TA you are more a patriotic citizen.May God bless you.Malawi is lacking such leaders even in religious and political fields.
@FelixChimsNyirenda28 күн бұрын
That's great, we need such good and courageous chiefs like this one. God bless.
@rosebanda3613 Жыл бұрын
Ulemu wanu manjolo and hands up to Ta. TA you are wise like king Solomon may God bless you with more wisdom
@charlesmpaso2383 Жыл бұрын
Anthu awa akuyenera kukwezedwa udindo komaso akufunika chitetezo.....mulungu oziwa kusamala akutetezeni mu zonse pamodzi ndi ma family anu.... AMEN AND AMEN.U DESERVE AWARDS GUYS.
@AngellinaUsman Жыл бұрын
My God bless you mr manjolo ndi T/A mukhale ndi moyo fumu❤
@moseschizyibwa4463 Жыл бұрын
I like this program. Watching from zambia, Moses
@olivechikwindi9126 Жыл бұрын
😭😭😭😭YESU akuchedweranji kubwera koma?AMBUYE akudalitseni A/T ndipo akupatseni moyo wautali and Mr manjolo God bless you mukhale wotetedzedwa anthuwa
Tithokoze aT/A ndi Mr. Manjolo polimba mtima kupulumutsa moyo wa mwana ku imfa ngati imeneyi. Enatu anakakonda ndalama kusiyana ndi moyo wa munthu. God bless you.
@chrissyamanda5510 Жыл бұрын
Manjolo atetezedwe ndi mwazi wa Yesu Ndikutha kuwona kuti moyo wake uli pa chiopsezo koma Ambuye wanthu ngwa moyo ndipo ndi mgonjetsì
@gkay-striker11 ай бұрын
You did a great job
@Davison-jr6ev10 ай бұрын
Yes this guy and the TA must gain some thing from the the government for rescued the boys who was about to lose his life,
@HenryGulani-fq5js7 ай бұрын
Mlu dzikomo kwambili mulungu Akudalitseni 🙏🙏 ine ndili Joz
@WycliffChizingaАй бұрын
Our T/A is great man
@ausbonchimgolo9984 Жыл бұрын
Manjolo and T/A they deserve a medal
@promisemombah Жыл бұрын
Munabwera Inuyo
@lindsonexton8563 Жыл бұрын
Inu ndi akatundu odziwa kufufuza nkhani, you deserve a medal
@PempheroMkusangombe10 ай бұрын
T/A akutetezeni Mulungu ndi manjolo akupatseni moyo wautali
@PeacefulWildFlowers-sl8er11 ай бұрын
Mafumu a smart❤❤❤
@ephraimnjikho9307 Жыл бұрын
If all Malawians were like Manjolo and the TA, such cases could have been on the decrease. People are very hard hearted.
@usherkays4379 Жыл бұрын
Thanks to the TA for exposing the criminals and protecting the nation
@ChinsinsiMaseso Жыл бұрын
Boma lichitepo kanthu, big up Manjolo and T/A
@FatimaBanda-b3s9 ай бұрын
😭😭😭😭😭 God bless you my brother all the best in your life 🙏
@jamesngalande4345 Жыл бұрын
thats true your heros boma likuyenera kukuthokozani kuti anthu ena akawona atengelepo phunziro
@bjmtalimanja5073 Жыл бұрын
Pakufunika apasidwe unduna wa za chitetezo mdziko mino.wosati zisilu zomwe chakwera azisankha zija
@fosterphiri5366 Жыл бұрын
Mulungu akukwezeni afumu ndakutukulilani muma ja a yehova
@juniorbvumbwe9822 Жыл бұрын
Akanagwirisa mawu ot opha nzake aphedwe bas
@stuartchirambo-x6u2 ай бұрын
Very disappointed about this a Malawian killing each other because of money aaaaaash what if this man to be taken to court
@stuartchirambo-x6u2 ай бұрын
Stupid person
@williamchanza5338 Жыл бұрын
This guy s a hero
@TiwongeLuwe Жыл бұрын
Government give thanks to the people for sure they did great job 👏
@ChifundoJames-ks6pr3 ай бұрын
God bless u mr manjolo.
@PeacefulWildFlowers-sl8er11 ай бұрын
Ulemu wanu mr manjolo❤❤❤
@matiasncalaila4003 Жыл бұрын
Nanga Judgement yatha bwanji? Nanga anthu 5 womwe akugulisapo ndi ati? Amagulitsira kuti? Nanga anthu amenene anagula Boma lichita nawo chiyani? We need Justice. Manjolo Ambuye Akudalitse komanso a T.A pamaganizo yawo ya bwino yofuna munthu wamoyo, tikana luza mwana.
@KSylmo27 күн бұрын
Great job
@ThokoKaipa9 ай бұрын
God is revealing himself to people,,,that child is just innocent and God is watching upon him
@PeterMillionAntonio Жыл бұрын
Well done Mr T/A
@KondwaniKanduluАй бұрын
Nyimbo anapanga play kuti mwana uja amvere title yake Ndi chani??😢
@nkhwaziaeros18452 ай бұрын
Yall deserve honors
@dolikakamanga203 Жыл бұрын
Good job may God bless you guys
@noahmshanga-rb1xc Жыл бұрын
Mmmmm! MR MANJOLO and the headman they need to be on the better position and please my fellow youths do not be influenced in such calectors even if things can be bad in life try your best to do the right thing like what MR MANJOLO and the village HEADMAN.
@janetmanda6412 Жыл бұрын
After so many years now the secret is out, my question is is the police keep secrets also?
Keep it up Manjolo and T/A. May the almighty God, bless both of you.
@ShaicdesignerКүн бұрын
Anthu okuphawo anachajidwa zaka zingati ku prison pamenepo sanapatchule bwaa?
@marynkhata9707 Жыл бұрын
Afumu anzelu mulungu akudalitseni
@officefileofficefile4771 Жыл бұрын
Dziko la Malawi atulusidwa amenewo, chisanzo nachimpanti anamutulusa kale Ali kuno ku South Africa, nkhani ngati zimenezi athu m'boma zimakhala kuti zikuwakhuza
@oliviasullivan10595 ай бұрын
Nkhani yogulisa ziwalo zinayamba kale kale ndipo ine ndikukumbukira boma likuopyeza anthu kuti anthu asiye kunena boza kuchitisa anthu anzao mantha. Pano anthu ngati Manjolo ndi a T/A ndi osowa. Nchitidwe umenewu uthe mulungu achite nao opha anthu . Zikomo a Ntola nkhani Ambuye akutsogolereni mu nchito imenei. Mwapulumusa ena.
@dalitsochibisa2986 Жыл бұрын
Zikomo kwa bwana TA and the team who helped to rescue the boy
Moti zigawenga zija zikanatutumuka manjolo anali pamavuto agulupu aja akanamutembenukilanso kt iweyo mission ija wailepheresa pazifukwa zilibwino ubale wamanjolo ndi a T/A panopa kamba mission yatheka nduthu
@MadalitsoMada-g3l3 ай бұрын
. iyi ndi program ya bwino.isathere pa njila.( Ndine chikumbutso Sande : ck/T/A NGABU ,GVH SANDE ll SAOPA.
@usherkays4379 Жыл бұрын
Manjolo deserves a reward from the government
@abdulkatopola3612 Жыл бұрын
Iweyo ukungofunika ulandile award ndiwe wekha ungakwanise
@ayamijackson1443 Жыл бұрын
Ooooo my god 🤔🤔🤔🤔kama amalawi 🇲🇼 mmmmm
@PiliranTChimalizen9 ай бұрын
Km a T/A awa ngofunika award
@WysonJekapu10 ай бұрын
Nyamatayu Boma limupase kagalimoto
@SirpromiseMatabwa6 ай бұрын
Well amfumu amchacha
@greychizaka408810 ай бұрын
True hero
@carlossadimba59510 ай бұрын
Koma nanga mabwana omwe amagula Ku nchalo Ku chikwawao tiwadziwe nawo ife kwathu mkomweko
@BeautyMtambo9 ай бұрын
Amalawi tiyeni tigwilane manja kupewa nkadza Kwa abale athu tiyeni tikondani wina ndinzache
@JosephEthan-l6u10 ай бұрын
Trader manjolo
@user-np4xk9bx3e Жыл бұрын
Mulungu awaonjezere zeru Mr majolo and a T/A
@geee7672 Жыл бұрын
Mwana, wapezayi ndi scoop. Atolankhani akuluakulu amagulidwa ndi mapoliticians to avoid this. Break into this industry. This is nothing but tip of iceberg. Mpakana umupeza amene amagula ma albino. Ine ndimakaikila mzimai wakumwanza uja
@aleksawilliams710 Жыл бұрын
La 4o lakwana ,amenewo asatuluke,,,zinganizani aliwanu mwana