Kupha koma nditchimo koma ai poti atelo anthuyo nanga atapezeka wina amuphaso muthatu mudzi onse tisafulumile kulanga aziwa ndi mwini moyo chonde tisamatelo
@Marialongwe-nzlib Жыл бұрын
Kodi kumeneko Sikukhalako nkhani Zamsangulutso Basi Zakupha zokhazokha
@lucysimbani39712 жыл бұрын
Zovuta kwambili
@austinvincent7732 жыл бұрын
Connected
@zaithwachiwaya2 жыл бұрын
Eee Mozambique woyeee kkk koma amuchita bwino kumuphako Aaa azake azisowa mtendere iya kk
@mbawabuliyan97042 жыл бұрын
Achita bwino kumupha ndi osokoneza kwambiri
@jvpondan43322 жыл бұрын
Ayi osamatero kubwezera ndi kwake kwa mulungu abale imfa siyabwino