NDE MWAMVA? DZULO AWA AWULURA ZINSISI ZA KUSOWA KWA MAFUTA. ALIBE MANTHA ETI? ANG’ALUZA ZINSISI UKU

  Рет қаралды 20,655

BS Malawi

BS Malawi

Күн бұрын

Пікірлер: 23
@FulindaMuhamad
@FulindaMuhamad 9 сағат бұрын
Ngati ndalama yakunja dzikusowa nanga bwanji sitinaveko kt Chakwela walephela kuyenda chifukwa palibe ndalama
@LawrenceMkweu-u2f
@LawrenceMkweu-u2f 12 сағат бұрын
Very brilliant ideas koma vuto ndi spirit ya jealousy yomwe ikutivuta kuno kwathu no wonder sitikupita patsogolo even kuti akupagwile approve ma document ako uyenela kuvutikila
@MathewsMakina-z6n
@MathewsMakina-z6n 13 сағат бұрын
Ndalama zakunja zipezeka bwanji chikhalirecho achakwera ndalama zikapezeka zakunjazo achakwera amangoyendera ndiye zipezeka bwanji
@thomasbodo4099
@thomasbodo4099 11 сағат бұрын
Chakwera is a failed Leader amaulendo amene wakhala akuyenda ndi Opusa kwambiri amene sanapindulire dziko instead waononga ndalama zambiri za kinja but ma results amaulendo amenewo zero
@AllanBlack-lu8rq
@AllanBlack-lu8rq 13 сағат бұрын
Watching live from Chikanda City 🤣🤣🤣
@SimonBanda-b1f
@SimonBanda-b1f 10 сағат бұрын
Timamva kuti IMF mukagwetsa kwacha imakupatsani ngongole mumatchula ma billion ambiri ama dollar. Kodi amakupatsani ma kwacha or ma dollars?
@geraldlukhere1159
@geraldlukhere1159 9 сағат бұрын
Chikungodyera masoseji mbuzi ya munthu
@marryphili5419
@marryphili5419 12 сағат бұрын
Vuto safuna kuvomereza Kuti mwalephera kuyendesa dziko ndarama zakunja zipezeka bwanji pomwe kwanu kuyendayenda
@ChristopherManase-s1f
@ChristopherManase-s1f 9 сағат бұрын
Agalu inu kodi nthawi ya Bingu mafuta Samasowa?
@marryphili5419
@marryphili5419 9 сағат бұрын
@@ChristopherManase-s1f isi wesi
@Fanie-i7z
@Fanie-i7z 11 сағат бұрын
This country is Malawi
@JaphetSakala-u5j
@JaphetSakala-u5j 12 сағат бұрын
Kodi munyanja ya Malawi mulidi mafuta?
@GeoffreyEllias-m9l
@GeoffreyEllias-m9l 11 сағат бұрын
Ndlama zakunja zilipo zambirimbiri Kodi chakwera kunja amapita ndican?
@PatrickSomanje
@PatrickSomanje 10 сағат бұрын
Because chakwela felled for everything
@NajumuFriday
@NajumuFriday 6 сағат бұрын
Mafuta akusowa chifukwa chopepela ife amalawi ife timachejela pakudya poka basi
@khasimMusa-d3w
@khasimMusa-d3w 7 сағат бұрын
Mumakwana
@geraldlukhere1159
@geraldlukhere1159 9 сағат бұрын
Kodi ichi chichakwela ichi mumene chinayambira kugwetsa nkhongono za kwacha basi tizingolira basi ndani angandipatseko number yake ndichitukwane ndekha
@SimonBanda-b1f
@SimonBanda-b1f 10 сағат бұрын
Komanso kuyendayenda kwambiri ma leaders a boma
@AbdulsharifulKalipinde-m6u
@AbdulsharifulKalipinde-m6u 11 сағат бұрын
Inu fertilizer kulibe Ndiye olo kuti mulime katundu wambiri Fertilizer mukampeza kuti Beside fertilizer ali pa 100,000 kwacha ndiye kuti alime minda yambiri simungapeze profit Zangonkhala ngati chonchi pogula 2 bag chimanga ndi fertilizer 100,000 kwacha pabwino ndi pati
@CharlesfisheFrank
@CharlesfisheFrank 12 сағат бұрын
Which country is this 😂😂😂😂
@lyiemanganjira9708
@lyiemanganjira9708 11 сағат бұрын
Tangonenani ife tufuna solutions,, zinazo muona kuti mutani
@geraldlukhere1159
@geraldlukhere1159 9 сағат бұрын
Iwe ukuganizapo bwanji
@EmilyKanyika
@EmilyKanyika 13 сағат бұрын
Machimo
Afrikaans Nuus l 24 Oktober 2024
22:57
SABC Nuus
Рет қаралды 3,4 М.
🕊️Valera🕊️
00:34
DO$HIK
Рет қаралды 13 МЛН
CAN YOU DO THIS ?
00:23
STORROR
Рет қаралды 25 МЛН
Kluster Duo #настольныеигры #boardgames #игры #games #настолки #настольные_игры
00:47
didn't manage to catch the ball #tiktok
00:19
Анастасия Тарасова
Рет қаралды 34 МЛН
🕊️Valera🕊️
00:34
DO$HIK
Рет қаралды 13 МЛН