WOLEMEKEZEKA INU ABALE NDI ALONGO MU GULU LIMENELI LA MTHAWIRA SPIRITUAL MELODIES... ZIKOMO KWAMBIRI CHIFUKWA CHA MAYIMBIDWE WOKOMA WOTERE KUCHOKERA UKO KU MUDZI MACHINJIRI BLANTYRE (MALAWI) INE MALAWI NZANU KUNO KU DZIKO LA CHILENDO LA SOUTH AFRICA MU MZINDA WA CAPE TOWN WESTERN PROVINCE OF SOUTH AFRICA NDI KUTI : YEHOVA MLENGI WATHU AKUYANG'ANIRENI USANA NDI USIKU, AKUTSOGOLERENI MU MAGANIZO, NZERU, MACHITIDWE ANU A MASIKU ONSE, AKUDALITSENI NTHAWI ZONSE ❤❤❤AMEN.