No video

MCP yatengesedwa ndi nyamata wa ku Ntheu. Chakwera alibe mtendere wamtima

  Рет қаралды 25,770

Jay Kawere TV

Jay Kawere TV

Күн бұрын

Пікірлер: 146
@GanizaniKamvazaana
@GanizaniKamvazaana Ай бұрын
Zoona zake Zenizeni koma osadera nkhawa chaka chamawa kuvuta am from Ntcheu kwataine village koma mlungu adzatiyakha osaopa osafooka osatopa❤
@yowasschitsosa5348
@yowasschitsosa5348 Ай бұрын
@@GanizaniKamvazaana mukuenela osatopa kmaso osafooka nanga si moyo umaenda chifukwa cha vice president a chilima, moti ndimadandaula Kwambiri kut malova ngat inu tsopano muyamba kuba
@FrankSimfukwe-w1s
@FrankSimfukwe-w1s Ай бұрын
Ndipo sitikuopa izisitikungokamba chabe km sitikuopa ife tikufuna chilima wathu chomuphela ndichani atiuze chomwe anawalakwila iwowo
@austenbushiri-cx1kh
@austenbushiri-cx1kh Ай бұрын
Mawu! mawu! 🎉 big man
@Extratremendouszeus
@Extratremendouszeus Ай бұрын
Amalawi tonse timadziwa kut Chakwera anapha chilima mosogozedwa ndi Michael usi
@yowasschitsosa5348
@yowasschitsosa5348 Ай бұрын
@@Extratremendouszeus amalawi ake a ku nsipe komaso owelengeka palibe munthu ali ndi mphavu yakupha or yotembelera munthu mzake paja yesu anagonjetsa infa pokha-pokha mulungu akachivomeleza infa imabwela pamoyo wa munthu,
@Extratremendouszeus
@Extratremendouszeus Ай бұрын
@@yowasschitsosa5348 Izo ndizikhulipiliro za iwe Chikhulupiliro sagula Werenga ma verses awa ngat mumaopadi Mulungu Mark 14:48 (Yesu sanamugwire ) Mark 15:21 (Akukamupachika munthu ochokera kumunda osati yesu wanuyo) Kms mwa amalawi 100 aliwonse 99 akudziwa kut Chakwera killed chilima together with usi.ndipo Bakili Muluzi tv ananeneratu kut usi salankhula kanthu chifukwa amulonjeza u vice...nde lero azikalankhula ...zopusa basi..dziko loyendetsedwa ndi a ma dramma lingakhle dziko kapena manyaka
@EdwinHowardmkandawire
@EdwinHowardmkandawire Ай бұрын
Iweso kapolo ndege ija ankayendesa ndi chakwera?
@EdwinHowardmkandawire
@EdwinHowardmkandawire Ай бұрын
​@@yowasschitsosa5348kuswa zonene anthuwa
@Extratremendouszeus
@Extratremendouszeus Ай бұрын
@@EdwinHowardmkandawire sindilimbana ndi zifwamba za MCP...pano mwaluza mipando yonse ku Balaka,mangochi,Blantyre nd zomba..olo mmodzi owina....mesa anawatuma a Israel kuti akole ndege..pano report latulika koma sakunena,akukonza ulendonso opita kut German konko komwe kuli ofufuza...nde akukatani...iwe ndi chikangawa wakoyo are fools
@rashidadan2533
@rashidadan2533 Ай бұрын
Komanso kufatsakwina ndikopweteketsa , Kufatsakwina ndikopusanako , Amalawi ndife anthu ofatsa mopusa
@VeronicaChirwa-ct4os
@VeronicaChirwa-ct4os Ай бұрын
Zoonadi a Malawi ambiri ndi ofatsa koma kufatsa kwake kopusa. Koma ena alipo ochenjera koma chifukwa choti opusa 97% ochenjera amakanizidwa ndi opusawo kuchitapo kanthu. Mantha too much.
@SolomonNjolomole
@SolomonNjolomole Ай бұрын
100%facts brother mcp ndi zigawenga mbiri safuta lero taziona yalembedwaso ina apa.
@PIYASSFKGCHIWAYA
@PIYASSFKGCHIWAYA Ай бұрын
Ulemu wanu brother
@MeriaMasinga
@MeriaMasinga Ай бұрын
Olo Monica akuziwa kt amunanga apha chilima
@AdamYas-ec9oc
@AdamYas-ec9oc Ай бұрын
Mukunena dzona brather m c p kwake kuba ndi kupha
@AjibuTwalibu
@AjibuTwalibu Ай бұрын
Mmmm man mwalankhura zoona ok
@bamusmajawa1619
@bamusmajawa1619 Ай бұрын
Iye uja mpaka azafa akuzuzika
@yowasschitsosa5348
@yowasschitsosa5348 Ай бұрын
@@bamusmajawa1619 munamatu simulungu ameneo and palibe munthu ali ndi mphavu yotembelera mzake,
@esaMoha-dm4kj
@esaMoha-dm4kj Ай бұрын
Bg ulemu wanuw mulungu adalise inuyyo nkwamasinku osse tiutseni soona sandege bg mn ashankwela angompedwa nawosso sikut wawaw kobas skc anashita nkumupha ndi ashankwela yemwyyo mfiti yyamundu😮😢
@Martha-m6e
@Martha-m6e Ай бұрын
Ndipo zowonadi zake. Ulemu umasowa.
@MabvutoMichaelPanagona
@MabvutoMichaelPanagona Ай бұрын
Ndithu iwe wa ku ntcheu ukunena zoona inenso ndine wa ku ntcheu ndithu MCP ndiyakupha kuyambira kale mtima umatiwawa koma mulungu akudziwa zonse ndithu patenge nthawi bwanji koma adzatiyankha amalawi
@hamiltonsolomon3756
@hamiltonsolomon3756 Ай бұрын
Brother More Fire 🔥....Auza Amenewo....Nthawi zonse chilungamo chimamphweteka muona mufa nd ma BP. MCP yakumpha
@user-yv3jp3it2t
@user-yv3jp3it2t Ай бұрын
Osaopa man chakwela anapha chilima sibodzatso ayi
@RobertLuka-wy9cl
@RobertLuka-wy9cl Ай бұрын
Mau amenewo mulungu akudalisa mcp ndi yakupha auzeni ndi mbusi za anthu awa
@user-hl3st3cc4v
@user-hl3st3cc4v Ай бұрын
Komaso kuyakhula chilungamo MCP sikanawina kapanda chilima olo akamayakhula mwamatama akhala dzaka zingati osawina
@RafiqueChibwana
@RafiqueChibwana Ай бұрын
Inuyo mwalankhuladiii boss ulemu wanu
@mollymasangano473
@mollymasangano473 Ай бұрын
Zoona auzeni Amalawi wokomedwa Chiliungamo chimawawa A words without aparch mau Mau Mau Mau, anthu ena akumayakhula choncho chifukwa anatisiyawo sa abale awo.
@Mervic-vm8eo
@Mervic-vm8eo Ай бұрын
Osatopa osafooka osawopa 💪💪💪 chakwera machende Ako aise
@user-hm9nc7lz6e
@user-hm9nc7lz6e Ай бұрын
Kuyakhula kwachilungamo chakwera anapha chilima
@StevoZimba
@StevoZimba Ай бұрын
Wa Bakili Muluzi VT amanena zoona😊
@WilliamLimwalwo
@WilliamLimwalwo Ай бұрын
Zoonadi dzake, more fire,the truth will prevail 😂😂😂😂😂😂.
@JowasiMasina-fy8ji
@JowasiMasina-fy8ji Ай бұрын
Ndi chipani chakupha chimenecho Cha MCP ndikukuba ndiye chitukuko chawo cha MCP basi
@Lingstone-r3z
@Lingstone-r3z Ай бұрын
To stand on the bright side with truth and faith for all Malawian ❤
@peterlowole7841
@peterlowole7841 Ай бұрын
Malawi ife ndife amantha ausilu , big mwalankhula ngamo Amen
@KaungaYawaka
@KaungaYawaka Ай бұрын
Chakwera ndiwakupha vuto anzathu achewa kuberekana nde chimene chikumlimbisani mtima mumadya naye
@AchinaKellz
@AchinaKellz Ай бұрын
mcp tidakwilira limodzi ndi chilima zimu uwakwatha Wina ayelekeze kuyimila ku ntcheu mcp timpha timuyatsira nyumba osatiseweletsa😢
@chrisschikozera7271
@chrisschikozera7271 Ай бұрын
Zoona mcpbinapha chilima zoona chakwera akuziwa ndipo ife ku mwera tizailowerela amaona ngati amalawi ndiopusa
@ChisomoMsiska-oi2vg
@ChisomoMsiska-oi2vg Ай бұрын
Koma nkulu uyu wayankhula za nzeru kwambiri
@user-cn3gi2vf5n
@user-cn3gi2vf5n Ай бұрын
Catholic bishops are very sharp amaima pa chilungamo Mcp ndi yokupha
@mcsellahntv6896
@mcsellahntv6896 Ай бұрын
Auze aise,
@ElphinaChirwa-qk3cy
@ElphinaChirwa-qk3cy Ай бұрын
Straight talk eeeee anthu munatipweteka kwabasi imfa iyiyiyi Ndipo mabala akupweteka
@user-db3mh9wr9v
@user-db3mh9wr9v Ай бұрын
Chilungamo aise Chakwera ndiyemwe anapha Chilima chifukwa cha udindo
@MrBone-zj1wq
@MrBone-zj1wq Ай бұрын
Zitsiru zimenezo zimene zikuti zalowawa ndale,mbole zawo kwambiri
@corretabanda7685
@corretabanda7685 Ай бұрын
Walankhula bwino brother
@user-wl4nd7ic1s
@user-wl4nd7ic1s Ай бұрын
Kwambliii Mr your talking the truethhh
@user-gg9hw4oj2v
@user-gg9hw4oj2v Ай бұрын
Zoona chakwera anamupha chilima
@marthansaliwa7732
@marthansaliwa7732 Ай бұрын
Zoona zokhazoka ndithu. Mulungu Ali pampando
@JumaJuma-i9t
@JumaJuma-i9t Ай бұрын
Ndipo kumeneko ndiye kuyankhula
@UsenLashid
@UsenLashid Ай бұрын
Chakwela Tu wapanga chitukuko tisaname Ayi Koma chitukuko chake ndi cha kumaliseche Kwa azikazi ayeni osati chitukuko cha amalawi Ayi mu andiloko chakwela pamodzi ndi uyu wakuzimbabweyu usi
@user-vu4cz1mt4f
@user-vu4cz1mt4f Ай бұрын
Chakwera wakupha tonse tikuzwa
@lysonkaselema7321
@lysonkaselema7321 Ай бұрын
Ntcheu ndimaiziwa ndiimeneyi
@SandlessWakhuluma-ns1io
@SandlessWakhuluma-ns1io Ай бұрын
Mau ndiwo mweo ayakhula munthu.
@LouisAndrew-jr1yj
@LouisAndrew-jr1yj Ай бұрын
Ukavomereza kuti Yesu ndi Ambuye, udzapulumuka🙏🙏
@user-my4gr1pv8h
@user-my4gr1pv8h Ай бұрын
Tizamusinja amweneo big ngamo
@KennedyPhiri-h9h
@KennedyPhiri-h9h Ай бұрын
Chakwela achoke and ngati Pali munthu woti akuyenela kumangidwa ndi chakwela ndi nduna zake
@user-gr5zt6kw3s
@user-gr5zt6kw3s Ай бұрын
Well said bro
@AlexKaunda-ny2eg
@AlexKaunda-ny2eg Ай бұрын
Chakwera Mutu Ngati machende amkango
@FrankSimfukwe-w1s
@FrankSimfukwe-w1s Ай бұрын
Kkkkkkkkkk km
@BlessingsTembenu
@BlessingsTembenu Ай бұрын
Zoona bro,ndipo anthu awawa ndi oyipa ndiposo ineyo amandinyasa heavy ndipo moyo wanga sindifuna kumawona,ndimava kuphweteka ndipo ineyo ndikanakha nfiti tikanaphweteka ndithu
@OwamiSimeon
@OwamiSimeon Ай бұрын
😂😂😂😂 amati wina ludo kkkkkkk😅😅😅😅
@KhonzoBlose-wq7zm
@KhonzoBlose-wq7zm Ай бұрын
Mau amphavu bro MCP ndiyakupha idapha anthu ambiri
@user-xt2gu9yt9q
@user-xt2gu9yt9q Ай бұрын
Mawu oveka chakwela dzelu alive mamuna ndi wabakili muluzi tv ameneuja amaganiza hsve
@CHIWSABINYAMBOSE
@CHIWSABINYAMBOSE Ай бұрын
Kunoso ku mzimba ndife okwiya kwambiri
@ErnestChansa
@ErnestChansa Ай бұрын
Sindinu nokha akuntchewu ai even boma lakhotakota ndife okwita big pafupi ziko lose nyani chakwela mbuzi akupha
@misoMoyo
@misoMoyo Ай бұрын
Sindikuona chifukwa chopangidwira remove nkhani aliense akuona yekha Mene zinaendera Kodi chilungamo mukufuna chotani kuchita kuoneka zokha kuti anamupha mukufunanso chani Chakwera ngoipa anatiphera mngoni wathu Rip skc
@Patricklichakala
@Patricklichakala Ай бұрын
Thanksyou big
@MarcosDjussa
@MarcosDjussa Ай бұрын
Zoonad brother umakwana
@JosephChikabadwa
@JosephChikabadwa Ай бұрын
Ngakhale Mulungu Kumwambako akuwona Lingatalike bwanji Tsiku Lina Oyipayo Adzagonja Ndithu Mulungu Wathu Ndiwam'kulu Ali ndi NTHAWI YAKEEE AYANKHA M'mapemphero Athu
@LinesiKanzota-fw7sj
@LinesiKanzota-fw7sj Ай бұрын
Zowonadi ndi zowawadi chakwera ndi Muthu oyipa
@patrickmacheso5062
@patrickmacheso5062 Ай бұрын
Well spoken my brother ❤❤❤
@AliceChipeta-pc3nb
@AliceChipeta-pc3nb Ай бұрын
Chilungamo chimawawa
@ElizabethMajiga
@ElizabethMajiga Ай бұрын
Ndimwana yemwe akuziwa kuti chakwela anampha VP wake basi
@user-db3mh9wr9v
@user-db3mh9wr9v Ай бұрын
Zoona big palibenso munthu oganiza bwino angazavotere Chikangawa mcp anthu panopa ndiokwiya
@EdwinHowardmkandawire
@EdwinHowardmkandawire Ай бұрын
Inuyo chikhala mmaziwa kusaka ndege munkalekelanji kupita kusaka ndege a kapolo a anthu
@kondwamlungu8384
@kondwamlungu8384 Ай бұрын
Ukuteta yayi àuze zowona
@DONNEXKhama-bk1gy
@DONNEXKhama-bk1gy Ай бұрын
Ndipo live zoona zake tikuziwa bwino lomwe
@ErnestChansa
@ErnestChansa Ай бұрын
Zowona sikunama ai mcp ndi akupha anthu zisiru za mcp mafiti
@dumisanimoyo3152
@dumisanimoyo3152 Ай бұрын
Usawope muphwanga chilungamo chake nchakuti chilima anachita kupha a mcp ndichakwera
@EdwinHowardmkandawire
@EdwinHowardmkandawire Ай бұрын
Fotseki chikwera sangasowe ntendele ndipo mutaya nthawi
@actuarialscience2283
@actuarialscience2283 Ай бұрын
Tiphe zinyau zinayi kuti tibwenze zomwe chipani cha nyau chimachita.
@user-fm8ed7eo3i
@user-fm8ed7eo3i Ай бұрын
Mwakhwana brother uko ndiko kukamba
@LilianMbaisa
@LilianMbaisa Ай бұрын
Ndipo asabweredi
@TimexKaufa
@TimexKaufa 27 күн бұрын
Chilima adakwera mundenge ndi dzigawenga ndi chifukwa a mcp adakana kukweranao
@FrankSimfukwe-w1s
@FrankSimfukwe-w1s Ай бұрын
Ife tikudziwa bwino kt anapha chilima
@FrankAdonis-zl6qc
@FrankAdonis-zl6qc Ай бұрын
Ndukugwirizana nazo mbale zoonadi zimenezo mcp chipani chongokhalira kupha
@PartsonKamkuzi
@PartsonKamkuzi Ай бұрын
Fire
@user-ld8gb9xm7v
@user-ld8gb9xm7v Ай бұрын
Thanks brother
@MaritaBanda-p4z
@MaritaBanda-p4z Ай бұрын
amenewa akufunika azasinjidwe kumene komas kunena zona palibe wa mcp angapite ku ntcheu azikalakhula mbwelera
@FelixBoss-yn9pe
@FelixBoss-yn9pe Ай бұрын
Palibe zandale apa Koma choonadi
@isaaczuze
@isaaczuze Ай бұрын
Chakwera ndi munthu yemwe anapha chilima ....kuyipa mtima
@AiameAdamo-su1nt
@AiameAdamo-su1nt Ай бұрын
Ulemu waanu brother. Osawanyengelela a MCP ndi makape opanda ntchito.
@SimeonAbraham-u2j
@SimeonAbraham-u2j Ай бұрын
Lero mutenthedwa ndi message yoti inaperekedwa kale kale mukanakhala ozindikila a MCP bwenzi siku lomwe uthengawu inaperekedwa mutaumva
@patassonelucaszovuta3431
@patassonelucaszovuta3431 Ай бұрын
Koma olo zitalowa ndale palibe vuto chifukwa anthu adafawa ndi andale ndie sindikuona vuto
@RitaKainga
@RitaKainga Ай бұрын
Komanso ndege inagwera poyeratu eehh
@UsenLashid
@UsenLashid Ай бұрын
Zaphabvu brother
@Marymahendra
@Marymahendra Ай бұрын
That’s true chakwara killed Chilima for president and is everywhere in world know that Mcp party is not good people and l love Chilima behaviour than chakwara is to man .
@chipiesato-ut7hx
@chipiesato-ut7hx Ай бұрын
Osaopa osatopa osafooka mcp yakupha ndizoona
@user-ec4jo9cu4d
@user-ec4jo9cu4d Ай бұрын
Izi nde zoona ine okhara mchewa km imfa iyi yokha idandipweteka😭😭😭😭💔💔💔
@spargomw
@spargomw Ай бұрын
😭😭😭😭😭😭😭
@user-ww9rj2wx8d
@user-ww9rj2wx8d Ай бұрын
Zowonadi brother
@AndrewMagombo
@AndrewMagombo Ай бұрын
Zoona anthu a mcp okumpha
@AlexPhiri-in1re
@AlexPhiri-in1re Ай бұрын
Zoona bro
@moseskapelekeza8849
@moseskapelekeza8849 Ай бұрын
Kodi muli joz
@ELLENKANJERE
@ELLENKANJERE Ай бұрын
Zimawawa kwambiri ighowa ngati anali amai ake or achimwene mhu akhoza kumva motani akaona muthu akangwa pamseu anthu mosachendwa akufika pamalo ngati anali pafupi koma mmmm za chisoni
@ShentrycChinoko
@ShentrycChinoko Ай бұрын
Mudzayese ngat inuso elazi mudzayipomde
@shadreckphiri1799
@shadreckphiri1799 Ай бұрын
This is the truth
@user-do2cs8nf4b
@user-do2cs8nf4b Ай бұрын
Auzeni chilungamo afitiwo
@user-tw2zf7bj3e
@user-tw2zf7bj3e Ай бұрын
Asakuopyeze mchimwene auzeni chilungamo
@CorneliusSande
@CorneliusSande Ай бұрын
Eeeee koma Mulungu yekha adzamenya nkhondo
@gracemkandawire8769
@gracemkandawire8769 Ай бұрын
Chizaone chipande powomola
BON KALINDO WABWERANSO NDIIZI TAMVERANI 05/09/2024
16:42
LIKI-LIKI Ladies
Рет қаралды 15 М.
Чёрная ДЫРА 🕳️ | WICSUR #shorts
00:49
Бискас
Рет қаралды 7 МЛН
Люблю детей 💕💕💕🥰 #aminkavitaminka #aminokka #miminka #дети
00:24
Аминка Витаминка
Рет қаралды 1,2 МЛН
АЗАРТНИК 4 |СЕЗОН 1 Серия
40:47
Inter Production
Рет қаралды 1,1 МЛН
Мы сделали гигантские сухарики!  #большаяеда
00:44
NKHANI ZALERO KU TIMES 4 September 2024
19:35
HOT 265
Рет қаралды 17 М.
Zathu Band - Zimatere Zimatere (Chichewa) HD
7:06
ZATHU
Рет қаралды 127 М.
GWEDEGWEDE LERO PA 5 SEPTEMBER  2024 |
30:28
DZIWE TV
Рет қаралды 6 М.
A MOSES KUNKUYU KU PROGRAM YA KULINJI
39:13
HOT 265
Рет қаралды 17 М.
Malawi anachuka ku DRC Kamba Silikali ameneyo koma MCP yamupha
5:09
ACHAKWERA KU DOWA PA MTENGO WANTHENGA 🤔🤔🤔
17:04
HOT 265
Рет қаралды 61 М.
Чёрная ДЫРА 🕳️ | WICSUR #shorts
00:49
Бискас
Рет қаралды 7 МЛН