Michael Usi - Anayenda chothawa kuopa kumenyedwa ( zambili wafotokoza yekha mu video iyi )

  Рет қаралды 12,426

Malawi Top Talent

Malawi Top Talent

Күн бұрын

Michael Usi - Anayenda chothawa kuopa kumenyedwa ( zambili wafotokoza yekha mu video iyi )
Make sure to like, share, and subscribe so you don't miss any of the exciting new content coming soon! Comment below on what you think about the changes.
Subscribe / @malawitoptalent
Follow me on Instagram: www.instagram....
Follow me on Facebook: / malawitoptalent
Chris II 👇
Subscribehttps:
/ @officialchrisii
Follow me on Instagram: www.instagram....
Follow me on Facebook: / officialchrisii
#Malawitoptalent #ChrsII #MichaelUsi

Пікірлер: 25
@allahslave7177
@allahslave7177 5 сағат бұрын
Akaka vuto kamazimva nzeru kwambiri ndinso kamaziona kuchenjera , , , , , ,ichi ndi mwq china chifukwa chomwe anthu ambiri akunyasidwa naye especially awo ali ndi nzeru , , , ,, komanso at the same time akuluwa ndi andale zoopsa zedi atha kukupha awa !!!!
@AndersonBishop-i2t
@AndersonBishop-i2t 2 сағат бұрын
Ndiposo Michael ussi ali ndi chipani chake wodya zake alibe mulandu ndie asakunamizeni kuti ndi wa UTM 😂😂😂😂
@FilbertKomba-fi2nl
@FilbertKomba-fi2nl 49 минут бұрын
Zabodza iziii musakulupilile amalawi chonde
@Edson-sj8vn
@Edson-sj8vn 8 сағат бұрын
Pepani bwana muzifunse nokha kut zimenezi inunokha chifukwa chan?
@MayamikoYMsusa
@MayamikoYMsusa 27 минут бұрын
Anthu::ndi asatana:::munthu osachita manyazi kunama bodza::ndrama mumatenga kuboma gati ndani::bodza lankhunkhuniza
@RudoChirambo-hy2jz
@RudoChirambo-hy2jz 31 минут бұрын
Uyu Siwa UTM
@MayamikoYMsusa
@MayamikoYMsusa 31 минут бұрын
Bodza ilo::sanakamumenya
@vinceynyone6693
@vinceynyone6693 8 сағат бұрын
Apaapa UTM inabaiza posankha kaManganya as VP
@wisdomsadyalunda2001
@wisdomsadyalunda2001 5 сағат бұрын
tambwali uyu asakutayiseni nthawi
@MeckwellGhambi-q5n
@MeckwellGhambi-q5n 16 сағат бұрын
wamisala uyu 😂😂
@ErickTym-u2m
@ErickTym-u2m 20 сағат бұрын
Sikuti zatha akumenya ndipo umenyedwadi sunati
@RabeccaMwikho-f9h
@RabeccaMwikho-f9h 18 сағат бұрын
Ndipo agazidwadi angodekha
@GraceKondowe-sp9yz
@GraceKondowe-sp9yz 17 сағат бұрын
Kkkk apondedwe bas
@RabeccaMwikho-f9h
@RabeccaMwikho-f9h 18 сағат бұрын
Dekhan bwana mupondedwadi😁😁😁🙌
@Jassie-x1n
@Jassie-x1n 4 сағат бұрын
Kkkkk kma adhaaaa
@MtnhtriKid
@MtnhtriKid 7 сағат бұрын
Zovuta boss
@ElsaMalunga
@ElsaMalunga 16 сағат бұрын
Ukhaula uva kuwawa wava utiuze bari uli iweyo wanva
@VincentChikopa-z6c
@VincentChikopa-z6c 6 сағат бұрын
Kkkkkkk ukuopa uyu
@giftlisimba6628
@giftlisimba6628 5 сағат бұрын
Koma nde anamasukatu
@WinstonNyadaufe-d1o
@WinstonNyadaufe-d1o 17 сағат бұрын
Uzitenge bwino akupondadi anthu Ali ndi mkwiyo
@andreabanda7838
@andreabanda7838 36 минут бұрын
😅za ma dramma izi. Don’t waste ur time Mr reporter.
@S-rr1eu
@S-rr1eu 17 сағат бұрын
😂😂😂😂😂😂 sorry bwana
@mphatsomonjeza4371
@mphatsomonjeza4371 17 сағат бұрын
🤣🤣🤣🤣🤣
@vinceynyone6693
@vinceynyone6693 8 сағат бұрын
This is guy is empty backet
@ImraanYaseen25
@ImraanYaseen25 Сағат бұрын
@@vinceynyone6693 I knew kut you hate the truth
Michael Usi - Wayankha zodabwisa atafunsidwa za Saulos Chilima
10:03
Malawi Top Talent
Рет қаралды 7 М.
Amazing remote control#devil  #lilith #funny #shorts
00:30
Devil Lilith
Рет қаралды 9 МЛН
1, 2, 3, 4, 5, 6, 7, 8, 9 🙈⚽️
00:46
Celine Dept
Рет қаралды 59 МЛН
JB ali ndi plan yoti APHE MUNTHU ( apapa nkhondo yayambika )
22:58
Malawi Top Talent
Рет қаралды 9 М.
Utumiki wa a Twaibu - Kufotokoza zochitika pa 6 NOVEMBER 2024
1:08:21
Living for Christ - Malawi
Рет қаралды 232
mota yotaura paBudiriro
15:36
Drewmas Media
Рет қаралды 929 М.
MUIMBI HOSIAH CHIPANGA MUDARE RAMAMBO MUTASA VS LEON MATESVA  KARANGANDA TV KUTORWA KWEMUNDA
18:01