Koma mwati ku UTM ko simukhapanako koma😂😂😂😂 DPP my Vote Koma malemu saulos chilima sindiza wayiwala makamaka manganya azalongosola bwino 2025 akachoka mu boma
@AlexisKantondoАй бұрын
History is the best teacher be careful
@AgrihortSuppliers-s7mАй бұрын
Utsi ngati uli ndi misala . iwe Ku mnsonkhano waukulu sunapiteko ndipo sunasankhidwe, ndipo omwe akukusatilawo ndi odwala anzako.
@IsaacChitaroАй бұрын
Ndikape usi
@WisikiBlack-gj4guАй бұрын
Usi iweyo osokoneza isiye utm ukulimbana chani ndi utm
@AdamJuma-q7mАй бұрын
Musamasokoneze ,anthu wo ndi a odya zake alibe mlandu , not UTM 😂😂😂😂
@giftmeckАй бұрын
A usi ndinu mbambade
@giftmeckАй бұрын
🔥🔥🔥🔥
@MartinKapangaАй бұрын
manganya ndikufuse Kuti ngati church mulibe ndale chakwela zinantheka bwanji kukhala president iyeyo sinali ndale popedza akuti ndi busa