an MCP pumpkin hence he has no future in Malawi politics. UTM must go for Kambala.
@BensonJere-i9k
@BensonJere-i9k 2 күн бұрын
Kkkkkkk akuti bwana Utsi Ali ku mgwirizano,,, osati UTM.
@JaneMoyo-b7i
@JaneMoyo-b7i 2 күн бұрын
Kani a Newton Kambala ndi nzeru chonchi. Big boss🔥
@hastingskalambo8502
@hastingskalambo8502 Күн бұрын
Kambala ali ndi ndale za a chair😅
@UchizieFMtemela
@UchizieFMtemela Күн бұрын
UTM ndi allience payokha aliyense ali nkagulu kake. Koma awawa akundimvekera mwamabodza bolakonso USI
@BrieMajoni
@BrieMajoni 2 күн бұрын
Eeee nkanakhala ku Malawi nkanakavolela this man on Sunday 🙌🙌🙌🙌
@beinhardkausiwa7107
@beinhardkausiwa7107 2 күн бұрын
Now am convinced kuti mr kambala simunthu wamba.....please let him lead utm
@AlickMDayi
@AlickMDayi 2 күн бұрын
He's a man with a brain i too i give him my vote
@PAULMOSES-y3e
@PAULMOSES-y3e 2 күн бұрын
Dzikoli kuli anthu anzeru zofuna kutukura amalawi koma anthu oterewa sapatsidwa mwayi oti awonetse zomwe angathe koma amatcheredwa ndale politically 😂😂😂
@peterchiutsi
@peterchiutsi Күн бұрын
Kambala Ukuyankhula za Mzeru koma ngati ukuyankhuladi moona mtima i can adverse you that Usakhale president look for this guy so call McBride Nkhalamba and talk to him believe me you guys you will make it
@SolomonNjolomole
@SolomonNjolomole 2 күн бұрын
Mr kambala ndikumvetsera mwa chidwi km ndakhudzika kwambiri.
@liliantamaona1669
@liliantamaona1669 2 күн бұрын
Intelligent man
@MzikaPhiri
@MzikaPhiri Күн бұрын
Mbambande Mr Kambala
@jowiemhango5058
@jowiemhango5058 2 күн бұрын
I love u already mr
@giftmakoyo1441
@giftmakoyo1441 2 күн бұрын
Ku utm mmmm kuli zinthu what if Kabambe wawina Newton uzavomereza Koma l dout
@yamikanimdala5955
@yamikanimdala5955 Күн бұрын
Kambala uja ndi headidi
@worldfamous_23
@worldfamous_23 2 күн бұрын
18:22 mwaona? Politician above the law, nanga kumamgidwa kwa munthu guilty or innocent president zikumukhudza? Kodi president ndi prosecutor? 😢
@lovemorengwira
@lovemorengwira 2 күн бұрын
Truly ndege sinagwe kungoti kugwa koma anyani ndi amene anayi gwetsa ku chikangawa
@IsaacNgoma-g9x
@IsaacNgoma-g9x 2 күн бұрын
Kambala ndimunthu wankulu more 🔥🔥🔥🔥🔥
@RemitterFlik1130
@RemitterFlik1130 2 күн бұрын
Inetu ndinalota kale izi za kambala kuti azakhala msogoleri wa UTM
@EliSMpuka
@EliSMpuka Күн бұрын
Osalimbikitsa tsankho akambala utm tilibe mwinimwini
@MaliGomani-z4k
@MaliGomani-z4k 2 күн бұрын
Kod aliyense amangoti amandiuza zonsinsi 😂😂😂 aaaa koma guys
@KazembeGwedeza-b9u
@KazembeGwedeza-b9u 2 күн бұрын
Mukakapusa anthu a UTM pa seventeen, mutha kukasankha munthu amene sakuziwa chiyambi cha UTM azakutengerani kuphompho komanso UTM izatha.Chifukwa anthu enawo abwera zulo UTM sakuyiziwa azayipititsa komwe achikera,chifukwa anthuwo achita kutumidwa ndizipani zomwe zinamuchita chipongwe malemu Chilima.Chifukwa tisayiwale kuti zipani ziwilizi zinachita chipongwe malemu Chilima.
@MzikaPhiri
@MzikaPhiri Күн бұрын
Usi ngobalalikadi
@aubreymagombo5907
@aubreymagombo5907 2 күн бұрын
Ndale ndi kanyama koyipa
@MaryNgola
@MaryNgola 2 күн бұрын
Kd a Lea malekano mimba ija mwabelekano kkkk
@giftmakoyo1441
@giftmakoyo1441 2 күн бұрын
Anthu a ndale ndiinu anthu oyipa kwambiri
@makhalidwemclean1987
@makhalidwemclean1987 2 күн бұрын
You don't want any political positions because you want to play them as puppets.
@verinachiponde6922
@verinachiponde6922 2 күн бұрын
Ine nsalu ya UTP ndili nayo
@WanangwaChisi
@WanangwaChisi 2 күн бұрын
Koma chi kambalachi chachabe amwene
@ruthmissi7766
@ruthmissi7766 2 күн бұрын
True he died a hated person by few selfish individual s may the Lord be the best judge
@Mavisbunny346
@Mavisbunny346 2 күн бұрын
Andale ambiri safuna kunena zoona. Munthu akafa amakhala wabwino. Chikhalidwe cha A Malawi timafuna kuoneka abwino kuti anthu atikonde. Tisinthe khalidwe limeneli.
@GraceChenda-q2g
@GraceChenda-q2g 2 күн бұрын
Misonkhano yonse samafuna kupitako,koma kudandaula chilichonse,,kanzibambo kameneka,,ife tinatulukako ku Tonse
@senaherbo3714
@senaherbo3714 2 күн бұрын
Munatinamiza kuti tidzadya katatu pamene munalibe njira yodalilika yoti anthu adzadyadi katatu Look what is happening now all today's problems are coming from vision yori tidzadya katatu
@asahelmachila3026
@asahelmachila3026 2 күн бұрын
Kambala is a lier and indeed a divisive person who should not be allowed near any serious party. He misinformed Chilima into forming UTM. Choka apo Newton, nzeru ulibe
@GloryKhondiwa
@GloryKhondiwa 2 күн бұрын
Eeeeh 😂 mwakwiyatu
@EmilyKanyika
@EmilyKanyika 2 күн бұрын
Eya zoona
@MsondaBanda
@MsondaBanda 2 күн бұрын
Utm mulije ulongozgi
@TrinityMalimba
@TrinityMalimba 2 күн бұрын
. Mhuuu
@GraceChenda-q2g
@GraceChenda-q2g 2 күн бұрын
A kambala mwandisintha maganizo anga
@FrankSubili-fv2sf
@FrankSubili-fv2sf 2 күн бұрын
This man looks igneous
@NosiphoMazibuko-e9z
@NosiphoMazibuko-e9z 2 күн бұрын
Kodi ndiwe Newton amene ukupangidza idziko lamalawi chigukwa iwe ndamene udamuwudza chilima kuti ayike mcp boma ndeno ukuganidza kuti mcp ungayichotse boma mudatilakwila inu dyela anthu adyela inu chilima adamwalila chifukwa cha iwe chilima amaganizo ake amayendela ayinuyo mwini chipani
@James-v8v8d
@James-v8v8d 2 күн бұрын
Dangers for chilima
@James-v8v8d
@James-v8v8d 2 күн бұрын
This is not good in politics Mr kamala
@MagieJames
@MagieJames 2 күн бұрын
Akambalanu mukakhala munthu wabwino munalola bwanji kt chilima akwere dege ija akafe osamuuza kt akwere galimoto mwasowa zoyankhula chifukwa kulibe chilimayo musanamizille
@James-v8v8d
@James-v8v8d 2 күн бұрын
Akulu inu akambala mmmmm
@FredKanyerere
@FredKanyerere 2 күн бұрын
Zoonadi kambala maganizo abwino.
@BensonJere-i9k
@BensonJere-i9k 2 күн бұрын
A Lea mukuthira mafunsotu
@GraceChenda-q2g
@GraceChenda-q2g 2 күн бұрын
Amauzidwa adada awo koma Ali ndimoyo wa mkazi wamitala
@James-v8v8d
@James-v8v8d 2 күн бұрын
Mmmm mpópsa apo samamufuna
@ChrissyBhima
@ChrissyBhima 2 күн бұрын
Akambala chirima sananzunzike Ku DPP,koma anthu ngati inu akambala ndiamene munapangisa kuti chilima azipanga mavuvu Ku DPP ndinuyo,Malo mowauza nkhani ya nkhanza zomwe wakumananazo Ku MCP,lero muli buzy kukamba za DPP,anthu andale ndikovuta kuwakhulupilira
@JulietMakataMakata
@JulietMakataMakata 2 күн бұрын
Akambala sinkukukhulupililani coz inuyo ngati munthu wankulu wachipani bwenzi mutapanga anthu kuti amuone Usi bwinobwino not the way munalolela kuti Usi azinyozeka zuchita kuonetselatu kuti Usi mumamupangila ma plan achabe kumbali ndithu.
Миллионер | 3 - серия
36:09
Million Show
Рет қаралды 1,5 МЛН
風船をキャッチしろ!🎈 Balloon catch Challenges
00:57
はじめしゃちょー(hajime)
Рет қаралды 82 МЛН
ЛУЧШИЙ ФОКУС + секрет! #shorts
00:12
Роман Magic
Рет қаралды 37 МЛН
prophesy about 2025 presidential election
26:15
Senior Prophet Mtupa
Рет қаралды 148 М.
Миллионер | 3 - серия
36:09
Million Show
Рет қаралды 1,5 МЛН