NDEKUTI BWEZI PANOPA THUPI LA SULEMAN LILI MMANDA? KODI ABALE WALAKWASO CHANI? KU MALAWIN KWAVUTA

  Рет қаралды 42,346

BS Malawi

BS Malawi

Күн бұрын

Пікірлер
@JacobMsukwa-q6v
@JacobMsukwa-q6v 23 сағат бұрын
Ineo mnakakonda Sulemani atapasidwa unduna despite wa DPP but got the capacity to take malawians to another level ❤❤ believe me or not ,,,this guy is different from anthu ambiri a ndale💪💪💯💯I salute mr man
@michaelkunje5370
@michaelkunje5370 Күн бұрын
VERY POWERFUL AND JUSTICE MAN 💯👌👌
@Yungjoe786
@Yungjoe786 2 күн бұрын
Our country needs peoples like you,Bravo Suleman you’re our last hope
@AshraffhAlieh
@AshraffhAlieh 2 күн бұрын
Ubweleso mawa Suleman ukundisangalasa kwambili am in love with you
@GraceMasiye
@GraceMasiye 2 күн бұрын
Big up Mr Suleman,mumatiyimira Ku parliament kuja osamamva malodza chonchija, asamajaire
@IsaqueFernandoAntônioAntônio
@IsaqueFernandoAntônioAntônio 2 күн бұрын
Your a king of truth,we love &like u, very very much
@michaelkunje5370
@michaelkunje5370 Күн бұрын
Dr Suleman muli SKC spirit 💯🙏
@SherifaG.Mlelemba
@SherifaG.Mlelemba 17 сағат бұрын
Kip fire burning🔥🔥🔥 Do not Worry, you have the best protector.... GOD (ALLAH)
@hashimmakwemba3612
@hashimmakwemba3612 2 күн бұрын
Chakwela apeleke black box mwachangu Chakwela akanakhala sanaphe Chilima sibwenzi atabisa black box ya ndege
@yamikanikandikole3511
@yamikanikandikole3511 20 сағат бұрын
I like this man amalankhura zothandiza a Malawi
@jackiendlovu9564
@jackiendlovu9564 2 күн бұрын
Mr your are nomber one and I like it your speech
@jackiendlovu9564
@jackiendlovu9564 2 күн бұрын
Ndipo Mulungu akufungatileni ndinu oyenera kukhaka mfumu yathu mdziko muno
@Mosa-b6g
@Mosa-b6g Күн бұрын
We are proud of you Mr Suleman ❤❤❤❤❤❤❤❤
@ImedKunje
@ImedKunje 2 күн бұрын
Komatu kugoyelekeza kupha suleman tizagawanapo malawiyu sure
@FrankFrancis-ch3xv
@FrankFrancis-ch3xv 2 күн бұрын
Vuto timangoyankhura komano kuchita,Malawi ndife anthu opanda mgwirizano
@MillieMalakam
@MillieMalakam Күн бұрын
Sameer thanks for your scripture
@ChisomoMandawala
@ChisomoMandawala Күн бұрын
Thanks Mr Suleman, kma mudzimuuza Daud m'balewanu asamangosatira zilizonse
@JacobMsukwa-q6v
@JacobMsukwa-q6v 23 сағат бұрын
Musamadane ndi chilungamo malume,,, you're in Malawi en you really know what is happening to our country feel ashamed 😢
@OmarManjawira-up3ns
@OmarManjawira-up3ns 2 күн бұрын
Go deeper Sameer ❤ Allah is with you fear nomoree
@CharlesChingwalu-q9u
@CharlesChingwalu-q9u 2 күн бұрын
Big up sulemani 🎉
@RoseBwanali
@RoseBwanali 2 күн бұрын
My pangolin 🎉
@EliasYusufu-f5i
@EliasYusufu-f5i 2 күн бұрын
Chitetezo chachikulu chili mmanja mwa Allah mkaona amatsatira galimoto Yoti siiyo (history is best teacher) we have same history beyond sulumain God will protect Sulumain
@veronicajana5225
@veronicajana5225 2 күн бұрын
May the good Lord protect you guys
@RosinaPatel
@RosinaPatel 2 күн бұрын
Allah is protecting you my brother..
@CharlesWitness-vp6dw
@CharlesWitness-vp6dw 2 күн бұрын
Mr Suleiman please please take care Malawian they don't want to lost any political person
@LindaChikwawa
@LindaChikwawa 2 күн бұрын
May God protect you mr sureman
@MartinNice-z9n
@MartinNice-z9n Күн бұрын
Sereman tork really as Bon kalindo, The Dc
@WonderfulMaulana-q6d
@WonderfulMaulana-q6d 2 күн бұрын
Big up bwana Suleman
@AshraffhAlieh
@AshraffhAlieh 2 күн бұрын
Peacefully Apm Mr man
@stormchatepa134
@stormchatepa134 Күн бұрын
Eish
@GamahCharles
@GamahCharles 2 күн бұрын
Brave man Mr Suleman, God is on your side
@yamikanikandikole3511
@yamikanikandikole3511 20 сағат бұрын
Malawi pangolini Sureman
@KazembeFoster-jw1ww
@KazembeFoster-jw1ww 2 күн бұрын
Respectfull boss
@GiftVillage-v7v
@GiftVillage-v7v 2 күн бұрын
LifeLong Bwana,, you're our last hope after Chilima
@JulitaBotoman
@JulitaBotoman 2 күн бұрын
Suleman tu ndiakatundu enieni oganiza bho ngati m'bale wake Chilima mzimu wake uwuse mumtendere as he has already been said himself 💪💪💪
@HarrisonMwanga-xy4sc
@HarrisonMwanga-xy4sc 2 күн бұрын
Amalawi, Anthu ngati awa,sangamenye, nkhondo yi,okha.amalawi, tiyeni tithandizane,polimbana,ndi zigawenga zimenezi.chifukwa,abwanawa,ali ndi family koma akusiya, family yawo kukaimila amalawi.chomwe, ndi kupepha,potetedza,anthuwa,tonse tikhale,boma.pothana,ndi zigawenga.tisaone,galimoto la chilendo mu dela lathu, ndi kumangoyang'ana.mpaka, Anthu kutuluka mu galimoto atabvala mask ndiye kuti ndi zigawenga zimenezo.muzi,tulukani, nthandidzani,ndikuona ngati titatelo, Malawi athakukhalatso, wabwino.
@GiftGondwe-do2ut
@GiftGondwe-do2ut 2 күн бұрын
God protect suleman malawi people need him
@RhonexKandiero-ig4mr
@RhonexKandiero-ig4mr 2 күн бұрын
Nice analysis
@GiftKossahBangoh
@GiftKossahBangoh Күн бұрын
Machine
@JOHNMATIASI-q7g
@JOHNMATIASI-q7g Күн бұрын
Mbambande bigman suleman mumakwana bigman osaopa
@AndrewMakata
@AndrewMakata 2 күн бұрын
Mr Suleman the machine🎉
@HenryKatopola
@HenryKatopola Күн бұрын
Double salute suleiman
@AmosiChauluka
@AmosiChauluka 2 күн бұрын
The pangorini ❤❤❤❤🎉
@YankhoMtchilima
@YankhoMtchilima 2 күн бұрын
Suleman you are Machine
@ChifundoKaphirikwete
@ChifundoKaphirikwete Күн бұрын
Big up Mr suleman anthu ngati inu ndiamene tikuwafuna pa ballot paper ganizanipo pamenepo bwana
@JosephKayira-j2p
@JosephKayira-j2p Күн бұрын
Koma kumalawi 😢😢😢
@KENBILLY-m3u
@KENBILLY-m3u Күн бұрын
Suleman mulungu axikudalitsa kwambiri ndipo muxakhala president wa dxiko osaopa ndithu ine ndimakhulupira mulungu kut aliyense axalawa imfa tikuneyenera pray hard
@LomosiKanzingeni
@LomosiKanzingeni 2 күн бұрын
More fire me Suleman we are on your back
@StevenDastan-f5y
@StevenDastan-f5y 2 күн бұрын
Suleman akufunika chitetezo chokwanila kwambili
@CharlesChingwalu-q9u
@CharlesChingwalu-q9u 2 күн бұрын
God is with him,he has been protected so God will protect him still
@neemahkapatamoyo9563
@neemahkapatamoyo9563 2 күн бұрын
Amen​@@CharlesChingwalu-q9u
@PeterMorgen-k4b
@PeterMorgen-k4b 2 күн бұрын
The problem about Malawi's politics.All those people you see ku MCP ko azakhamukila kuchipani chomwe chingazawinecho.The worst part of it nothing will change. Same people same mindset
@AimanTwalid-o6o
@AimanTwalid-o6o 2 күн бұрын
Big man big up
@HaloonChikoko
@HaloonChikoko 2 күн бұрын
Bwana Suleman pitilizani ndipo mulungu azikutetexelani ndinu mphangala ya malawi
@terezazakeyo2285
@terezazakeyo2285 2 күн бұрын
Bravo suleiman
@BrianSandrum
@BrianSandrum 2 күн бұрын
God bless u
@SymonMwingitsa
@SymonMwingitsa 2 күн бұрын
Wakula apapa ndi umbuli wawukulu
@PazAutomb
@PazAutomb 2 күн бұрын
That's real... Let's look the plain first and after the plain clush.... Or mwana sangakhulupilile
@RedsonKamzati
@RedsonKamzati 2 күн бұрын
30 years+ MCP ili Ku opposition lero mwai wapzeka m'boma, akuphani nonse olimbana nawo ngati adakwanitsa kuluma Chala chomwe chidawakombela phala inu ndi ndani! Akuphani, Ife ndie sangalimbane nafe angotifinya mkutitumizila njala basi Ife gwaaaaa, koma mudzipemphera anthu inu
@MillieMalakam
@MillieMalakam Күн бұрын
Mcp muziwe izi ngati mapulani anu ozabela mavot tizagawanapo Malawi I'm sure indeed
@GeraldMwamlima
@GeraldMwamlima 2 күн бұрын
Mabodza apa Malawi. Ma vote avuta!
@samueljosephngomwa5331
@samueljosephngomwa5331 2 күн бұрын
True Patriot
@GuejendraMk
@GuejendraMk Күн бұрын
Commentator musamavhulukise kulongolola nsiie I mwini atilankhule than inuyo
@bs-malawi
@bs-malawi Күн бұрын
Kupanda kulankhulira KZbin itidomola. Video yokuti si yathu amafuna tichite contribute mau athu. Tizangochepesa kulankhula zambiri koma sitingasiye
@austenbushiri-cx1kh
@austenbushiri-cx1kh 2 күн бұрын
The pangolin 🎉
@MoreBlessed1234
@MoreBlessed1234 2 күн бұрын
Your indeed
@TamUs-u2h
@TamUs-u2h Сағат бұрын
Muchredwa nazo izi, MCP sikuchoka m"boma
@TamUs-u2h
@TamUs-u2h Сағат бұрын
Ngati Kuli chitsiru cha munthu ndi Suleiman, everything he speaks it's all about politics, ngati Ku Malawi kukhale nkhondo amene ayambitse ndi Alomwe, provoking Chewa tribe don't expect any vote from central region, mukunypza kwambiri achewa. DPP mwalamulira Kwa zaka 13 if not 14, chitukuko chomwe munapanga za ziiii
@AyubTime-x4f
@AyubTime-x4f 2 күн бұрын
SAMIREE IFE TONSE AMALAWI TAKUDALIRA NGATI JOHN CHILEMBWE WATHU .UMAKHWANA .NAMIYANGO, CHIGUMULA CHISWE MANJE MISESA TIKUKWEZASO PAMPANDO UMENEWO
@GiftMusorola-l2o
@GiftMusorola-l2o 2 күн бұрын
Mtolankhani wosaphunzira
@WilfredKazembe-i6q
@WilfredKazembe-i6q 2 күн бұрын
Iwe ngati uli wophuzira vuto lako ñdi chani?
@JafarWiati
@JafarWiati 2 күн бұрын
Iweyo osakhala ntolankhani bwanji kapena school inaku gayani
@SymonMwingitsa
@SymonMwingitsa 2 күн бұрын
Osewa ali apawa ndi mbuli palibe hhi apa
@mchipengule
@mchipengule 2 күн бұрын
Chitsilu ndi iweyo opanda chochitawe!! Chakwera my vote.
@MussaAli-h4i
@MussaAli-h4i 2 күн бұрын
Aaaaaa olo manyazi kumayakhe osakapanga tv yanu bwanji
@SprianoJeke
@SprianoJeke 2 күн бұрын
Inu mulinchochita kupusa
@MussaAli-h4i
@MussaAli-h4i 2 күн бұрын
Iwe ungafane ND ine kkkkkk ine sindnyamula chkwanje kumayenda ntown kut nkut ndpeze chakudya chalelo ayi sindchemelelaso wandle km iye ya ndege Inu ND boma lanu mumaziwapo kathu chfukwa simungamakayakhe ulaliki kkkkkkkkkkkkk chakwera ND olephera
@LamseyLazarous-dl5qd
@LamseyLazarous-dl5qd 2 күн бұрын
Wakamba za chikangawayo ndani apa
@MussaAli-h4i
@MussaAli-h4i 2 күн бұрын
Iwe wanyoza ziti
@emmanuelnyirenda3289
@emmanuelnyirenda3289 2 күн бұрын
Nzeru zosenzi mudakanika kukana APM kukhala nsogoleri bwa?
@MercyChikutubwe
@MercyChikutubwe 2 күн бұрын
Dpp my vote
@finchiadriano
@finchiadriano 2 күн бұрын
Mmmmm mbala izi .,,,,,,,,,,mcp idzawina ndi ma percentage ambiri zed , take my word
@LucyJoacquim
@LucyJoacquim 2 күн бұрын
Over my dead body
@NizigiyimanaChantal-c2p
@NizigiyimanaChantal-c2p 2 күн бұрын
😂😂😂😂😂 hmmmmm chimene Mulungu wakomza sitikuzidziwa timusiye akhalebe Mulungu​@@LucyJoacquim
@HendrickBanda
@HendrickBanda 2 күн бұрын
🙏🙏🙏
@felixcosmas4185
@felixcosmas4185 2 күн бұрын
What do you want to tell us?
@RonaldGama-gz9ug
@RonaldGama-gz9ug 2 күн бұрын
You can not hear what he is saying coz your blinded ear .....Kudabwe ndi Nyau zinakuonongani
@RhodSherif
@RhodSherif 2 күн бұрын
Patumbo pako ndi chakwera wakoyo...
@hashimmakwemba3612
@hashimmakwemba3612 2 күн бұрын
MCP must go pls
@RhodSherif
@RhodSherif 2 күн бұрын
Akubisa black box chifukwaso akudziwa Kuti chilungamo chidziwika....
@CharlesChingwalu-q9u
@CharlesChingwalu-q9u 2 күн бұрын
Big up, sulemani should be the minister of agriculture,big up sulemani
@daviechannel8603
@daviechannel8603 2 күн бұрын
Mmmmmm🎉
@JulyLukas
@JulyLukas 2 күн бұрын
So feeding good man
@GodsFavourite1
@GodsFavourite1 2 күн бұрын
Mulungu akufungatireni bwana Semeer🙏🙌
@AngellaAnge-p7x
@AngellaAnge-p7x 2 күн бұрын
Moyo wanu uli mmanja mwa yehova
@MillieMalakam
@MillieMalakam Күн бұрын
Mcp palibe abadani nothing chimene yachita koma kupha basi Khaza kwa amalawi zovuta kwambili koma chakwela iiiii lazaro wa bible Allah akukwapule ase ndipo amec mukukakamila ndichilungamo kuti muzamuwinise chakwela mukuti azawine koma amec mukupanga mistake kwambili tizagawana ndithu dziko lamalawi
@VAILETBANDA-t1g
@VAILETBANDA-t1g 2 күн бұрын
Kikikik munthu wa mkulu selemani mulungu akusamalileni kwambiri
@AliceChipeta-pc3nb
@AliceChipeta-pc3nb 2 күн бұрын
Ine koma chomwe chinandikhuza kwambili ndi ichi. Anangwirizana kuti ine ndiimila pano iwe ulendo wina koma tinaona akumukana sk poyela
@ChimwemweMkandawile
@ChimwemweMkandawile 2 күн бұрын
Our pangolin
@RelaxCool-dp9jn
@RelaxCool-dp9jn 19 сағат бұрын
Soleimani wulemu wano osaopa osafowoka
@MillieMalakam
@MillieMalakam Күн бұрын
Chakwela ukazangola ma vote kuti ndiwe wawina ase lazaro ndiyazako muzayenda chothawa Malawi muno
@owenchikopa7266
@owenchikopa7266 2 күн бұрын
A DPP mulembe ntchito Leah Malekano azikupangirani program imeneyi.
@JumbeGRASTON
@JumbeGRASTON 2 күн бұрын
DPP
@FrancisLuke-g6i
@FrancisLuke-g6i 2 күн бұрын
Ndipo sitizaiwala zomwe zachitika mchaka ichi cha 2024 kuno ku Malawi.
@ChisomoKapingasa
@ChisomoKapingasa 2 күн бұрын
Mt Muthu ot ndiwachimbu anganene kut timafuna wakut ayamba kuchita
@LydiaMushala
@LydiaMushala 2 күн бұрын
Awatu ndi ma kaladi samaopaaa muyaluka nazo zinazi
@MillieMalakam
@MillieMalakam Күн бұрын
Ndipo sukunama khaladi sasamala zokuva ase ndikuzuwona kuno Cape Town mitchells plain town centre
@AndisoniImuran
@AndisoniImuran 2 күн бұрын
Kodi akufuna atiphe tons?
@BrightonJosilawaka
@BrightonJosilawaka Күн бұрын
Amay mukuyankhulitsa siyani timwere tokha
@GiftBello-v1i
@GiftBello-v1i 2 күн бұрын
They try to silence you , tell them those salvage
@ErnestZagwa
@ErnestZagwa 2 күн бұрын
Ticitepo kathu amalaw 3:16
@MillieMalakam
@MillieMalakam Күн бұрын
Chakwela ndi president ochitisa manyazi kwambili
@MuhammadAlie-b7v
@MuhammadAlie-b7v 2 күн бұрын
We l love you sereman
@AfyawylessKachepa
@AfyawylessKachepa 2 күн бұрын
Chikangawa party sizathek ndizammagaz zokuphaz
@MubarackKathumba-w9t
@MubarackKathumba-w9t 2 күн бұрын
Katundu opanda matha ngat uyu pa Malawi palibe, Mulungu adzitetedza moyo wako.
@Ruthgomonda
@Ruthgomonda 2 күн бұрын
Suleman moto kuti buuu munthu wolimba mtima 🙏
@ChipiriloSandarack
@ChipiriloSandarack Күн бұрын
Khan imeneyo ndiyoona ndpo ndnapanga chisakho choti sizavotaso km pano ndinatha ndpo ndizachita kulawira kukavota APM 2025 boma
@JosephKayira-j2p
@JosephKayira-j2p Күн бұрын
Mumanena bho andale koma mukalowa m'boma eeh
@AnishaMoosa-ej7yr
@AnishaMoosa-ej7yr 16 сағат бұрын
chipolopolo cha Dpp
Thousands gather to celebrate MK party's first anniversary
6:48
Newzroom Afrika
Рет қаралды 23 М.
MDYANGU | 3 JANUARY 2025
26:20
Malawi News Update
Рет қаралды 3 М.
From poverty to progress: 1 year of cash impact | GiveDirectly
3:49
BON KALINDO LERO KUING'ALULA __1 January 2025
18:04
HOT 265
Рет қаралды 80 М.
Saulos Chilima - Mzimu wake wakwiya  zobisika zawululika
4:51
Malawi Top Talent
Рет қаралды 6 М.
Nkhani ya Blackbox si yokambirana; Anthu atopa ndi mabodza a kongeresi
12:07
The Last Fishing Boat - a film by Shemu Joyah
1:49:51
C. Shemu Joyah
Рет қаралды 266 М.