Achimwene ameneo ndi mbali imodzi ya maitanidwe anu dzukani ndikupeleka moyo wanu kwa mulungu chotsani mantha pemphelo pakamwa landilani yesu akhale mbuye ndi mpulumusi wa moyo wanu iyi siya kwa sing'angaso ayi koma mwini chilengedwe
@agnessjuttah74912 ай бұрын
Amen
@ruthkundwe74482 ай бұрын
God thanks ,mayi ako was ur prayer wourrior, Praise God
@ClementELIJAH-h6t22 күн бұрын
Kom Ka sound kamaveka pansipo kuopsa kwakeko ayeeeee yeeeee
@IvyNyandule2 ай бұрын
Achimwene musaganizenso za msing'ang'a, inuyotu midalire Mulungu pa moyo wanu. Mukangoyerekeza kupanga za sing'ang'a afiti amenewo akugonjetsani basi. Imani pa maso pa Mulungu ndipo muona akukupangirani zazikulu. Kumbukirani ana a Israel ali paulendo wawo opita ku dziko la malonjezano, aigupto amawalondora koma Yehova anamuudze Mose kuti awaudze aziyenda lupita chitsogolo. Ndiye inu mukangocheuka paulendo wanuwo, simupambana china chili chonse koma muimebe pamaso pa Mulungu ndipo mukuyenera kusala kudya ndi kupemphera. Mukumbukireni Estery mmene amafuna kupulumutsa mtundu wake, analowa pa emergency fasting ndipo zazikulu zinachitika
@PETROLJ-n1t2 ай бұрын
Ndipo nkhaniyo ndiyoona mukuyenera mulimbe ndi mapemphera bac
@ElijahTheprophet-y9m2 ай бұрын
Aise umpeze sheikh amene ukumudziwa wapafupi umufotokozele akusomela surat ruqia ndi surah yamphavu kwambiri ziwanda zonse zichoka
@aneeshakhan21842 ай бұрын
Mulungu amatha ndipo salephera mulandireni yesu kukhala bwenzi ndi mpulumusi wa moyo wanu coz singa'nga ndi mfiti net work yawo ndi imodzi komanso munthu amalephera koma mulungu salephera.mukatero pezani munthu wa mulungu akupempheleleni.zonse zitha mu dzina la yesu ziwanda zimanjenjemera,matenda amathawa,kalikonse ndikotheka iye amene anakulengani ndi amene angakumasuleni.
@maryjailosi6522 ай бұрын
Mavuto onsewa pitani Kwa mulungu ndipo zitha
@joycengambi33342 ай бұрын
Ambuye achitepo kanthu
@AlbertMatola-u9r2 ай бұрын
Ine afiti adasiya kundidinikiza chifukwa chodziwa kapempheledwe kake ndisanagone Pemphelo lokagona lidzikhala chonchi! 1. Lapa machimo ako. 2. Akhululukile onse okulakwila ndipo onse mwawalakwila mupemphele kuti akukhululukileni. Yahuah ndi chikondi sichidani ayi 3 Wazani mwazi wa Yahusha munyumba mwanu. Dzikutileni ndi mwaziwo. "Dzina la Yahusha and Yahuah ndi moto onyeketsa"(nenani katatu) Mangani mpanda wamoto kuzungulira nyumba yanu. Kenako nenani "pemphelo langa ndikulitumizila moto wa Yahuah 4 Nena "chilichonse choipa chagonja". Chilichonse chogwila ntchito ya satana chisafike pamalo ano". Pomaliza musanene kuti "amen", "Jesus", "God". Ayi Ntchulani original names "Yahusha and Yahuah" basi " You can pray for 5 minutes and over
@BatchEvance27 күн бұрын
Amen mulungu ndi chida cha chilichose
@JessicaManda-zm1ug2 ай бұрын
Pephero lonkha achimwene afiti ndimasingangawo ndi muzingolimbanapo just trust in God ✋hands. Amen
@HERMANMALIWA3 ай бұрын
Kkkkkkkkkk aisey dzimachitika koma kumusiya munthu chifukwa chaufiti its big mistake 😢
@FrancesMitengo2 ай бұрын
Inutu mungolimbikila kupemphela . Ife pakwathu pali za ufiti tayesa kuyenda mwa asing'anga zalepheleka pano timangopemphela basi ndipo zikutheka ndichikhulupililo mwa yesu khristu
@Grace-x8b2p2 ай бұрын
Mukamagona komanso 12am dzukani muzipephera zonse zitha musayerekeze kudalira amakhwala muluza nazo moyo wanu broo dalirani yesu basi
Ase zimenezo za simple kutha and siku limodz km sitiyuz asing'anga paja sing'angaso ndi mfiti so ngt ukufuna ndyakhulen tikuuzen zochita zosezo zithu insha Allah nde ndyakhulen
Brother yambani kupemphera kwambiri usiku muzidzuka kupemphera Koma pezani zaitumiki enieni azikupemoherrera Tiima Nanu a Jojo Yesu Yekha ndeyankho
@FunnyDimSum-hk1so2 ай бұрын
Musagwirise ntchito zamakhwara inu mukaikamo zamakhwara siziyenda ai taiman pa maso pa mulungu mulungu ndiye chida chachilichose iwe bare ili mbari it or mukanaperaka number zikufunika mapephero izi
@LemisonMchepa2 ай бұрын
pezani munthu amene ali odzozedwa ndi mzimu woyera akupempherereni mumasulidwe ndipo musaphstikize ndi kwa a sing'anga dalirani Yesu yekha. m Mukaphatikiza zitsamba ndi zauzimu palibe chimene chisinthe mapeto ake akuphani.
@WarriorKB-l3i2 ай бұрын
Coyamba ndinene kuti nonse amene munasjya akazi ku malawi muli pa mavuto, simunakwatile cifukwa akaziwo akungonyengetsa izizi mufune,musafune muvomeleze cifukwa inenso ndanyengapo mkazi oti mwamuna wake ali ku jonz, mabanja anali akale masiku ano kulibe mabanja ndikukuzani gyz. Baleyu apite ku malawi makolo akamuthandize akacedwa akhoza kutaya moyo wake we wll pray 4 u my brah.
@ChimwemweZuze2 ай бұрын
Inu omweo munawanyengawo ,nanga minanyenga aliyense ngati mwamuna wake Ali ku John hiya ,sionse Koma enawo ,nanga ndionse Azibambo omwe anakwatira kujohn omwe anasiya azikazi awo??
@Umalikandu18 күн бұрын
Mmhh muzafera nmanja inu anthu alusa
@IvániaMoisés-u7c2 ай бұрын
Pephelo limatha zose
@ireenmusende95272 ай бұрын
Kuona kwanga musaikepo Zamakhwala chifukwa asing'anga ndi network Yao km pemphero ndy chida chothera vuto lonselo or amfiti atachuluka bwanji palibe angafane nawo ine ndi mboni wapemphero ndi pembedzero chifukwa pa 4 January chaka chomwechi ena amayesa zida kundimenya ndihamala yaumfiti km ndinachira Ndipo mwadzi wanga sanapindulile ndy inuyo muyang'ane kwambiri Mtanda imene Yesu waku Nazareth anafera
Pempheran kolimba mulungu ndiye amatha basi osadalila asinganga koma yesu basi
@EllinaTausi2 ай бұрын
Jesus 😢
@nerrcejngulube2 ай бұрын
Nthandizo ndipemphero achimwe mulungu ndiwamphavu
@JullFlimonАй бұрын
Kumangolimbikira pephero basi
@FelixBoss-yn9pe2 ай бұрын
Bwelani kumalawi kuno muzathandizidwe
@MADALITSOCHITSEKO-y1m2 ай бұрын
Mmmmmmmm😢😢😢😢
@RoseMsonkhoMalele2 ай бұрын
Mulunhu. ndiye chida chachikuluu
@MiddayDeleza2 ай бұрын
Eishhhhhh koma nde zowopsyatu
@EmmanuelMgona-ij7ew2 ай бұрын
Ndilankhuleni please kuthekera kulipo kuno chonde
@BettieMaseko2 ай бұрын
Za mankhwalazo ayi annon pempherani kosalekeza mpakana china chake chitachitika
@stevezulu21082 ай бұрын
Ufiti ndiye entertainment ya kumudzi.😂😂. Masalamusi
@ReginaMandawala2 ай бұрын
Pena pali ponse osati kumudzi kokha
@TameeraInglis2 ай бұрын
Munthu ameneyu andiyankhule ku inbox kwanga
@ThomasChiwaya-qx9mf2 ай бұрын
Ine ndikuvutika kom iwe zanga wapambana ine
@PatrickMtirah2 ай бұрын
Uli mbari iti ya kuno ku south Africa ase tipatse number yako ngati uli kumarawi tikuthandize ngati uli kuno ku South Africa tikuthandizaso zimenezo zitha mu dzuna la mulengi mwini moyo
Pofunika ma pemphero achimwene chifukwa dziko ili laipa. Timaonana kunja kwa thupi koma zamumutima wazako zimakhala zochuluka. Koma chigonjeso cha zose ndikuyima pa maso pa mulungu siku ndi siku.
Ulore luti moyo wako uyikidze manja mwa mulungu osalore kuti chikhulupiliro chako chonse uchitsiye kwa asing'anga peleka zovuta zako zonse kwa mulungu basi mavuto Ako onse azatha
@LoydKameza2 ай бұрын
Koma añthu amapanga zinthu mmm
@MustafaLoyd2 ай бұрын
Eish ndip
@ChimwemweMathyola2 ай бұрын
Kunjakuno anthu ambili amakhululupilila za ufiti kwambiri
@DanChimaliroАй бұрын
Wuzikhulupila kwambir popephelapo
@mayesojameskatete3 ай бұрын
Ineyo ndikuthandizani baba
@HannaMkhalipi2 ай бұрын
Tiyakhuleni amavuto tili ambiri
@MaggieMkandawire-ki5mu2 ай бұрын
Upte kwa asilam akuthandiza
@azizhunter37892 ай бұрын
Lakhula nane tinzathetsa dzonse
@MikeChinomba-d8r2 ай бұрын
dziko liziti Ufiti kulibe kumsunu Kwa_____
@IMMACULATEKAMBALAME2 ай бұрын
Eeeee tidzakwatiwa nazo ndi afiti tisakudzwa....ambuye azititetezera
@AlasonPaulo-ht7zb2 ай бұрын
Koma zosakhala bwino
@FunnyDimSum-hk1so2 ай бұрын
Sono zosezi umaonaz sumapephera bwanji mulungu salephera ndipo sanarepherepo muzina ra yesu khristu
Muyenera kukhala mu moyo wa pemphero nthawi zonse, pezani anthu omwe amapemphera mu mzimu ndi mchoonadi, koma musankhe njira imodzi osati kuyangana kwa Mulungu komanso kwa satana, sankhani njira imodzi
@AmosiChiwa2 ай бұрын
Hy
@isabelmartin75672 ай бұрын
😢😢😢😢
@EsetaGerate2 ай бұрын
Ayi pepani limbikirani kupemphera basi
@khoviwaedward2 ай бұрын
Malodza
@MercyMjima-tv5py2 ай бұрын
Ambuye akumenyele khondo thawi zonse
@EfremoMiguel2 ай бұрын
Tithokoze mukuyitha kwambiri Muziponyabe pa youtube