MOSES KUNKUYU MUTU SUKUKOKA UKU KWANUNKHA UTSI

  Рет қаралды 48,099

Mpungwe-Pungwe mw

Mpungwe-Pungwe mw

Күн бұрын

Пікірлер: 96
@user-iv6iw1ck8s
@user-iv6iw1ck8s Ай бұрын
Times 360 it's my best, Brian Banda and your Team pitilizani kutidziwitsa ndi kutivetsa kukoma, Brian Stanley Nowa, Capetown # from Monkey Bay chantulo
@gradsonmayira9336
@gradsonmayira9336 Ай бұрын
Brian ntchito muyigwira🔥🔥
@BrianMaganga
@BrianMaganga Ай бұрын
Mai chindevu mumakwana mwati Olira alile mwandisangalatsa
@LenoMvula
@LenoMvula Ай бұрын
Times mmatha mmatiimilira kuno ku malawi nice job
@user-um2es1yp5y
@user-um2es1yp5y Ай бұрын
Wonder chipongwe mzako akwatire 😅😅😅😅
@EllinaBitto
@EllinaBitto Ай бұрын
Watching live fro RSA😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂
@PortiaMhlambi-y4g
@PortiaMhlambi-y4g Ай бұрын
Brian Banda and ur team mumakwana
@annembepula
@annembepula Ай бұрын
Omse okupha sadutsa munali buzy kupha,kumanga amzanu kuophyeza anthu muziwona zangoyambapo 2025 mulila munanyanyanya mmayesa mzamuyaya
@simonejose8925
@simonejose8925 Ай бұрын
KUCHOKERS KUMOZAMBIKI A FELIX CATONHEZA TEMBO NSANJE SOUTH CONSITUENCY NSAMBA POLING CENTER PAMWAMBA A CHAKWERA 365TIMES
@JafaliAkimu-ll1bf
@JafaliAkimu-ll1bf Ай бұрын
zigawenga za mcp pamenepo manyazi bwaa BICC chitukuko chandan inu 5yrs chitukuko chanu kupha mr chikangawa ndi umbava
@Martha-m6e
@Martha-m6e Ай бұрын
Times mumandipangitsa ngati ndili komweko ❤❤❤
@mphatsosadiki4983
@mphatsosadiki4983 Ай бұрын
Wamenya campaign yomwaza chuma chochuluka ndiye aluzeso eeeehhh timva ena atamwalira ndima BP sure
@Eric-gb9ms
@Eric-gb9ms Ай бұрын
😂😂😂😂😂😂
@user-ko6kp7jl4d
@user-ko6kp7jl4d Ай бұрын
Wishing mcp.all.the best.choose patriotic leaders please!!!
@user-ij1yz4ex2v
@user-ij1yz4ex2v Ай бұрын
Eeee koma Brian ndi wonder ayi ndithu nkhawa zomaopa chikangawa munapachika
@user-le9su3mt7r
@user-le9su3mt7r 24 күн бұрын
Zisilu mcp kupha anthu apule chikangawa party
@TimothyKabumbuKendrix
@TimothyKabumbuKendrix Ай бұрын
Mr Brian Banda zabwino zonse ndi timu yanu kumeneko, ndine Hendrix Timothy kuno ku Botswana
@user-ko6kp7jl4d
@user-ko6kp7jl4d Ай бұрын
Well organised,convention kuyipasa moto viva mcp😮😮😅
@munashemoyo4190
@munashemoyo4190 Ай бұрын
😂😂😂😂😂 kumkuyu wandiwaza zed ndinapemphera kut usawine ai 😂😂😂😂😂
@chitanibenito1109
@chitanibenito1109 Ай бұрын
Onse okupha sakudusa kkkkkk
@MadalitsoGama
@MadalitsoGama Ай бұрын
Zoledzera izi
@RichmanIssah
@RichmanIssah Ай бұрын
😂ine Koma mayi chindevu😂
@RichardChirwa-em6qj
@RichardChirwa-em6qj Ай бұрын
Agaluwo asakozele makoma kumeneko paja ndi khalidwe lawo lowononga
@BrianMaganga
@BrianMaganga Ай бұрын
Wina athawà
@simonejose8925
@simonejose8925 Ай бұрын
ABALE ANGA PANGANI CHILONGAMO POPANDA CHIWAWA DZIKO LOWOPA MLUNGU YEKHA NDIWAMKULU MLUNGU ALANGE OPANGA ZOIPA NAWONSO APANGE
@CassimCawanga
@CassimCawanga Ай бұрын
Best television n plograms in malawi
@MichaelMbona-ch2kc
@MichaelMbona-ch2kc 29 күн бұрын
Chikangawa aut
@samdiverson9733
@samdiverson9733 Ай бұрын
Time group machine machine ❤
@ConeriasPhiri
@ConeriasPhiri Ай бұрын
Times 360 mumatiimilira mumativesa kukoma zukachitika tivera kwa inu
@MandalaChaona
@MandalaChaona Ай бұрын
" Pakuti Malamulo a Dziko lino amalora, choncho dzina langa likakatulukanso Ku Ballot, ine mkayimanso" Mr Lazarus Macathy Chikangawa ndinu munayankhula mawu amenewa pamaso pa yemwe munasayinira naye mgwirizano . Tulusani za kafukufuku wa ngozi ku Chikangawa simukutulusa. Pali ??????? Munthu woyipa iwe, M'busa okuba ndi okupha. God Will judge you evil man 👹🔨⛏️⚒️🔨👹. Lero zisangalala koma Amalawi sangayiwale Kuti unapha kufuna zonse zikhale zako.
@honourablebanda1961
@honourablebanda1961 Ай бұрын
Times 360 is the best. Allan Banda pritoria(RSA) #ing'aluleni azibambo
@johnkatumbu6846
@johnkatumbu6846 Ай бұрын
Waitchela kale mwati kuluyo?🤣
@simonejose8925
@simonejose8925 Ай бұрын
GWIRANI NTCHITO A TMS
@BlessingsSeleman
@BlessingsSeleman Ай бұрын
Kod brian unayamba mwazifusa chifukwa chomwe asilikali Ena mwati safuna kuti camera yaonese
@DanielKatengeza
@DanielKatengeza Ай бұрын
Times ilengezenso kuti Brian Banda president wa Malawi nzakoyo akhale Vice President I think dzikoli liyenda bwino popanda corruption
@SelinaGamaliyere-q8v
@SelinaGamaliyere-q8v Ай бұрын
Onse omwe anapha chilima asawine anthu oyipa
@user-hl3st3cc4v
@user-hl3st3cc4v Ай бұрын
Ubwino wake zomvota wochewa wokha wokha ndemukaluza muphanaso nokha nokha ma pb muzikomoka nawo zindalama mumamwaza zija
@pauljosephmakaula6835
@pauljosephmakaula6835 Ай бұрын
Katundu Vitumbiko Mumba all the best...new political dimensions
@FredPondamwala
@FredPondamwala Ай бұрын
Vituuuuu
@SelemanSimoni
@SelemanSimoni Ай бұрын
Thomas chibade
@ChifundoNinje
@ChifundoNinje Ай бұрын
Eeeee km times mukuigwila tchito yopambana
@user-ul1fb4yn5o
@user-ul1fb4yn5o Ай бұрын
Times team mumakwanisa
@isaacgmc
@isaacgmc Ай бұрын
Koma amalawi mukadali kuivotela MCP mmmmmm😂😂😂😂
@user-kh4qp1ji1i
@user-kh4qp1ji1i Ай бұрын
Tea sitidya Brian 😂 timamwa!
@TriceGulani
@TriceGulani Ай бұрын
Kkkkkkkkkkkk zavuta achimwene amosesi
@CatherineKamsare-cy3yo
@CatherineKamsare-cy3yo Ай бұрын
Kwachema🤣🤣🤣🤣
@user-ww9rj2wx8d
@user-ww9rj2wx8d Ай бұрын
Bolani asamupheso Brian Banda mtola nkhani mbambande
@KingsleySymon
@KingsleySymon Ай бұрын
Nanga Nanu mtentha ndevuyo bwanj???? kkkkkkk am Kingsley Symon kusalima
@EnerstBanda-m4s
@EnerstBanda-m4s Ай бұрын
President sanalakhule bwino sungadzudzule opeleka ndalama tsiku lovota ai pomwe Anthu ataononga kale ndalama zawo akanawauza nthawi yomwe amapanga kampeni kuti asagwiritse ntchito ndalama komaso akanauza omwe amaletsa enakuti asaime nawo chifukwa sanakhale mu chipani zaka ziwiri izi zapangitsa atidye nawo mong Dausi, Brown Mpinganjira,Uladi Mussa ndi Ken nsonda kuti asapeze nawo mwai opikisana nawo zomwe President akanatha kuzikhoza before not tsiku la master mansakho kumenekuku wapangira kampeni ena wichs not good
@zacchaeusbvumbwe391
@zacchaeusbvumbwe391 Ай бұрын
Ntchito mwayigwira
@RichardChirwa-em6qj
@RichardChirwa-em6qj Ай бұрын
Mkasa paja ankati sazatamandanso wa ndale waywala cruise 5 pa zodiac ndi joab, yedye
@NewtonSikwese
@NewtonSikwese Ай бұрын
Koma kuyakhura chilungamo ndongotsolo lake likuyenda bwino koma mapeto ake Akala bwino
@MaggieKaufa
@MaggieKaufa Ай бұрын
Koma kwachematu😅
@andiwochishadreck3753
@andiwochishadreck3753 Ай бұрын
Ndalama zakuba zabwerera kwawo
@CatherineMakina-d5o
@CatherineMakina-d5o Ай бұрын
Uncle b
@LikangaManuel-sk8yp
@LikangaManuel-sk8yp Ай бұрын
Achewa okha okha kunva kamwamo ochewa weni weni 😂😂😂
@SolomonBewula
@SolomonBewula Ай бұрын
Kunkuyu asowe
@annembepula
@annembepula Ай бұрын
Komatu mkasa dyela uyu kwa Dad uli nkomko ukunsi eeeee
@HenryGoba-m7q
@HenryGoba-m7q Ай бұрын
Anthu akuvotela zigawenga zachilendo ziphe manganyaa
@user-le9su3mt7r
@user-le9su3mt7r 24 күн бұрын
Kkkk yunda sikalioti
@whatsonbanda4277
@whatsonbanda4277 Ай бұрын
Mcp chipani Cha mtendele.
@EmmaMbewe-vg4td
@EmmaMbewe-vg4td Ай бұрын
Onetsetsani kuti Mkaka asalowenso
@courageouslondo1986
@courageouslondo1986 Ай бұрын
Mumatha mabwana
@RichardChirwa-em6qj
@RichardChirwa-em6qj Ай бұрын
Mizimu anaononga ku chikangawa iwakanthe ndithu anthu akuphawo
@NedsonJosaya-pn1te
@NedsonJosaya-pn1te Ай бұрын
Mwayedzeka kale?
@ZaithwaMatchado
@ZaithwaMatchado Ай бұрын
Kukuyu 😂😂😂😂
@GiftPaulBrownBrown
@GiftPaulBrownBrown Ай бұрын
Kwachema ku LL ine Gift Paul Brown from Mozambique
@user-zq3uf5bc8v
@user-zq3uf5bc8v Ай бұрын
Issa manyaka ife tikulira biyeni wathu chauta Ave mapemphero amalawi kuti tidzadziwe chilungamo pokhapokha mcp itagwa muboma kuno ku katonga
@RuthChilobwe
@RuthChilobwe Ай бұрын
Kkkk Amwe tea wa poison ndi zakudya za poison wa Achakwera..anthuwo asadye chakwera wakupha samalani naye angakudyeni
@user-lk8kj9zv6x
@user-lk8kj9zv6x Ай бұрын
Inuyo guys ndi chuma cha boma ma pongolin athu
@user-ty1vq9lq6w
@user-ty1vq9lq6w Ай бұрын
Chitukuko chao, ndikupha, kuba ndikuononga
@user-zw8ns7bk7s
@user-zw8ns7bk7s Ай бұрын
Aichinja mozey
@Maliet-nh6kf
@Maliet-nh6kf Ай бұрын
Panyo pachakwera kuno kuli holiday
@inessmsiyambiri8517
@inessmsiyambiri8517 Ай бұрын
Sopano zokudyaxo zokanganilana
@victorbanda9039
@victorbanda9039 Ай бұрын
Achikhala a DPP akanakuswa brain muja umawanyozeramu a mcp wo aise Koma poti awa ndi anthu amtendere ukuyenda momasuka
@user-ww9rj2wx8d
@user-ww9rj2wx8d Ай бұрын
Mwayiwala za kuchikangawa eti
@MzadziWanga
@MzadziWanga Ай бұрын
Ku state house munamuthamangisiranji ngt muli a mtendere, osati ma vote akuzunguzan mkanamupheraso konko paja zaugawenga ndinu # 1
@uzaleuzale8603
@uzaleuzale8603 Ай бұрын
Mwaiwara kt mwamuika mu list ya anthu ophedwa anthu akupha inu
@CathrineBizza
@CathrineBizza Ай бұрын
Kwachema wina alira kuwononga ndrama zaziiiiii
@KingsleySymon
@KingsleySymon Ай бұрын
Brain amatha kkkkkkk
@DesmondChavula
@DesmondChavula Ай бұрын
Brain ntchito umatha
@KHWENGWEYAMAPEMBA-l4w
@KHWENGWEYAMAPEMBA-l4w Ай бұрын
Kwayaka moto kumeneko
@GospelSoldiers-sr7np
@GospelSoldiers-sr7np Ай бұрын
Wochakwera amafuna choncho basi kusogoza chilima...mwataya chipangano agalatiya.
@CynthiaLusubiroMwalwanda
@CynthiaLusubiroMwalwanda Ай бұрын
<a href="#" class="seekto" data-time="136">2:16</a> am
@ChrispinJohnson-py5ie
@ChrispinJohnson-py5ie Ай бұрын
kunkuyu dyela
@Lazarus-qo1sl
@Lazarus-qo1sl Ай бұрын
Kwachema
@hezekiayelemia
@hezekiayelemia Ай бұрын
Brian Banda eiiish experience ikumuthawa
@peterkinsLekera
@peterkinsLekera Ай бұрын
Kodi mec ndiyoyang'ana za chisankho cha chipani chimodzi ? Ndikudabwa
@user-gy8yn6qw2k
@user-gy8yn6qw2k Ай бұрын
😂😂😂😂😂
@SebastiaoErnesto-mh6ec
@SebastiaoErnesto-mh6ec Ай бұрын
🎉🎉🎉🎉😢😢
@CynthiaLusubiroMwalwanda
@CynthiaLusubiroMwalwanda Ай бұрын
Aichinja 😂😂😂😂😂😂😂 koma Wanda Msisya kkkkk
@peterkinsLekera
@peterkinsLekera Ай бұрын
Kodi ndizololedwa kuti asirikali atenge nawo gawo ku conversation yachiani? Awapanga hire ngati chipani kapena angwiritsa ntchito misokho yathu
@user-ko6kp7jl4d
@user-ko6kp7jl4d Ай бұрын
Palibenso chipani chingakututumuseni pitirizani.mfimdo.zanu.zotukula.dzikoli,linali mkamwa.mwa mimbulu more.fite
@BiliatMzungudala
@BiliatMzungudala Ай бұрын
<a href="#" class="seekto" data-time="1035">17:15</a> <a href="#" class="seekto" data-time="1038">17:18</a> Ife sitigona a times tili nanu
@StevieChauluka-r4v
@StevieChauluka-r4v Ай бұрын
Chithyola Banda adutsa pa SG basi, am Stevie Chauluka from area 25.
@thomasmilanzi6442
@thomasmilanzi6442 Ай бұрын
Kunkuyu moto
COMRADE NTANYIWA PA LIMPOPO FM - AMAFUNA ANDIPHE KOMA ZAKANIKA.
32:39
Mpungwe-Pungwe mw
Рет қаралды 10 М.
Will A Guitar Boat Hold My Weight?
00:20
MrBeast
Рет қаралды 98 МЛН
POV: Your kids ask to play the claw machine
00:20
Hungry FAM
Рет қаралды 9 МЛН
Самое неинтересное видео
00:32
Miracle
Рет қаралды 1,4 МЛН
NDEU DZURO INATSALA PANG'ONO UKU👐👐👐
43:04
Mpungwe-Pungwe mw
Рет қаралды 18 М.
BON KALINDO LERO PA 09/09/2024
16:02
Mpungwe-Pungwe mw
Рет қаралды 10 М.
2025 zisankho ZIZAKHALA ZAMWAZI - BON KALINDO 09/09/2024.
16:02
Mpungwe-Pungwe mw
Рет қаралды 4,9 М.
COMRADE MTANYIWA PA LIMPOMPO FM
15:57
Mpungwe-Pungwe mw
Рет қаралды 26 М.
KAMULEPO KALUA - KALINDO THE PROPHET TINKAMUONA NGATI WAMISALA 07/09/24.
10:31
TIMES TV KUING'ALULA MBC TV - APWETEKANA AWA🙌🙌
30:44
HOT 265
Рет қаралды 17 М.
Will A Guitar Boat Hold My Weight?
00:20
MrBeast
Рет қаралды 98 МЛН