Anakubelekayo sanaluze I never see I faithful and trusted person like you
@chrisboyce23 ай бұрын
Uyuyu akufunika award (2024 the best political activist Ndi Comrade NAMIWA 💪🔥) 2024 the best Tv ndi Bakili Muluzi Tv 🔥 Kalindo ndiye pangolin wathu 💪
@RiteRoderick3 ай бұрын
Ndipo zoonad zed brother
@Belinda-c6e3 ай бұрын
Ndipo bro sukunamai ma guyz awawa amatiimilira
@patrickmacheso50623 ай бұрын
Really agree with you my brother.
@HajraTar3 ай бұрын
Ndipo tikanakhala ndi anthu okwana ngat 10 okhala ngt uyu malawi sakanafika apa ayi I really like his speach ,mulungu amuteteze ndithu
@PraiseShongwe3 ай бұрын
Please Brian Banda pezani nthawi mukamupangeso interview Namiwa the most powerful and brilliant guy in this country. God protect these men Namiwa and Brian from devils.
@patrickmacheso50623 ай бұрын
I really agree with you my brother
@MkuwaCharles3 ай бұрын
Namiwa ndli pa mbuyo pako
@montfortGhobede3 ай бұрын
Surely Mr Namiwa needs a lot of support from all of us Malawians.
@johngrem28383 ай бұрын
A Man of great knowledge and ideas, Namiwa knows what he is saying and he is a true son of Malawi osati zinazi, this guys Namiwa deserve a great respect and security chifukwa Chakwera ndi Crook akhodza kumupangila chiwembu munthu oyipa ameneuja anapha Chilima ndi anthu ena 8. Pa Chakuti pake Chakwera and Big Up! Mr Namiwa ndipo Osatopa, Osafooka komanso osaopa❤❤❤❤❤❤❤❤❤❤
@McshonWilliam3 ай бұрын
Mr namiwa anakubelekani wo sanaluze ai ndipo komwe aliko alandile maulemu and isaid may god continued kuwapasa zosowa zawo 🙏🙏🙏🙏
Big up Mr Namiwa, dzikoli likufunika people like you
@WisikiBlack-gj4gu3 ай бұрын
Ndakumvetsela Mr namiwa ndiwe big man more fire 🔥 ipulumutse malawi 🇲🇼 malawi 🇲🇼 akufuna athu onena chilungamo ndimopanda matha ndimomasula more fire 🔥
@mohamedriazshreef86973 ай бұрын
Mai amene anabeleka namiwa my god bless them always
@pastorjamesseyama31473 ай бұрын
Keep up the good work sir Mr Namiwa and whole CDEDI team. God bless you for representing Malawians 🎉🎉❤
@MiddayDeleza3 ай бұрын
Well done, your a great man indeed, I silute you, God bless and protect you wherever you shall go in Jesus name ❤
@montfortGhobede3 ай бұрын
I didn't know that Mr Namiwa is like this. Very brave! Malawi needs many Namiwas for it to transform. May the good Lord bless Mr Namiwa.
@cynthiakananji16083 ай бұрын
May the good Lord continue to give you strength 💪 eeee your the best fighter,ndiwe mamuna olimba mtima.mai ako anakubeleka ndipo she is blessed 💞
@NelsonNyirenda-m5q2 ай бұрын
Namiwa you are doing a great job please we are behind and praying for you God bless 🙏
@mohamedriazshreef86973 ай бұрын
Malawi akukufunika akunikafa ngati inuyo mr namiwa my god bless you All the time ❤❤❤❤❤❤❤❤❤❤❤❤❤❤❤❤❤❤❤❤❤❤❤❤❤❤❤❤❤
@thatgirrroskrr35703 ай бұрын
Mtolakhaniyi nde ayi. Namiwa akumane ndi Byani Banda interview izakoma
@MaggieBanda-ft5tu3 ай бұрын
Tolakhani wachinyengo eeee shame
@OmarManjawira-up3ns3 ай бұрын
Following dude ,,,, very soft and clear ❤
@DarlingtonChaura3 ай бұрын
Mtolankhani yu alibe mfundo, Namiwa is on the right track.
@Russell-sq9rm3 ай бұрын
Mtolankhaniyu nd kape Ali nd mafunso ofoila ngat mwana
@umalibudala91213 ай бұрын
Ndichitsiru mtolankhani uyu. Ndikanamutukwana koma ndimapemphera
@GeoffreyKaluwa-em7eb3 ай бұрын
This a man of confidence! Mr Namiwa we need more of you.
@EmmanuelNgambi-y6h3 ай бұрын
Umakwana Namiwa,,,,may God bless and protect you
@ManfredNakhuba3 ай бұрын
Mtolankhani uyu akhalangat wasyetsedwa banzi akufunsa zoti wafotojoza kale aaaaa
@chikondisatchipa76763 ай бұрын
Ndiposo ndiwobhowa bwanj
@bennihope32723 ай бұрын
A very patriotic gentleman. The country needs immensely. Take your fight to a bigger level. In short just 2 Biyeni. I rest my case
@patrickmacheso50623 ай бұрын
Exactly
@PaulMapala3 ай бұрын
May the almighty God protect you mr namiwa the true reflection of trustworthy,passionate and freedom fighter 🔥🔥🔥 with God's hand we wu sing a victory song
@graciouskamwendo18733 ай бұрын
Mtola nkhani uyuyu ntchito yake ikuoneka ngati amangofuna kupeza vuto mwa a Namiwa. Sakuoneka ngati akupanga zosaka chilungamo ayi
@bobkatas19743 ай бұрын
Exactly my point,,,,,akukhala ngati sintola nkhani,,, chifuwa zoti commission of inquiry imeneyi anthu anaikaikilla ndi zoona and iyeyu ngati ntola nkhani anamva zimenezo
@SheenahMwalabu-iz3pr3 ай бұрын
Pajatu zodiac ikuyendetsedwa ndi mcp gospel kazako. pano radio station yanzeru ndi times television and radio and mibawa TV ilikonse bhoo
@MoosaSame3 ай бұрын
Congrats mr Namiwa atolakhaniwa ndi ogudwa onse musalimbane nawo
@YaseenJohn-l5y3 ай бұрын
I like the way u have spoken for us. Namiwa brave mn
@SamKaposa-i5c3 ай бұрын
And me too
@ThomuChiwanga3 ай бұрын
Mr your number one In my country thanks mr namiwa keep up malawi
@JoelTchuma-g3s3 ай бұрын
Mr S.Namiwa you are a man of Kafanikhale,Smartmatic must go out of MEC,please!
@DONNEXKhama-bk1gy3 ай бұрын
God bless you Mulungu akupase Moyo wautali
@ElizaOsman-y5r3 ай бұрын
Munadalitsidwa mwene and i support you i ll always support you ndinu munthu wanzelu mumaziwa kuongala ndinu munthu ofunikila mdziko muno ndili pambuyo panu and i ll always be there for you ❤❤❤❤❤❤❤❤❤❤❤❤❤❤ well said and i love it i support it i appreciate it thanks
Keep it up sir.may God continue protect u and bless u.
@CollinsChimsendenji3 ай бұрын
Host akanakhala Joab Frank Chakhadza
@InnohPhili2 ай бұрын
❤mumayitha brother mulungu akudaliseni
@DeliphDevi3 ай бұрын
Tola khaniyi ndopusa kwambili alibeso nzelu akufusa mafuso ngati sanapite ku school
@KondwaniBMnyontho3 ай бұрын
Zoona ndikape kwambili
@AlexGomani-ss5nj3 ай бұрын
The great man of our country, continue fighting for the truth
@GraceShaibu-i9d3 ай бұрын
god bless you namiwa ndiwe muthu wachilungamo kwambili ambuye akudalitse manja mwanu mulibe mwaziiii
@lorainemponela2 ай бұрын
✊🏿✊🏿✊🏿As a far left activist I agree with Namiwa. He didn't go there to be a tick box. ✊🏿✊🏿✊🏿
@MagretNsopera3 ай бұрын
God bless Mr namiwa mukutiimilila
@frankwilliam98443 ай бұрын
Mr namiwa is so genius and brave,big hand to him!!!!
@Mobilot2android3 ай бұрын
Mr Namiwa ambuye azikudalisani u r more than the millions people and it's our prayer for you long live🎉
@YamikaniWitness-vw3jl3 ай бұрын
Namiwa ndakamuna mmmm! Iwe umabwera ndithu. Big up bro.
@JimmyMaster-l1x3 ай бұрын
Mr Namiwa your a the greatifull Man kuyionera patali Game ndinali ndinkhawa nditambva kt mwapita nokha koma pokumbva kuti mwatuluka moyo wanga uli osangalala kooopya 🎉🎉🎉🎉🎉
@MakesoMjuma3 ай бұрын
Anamiwa amai anu anamvadi kuwawa chifukwa chainu mulungu anamiwa adzadalitsa Mai anu bambo anu chifukwa anabala mwana muombori WA dziko la pansi❤❤❤
God bless you sir ,umuthu wavuta ku malawi athu akusowekera umuthu ngati wanuwo sir
@mikebernabechimundi34723 ай бұрын
Salute Namiwa, you are a commission of enquiry at your own
@cynthiakananji16083 ай бұрын
Eeee Koma Namiwa ndiwanzeru ndipo ndimutu,EEE anabadwa munthu uyu,anthu akaikila kale ndipo takaikila,chimene munthu uyuyu wagunitsitsa nkuchotsa kuyeletsa dzina lake,munthu uyuyu amaimiladi anthu,and akanangokhalapo uyuyu ma millions akanadana naye he is very clever,he is 💯 perfect munzeru.
@JohnFrank-cg1yh3 ай бұрын
Yes am agreed with namiwa, president ananena kut dege inafika ku mzuzu, kumkuyu ananena kut black box ilipo ndipo yasungidwa Malo abwino, chimwendo Banda anati adauzidwa kut dege idazaza,so palibe zomaononga ndrama kungowakoka akuluakuluwa kupita nawo ku court akazengedwe milandu
@stevendemanje3 ай бұрын
Yehovah akutetezeni kwa mikango ya mcp mr namiwa
@BrotherLester2 ай бұрын
This is very sensible he force the president to set the commission of inquiry and he would not be surprised to seat for the meeting but to follow after finalize
@JasonMailos3 ай бұрын
Namiwa number one, Koma MCP isaonengati ikuchenjela
@AlexNjovu-j4z3 ай бұрын
Ifetikuwavesa anamiwa🙏🙏
@KondwaniLingisoni3 ай бұрын
Uyu ndie munthu anamiwa
@bridgetmajor36463 ай бұрын
Heavy
@vitumbikomunthali81853 ай бұрын
Namiwa for presidency. I would vote for this guy if he could be one of the contenders.
@andrewnkhoma35663 ай бұрын
Namiwa he is wonderful man and he is real man of god!!!!!
@hopesonmathafu23462 ай бұрын
Truth Carrie's waight and heavy to handle.... The truth is a sin not a liar' in this world....
@dysonmasiye57363 ай бұрын
Brovo to Mr. Namiwa....mwapangazo nzofunikira kwambiri...izi za majority rule izi nzopoila kwambiri. I remember nnakhalapo elder wa mpingo wina ndipo anakhadzikitsa lamulo loti zomwe mwakambirana ku council ko ngati sukugwirizana nazo koma anthu onse agwirizana nazo iweyo ulibe say and umakhala m'kati mwa zomwe enawo agwirizana zomwe nzopoila kwambiri. Now mwapanga bwino kutuluka and chomvetsa chisoni ndi chakuti kuli amipingo kumeneko koma mwatiuza kuti anali mbali inayo 🤔🤔🤔 chipulumutso ndithu ngati sitisamala
@kadijachilwan9673 ай бұрын
I was misunderstood Namiwa ndimamuongati ndiwa dpp bt the way he spoke here ndayamba kumukonda ndi real freedom fighter
@FebbieNjewa-g3k3 ай бұрын
God bless yu more sir,,God has a final say
@HannifordWitness3 ай бұрын
This is one of the reason zodiak inatsika value atolankhani anzeru ngochepa better times
@rangersonngirazi67413 ай бұрын
Satha ntchito uyu, Namiwa amafunikira Chakhaza or achina Brian Banda
@patrickmacheso50623 ай бұрын
Eya Zodiac ndiya MCP paja mwini wake ndi Gospel Kazako emwe anali spokesperson wa MCP Government and President.
@mohamedriazshreef86973 ай бұрын
God bless you mr namiwa my god be with you always
@HassanChibwana-m8j3 ай бұрын
We love you Sir Keep it up.we trust you
@PeterGrant-ih1sr3 ай бұрын
Nzimu wamuthu ndi nkhan zina chaka Chino ziliko
@MavutomandaMandamavuto2 ай бұрын
Mr namiwa big up don,t big up we trust coded 🎉🎉🎉🎉
@ChristinaStambuli-q3e3 ай бұрын
Commission of inquiry izakhalapo 2025 just after a new elected president ..Mcp ndi Caikwera waoyo ali pa bench anzao akuvinamo ngat momwe akuvinra Chikangawa ndi kunkuyu,Chimwendo Banda..,iyiyi com of inquiry ndiya mcp anthu aja akochedwa kale palibepo phindu amalawi sitipezamo mayankho.Rip Skc and all the victims
@wisdombwanali79563 ай бұрын
We are for this movement Mr Namiwa
@PraiseShongwe3 ай бұрын
Silvester Namiwa you are really different character. I wish you were Malawi's president. Hopefully god will touch your mind to one day contest for presidency and Malawi will vote for you so that you are given room to change Malawi for the best.
@InnocentMtafya3 ай бұрын
Hopefully your are ................
@MisheckChinjala2 ай бұрын
Mulungu Ali payinu Mr Namiwa,ndipo musaseweletse Mzimu Wa Mulungu ulipayi please please please 🙏 in Jesus name
@JonesBenNgaiyaye3 ай бұрын
Mmmmmmmm Namiwa bravo bravo,lets join hands and support each other for the truth to prevail and make Malawi should be freed from all these nonsense leadership
@ALICESHEKI15 күн бұрын
Namiwa you are right ndipo iweyo Moyo Wautali chifukwa Mantha amaononga zithu
@JudithMaida-ug4oi3 ай бұрын
Big up Mr Namiwa amfumu aku tcheu wo aza seva ndende ya chikumbu mtima afta mzimu wa chilima ukuwasautsa
@HamiltonwaNamuwah3 ай бұрын
Keep it up Mr. Namiwa. Kupanda kuwuwawuwa andalewa ndioyipa kwambiri