NKHANI YA KAFUKUFUKU WA IMFA YA ACHILIMA YAVUTA KU PARLIAMENT MA MP ALIULIRA BOMA

  Рет қаралды 24,892

Makosana

Makosana

Күн бұрын

Пікірлер: 51
@BrightZionga
@BrightZionga 2 ай бұрын
Oku ndiye timati kubwela honorable chaponda osamagona keep it up
@RobertGoliat-gt2qh
@RobertGoliat-gt2qh 2 ай бұрын
Kut Khaa ❤uku ndy kubwerako Mr George Chaponda keep it up
@emmanueljelemani4203
@emmanueljelemani4203 2 ай бұрын
Thanks Hon Chaponda for speaking out for the common citizens of Malawi
@ElizahMadi
@ElizahMadi 2 ай бұрын
Salute chaponda
@ChimwemweJuwao
@ChimwemweJuwao 2 ай бұрын
Salute mr chaponda
@ExcitedBreakingWaves-oh3zb
@ExcitedBreakingWaves-oh3zb 2 ай бұрын
Agawana ndalama imeneyo
@EdsonKamwendo
@EdsonKamwendo 2 ай бұрын
More fire Thapa One
@EsetaGerate
@EsetaGerate 2 ай бұрын
Kubwera kumeneko ayake basi candle
@LeyvanSamuel-pe5tc
@LeyvanSamuel-pe5tc 2 ай бұрын
Bola pamenepo Chaponda wazuka soprano💪💪💪
@KennedyPhiri-h9h
@KennedyPhiri-h9h 2 ай бұрын
Yes we need people like you achaponda
@MPHATSOKALUWA-lm2uy
@MPHATSOKALUWA-lm2uy 2 ай бұрын
Ndpo akutulutsa zake kumkuyu zmne zili zosiyana kwambr nd zmne wayankhula chakwera ku German
@ChriKezi
@ChriKezi 2 ай бұрын
matenda kulibe kumalawi koma ngozi ndizomwe ziliko now so iys beter kupeza njira zothesela ngozi
@FelixGadama-q3v
@FelixGadama-q3v 2 ай бұрын
Chidyola
@WesleyKalimwayi
@WesleyKalimwayi 2 ай бұрын
Ameneyo sikaswili wandale Koma ndi gulu la chikangawa ameneyo Kodi muthu wakuphela bambo ako mwana ungamapite ku nyumba ya muthu wakuphayo ndi kape
@AllieKaisi-je6rm
@AllieKaisi-je6rm 2 ай бұрын
Mr chikangawa amakakamila chidzungu ngati mai ake ndi bambo ake anali adzungu bwanji 😊
@WesleyKalimwayi
@WesleyKalimwayi 2 ай бұрын
Chaponda ndi katundu musaone Ngati chitsilu chinja chadyela chinakhomwa
@ManMen-kp2ze
@ManMen-kp2ze 2 ай бұрын
Keep it up our opposition, without fear this is the only Malawi for us , there is no where we can borrow another Malawi, don't let them play games with us,
@frankdomingo1109
@frankdomingo1109 2 ай бұрын
Timadabwatu kuti PAC ilikuti.... accountability is needed...this current gaffment canti do things with impunity....this is a democratic state.
@FatimaLesson
@FatimaLesson 2 ай бұрын
Anenetu ameneyo oho
@DumisanPhiri
@DumisanPhiri 2 ай бұрын
Zimenezo nde kutisewelesa nkhani ndi yoti ayipase lipoti lomwe lilipolo timve. Nde inu mukut akayambileso kufufuza aaaaaaa mwina nanu mukukhuzidwa nde mukuwopa apeleke liport basi la MDF Ndi linalo
@MichealSigoloti-q3i
@MichealSigoloti-q3i 2 ай бұрын
Mukulimbana ndimunthu woti amwalira kale Moti muzikambirana Za njala ili mumalawi
@WilliamSimkoko-t2v
@WilliamSimkoko-t2v 2 ай бұрын
Tikufuna chilungamo Cha imfa ya Chilima
@BizweckPhwete-c3r
@BizweckPhwete-c3r 2 ай бұрын
Pitilizani kufufuzaku kt tiziwe choona ife amalawi
@joyahmedjoma4615
@joyahmedjoma4615 2 ай бұрын
Muzisya zimenezo azapitilidza ena inu achina chikangawa watilephera aaaaaa
@CathleenMsaya
@CathleenMsaya 2 ай бұрын
George chaima Siya zopusa zakozo
@AlexNjanje
@AlexNjanje 2 ай бұрын
Eeeee aaaaiiiiii tathandizidwa bola mugawane pang'ono osati zonse mulitu njala ndziko muno
@DevisonHala
@DevisonHala 2 ай бұрын
Iwe amene ubapa chakwera payifa ya chilima ndi azawo ndiwe fiti yotamba masana pa modzi ndi amako rip chilima palibe wa mbewu
@brightkaiya4370
@brightkaiya4370 2 ай бұрын
Koma iwe unaotcha ministry of agriculture kubisa chilungamo .ndiye dziko ili likufunaso chilungamo.mwatinamiza zambiri but tell us zoona takutoperani anthu inu ku parliament mudzikamba zokomera Malawi
@CharlesBanda-pm2oe
@CharlesBanda-pm2oe 2 ай бұрын
Chaponda ndi galu ameneyi amvere zomwe eni Ake Aku German anena mbuli za kumalawi,chakwera simumutha Mapeto Ake mukodzedwa mu parliament momwemo dikirani
@mcmillanndau3360
@mcmillanndau3360 2 ай бұрын
Dpp kufunsa kuonetsa ngati anthu abwino. Mukayasenso for Robert chasowa, njaunju, komanso 20 pipo Ku mzuzu. Osaiwala mulandu wa ma albino
@PaulBeyad
@PaulBeyad 2 ай бұрын
Atiuze zoonad zaimfa ya Achilima
@MarkBannda
@MarkBannda 2 ай бұрын
Mama kaliyati ngwakubendezga, ndipo wabendezgenge wanthu wanandi,
@BenjaminKamanga-p8w
@BenjaminKamanga-p8w 2 ай бұрын
😂😂😂😂😂 imwe namwe uli kasi
@WilliamSimkoko-t2v
@WilliamSimkoko-t2v 2 ай бұрын
Kapena mwina tidikire bakili muluzi tv
@ElizahMadi
@ElizahMadi 2 ай бұрын
Mugawana agalu inu
@VictoriaKumwenda-k6o
@VictoriaKumwenda-k6o 2 ай бұрын
Akaliyati kupupuluma ngati ntchentche akufuna upule kod nthawi yachilima mesa anthu ankaavala nsalu zautm chaipila ausi nsanje akaliyati
@LukaThawe
@LukaThawe 2 ай бұрын
Kupanda zochita Kodi simuziwa Kuti ndege yimampha zachamba basi
@paulnyondo7572
@paulnyondo7572 2 ай бұрын
Akaliyati sakulakwisa akunena chilungamo poteteza kugulitsidwa kwa chipani.ku mcp
@EvansNkumba-q7t
@EvansNkumba-q7t 2 ай бұрын
Simrex tithyola bbava
@WesleyKalimwayi
@WesleyKalimwayi 2 ай бұрын
Achitchola ndalama pamenepo mwana kale kudako
@chimwemwechiundira6002
@chimwemwechiundira6002 2 ай бұрын
Good
@LasieMolebatsi
@LasieMolebatsi 2 ай бұрын
Chikangawa ziyakhula Africans basi
@DanielJuwawo
@DanielJuwawo 2 ай бұрын
Mudzingoyankhula chichewa achikangawa
@RichardThera-i1p
@RichardThera-i1p 2 ай бұрын
So, there's no freedom n rights of participation in UTM party? Where is Democray? Akweni, don't personise politics, party colour is not your property! Thanks
@SuzgoMkandawire-ss4kh
@SuzgoMkandawire-ss4kh 2 ай бұрын
She doesn't want utm members to attend any chikangawa party's activities
@WesleyKalimwayi
@WesleyKalimwayi 2 ай бұрын
Wakupha uyu chakwela
@paulkalizangoma5904
@paulkalizangoma5904 2 ай бұрын
Mubeso kuti mupangile kampeni
@SebastiaoErnesto-mh6ec
@SebastiaoErnesto-mh6ec 2 ай бұрын
Chaponda oe
@CharlesBanda-pm2oe
@CharlesBanda-pm2oe 2 ай бұрын
Chaponda mbava ya kaloswe maize gate ungayese kuti amalawi adayiwala, ndalama zija umachita pilozi tikukumbukabe
Wait for the last one 🤣🤣 #shorts #minecraft
00:28
Cosmo Guy
Рет қаралды 18 МЛН
黑的奸计得逞 #古风
00:24
Black and white double fury
Рет қаралды 28 МЛН
У вас там какие таланты ?😂
00:19
Карина Хафизова
Рет қаралды 13 МЛН
Wait for it 😂
00:19
ILYA BORZOV
Рет қаралды 9 МЛН
Wait for the last one 🤣🤣 #shorts #minecraft
00:28
Cosmo Guy
Рет қаралды 18 МЛН