Lululuuuuu Moto Moto moto kuti buuuuu ntchito ndiyosayamba chifukwa ndikuona mbali inayi danken ndi achisime Pali kukhulana mbali inayi chisime ndi nkadzi wake Pali kufunsana mbali inayi padera kubwalo ndi namoyo palibenso xoonoera macomedy akunja mfumu nkadzi tirinayo buuuuuuu ❤❤❤❤❤. Nankha kubwera kwa masamba pakhomo lamfumu zitha bwanji ? Nankha giring'anthe kokatenga Maninjala nankha farai mankhwala uyiwalisa kokatenga Maninjala anapedza?
@kaiimbansofwa91545 ай бұрын
I would love to have the songs in this drama. Where and how can i access them.
@BethsiderTavares-ug4sv5 ай бұрын
I watch this soap because if the Angolan therapeutic drums. Very soothing and calming in a way. African drums beats rhythm is really connected and the same.
@gilbertkumlinde-id9nc5 ай бұрын
Frora suya and the whole team, great work!!!
@AbdullahSaeed-e7z5 ай бұрын
Padela my guy.... Ati simunaoneko mzungu 😂😂😂
@bilalisipikini80615 ай бұрын
I'm first view and like ❤🎉
@JamesJalas-bb1xk5 ай бұрын
Mfumukaz ndi giling'ande mumakwana❤ pitilizani mumatinvesa phalombe kuno ku Capetown
@maliyusuf46295 ай бұрын
Padela musitheko ka t shirt next mfumukazi aaaa😅
@OliveaMapanga5 ай бұрын
Apadela banja lakoma kwambili mwanva ,zoti nsima ispa ndakaika 😂😂😂😂😂
@Mahirublackchimzy5 ай бұрын
Ndikubwela konko next year wanna be part of this team, watching from cape town 😂😂😂😂😂 the original Pangolin
@pybenmbewe84625 ай бұрын
Very interesting comedy 😂😂😂 keep it up guys 👍
@KumbukaniChalunda5 ай бұрын
Izo ndi za pa mtundu wanu 😂😂😂😂😂 wandipangira chiyani iwe 😂😂😂😂baibulo makati😂😂😂😂😂
@CollinsLingu5 ай бұрын
😂😂😂 mwachidule I have got not money Mr pangolin original kkkkkkkk