MANGANYA SIZIKUMUKHUDZA OLO PANG'ONO UDINDO ONONA UNAMUCHOTSERA UMUNTHU.

  Рет қаралды 3,844

MPUNGWE-PUNGWE MW

MPUNGWE-PUNGWE MW

Күн бұрын

Пікірлер: 27
@SolomonNjolomole
@SolomonNjolomole 2 сағат бұрын
Usi ndi chilombo uyu ndipo mphuno salota RIP SKC.
@WysonChilonga
@WysonChilonga Сағат бұрын
Zoti Manganya ndi wa UTM amazidziwa yekha😢,ndipo asatinyasepo apa iiya,nthakati wachabechabe
@EsterManiya
@EsterManiya Сағат бұрын
Kkkkk bambo asikono kuteroko
@YousufuJohn
@YousufuJohn Сағат бұрын
Usi azanya manyi pa conversation ataluza chifukwa palibe uyo azamuvotele
@YousufuJohn
@YousufuJohn Сағат бұрын
Usi pantumbo pake azavota yekha ndimkazi wake
@RaphaelKatimba
@RaphaelKatimba 2 сағат бұрын
Manganya si president wa UTM ai Manganya ndi kazitape wa MCP ndipo ndi galu fisi nkhumba yeniyeni
@MusaLion-os1lx
@MusaLion-os1lx Сағат бұрын
Ndikunenetsa kut izitu akuchita ndiyeyo guys ndani yemwe anagalore kut mwana wake wamagidwa otsapitako aaaaa atsatiputsitse ife serious
@S-rr1eu
@S-rr1eu Сағат бұрын
Usi,,,, ndiwa MCP not UTM
@RiteRoderick
@RiteRoderick 2 сағат бұрын
Utsi ndioyipa zedi Koma guys let's fight strongly for our freedom
@stevenmwamadi3035
@stevenmwamadi3035 2 сағат бұрын
Usi ndi galu yamuthu ndi snake ameneyo anatengapo gawo pa khani ya dege ija koma thawi ndi nyengo ikubwera pompano muthawa kumalawi kuli kwanu pompano sikale
@RemitterFlik1130
@RemitterFlik1130 2 сағат бұрын
Kuyipa mkhope ndi mtima omwe
@BrianMamiwa-k8m
@BrianMamiwa-k8m 2 сағат бұрын
Ngati kuli fisi ndi usi ndipo onse osatila utm achenjele kwambili
@BiliatMzungudala
@BiliatMzungudala 2 сағат бұрын
Ndipo inu kod ameneyu akudabwitsatu kwambiri
@trifoniachilunda6263
@trifoniachilunda6263 2 сағат бұрын
Sitsanikoni nyimbo
@Mpungwe123
@Mpungwe123 22 минут бұрын
Takumvani tizipanga zomwezo
@OsmanChisi
@OsmanChisi 2 сағат бұрын
Utsi umunthu mulibe apa Zanu Zada mukufuna mupereketso uyu mmmmm
@mussayassin3868
@mussayassin3868 2 сағат бұрын
Usi ndi amene akumapeleka azake iyeyu ali gulu lokupha
@amosnyirenda-pl1ss
@amosnyirenda-pl1ss Сағат бұрын
kaliyati aziwe kut malamulo Alibe kuti nindani amangindwe basi bwanji akufuna kumpha usi chifukwa chani mayi oyipa uyu
@MzadziWanga
@MzadziWanga Сағат бұрын
Mwaupeza kale umboni oti amafuna kupha usi?? Mesa dzulo mmati akufuna kupha chakwera lero mwasinthaso ndekt simukudziwa chomwe mukupanga mungofuna anthu aiware zakuvuta kwa mafuta ndi commission of inquiry ija ana anjoka inu
@YousufuJohn
@YousufuJohn 4 минут бұрын
iwe galu eti iwe siwukudziwa kuti mbuzi yakoyo ndiyakupha komaso ngakhale atamanga anthu sangawinebe ku conversation palibe angamuvotele manganya ayiwale azamuvotela mkazi wake ndi ana ake wamva kapolo iwe?
@StevenKupheka-k6b
@StevenKupheka-k6b 2 сағат бұрын
Usi ndi mbuzi and galu ya munthu
@NyirendaAndrew-w8q
@NyirendaAndrew-w8q 23 минут бұрын
Manganya otsamunenapo autsi ali chabe bwino
@CassimMbalaka
@CassimMbalaka 15 минут бұрын
Mulungu salakwitsa kalikose akuwoneni pokuyikani nose wokhudxidwa pa ifa ya chilima
@wisdomsadyalunda2001
@wisdomsadyalunda2001 23 секунд бұрын
your a fool and very stupit
@wishartmalinga1882
@wishartmalinga1882 Сағат бұрын
Poor sound. Please improve on it
@Randy-er2xo
@Randy-er2xo Сағат бұрын
Kkkkkkk dirty song
@Mpungwe123
@Mpungwe123 22 минут бұрын
Takumvani bossman its a learning process
ZOMWE FREDOKISS NDI ANJAWALA AYANKHULA___25 October 2024
19:56
啊?就这么水灵灵的穿上了?
00:18
一航1
Рет қаралды 83 МЛН
Kluster Duo #настольныеигры #boardgames #игры #games #настолки #настольные_игры
00:47
CAN YOU DO THIS ?
00:23
STORROR
Рет қаралды 32 МЛН
UTHENGA OCHOKERA KU AZITSOGOLERI A UTM
19:22
MPUNGWE-PUNGWE MW
Рет қаралды 16
Patricia Kaliati wamangidwa pa mlandu wa treason
9:15
Bakili Muluzi TV
Рет қаралды 56 М.
COMRADE FRANK -TAMVANI ZENI ZENI ZOMWE AMUMANGIRA KALIATI UJA AMALAWI.
9:04
COMRADE NTANYIWA PA LIMPOPO FM -ATUMA ANYAMATA KUKANDISAKA KU LUNCHENZA
10:39
啊?就这么水灵灵的穿上了?
00:18
一航1
Рет қаралды 83 МЛН