Perfect said but pomuika Bon Kalindo mu gulu limenelo nde mukulakwitsa Bon Kalindo ndi president wa amphawife we proud of him
@meganabigail-ye7fwАй бұрын
Walakwisa kwambiri
@LubabaloNziyanziyaАй бұрын
❤❤Zikomo
@user-fm8ed7eo3iАй бұрын
Madala mulungu akudaliseni ndi mau omwe mwawagawira anthu onse mudziko lathu la Malawi. Mwalankhula bwino mopanda manthu, ndipo anthu ngati inu ndi amene akusowekela kuti dziko lathu liphulidwe mu msinga za moto. Well done papa
@KenedyBizwick-lh8buАй бұрын
Aaa akulu mwapalatu pamenepo kalindo anapepesa ndipo amalankhula zonveka zonzeka mwinatso kupotsa inuyo the DC nd katundu omanga ndimalamba
@WisikiBlack-gj4guАй бұрын
Born kalindo anapepesa mukululukileni, koma pachiyambi anasokonekela, koma anatutumuka athu atataisa kale, koma uyuyu uyu aaaaa tayeni akufuna kusokoneza wabhaletayu ndimagalaziyu,,
@user-xd1cm7tm7tАй бұрын
The dc trusted for us
@AleksaWilliams-qc6cnАй бұрын
After all a bon kalindo anapepesa komanso saliku chipani chilichonse
@mkupabanda-nd2vbАй бұрын
DC msiyeni,kwinako tamva
@GolaMwanza-oi3ojАй бұрын
Zingayambe kuyiwalika
@GraceLimani-zw7dxАй бұрын
Ameneyu atisamale mambo chitsiru cha munthu kuchoka ku Zambia uko
@richardskumwendah9072Ай бұрын
Iyi ndimisala to the maximum. Nonse ndi ntambo mix MCP
Malawi it's for us let's stand en fight for our rights we nid to make malawi better dats it guys malawi yapoila hvy
@yusufuadamu5476Ай бұрын
Komano mukudziwa kuti Bon kalindo adapepesa kwa A Malawi pachimene chidachitikaAnd We all know that no One is perfect,Freedom fighter Mr Bon kalindo is trying His Best.
@user-ln3zx6wo4w29 күн бұрын
Kumpoto nkwachilima ndi afod not dpp nde 50+1 mukaitengakut
@uchizJoelMumbaАй бұрын
Ife takhala tikunena boni kalindo ndiwamisala Bambo awa akulakhula zazelu osati za boni kalindo Zija ai koma macadet opanda zelu basi bze kuombela mmanja boni zazii
Yes your right but only kalindo Leave him he is innocent man
@chipi892Ай бұрын
Amen
@LysonMtalika-tb6fkАй бұрын
Well spoken but leave our president alone, Bon Kalindo doesn't have issues only fighting for the poor Malawians.
@user-nc4vi1jt5gАй бұрын
Akulu musakhale oweluza musireni mulungu
@meganabigail-ye7fwАй бұрын
@@user-nc4vi1jt5g aaaa aaaa waweluza ndani apa? Muzachila 2025
@user-zq5ob7xz4lАй бұрын
Bon kalindooooooo
@user-db3mh9wr9vАй бұрын
Zimenezo ndizakale kalindo adapepesa kale musiyeni pano ndi president wathu
@AnnieJuttaАй бұрын
Lankhulani Zina osati za born Kalindo mukusowa zonena ndimunthu yekhayo akufera ife Malawi osauka choti mudziwe
@IMEDISHAMILAАй бұрын
Kutokota kwabwino kwambli big man
@duncainjimmyАй бұрын
Komano Bon kalindo as omenyera ufulu sakuyenera kuimilira chipani komano aziyima pa choonadi . Kalindo is the last man standing indeed. Ndangokonza pa Bon kalindo kuti aime poyera ndikulowa DPP/UDF mm ndizomwetu Mtambo wathela zolowa chipani
@timothymhone2340Ай бұрын
Tangolankhulani zoti mzapange mkawina zanzeru please 25yrs Mndale koma zaziii
@Mike-du7ztАй бұрын
Eti ayise
@andrewnjawalaАй бұрын
Nice speech but kalindo anapepesa, so let's fight together
@user-jw5rx9ze8kАй бұрын
Bon kalindo yekhayo, muchotsemoni abale.
@nyanguoipa6996Ай бұрын
Nambo kweleko kkkkkk. Yakusawusya
@sparkdymon3429Ай бұрын
Muthu mulala wayowoya 200 %
@user-vh1cq5gs5uАй бұрын
Mdala uyu kwamuvuta mkunvetsetsa born kalindo amadzudzula ndipo sakunama born kalindo
@user-ve4yl1gq8eАй бұрын
Mwalankhula bwino koma koma pomutchula boni kalindo mwalakwitsa kozi iye anabwera poela nkupepesa ntundu wa amalawi ndipo amalawi anamukhululukila nchifukwa mukuona kut akalindo akalankhula amalawi akumawamvela ndi chidwi end next time osazanyozaso kalindo
@JacobKapangeАй бұрын
Awa ndi a DPP. akumva kuwawa mmene anachoseledwa muboma ndipo simuzawina wina even come 2025
KZbin yaphweka, munthu wandale kuyankhula zopepera chonchi, muzamanga mtambo, iwe ndi wa police? Kudzichemerera koma kuyankhula zopusa, paja umbuliwu ndi andale omwe eti? Tangoperekani maganizo anu osutsana ndi mtambo ndi andale koma akhale maganizo olongosoka osati zopusa ngati izi.
@Mike-du7ztАй бұрын
Uchisiru wanu ndiumene unakutulutsani dpp and udf ure not holy ndipo am promising yu guys simuzawina unless muzasinthe kachitidwe kanu
@WilfredMathews-yl6ijАй бұрын
Mdala iwey according to your speech tikuziwa kut ndiwazipani ziwiri watchulazo km born kalindo musiye pliz leave that Guy alone pliz,fundo zako ndizabwn ndithu km panga zako
@user-mj3ms4jt3bАй бұрын
Uyu ndichitsilu kwambiri, ife ngati amalawi amaliseche akumwera sitikuwanaso iyeyu afune asafune tonse alliance iwinaso. Padziko lonse lapansi tikati zitukuko ndikumanga maziko atsogolo la mawa. Galu iweyo tanena zomwe amaliseche akumwera ndi DPP ndi UDF zomwe anachita zomwe zikupindulila amalawi lero lino kwa zaka 6 zomwe analamulira amalisewo ukuwatamawo. Kumangoyika Miyala basi ndalamazo mkumagawa kwa anthu akumwera chimenecho ndi chitukuko? Mbombela university ndalama aGalu inu adpp ndi UDF mwakhala mukutenga kwa zaka 6 zonse pa budget yaboma koma mpaka tinakuchotsani m'boma musanamange mbombela university. Sizokhazo ndizambiri ndipo iwalani zoti muzalowaso m'bale aGalu inu loko MEC chair person akatakhala mwana wa amaliseche akumwera simungawine chisankho. Anthu oipa inu kwambiri akudya anthu ndi mafupa omwe
@ZelinaKisswellАй бұрын
😂😂😂 agalu kusekana zikundo , chakwera wako wapanga chani apart from devaluation, kukwera Kwa zinthu ndi corruption. Zogawa ndalamazo Aku Lilongwe kukasiya Mesa akumalandira ma 700 thousand pezan zina zolankhula akulu
@joelmakwinjakambalame9652Ай бұрын
Ameneyudi ndi ofoyila sangaone anthu mmene akangulula njinga zamoto ndi mmidzi momwe. Kabaza sanayamba nthawi ya DPP. Pano mumuuze akayime mmaboda akaowone ndi njinga zamoto zingati or zakapalasa zikulowa
@user-dw9zi6bo3oАй бұрын
I doubt the claiming here in that he is a seasoned and shrewd politician. Sound knows nothing other than being a blind royalists. He is a just a supporter of DPP and UDF as he voluntarily confesses herein. Cant understand what he is up to begging for DPP and UDF sympathy. He thinks he can advise Nankhumwa yet he needs advice himself. Nankhumwa will shame them by dividing the DPP vote. He understands very little about the Nankhumwa effect, talking about 'alibe ndarama zopangila' ma branch, what a warped political mindset. And praises fello tribesmen what do does he think he will succeeds from such mindset. He thinks kuyankhula bwino its about god washipping kkkkk and boot licking. The tongue can tell who what he is up to. To hell with your DPP
@fumumdolo7341Ай бұрын
Speaker has just expressed brutality no connection to the mentioned kongoresi munthuyundi mwana pa ndale. You are not even a political man. UDF komwe ipite uzizimuka. DPP AND UDF ilipo?
@MecyKamtsuko-me2kr19 күн бұрын
Ngulewakulu
@DanMhone-iw6xg27 күн бұрын
Mani tangokambani zina ngati zokamba zatha siyani kulankhula koma sitepe mwalowayo palibe chomwe mupezemo boooooooooooooooooon kaliiiiiiiiiiiiiiiiiiiiiiiiiidooooooooooooooo mmmm man timamukonda kwambili
@giftdulamkalenga7344Ай бұрын
Mutha kunyoza enawo koma The Dcccc analapa ndipo he is here to stay uyu alowa UDF /Dpp pompa
@YoxyKandawire-kj5vhАй бұрын
Musiyen bon kalindo ndi pulezindet wa anthu osauka ndipo ndiyenkhao akulimba mtima kumenyela nkhondo amalawi
@BillyKalambo-jx3vfАй бұрын
Inuyo mutu suli bwino ineyo sungandiyankhile zopusa iweyo ndalezo unapangapo chani kuchita kuzichemerera za ugalu basi