Frelimo sinawine yatoba eu stou a que memo e moçambique as pessoas já sta casados com frelimo nos queremos mudar governo ndiposo ndikilani zimenezo zichitikaso kumalawi next year 👋
@JasonMailos13 сағат бұрын
Chaka Chamawa ndikumalawi kuno
@kingssalema33649 сағат бұрын
Ndipo osakaikaaaaa.
@chifundocharles23486 сағат бұрын
Akungoyenera kutero basi iyaah dziko lapansi ili 😂😂
@VenançioZocueza2 сағат бұрын
Chilungamo tikudziwa ndife owina ndiotsutsa.
@MchachaGoodson8 сағат бұрын
Atekatenge mpando zitsilu za anthu onse oyendesa zicsakha.Anthu ayenela kuchita zi onetselo what ever it takes chipani cholamula chisalamulenso viva opposition leader we must fight against the the dictator's leaders.
@GodfreyWhayo-hh1dm12 сағат бұрын
Ku Malawi akudikira kuti mmene zithere ku Mpanyiraku ziwapatsa a Chakwera ndi Kongiresi chao kuganiza mofatsa . Anthu sangabvote malingana ndi maganizo awo , chipani china nkudzanena kuti iwowo ndiye opambana .
Dyera, mpandowu ndi wabwino chilichonse chaulere, sugula kanthu plus ufulu opondereza ndi kubera anthu ako opanda okufunsa.
@HalisonSolomon11 сағат бұрын
@@henryphiri6100 eish koma ndiyetu komano pafikira malawi ZINANGOVUTA kuti a malawi ndi a TULO akanakhala maiko ena atamatcha chakwera ACHOKE pampando koma ife kugona TULO ndithu
@henryphiri61009 сағат бұрын
@HalisonSolomon zoona school inavuta, sitidziwa chibwino ndi chiopa
@PatrickLongwe-yc9il11 сағат бұрын
Mulirabe boma ndilimweli basi
@MaliyaMwantan11 сағат бұрын
Panya pamako Mwana wa hure
@ShamilahSaizi10 сағат бұрын
Ku chikangawa nt malawi
@LastonMmanga-r2u8 сағат бұрын
Iwetu ukunama ndipo ulira ndi iweyo ambuyakowo Ali kundende 😂😂😂😂