Ndikuopsyezedwa Chifukwa Cha Ma VN - Pastor Shumba

  Рет қаралды 7,880

Nyasa VoiceBox

Nyasa VoiceBox

Күн бұрын

Пікірлер: 40
@JeanBanda-zy6wu
@JeanBanda-zy6wu 2 ай бұрын
Koma ndiye Agape Khombe watchukatu ndi zoyipa but wait a minute there is God in heaven
@isaaczuze
@isaaczuze 2 ай бұрын
Pali zisilu zambilimbili zomwe zikuyikila kumbuyo chakwera chifukwa choti akulamdila ndalama zokuba kuchokera kwa chakwera ....tiyeni muzidya ndalama zokubazo ...ife galu wanuyo sitikumufuna ayi
@ChristopherKazembe-c8t
@ChristopherKazembe-c8t 2 ай бұрын
More fire kuwang"alula agalu amenewa ataophyeze olo mpang'ono pomwe, nzitsilu ibvi kwawo mkuphaaaa basi
@Fanzo-h2l
@Fanzo-h2l 2 ай бұрын
Wabodza bwanji poti Màu Ali pomwepo anthu mumaikira k7mbuyo boma lakuphali bwanji imfa ya chilimatu ikutiwawa amalawi chakwera wavomera kuti report Lori ku state house akufuna kulipeleka ku office yoyenelera wina ndikumakana kuti report silimabwere agalu ife mtanyiwa watiuza kale zalipoti munapha anthu aja muziyenda mothawa thawa Mulungu akukantheni pano mukufuna kuphanso ena kuzolowera koma magazi amunthu akuyenda agalu
@TracyBanda-i2g
@TracyBanda-i2g 2 ай бұрын
MCP ichoke ikudzuza anthu kwambili ,kodi amcp chipani chanji? Utsogoleri oyipa oterewu wabwanji? Mudachosa peter muthari kuti akulakwisa ,Kodi pafika MCP pa sakuyenera Ku chosedwa? MCP yalozedwa ,ndipo Yehova wakuyezani mwaperewera inu anthu achewa oyipa umburi
@LamiziIgshaan
@LamiziIgshaan 2 ай бұрын
mukupanga vn Kut anthu evele kupezeka Kut pambalipo palinso ena akulankhula lankhula ndenkumati anthu amve ziti agalu inu
@StalloneButao
@StalloneButao 2 ай бұрын
Where is our Malawi? Zoopsa kwabas
@YasenYasen-q9g
@YasenYasen-q9g 2 ай бұрын
Osandanda ula hallah mulungu alipo tilinanu
@isaacchiwaula731
@isaacchiwaula731 2 ай бұрын
Kod a pastor anji oyankhula zadziko mmalo mophunzitsa anthu za mau amulungu
@CleverChiumia
@CleverChiumia 2 ай бұрын
Kodi Agape Khombe ali ndi udindo wanting mu MALAWI CHIKANGAWA PARTY?
@isaaczuze
@isaaczuze 2 ай бұрын
Boma la oathu okuba komanso mbava ....boma ili palibe akulifuna .....agape khombe ndi billy malata ndi amene akudya ndalama zokuba kuchokela kwa chakwera . .agalu inu .....mukuonjezela mkwiyo wa amalawi agalu inu
@isaaczuze
@isaaczuze 2 ай бұрын
Chakwera ndi mbuzi ya munthu ....akulimbana ndi anthu oti ankusiya pampando osakonza mavuto amane anthu akudandaula ......chakwera satana iwe .....masiku ako akuwelengeka
@StevenGJohn
@StevenGJohn 2 ай бұрын
Chakwera Chikangawa aziwe kuti nthawi yako yatha unapha Chilima machende ako
@ErnestChansa
@ErnestChansa 2 ай бұрын
Tinganeneso bwanji popeza MCP ndichipani chakupha chipani chovesa chisoni
@francismungu7749
@francismungu7749 2 ай бұрын
Tizikupemphelelani, gulu amati lomenyela ufulu lija 😅 Kodi akumenyela ufulu wa MCP 😂
@isaacchiwaula731
@isaacchiwaula731 2 ай бұрын
Osamatchula dzina la Mulungu pachabe aise, Mulungu siopusa wanva, akuphabe mesa wazishosha wekha😅😅😅 mbusa wanji olowera zadziko
@blessingsnyalo-rp9ko
@blessingsnyalo-rp9ko 2 ай бұрын
Mulungu alinanu ndipo sazalola kuti chifunilo cha satana chichitike pa inu
@SibwenzaLevisoni-gm6rv
@SibwenzaLevisoni-gm6rv 2 ай бұрын
Mcp chipani chamagazi
@giftsululu4274
@giftsululu4274 2 ай бұрын
Kapolo ngat iwe ulinchani kut boma likusake
@GladysndilimbiraBonongwe-g6c
@GladysndilimbiraBonongwe-g6c 2 ай бұрын
Osaopa dziko silachakwera
@MaryNgola
@MaryNgola 2 ай бұрын
Km nde apha anthu angat a mcp wo?
@YellowmanMalawi-qe8zh
@YellowmanMalawi-qe8zh 2 ай бұрын
Mcp nyau zenizeni
@GeshoMwakitwile
@GeshoMwakitwile 2 ай бұрын
Choka chitsiru iwe
@alexandermeke6994
@alexandermeke6994 2 ай бұрын
Iweyo ukuti ndiwe mbusa koma ukupanga nawo izi ukutsogolera nkhosa zake ziti examine yourself fake pastors
@OmegaChingamuka
@OmegaChingamuka 2 ай бұрын
Report ya dege ikufunika kupha anthu 9 kuphatikizapo vice president Chilima anthu inu mudziwe kuti anthu ndi okwiya
@robsonmapeto1911
@robsonmapeto1911 2 ай бұрын
Apha angati agalu achabechabe Iwo adzapita kutiko
@AlexanderBilliat
@AlexanderBilliat 2 ай бұрын
Kwasala pang'ono kucha osadandaula
@ABMWALEBorder
@ABMWALEBorder 2 ай бұрын
Aaaa kaya inu
@lyiemax
@lyiemax 2 ай бұрын
Too bad
@chesterkumwenda
@chesterkumwenda 2 ай бұрын
chakwela machende ake ndi chimwendo
@kondwanivyalema9449
@kondwanivyalema9449 2 ай бұрын
KHOMBE NDI MALATA ZISILU ZA ANTHU
@SydneyMwale-u9w
@SydneyMwale-u9w 2 ай бұрын
Khombe amadutsa apa timuona
@patsonmdwazika3108
@patsonmdwazika3108 2 ай бұрын
Apatu edit inavuttilapo
@VictoriaKumwenda-k6o
@VictoriaKumwenda-k6o 2 ай бұрын
Zisilu ashumbawo sim busa ayi ndichisilu chamunthu
@SaidiMbawa-st6bj
@SaidiMbawa-st6bj 2 ай бұрын
Wabodza uyu uchisilu okhaokha
@VictoriaKumwenda-k6o
@VictoriaKumwenda-k6o 2 ай бұрын
Inu ndinu mtumiki wamlungu bwanj mkupanga ziwiri zwiri anakumanani udindo ndinu achisilu ndi kalindo wanuyo
@ChifundoJohn-w3t
@ChifundoJohn-w3t 2 ай бұрын
Panyelo Pako iweyo wamva usalimbane ndi boni kalindo chonsecho ndiwe wa chikangawa party
@MiddayDeleza
@MiddayDeleza 2 ай бұрын
Amene ali mgulu la chikangawa party sasowo amayikirana ku mbuyo ngakhale akuwona kuti zikulakwika manyazi akugwireni
@DalitsoMatope
@DalitsoMatope 2 ай бұрын
Chakwera adali nda
Namiwa Ndiwe Dolo - Mzika Yokhudzidwa
3:59
Nyasa VoiceBox
Рет қаралды 2,4 М.
A Malawi Akusowa Mtengo Ogwila - Billy Banda
26:24
Nyasa VoiceBox
Рет қаралды 136
Seja Gentil com os Pequenos Animais 😿
00:20
Los Wagners
Рет қаралды 69 МЛН
Человек паук уже не тот
00:32
Miracle
Рет қаралды 2,6 МЛН
Última hora, FRELIMO sem saída
Moz na diáspora
Рет қаралды 1,2 М.
A Chakwera Alibe Mzeru Zoyendetsela Boma - L Pokani Mtimbura Luhanga
19:59
Report La Ndege Ndi Manyaka - Pastor G Shumba
11:53
Nyasa VoiceBox
Рет қаралды 14 М.
Opposition Mphamvu Imaonekela Ku Parliament  - Jaffer Mussah
5:48
Black box and Moses Kunkuyu. 18 June 2024
2:23
Bakili Muluzi TV
Рет қаралды 1,7 М.
Anthu Awa Ayenela Ku Khala M'Boma 2025   Jaffa Mussa
7:38
Nyasa VoiceBox
Рет қаралды 2,1 М.