President watundu wanji akadzuzulidwa kumanga athu.peter akadzuzulidwa samaphya mtima ayiii
@LukaAfromadАй бұрын
Komanso akadzudzulidwa amamva nkusintha zochita km si awawa mmmmm zokanika
@BlessingsLuclusАй бұрын
Watching form south Africa apm my vote
@Macrina-vv3usАй бұрын
APM my vote ❤ chikangawa airport ikagwere
@SolomonNjolomoleАй бұрын
Ndineyani pamaso panu APM 🔥 💙💙💙💙
@GraceZumazumaАй бұрын
Chakwera si president anatsikila ku Malawi kudzaba kudzapha ndikudzaononga tsogolo la ana anthu ndi chinzake chachikulu mutu asatana oipa mtima
@WilliamChopika-u5bАй бұрын
I love my country Malawi, Malawi my vote
@JamesALLi-m8iАй бұрын
More fire 🔥 Namalomba Apm is my vote 🗳 2025 boma
@ReginaMulipaАй бұрын
Koma abale nde kwatarikatu kovota paka September Chaka chamawa iiiiiii koma nde tishilikadtu
@DONNEXKhama-bk1gyАй бұрын
More fire 🔥🔥🔥🔥🔥 APM 💙💙💙💙
@festonkapesi3771Ай бұрын
More fire Apm
@fredgabrielnyanguluАй бұрын
Koma muwauze a Dad wo kuti asagone kwambiri ai ayambepo Campaign coz kugona pakati ndikuyambilira akufunika azipanga Campaign asamangogona ku Page House ai
@AlfaKatulaАй бұрын
Abale mpaka kudya chitedze eish Ambuye atikhululukire zachilendo😭
@FatimaChibwanaАй бұрын
ADAD it's ma vote
@BrightonNdalama-x2bАй бұрын
DPP our hope
@PeterRabson-z3wАй бұрын
Dpp my party
@AlinfeJereАй бұрын
Khaaaaaaa 🔥🔥🔥
@WillmotChiuimia-vr6ouАй бұрын
DPP woyeeee ❤❤❤❤❤, APM Boma, osati okumpha winayu ndi kubaa
@AlexKaunda-ny2egАй бұрын
A MCP tatopa Nanu pankhani yopha anthu iwe chimwendo Banda machende ako plus yr boss and his wife
@0wenNkhambuleАй бұрын
Good message Mr namalomba number ❤
@FosterDouglas-u9uАй бұрын
Akulu akulu DPP tiyiope ndithu.mark my ward
@McDonaldbeketeNkhata-n4lАй бұрын
DPP yilowe muboma
@EvanceRazakiАй бұрын
❤❤❤❤ a mcp asavutike boma ndilomweli bas boma lopand khaza
Sukunama!!! The surport was Demure 🎉 chikangawa kukuwidwa mpaka anasitha njira ,Dppp ipatseee motsooo 🎉🎉🎉🎉
@ShillaShamil-v2yАй бұрын
Boma APM❤❤❤❤❤❤❤
@JonesChilongaАй бұрын
Amalawi akufuna chakwera achoke basi apume kudya chitedze
@VeronicaChimkondeАй бұрын
💙💙💙💙
@DannyKalumbaWaBanda-q7oАй бұрын
AMP my vote💙💙💙💙💙
@SamuelWysonАй бұрын
Dpp more fire
@MavisGamahАй бұрын
Koma ❤❤❤❤
@samanthamuller7643Ай бұрын
My vote Dpp woyeeeeee
@omarajibu860Ай бұрын
APM sanali wosakadza chuma. He made everything stable.
@PaulSimon-h1fАй бұрын
Ing'alule namalomba
@JosephFulayiАй бұрын
Apm my vote
@HINJESPHIRI-r5yАй бұрын
more fire APM
@LightonKamwanaАй бұрын
🎉zakale zimenezo dala
@SAMARTEDWART-b1jАй бұрын
Bola foteleza mzatisisire plz
@LeoMisokweАй бұрын
Blue is wisdom lowani mboma red is blood
@ChichiChitulu-d6eАй бұрын
Boma ilooo
@isaaczuzeАй бұрын
Ma bouncer ake amenewa wa mcp angapange chiyani .....my vote is for Apm osati mbuzi tili nayo leloyi ayi ......wasiya njala ili nyoo kuno koma iye kumakaononga misonkho yathu ndi zibwenzi ku unga
@BrianAmos-s2kАй бұрын
Ndibamvadi chisoni nditawona azimayi ana kumbuyo kumatolela chitedze eish 😊😊😊
@MokongolaMbalangweАй бұрын
Mankhwala a moto ndi moto usazimesonkhezelani mwayakamoto big five
@JohnJohn-og8rtАй бұрын
Good nice asiyeni achakwela wo alibe umuthu
@SamuelNsinganoАй бұрын
A Tonse Alliance atikwana, anatinamiza kut fees itsika ma University koma pano ophunzira tikuvutika kwambiri
@Halima-i4xАй бұрын
D PP oyeeeeee🎉🎉🎉🎉🎉
@davidsnkhomah2688Ай бұрын
DPP it's worse of time, and someone with all 5 senses working cannot forget what DPP did during they time
@FRANKMUSSA-u8hАй бұрын
Koma nde zimabausatu. MCP uyelekeze zachamba akuponda
@SalomeManda-c1iАй бұрын
Palibe kuchitira mwina DPP ikuwina bc
@chrisschikozera7271Ай бұрын
Amp ❤❤❤❤❤ .moto
@MavisGamahАй бұрын
Achoke chikangawa
@LeyvanSamuel-pe5tcАй бұрын
DPP 🔥🔥 boma ilooo!!!!!
@dexzimba4082Ай бұрын
❤❤❤❤❤
@EsnartSimentiАй бұрын
❤
@AlickJamАй бұрын
Ndipo bread anali pa 350 not 500ha
@EvanceRazakiАй бұрын
Kumenek ndye kuyakhula zithu zimachipa
@LacksonLombwa-b6xАй бұрын
Vuto anthu akumwera ulesi ndiye mmafuna president azikhala wakwanuko kuti azikulandiritsani zinthu zaulere,, central region ife timalima ndipo timazidalira pankhani yachakudya
@FrankSomanje-c4qАй бұрын
Olokuno Ku South Africa tikuti Dpp woooooooye
@paulmanyamba5437Ай бұрын
Ayi bwana mwalakwitsa fanta 800 pano
@YusufTwaibu-z1eАй бұрын
APM isafowoke tilipambuyo
@JohnYoweliАй бұрын
Anthu vinavi ndiyani aja omenyawa kapena
@FresherShabaАй бұрын
MCP🎉🎉🎉🎉🎉🎉🎉🎉🎉🎉🎉🎉🎉🎉❤❤❤❤❤❤❤❤
@PatricaTchuwaАй бұрын
Olo.manyazi ulibe hahahaha 😱😭
@blessingsgeoffrey9414Ай бұрын
🎉🎉🙏🙏🙏
@yusufbakaliАй бұрын
❤😂 ADAD
@EvanceSungani-cv9jkАй бұрын
DPP❤❤❤❤❤❤❤❤my Life
@AshimayeGamaАй бұрын
Ndipo chakwela wapita ku USA 🇺🇸 komatu ramaphosa sanapite watumidza nduna iyeyu bwanji
@AgnessKalindoАй бұрын
Ifetu tipephera mwa mphamvu kuti peter adzalamulire. Mr chikangawa achoke kmaso a peter musadzaiwale kuwathandiza anthu amene akuyikani pa mpando. Zikomo
@KennethDavieАй бұрын
ADAD WOYEEEE
@ConfusedAstronaut-qv6wqАй бұрын
This is one of the worsted party mcp than the old mcp.
@ThokohKalongaАй бұрын
Security mbambande💪💪💪
@JohnYoweliАй бұрын
Mmmmmmmmm mcp singaluze tikunamizana guyz
@RabbeccaChitimbeАй бұрын
Nsima first DPP woyeee
@ChristopherManase-s1fАй бұрын
Zankutu zaziiii. Lero muzikanena Zama techcor college? Agalu inu, 6 six years munapanga chiyani?
@DuncanAbdulАй бұрын
Boma ilooooo!
@DoriceMagawaАй бұрын
Tilikonko 16 September ngat ikhale mawa bwanj
@IigIgfАй бұрын
Chala mmwamba ❤❤❤
@BiliatMzungudalaАй бұрын
Ili ndiye boma
@RodgersMtongaАй бұрын
DPP inalid bwino especially ya Bingu koma peter sanali bwino kweni kweni mwina panopa atha kukhala kut naye waphuzilapo kanthu ku opposition
@HorriceBandaАй бұрын
Chlienjelani akapilikoni ali mseu wa kuprison atumeni bwana Chisale akaoneko.
@MagretSimbah-v1uАй бұрын
Munthu osapota MCP mmutu mwake mulivuto lofuna achipatala.Ngati DPP siiwina ndi bwino kuvotera chipan china than MCp.