KODI MWAZIMVA NKHANI ZA LERO?ASILIKALI ACHENJEZA ONSE OMWE AKUMAPANGA IZI NDIPO AKUTI ONSE ASIYILETU

  Рет қаралды 34,430

Makosana

Makosana

Күн бұрын

Пікірлер: 40
@JohnJohn-og8rt
@JohnJohn-og8rt 18 күн бұрын
Zoona mcp ayi palibe angavote chonde UDF dpp aford utm tililimosi
@MarySinjirani
@MarySinjirani 18 күн бұрын
Kananso ku Malawi kuli asilikali nanga bwanji kusowa okasaka ndenge nyanjanso atengedwa ndiye mkumati kuli asilikali ndakayika
@ToweraGama
@ToweraGama 18 күн бұрын
Amen akapanda kumanga nyumba YEHOVA wakuyimanga ayimanga chabe, akapanda kusunga mudzi Yehova mlonda alonda chabe, salimo 127 vs 1 ndi 2.
@STUARTKASEKA-i9d
@STUARTKASEKA-i9d 17 күн бұрын
Akulephela kuteteza ma border ntchito ya home affairs ndi chani kuti asilikali ndiwo aziteteza anthu zoona nyanja akutenga tikuona
@PeterMwakihana
@PeterMwakihana 18 күн бұрын
Tanzania ikulowelela kumalo anthu anyanja koma sitinave kena lalikose kuchokela kuboma. Komaso sithawi ya training iyi koma kubandulana basi. If we really have soldiers here akuyenela kutengapo gawo.
@ShamimuBisani
@ShamimuBisani 18 күн бұрын
Zaziii munalephera kukasaka ndge ku Chikangawa chfukwa chandale zmwez mukunamiza ndani
@henryphiri6100
@henryphiri6100 18 күн бұрын
Anauzidwa kuti ampatse report after 4 hrs chifukwa anali Ali mkati kupha kupopa magazi ndi mikodzo asanakataye ndege ku chikangawa. Anapha anthu 9 agalu. Akutichita treat ngati ku Zimbabwe.
@ZainabuMahomed-xw9jg
@ZainabuMahomed-xw9jg 18 күн бұрын
Ndiye amayenera azisunga malamulo awo asilikaliwo
@ManuelMagombo-m2u
@ManuelMagombo-m2u 18 күн бұрын
Bola asilikali a Burkina Fasso
@MagieJames
@MagieJames 15 күн бұрын
Zoonadi anatenga gawo amenewa chifukwa sanapite kuchikangawa kosaka ndege
@F30-Jet
@F30-Jet 18 күн бұрын
ka introduction voice ko kobhowa bwanji. kamamveka ngat uli pansi pa bedi
@yamikanijoseph9381
@yamikanijoseph9381 18 күн бұрын
Bishop uku ndiye kulankhula kwa nzeru, kobweretsa mtendere, osati zopusa analankhula nzawo uja,
@WarriorKB-l3i
@WarriorKB-l3i 18 күн бұрын
Zopusa zake ziti? Iweo mbuzi ya mcp eti? Ndicifukwa ukulankhula dzopusa nde tikudze iwe ndi zako chikangawa kuti tikufuna black box nde nkhaniyi itha kupanda apo aaah! Tisambisana pokumwa abakha.
@HenryManda-c4i
@HenryManda-c4i 18 күн бұрын
Ndiwe kape chabe aise.. Ifetu sitikusekerera zopusa
@AlihIbrahim-s7v
@AlihIbrahim-s7v 17 күн бұрын
Koma anthu ena ovetsa chisoni kwambili,,,m'mene adafela anthu aja,,,,ena akufuna chilungamo wina mkumabakila boma zoona???anthu akufuna black box,,,chifukwa zonse zimakhala mu black box,,,,ndege safufuza popanda Black Box anyani inu
@WarriorKB-l3i
@WarriorKB-l3i 17 күн бұрын
@AlihIbrahim-s7v Good bale apapa mwalasadi nkhani ndimeneo osati idzi akuti zosintha ma unduna za ziii mmene mavuto alili mmalawi muno mpaka nduna 32 dzachani? Mmutu mwa chikangawa mulibe chilichonse ,mamina okha okha.Nkhani ya black box sitisiya kukamba mpaka chinachake chichitike dzauchisilu sitikufuna mcp yatitola kwambiri
@symoldicky
@symoldicky 16 күн бұрын
akulu inu ndi mbuzi kwabasi , kod Munthu akalankhula chilungamo nde kudzesa chisokonezi? zopusa basi kudana ndichilungamo
@MaliadWalter
@MaliadWalter 16 күн бұрын
Paja asilikali amalawi Ali ndi kachisasati nkhondo saidziwa
@MacxwellStuarts-h9r
@MacxwellStuarts-h9r 16 күн бұрын
Zina lokha loti kumalawi kuli asilikali
@ArefriednNelson
@ArefriednNelson 16 күн бұрын
Mbuzi za silikari izii mnzawo adapheda mosakhalabwino nde akukondwerera chani pamenepo mesa silikari amakwanitsa kuyimilira athu mdziko koma athuwa nde iiiiiiiiiiiiiiiiiiiiiiiiiiiiiii ?
@DanielJuwawo-s5n
@DanielJuwawo-s5n 18 күн бұрын
Achita bwino kuwachenjeza
@JuliourMussi
@JuliourMussi 18 күн бұрын
Tatulusen akuba khuku kt Malo apezekemo
@ChifundoBeston
@ChifundoBeston 18 күн бұрын
Ndichifukwa chani ukumayika mutu wankhani oti munkhanimo mulibemo zamutu omwe waikawo? Ngati uli wa DPP Pepa izi sizikuthandiza ndipo sizithandi DPP ndi amaliseche ako akumwerawo wamva?
@peterkakhome6976
@peterkakhome6976 18 күн бұрын
Asilikali anapha nawo chilima ku chikangawa.
@STUARTKASEKA-i9d
@STUARTKASEKA-i9d 17 күн бұрын
Mmene zilili anthu madiku anno alive khalidwe ulemuso unatha kamba ka ma ufulu umwe tili nawo masiku ano
@AlihIbrahim-s7v
@AlihIbrahim-s7v 17 күн бұрын
Koma kusiyana ndinkhaza zinalipo mu chipani chimodzi cha mcp,,anthu amnyngedwa kuponyedwa kung'ona,,,sibwezi enafe kulibeso,,,,odana ndi umfulu ameneyo ndi mfiti
@ChiyeNangomba
@ChiyeNangomba 17 күн бұрын
Asilikari opha silikari zawo ku Chikangawa manyaka basi
@UseniMailosi
@UseniMailosi 18 күн бұрын
Nkhuku imosi paka sakateni nanga omwe anapa chilima aja
@HalimaUka
@HalimaUka 18 күн бұрын
Za ziiiiiii takamban za nyanja
@symoldicky
@symoldicky 16 күн бұрын
zazii mmesa Nyanjayo ndi part yadziko lomwe asilikaliwo analonjeza kut adzateteza nde ukat sizugwilizana zopusa eti
@LOUISCHEN-w7u
@LOUISCHEN-w7u 17 күн бұрын
walezela uyu nsilikali wamowa uyu
@BillyKalambo-jx3vf
@BillyKalambo-jx3vf 18 күн бұрын
Asilikali ndinu olephera kale musanamizire anthu kuti akulowerera malo Anu mudalephera nokha kuteteza SKC muchikangawa
@InusuKuchisanje
@InusuKuchisanje 18 күн бұрын
Zoona
@chippakaribafox2865
@chippakaribafox2865 18 күн бұрын
Akatswili amenewa anali kuti nthawi ya chikangawa????
@AaliyaKalembo
@AaliyaKalembo 17 күн бұрын
Kodi kumalawi kuno kuli asilikali
@MaliadWalter
@MaliadWalter 16 күн бұрын
Asilikali ake ati manyakawo😂
@joegibsonzulu2599
@joegibsonzulu2599 18 күн бұрын
Kulibe asilikali kuno ayi. Omwe tili nawo ndi "andumile mwenye" basi.
@MaliadWalter
@MaliadWalter 16 күн бұрын
Kkkkkk Osatha nkhondo koma tiyeni tikamenye anthu uku basi
БАБУШКА ШАРИТ #shorts
0:16
Паша Осадчий
Рет қаралды 4,1 МЛН
Counter-Strike 2 - Новый кс. Cтарый я
13:10
Marmok
Рет қаралды 2,8 МЛН
Jaidarman TOP / Жоғары лига-2023 / Жекпе-жек 1-ТУР / 1-топ
1:30:54
Afrikaans Nuus | 19 Januarie 2025
12:34
SABC Nuus
Рет қаралды 19 М.
The Week Ahead | 12 January 2025
1:43:52
SABC News
Рет қаралды 25 М.
БАБУШКА ШАРИТ #shorts
0:16
Паша Осадчий
Рет қаралды 4,1 МЛН