Misomali Ya Six Inches Yothana Ndi Zipani Zotsutsa - Bon Kalindo

  Рет қаралды 19,554

Nyasa VoiceBox

Nyasa VoiceBox

Ай бұрын

On Nyasa VoiceBox, Bon Kalindo says the biggest threat to MCP in 2025 is Professor Athur Peter Mutharika.
Pa Nyasa VoiceBox, Bon Kalindo wati yemwe akuwopseza kwambiri MCP mu 2025 ndi Professor Athur Peter Mutharika.

Пікірлер: 76
@JuliusChipondaEphraim
@JuliusChipondaEphraim Ай бұрын
Katundu uyi ndi wachilungamo bas amangong'alura bas that's why I like him
@ChristopherMadulira
@ChristopherMadulira 9 сағат бұрын
Thanks again
@marryphili5419
@marryphili5419 29 күн бұрын
Koma anthu enawa akamayakhura akukhara ngati iwowo mavuto alibe mwina chakwera ndi bamboo awo
@MaxwellKawuwa
@MaxwellKawuwa 28 күн бұрын
Bon kalindooooo! Munthu wankulu.
@charleslimbani8590
@charleslimbani8590 Ай бұрын
Address upite ku south Africa ukaone ubwino wa address pa Malo pamene ukukhara kuti ndi yofunika bwanji,, musaputsitse anthu kalindooo......pomwe ndimakhara ineyo Pali address ndipo mtakupatsa undipeza mosavuta olo utakhara kuti ukugwiritsa ntchito phone yako opanda kufunsa munthu aliyense undipeza ....koma kupepera kwanuko boma pamene likukhazikitsa zinthu zofuna kupindulira a Malawi mukuona ndale bas ....ofoira ndi a Malawi amene amatenga zoyankhura za kalindo nkumaona ngati zofunika kwambiri....
@DeveliousMasinja
@DeveliousMasinja Ай бұрын
Umbulitu bas 😂😂😂😂
@rasulmaulidi2224
@rasulmaulidi2224 Ай бұрын
iwe nawe khala chete what do you know about address?? wa MCP galu iwe
@charleslimbani8590
@charleslimbani8590 Ай бұрын
@@rasulmaulidi2224 komatu ndiye mukhauladi chifukwa zikuoneka kuti chimene mmachifuna simuchiziwa komanso boma silimagonjeratu munthu limapanga zomwe likufuna pa nthawi imeneyo
@rasulmaulidi2224
@rasulmaulidi2224 Ай бұрын
Ulendo uno ligonjatu ukuganiza kuti amalawife ndizitsilu??
@user-yj5xv4cy8x
@user-yj5xv4cy8x 27 күн бұрын
Nanyongo wamako
@uchizJoelMumba
@uchizJoelMumba Ай бұрын
Akalindo please tatopa ndikubva mabodza kodi kupatula kunyoza mcp Palibe khani Zina mdziko muno zoti mungawaize anthu abale?
@mbwindinga
@mbwindinga Ай бұрын
Opusa ndiwe umasegula ma audio ndikumavela
@JamesChimera-hw1nv
@JamesChimera-hw1nv Ай бұрын
Palibe kouluka kamene kasanaterepo uyu atela posachedwapa mutharika simunthu omuopa ayi aonanso ameneyu
@JamesChimera-hw1nv
@JamesChimera-hw1nv Ай бұрын
Yakuvuta imèneyo mukadzaluza mufunamuzidzanena kuti mwaberedwa ayi abwana ndi mmadzi mukulembamo
@homeremedys3748
@homeremedys3748 Ай бұрын
Komatu simutop akalindo ndi ma audio? Zatopetsatu izi
@mbwindinga
@mbwindinga Ай бұрын
Opusa ndiwe umasegula ma audio ndikumavela
@user-pl2lj6mh1z
@user-pl2lj6mh1z Ай бұрын
My vote apm
@PiusChawinga
@PiusChawinga Ай бұрын
Akamatseka kalindo pamawawatu
@user-gs7wc3nx3q
@user-gs7wc3nx3q 27 күн бұрын
Iweso boni ukuchemerara apa koma akawinaa Dpp sikuzakharasokusitha ayi zinthu zizangokwerera.basi bolani bushiri akugwawa.chimanga
@Donnex-gn2sf
@Donnex-gn2sf Ай бұрын
Awa chamba chiwapweteka akuwona ngati chakwera angawapase ndalama yosayigwirira ntchito pitani Kwa Peter konko
@HussenSadiq-ot7fm
@HussenSadiq-ot7fm Ай бұрын
Boni kalindo ndi muthwakulu wulemuwanu enawa ndiavumbwe
@charleslimbani8590
@charleslimbani8590 Ай бұрын
Komatu ndale zimene mukusewera a kalindo nzobwezeretsa ziko la Malawi pambuyo......mmalo moti mufufuze njira zoti ziziwapindulira achinyamata ku Malawi mukuwauza zinthu zoti zikakhara mmitu mwawo sizingasinthe kanthu kwa mmalawi oganizaa booo......awuzeni a Malawi zaphindu osati zopoira zimene mmayankhura pa page yanuyiii....Peter Author Munthalika a Malawi anathana nawo kaleee......mu 2019...panopa tawauzeni anthu azichita pa nthawi ino pamene nyengo zikavuta ku Malawi pamene mvura ikuvuta a Malawi apange bwanji.....osati zandale zimene mmayankhura apaaa anthutu samadyaa ndaleee
@user-ez1kc7zp9m
@user-ez1kc7zp9m Ай бұрын
Inu ndi katundu Mr kalindo,APM my vote.mumatiimilira
@Donnex-gn2sf
@Donnex-gn2sf Ай бұрын
Akuba ndi a DPP chifukwa chake chinatuluka mboma mantha bwanji ma cadet
@user-fg5he5xk1r
@user-fg5he5xk1r Ай бұрын
Zoika ma address zinayamba kale kale aaahh tiyeni tizikhala serious
@MphasoChikaonda
@MphasoChikaonda 29 күн бұрын
Inu simunthu othandiza inu kwalimba uta adyera
@user-jc7zq1zr7e
@user-jc7zq1zr7e Ай бұрын
Nkhani ya ma Address yo nde mwapala
@MaritaAubrey
@MaritaAubrey 27 күн бұрын
Aitenga Ku 4 billion anaba Boma lero ukulankhula mokweza kuteteza ndalama zomwe anatibera Malawi Mutu wako ukugwira Ufilu ukumenyerawo ndi UTI
@user-lk8kj9zv6x
@user-lk8kj9zv6x Ай бұрын
Pangolin pangolin wathu wathu pitilizan kutiimilan
@user-vh9uk1jy7w
@user-vh9uk1jy7w Ай бұрын
Kkkkkkk APM my vote ❤❤❤❤
@EvanceMponda
@EvanceMponda Ай бұрын
Koma ojiya ulere mwachulukadi eeee!!! Baasi nonse pamatako panu pamatentha mukangomva APM, mufunse Joyce Banda anayesera njira zambiri kuti athane ndi APM koma zinavuta so let's wait and see.
@user-mb4tc2dx1p
@user-mb4tc2dx1p 18 күн бұрын
Katundu kkkk
@user-fg5he5xk1r
@user-fg5he5xk1r Ай бұрын
Osangobwerera ku DPP bwanji
@mamulemathekga
@mamulemathekga Ай бұрын
❤❤❤❤❤mtimakunya dilani bon kalindo ❤❤
@kphoneunlockservice7266
@kphoneunlockservice7266 Ай бұрын
Mumantha mr born kalindo ndipo timakunyadilani
@WilsonLimited-fh1mz
@WilsonLimited-fh1mz Ай бұрын
The Dc❤❤❤❤❤❤
@HappyKambani
@HappyKambani Ай бұрын
Ndiye zimenezo tiziva ife kkkkk
@giftsululu4274
@giftsululu4274 Ай бұрын
Chimwamuna chakukamwa ngat nkhoswe nde iwe kalindo Mcp inabwera kuzayala mphasa
@user-ec3xh4pc6t
@user-ec3xh4pc6t Ай бұрын
❤❤❤
@jumbradoone4164
@jumbradoone4164 Ай бұрын
The DC--- Chimandivetsa kukoma.
@TonicBeza
@TonicBeza Ай бұрын
Imilani u MP kwanuko anthu akuvoteleni as munthu wabwino 😅
@MikeMalinga-xx8ys
@MikeMalinga-xx8ys Ай бұрын
MR limbani.. inu mukuona kuti ndale zakumalawi zizatheka?? Kalindo sakulakwika.. APA zinthu zionongeke basi.. CHAKWELA ndi nzake CHIRIMA.. awononga zikoli Tien ifenso ayini ake tiliononge..basi afiti awiri awa tilibe nao ntchito Bola APM Yemweo
@richardbanda9997
@richardbanda9997 Ай бұрын
Kawawa chakwera chirichonse Lazaro chakwera kkkkkkk. Inu ndi madala Booooon
@GaletaMakosa
@GaletaMakosa Ай бұрын
Munthuyitu akunena zoona
@TonicBeza
@TonicBeza Ай бұрын
Oloitawina dpp inuyo simzaona udindi chifukwa ndinu mbuli kwambiri
@user-sm4vo2uo7g
@user-sm4vo2uo7g Ай бұрын
The dc mwana oopya kwambiri
@user-fp5qn5ci2v
@user-fp5qn5ci2v Ай бұрын
Nawe ngati umasowa zonena uzingokhala chete
@user-zk7jw9up6m
@user-zk7jw9up6m Ай бұрын
Opposition chenjelani
@JohnConar-kq4hi
@JohnConar-kq4hi Ай бұрын
The DDDDDDDDDDDDDCCCCCCCCCCCCCCC😂😂😂😂😂
@henryhenry6632
@henryhenry6632 Ай бұрын
Kodi iwe napanyelo peter munthalika akupatsa ndalama zingati, pamtumbo panu nonse alhomwe dzi anthu dzothawa nkhondo ku Mozambique
@andrewmandawalaphirithepillar
@andrewmandawalaphirithepillar Ай бұрын
Achitsiru inu
@GiftKamwaza-tt2tr
@GiftKamwaza-tt2tr Ай бұрын
Iwe unachoka kut
@yusufjab786
@yusufjab786 Ай бұрын
😂😂😂
@user-gj4li2gc8o
@user-gj4li2gc8o Ай бұрын
Iwe bon kalindo Kodi ndiwe wowopsa kwambiri kwen kwen Kwa ndani chitsiru iwe mwina ku alomwe anzako
@mbwindinga
@mbwindinga Ай бұрын
Opusa ndiwe umasegula ma audio ndikumavela
@GiftKamwaza-tt2tr
@GiftKamwaza-tt2tr Ай бұрын
Ndi ufulu wake kuyakhula zakukhosi kwake iwenso uli nd ufulu
@user-sr5es5kc1m
@user-sr5es5kc1m 29 күн бұрын
Mayazi bon kalindo ndiwakhulu ..
@ChisomoChikafa-dd3sj
@ChisomoChikafa-dd3sj Ай бұрын
Peter mutharika ndi munthu so oti chakwera angamuope? Nkhalamba osaipumitsa bwanji idzigona ku Pege house ko.
@JafferTiles-hp4mu
@JafferTiles-hp4mu Ай бұрын
Tikudziwa kuti nyau wakoyo akuopadi APM Zaka is just a number koma tikufuna mnzeru zothandizira amalawi,tsekula masowo osakhale ngati wakhanda
@mellipherjohn7158
@mellipherjohn7158 Ай бұрын
DC wen wen samaopa kumenya kugwesa yaa
@DavidJackson-ox4xm
@DavidJackson-ox4xm Ай бұрын
The DCS umakwana
@WilsonLimited-fh1mz
@WilsonLimited-fh1mz Ай бұрын
Magazi magazi kukubweraku basi kuphana kuphana
@AleksaWilliams-qc6cn
@AleksaWilliams-qc6cn Ай бұрын
Dc❤❤❤❤❤❤❤ 4everq
@user-pt8wb4vw6r
@user-pt8wb4vw6r Ай бұрын
Kambwe akuti bwanji ngati sanauwe sakuva bwino sagona tulo mcp kaindo kambwe kapolo wadpp chisilu
@osmanjack4203
@osmanjack4203 Ай бұрын
Forming now is just wasting time
@AnaffSayamika-uh6vg
@AnaffSayamika-uh6vg Ай бұрын
Chakwela 🏌️‍♂️🏌️‍♂️
@user-vl8uw8mc3u
@user-vl8uw8mc3u Ай бұрын
Apm boma.Dpp 2025 bomaaaaaaaa
@user-eh1mg3ww6d
@user-eh1mg3ww6d Ай бұрын
Mulungu si Lazaro
@user-gj4li2gc8o
@user-gj4li2gc8o Ай бұрын
Bon now u r boring us
@tasmania527
@tasmania527 Ай бұрын
Amuope Peter Mutharika wongakhalira ma 35% kapena 38% pachisankho? Kkkkk. Koma Kalindo wapengadi ndipo akusowa zochita ndithu. Mutharika tinathana naye kale, nanji kumpoto ndi pakati nde ayi. Muzimuchemelera kwanu komweko. Masiko ano kulibe za tippex kuti akuthandizani. Have you heard Chakwera talk about Mutharika? The answer is NO. Chakwera sakukamba za Mutharika chifukwa akudziwa kuti ndi munthu wosaopeka pachisankho, adzamutibula mwa easy. So, all this phokoso kapena vyongo from people like you Kalindo and your cohorts, are a worst of time. MCP and Chakwera are here to stay. Ndipo iwe Kalindo,uzafuna kuthawa mdziko Chakwera atawinanso-I can see that happening kkkkkkk, ndakulasa!
@user-pt8wb4vw6r
@user-pt8wb4vw6r Ай бұрын
Galu ya alomwe
@FosterChakanga
@FosterChakanga Ай бұрын
Chakwela eti😅😅😅😅
@johnkambala692
@johnkambala692 29 күн бұрын
Nonsence
@user-cp8rz3qs8l
@user-cp8rz3qs8l Ай бұрын
No matter what God knows,He will choose himself to be a president of our nation ❤ pick up sir
@user-gj4li2gc8o
@user-gj4li2gc8o Ай бұрын
Mulila alomwe mpaka kale simuzalamulilaso zikoli
@rasulmaulidi2224
@rasulmaulidi2224 Ай бұрын
tiona
A Malawi Lyton Mangochi Musamukhulupilileso - Bon Kalindo
19:43
Nyasa VoiceBox
Рет қаралды 7 М.
[Vowel]물고기는 물에서 살아야 해🐟🤣Fish have to live in the water #funny
00:53
Miracle Doctor Saves Blind Girl ❤️
00:59
Alan Chikin Chow
Рет қаралды 25 МЛН
Mwana Mbuu Make Mbuu - Bon Kalindo
15:16
Nyasa VoiceBox
Рет қаралды 4,3 М.
SABC News Election Coverage | 29 May 2024
SABC News
Рет қаралды 2,3 М.
Abwana Asakhale Idle Atipange Accomodate - MCP Youth
7:49
Nyasa VoiceBox
Рет қаралды 1,4 М.
Mzika Yokhudzidwa Kudandaula Ma Passport
15:49
Nyasa VoiceBox
Рет қаралды 4,3 М.
Mumanga Anthu Angati? - Samuel Lwara
13:34
Nyasa VoiceBox
Рет қаралды 8 М.
Nelson Chamisa Gives SADC  Deadline , Or He Will Be The Answer..
4:53