Those that think that Dr. Joyce Banda is a spent force in Malawian politics are cheating themselves and at the same time misleading others. Dr.Joyce Banda is and will still continue to be a highly respectable force in Malawian politics. There are so many good and great things Dr. Joyce Banda has done for Malawians and continues to do which Malawians of good will and sound reasoning will never forget. Long Live Amayi!
@ZenakMatekenya-hp5ru3 ай бұрын
😅😮 10:22
@JeanKambala-gm1zr5 ай бұрын
Sangasiyane ngwilizana wawo ndi wamaganzi kuteloko mayi Joyce Bandah ,,ngankhale muli akulu Anga Koma lmfa yachilima mudziwapo kanthu inuyo ,,
@PhillspicJere5 ай бұрын
Mutu wanu ndiobonga amai Inu, mgwilizano wa DPP ndi UDF siwamagazi?
Joyce Banda nayeso NDI wa satanic please fuko Langa mtundu wanga , Chonde musakopeke NDI Joyce Banda, Mai Joyce Banda she is a Satanic member choose wisely...other wise mukutulutsa satanic chakwela mukulowetsa satanic so ...may God help us ..
A Joice Banda tazisiyani izi. That time you had that opportunity because of death and you can't win your dreams.
@PrinceTaibuBanda5 ай бұрын
Good
@FlywellThengo5 ай бұрын
Kunena zoona mulamuliro wanu amayi zinthu zimaenda km ife tili pambuyo panu mai 2024 moto kt buuuuuuuuuuiiiiiiiii
@MpapiParadise5 ай бұрын
Kkkkk Joyce banda amakhala mu fernbrook estate muno pa Stage wood street apa ife tinali kumuona tsiku ndi tsiku and olo amufunse anena kuti zoona. Ku America Joyce adakhalako liti ? Joyce amakhala mu fourways/ Johannesburg Fernbrook estate - kenako anasamukila ku Dainfern ndikomwe anamumangila kuti abwelere ku Malawi zaku America mukuzitenga kuti agalu inu
@SpiweJambo5 ай бұрын
Zee one films
@tobiousmtenje1395 ай бұрын
Ubwino wake mwavomereza kuti mafumu akuvutika.Mavutowo ndye akuta wina aliyense
@happynyirenda87905 ай бұрын
Kanyamata aka boza ngati katsikana ka 15 yrs old
@AlfredMachisawo3 ай бұрын
Uyu Nd wa MCP
@faidaceciliaYekha5 ай бұрын
Kkkkkk kuiyang'alura😂
@ShaidaJackson5 ай бұрын
Agalu inu asatanic okhha okha,tikumana 2025
@lastonekaponya76755 ай бұрын
Salu zikugawidwa koma sakuvala mudzifuse
@KensonMsiska5 ай бұрын
😂,,,😂😂 palibepo Cha nzeru apa
@MarvinDulani4 ай бұрын
Misala party
@ChristianMtambalika2 ай бұрын
Okubanso uyu add bas
@kingsleymsampha22605 ай бұрын
Kodi mukadali ku mcp eeeti?? Ayi tamva
@MabvutoMichaelPanagona5 ай бұрын
Mai Joice banda imfa ya chilima akuidziwa
@Paul-q2p5 ай бұрын
Mmphuno mwako
@voicedumathindwa5 ай бұрын
Joyce chipani chako ndi chakwanu konko ndi zisilu zakozo
@grantkangombe68045 ай бұрын
Ndiye ngati akukayikirana kuba chitenje what more ndalama za boma?
@TenNgwira4 ай бұрын
Apitirize mayi joice banda
@FosterZulu-b3j5 ай бұрын
Ingotulukani ku mcp inu
@INNOCENTMOFOLO-io8tg5 ай бұрын
kodí zílimótero et
@MangaDamiano5 ай бұрын
Mwasowa chochita Kodi ?
@Martinmkapangakapanga5 ай бұрын
koma ambuliwu amalawi changamukani
@SmilingFishingRod-zc4wx5 ай бұрын
Kkkkk koma anthu akafuna kum'bera wankulu eeeee amanama koopsya. M'bereni Ali ndi ndalama zomwe anaba kuzera mu Caschgate tuyeni naoni musamukhumudwise m'beleni
@ClementsKamanga5 ай бұрын
Chokhacho achimwene mwauponda mcp ndimbola
@LysonMkomadzinja4 ай бұрын
10:14
@AustinMilazi5 ай бұрын
Hi
@cynthiakananji16085 ай бұрын
Zilombo za chakwera
@ElizaLabson5 ай бұрын
Adadiiii moto buuu!!¡
@esaumtambo-d3h5 ай бұрын
Anthuwa atiwonjeza ife ovota atifuna pompano
@IgnatiousFote5 ай бұрын
chivunde ali nd mfundo mbambande koma chipanichi chamuchepela kwmbr
@esaumtambo-d3h5 ай бұрын
Chaka cha mawa chakwera no vot
@KennedyPhiri-h9h5 ай бұрын
Inu palibe chanu chipani cha satanic chakwela palibe za vote
@MoreenHussein5 ай бұрын
Tinadzidzukadi zoona Ng,alulula basi ,tachika nacho kutali
@johnkambala6925 ай бұрын
Aimed basi
@frankiechasokoneza58025 ай бұрын
Awa angomasuka basi atulukamo mu gwilizano wa Tonse alliance