NKHANGA ZAONA KOMANDA KWA SING’ANGA MZIMU WA BHIYENI WAVUTA NDE KULIBE TUROTU ABWANA

  Рет қаралды 30,963

Malawi Trends TV

Malawi Trends TV

Күн бұрын

Пікірлер: 202
@BenardThomas-p6o
@BenardThomas-p6o 3 күн бұрын
Kmatu mtanyiwa ndikatundu
@DalitsoMatope
@DalitsoMatope 3 күн бұрын
Bushiri 2025 asowe mdziko la Malawi
@JeffreyKambwemba-zs7wy
@JeffreyKambwemba-zs7wy 3 күн бұрын
Exactly
@mcsellahntv6896
@mcsellahntv6896 3 күн бұрын
Ameneyu ndipo ndiwofunika ma demo ake ake.
@DalitsoMatope
@DalitsoMatope 2 күн бұрын
@@mcsellahntv6896 sure,,,zopusa zake azikapangira kutali asationongele dziko
@chrissyamanda5510
@chrissyamanda5510 2 күн бұрын
@@DalitsoMatope ekizakitile Iyeyitu akumenya nkhondo yapansi
@UchizieFMtemela
@UchizieFMtemela 2 күн бұрын
Ndipo zoona olo ngozi zanyanya
@Alkalinebalakas
@Alkalinebalakas 3 күн бұрын
Amalawi anaiwala izi pano chiwanda chalowa mwa anthu avekele m'boma ndilomweli 😢😢😢
@chrissyamanda5510
@chrissyamanda5510 3 күн бұрын
Ndipo akuyesa kuchemelera kuti boma ndi lomweli Ndipo akundinyasamo anthu amenewa
@DoreenLivata
@DoreenLivata 3 күн бұрын
Ayaluka ndipo chilungamo chidziwika ife sitisiyabe kuyankhula za chilima
@eunicesaiti
@eunicesaiti 3 күн бұрын
No peace for the wicked. Rip 9 souls 😢😢😢😢😢😢😢😢😢
@JeffreyKambwemba-zs7wy
@JeffreyKambwemba-zs7wy 3 күн бұрын
No peace for these wicked people
@McDonaldbeketeNkhata-n4l
@McDonaldbeketeNkhata-n4l 3 күн бұрын
Chakwera ndi nduna zake pamozi ndi satana wawo bushiri azasowe muziko lamalawi
@LuciaKalumo
@LuciaKalumo 3 күн бұрын
Ambuye adzikutetexan bro
@MgGiftChivuza
@MgGiftChivuza 3 күн бұрын
Zoona ndithu bro
@Rose-wu5ef
@Rose-wu5ef 3 күн бұрын
Mr Comrade, well come back , mumatimvetsa kukoma
@GibsonMithi-n4y
@GibsonMithi-n4y Күн бұрын
Inenso ndikhumbo langa Kuti mzimu WA chilima ndi anthu ena aja mizimu yawo isagone ndipo isawasiye onse amene anatengapo mbali ndi moyo afe ndithu ifa yowawa
@JessyNellohThom
@JessyNellohThom 2 сағат бұрын
God protect you comrade.son of the soil
@jeanbotomani9081
@jeanbotomani9081 3 күн бұрын
Auze ntanyiwa kuswakuswa
@Rose-wu5ef
@Rose-wu5ef 3 күн бұрын
Chakwela olo atafa wa chititsa manyazi dziko la mw
@thatgirrroskrr3570
@thatgirrroskrr3570 3 күн бұрын
Timava nanu kukoma bro
@moureenmolesi
@moureenmolesi 17 сағат бұрын
chikangawa mulungu akulange pansi pompano ndipo muyaluka simunat a ntanyiwa ulemu wanu 🎉🎉🎉
@HawahMussah
@HawahMussah 3 күн бұрын
Wathu wathu comrade ntanyiwa Amos pa cape town salute
@LuskaMoses
@LuskaMoses 18 сағат бұрын
Amaiwa ndikaona Ngati Mai opeohera opa mulungu omva chisoni Mwana wa amzao eish Mai inu pepheni ambuye Sanga akukhululukireni mudzafa imfa yomvetsa chisoni ndachikangawa anuwo 😢😢 Mai mwandikhumudwitsa sure😢😢
@EllenGomani-i4f
@EllenGomani-i4f 2 күн бұрын
Best Radio ever❤❤❤🎉 mumatimvetsa kukoma Comrade
@DeenesNurudMeke
@DeenesNurudMeke Күн бұрын
Nzaulula ija sinyimbo wamba esh
@LuyoloTlhapane
@LuyoloTlhapane 5 сағат бұрын
Mhu Koma kaya ,misoz yaanthu Osauka ikugwela pathaka tilibeso mphamvu ndife osauka mau athu sapita Patali .God protect u all the time
@gmxplayboy6559
@gmxplayboy6559 3 күн бұрын
Ndipo a Malata sakupuma nanu bwino. Koma Osadandaulayi, munthu akamathamangitsidwa kenako okuthamangitsayo ukanva akukutukwana dziwa kuti wakulephera ameneyo. Asiyeni agaluwa adzikuwa, galu samakuwa galimoto yomwe yangoyima, galu amakuwa galimoto yomwe ikuyenda
@edwinnyasulu2088
@edwinnyasulu2088 3 күн бұрын
Welcome comrade
@S-rr1eu
@S-rr1eu 4 сағат бұрын
Bushiri 2025 ,,, south Africa ikubwera izakunyamule,,,, 10 yrs ukugwira jere ndi azako a MCP ( chikangawa imvi zizaonekera)
@HameedSaleem-o4v
@HameedSaleem-o4v 3 күн бұрын
God bless ntanyiwa tikuziwa kut MCP sikufunizabwino plz be safe Mr ntanyiwa
@lyiemax
@lyiemax 2 күн бұрын
Eeeeeh koma anthuwa ndi zilombo, very happy to have you comrade our redeemer, proud of you always ❤❤❤❤
@EsetaGerate
@EsetaGerate 3 күн бұрын
Verentino kukamwa ngati wadya manyi😂😂
@BlessingsMphamba
@BlessingsMphamba 3 күн бұрын
Ameyodi ayenda mwa sing'anga sanatiii....mzimu wa munthu ndowopsa 😢💔😢
@FunnyDimSum-hk1so
@FunnyDimSum-hk1so 3 күн бұрын
Ndipo sanati amva nyunyu mumakwana atanyiwa
@TimeAbilu
@TimeAbilu 8 сағат бұрын
Umakwana a comrade mtanyiwa more fire
@LuskaMoses
@LuskaMoses 17 сағат бұрын
Iwo akupita kotenga kakhara ife pomwe tupinda miyendo kupepherera kuti asowe mtendere ndi imfa ya chilima😢😢
@OjessTetezan
@OjessTetezan 2 күн бұрын
Mmakwana inuyo keep it up to inform us .
@khoviwaedward
@khoviwaedward 3 күн бұрын
Comrade Ntanyiwa ndiwe no 1 bro palibenso ayi. Joker yo musunge pa bwino brother adzapweteke mcp next year before election.
@FunaniChagwira-ue5pl
@FunaniChagwira-ue5pl 13 сағат бұрын
Mtanyiwa ndiwe a katundu God bless you
@IsaqueFernandoAntônioAntônio
@IsaqueFernandoAntônioAntônio 3 күн бұрын
Ndasangalala potidziwitsa zambili lero,mulungu akudalitseni komanso akutetezeni
@BeatriceKennedy-b1b
@BeatriceKennedy-b1b Күн бұрын
More fire comrade mtanyiwa
@AuphieBannet
@AuphieBannet 3 күн бұрын
Tili naanu ANTANYIWAAAAAA ❤ Ndipo MULUNGU adzikudalitsani ndikukutetezelani ameen 🤲
@fedson2050
@fedson2050 3 күн бұрын
Bwana Comrade Ntanyiwa mumakwana, ndipo mulungu azikutetezerani thawi zonse. Amen
@DeenesNurudMeke
@DeenesNurudMeke Күн бұрын
Nzaulula ija Sananame di esh
@SalomeManda-c1i
@SalomeManda-c1i 3 күн бұрын
Ndimadabwa kt a ntanyiwa not tingogona osamvera nkhanga zaona?
@TameeraInglis
@TameeraInglis 3 күн бұрын
Comrade Nthanyiwa may God protect you with the blood of Jesus christ.
@WarriorKB-u3k
@WarriorKB-u3k 14 сағат бұрын
Commander amenei chisilu ch a mache amenei bushiri,chikangawa pamodzi ndi MCP yonse akuyenera kufa ndithu.Mizimu imenei yonse isonkhane iwakutumule onse anthu a satanic opanda a mawo,zisilu inu tachioneni chimutu ngati fuwa la kachaso APM voti yathu.Ntanyiwa,kalindo ndi ena nonse timakunyadilani god bless u gyz we are in this 2gerthr
@YonaPearson
@YonaPearson 3 күн бұрын
Mwatulukira mundu wakulu tinakusowa kwambili nditu mulungu Akupase moyo wautali
@HajjAmadu-e1u
@HajjAmadu-e1u 3 күн бұрын
Tchimo kudzudzatu simuzingona muona
@DeenesNurudMeke
@DeenesNurudMeke Күн бұрын
Limpopo fm number 1
@Yoxym
@Yoxym 3 күн бұрын
Usamasowe choncho mtanyiwa uzatipha ndi bp🎉😢
@CassimJafali-g4l
@CassimJafali-g4l 3 күн бұрын
Chakwela agwa BP pompano
@DeenesNurudMeke
@DeenesNurudMeke Күн бұрын
Ndipo kwambiri
@WarriorKB-u3k
@WarriorKB-u3k 2 сағат бұрын
Ya comrade uwatchule ayaluke ,tiwadziwe b4 chisankho
@PatriciaAlomwe-oz8wc
@PatriciaAlomwe-oz8wc Күн бұрын
Mulungu wathu ndi wa moyo ndipo sagona sazagonaso skefa chimoto Thoko katimba mutuluke chigwirizano cha abambo musochelesa nkhosa za mulungu
@StarchJonas
@StarchJonas 3 күн бұрын
Ma MP amenewo adyeretu ndalama zamagazi zawozo koma mizimu izakwiya 2025 sakuzalowanso m'boma
@TioneManda
@TioneManda 3 күн бұрын
Mr mtanyiwa mulungu azikudaliseni nthawi zonse akutetezeni mumativesa kukoma tili pa mbuyo pano
@BysonPhiri-gu4io
@BysonPhiri-gu4io 2 күн бұрын
Fire 🔥🔥🔥
@berlz12k
@berlz12k 3 күн бұрын
UDF ikupanga ubale ndi MCP Kodi mesa anawaphera shanil and kuli ana komatu ndalama inamperekadi yesu mwamva🙌
@LameckNgwangwa
@LameckNgwangwa 3 күн бұрын
Machineee
@AnnieKalipo
@AnnieKalipo 3 күн бұрын
Mumatimenyela nkhondo , Mr m'tanyiwa mulungu yekha azikupatsani Moyo Wautali .
@IssahAluba
@IssahAluba 2 күн бұрын
😂😂😂 Esh zilikotu
@Lydia-t4b
@Lydia-t4b 2 күн бұрын
ankapangiranji akhaula kukatenga ziwanda kwa sing'angako
@VajraBanda
@VajraBanda 3 күн бұрын
Timava nanu kukoma bro
@VajraBanda
@VajraBanda 3 күн бұрын
🎉🎉🎉🎉🎉🎉😂😂😂😂
@AbuZunairaHanafie
@AbuZunairaHanafie 2 күн бұрын
Ntanyiwa mumatimilira osafooka tiyenao asatanawa
@ChipanganoMajawa
@ChipanganoMajawa 2 күн бұрын
Ndiri okondwa kuti kumalawi kwadzuka anthu olimba mtima ngati inuyo kuulura zinsisi zakuya ngati izi opanda mantha,May God protect you sir
@BerthaKasambala-y5k
@BerthaKasambala-y5k 2 күн бұрын
Tchimo rimazunza orichita rero ndi izo ndarama murinazo km simukugona usiku baibo rinat munthu wachuma ndikovuta kukondweresa yehova siizi kodi chakwera panopa aribeso nthawi or kungo ganizako kt kumwamba kuri chauta
@MussahWilliam-py1ff
@MussahWilliam-py1ff 2 күн бұрын
On fireeee comrade ,timakunyadiran bro
@MussaChilembwe
@MussaChilembwe 3 күн бұрын
Welcome back mr comrade ntanyiwa Allah alipo Akatisungabe mpaka Inshaa Allah next year achoke crocodile 🐊 pampando wakupha ameneyo ndi manganya koma Allah akulangani ndithu
@GraceLimani-zw7dx
@GraceLimani-zw7dx 2 күн бұрын
Mai joice banda shame on u masten mene maavetsera chisoni ndi kukhala mu chipani cha magazi mwana wanu munapereka nsembe kwa bushiiri pano kumapusitsa amalawi ambuye akulangeni mai joice banda munamuphaso chilima ndikumati mwana wanu
@BryantLusungu
@BryantLusungu 3 күн бұрын
Azafa chifufu
@LuyoloTlhapane
@LuyoloTlhapane 5 сағат бұрын
God protect you
@peterbyson6269
@peterbyson6269 17 сағат бұрын
Yes ziyawa manje guys nazoni ife vuto tilikutali ndikanajoina nawo
@AlexKaunda-ny2eg
@AlexKaunda-ny2eg 8 сағат бұрын
Osapotodza history chakufwa chihana ndiye mwini matipate
@MarkDominico
@MarkDominico 2 күн бұрын
Ena tidakwera yachakwera ❤❤
@felistasbunu9824
@felistasbunu9824 Сағат бұрын
17:46
@AndrewSimakweli
@AndrewSimakweli 2 күн бұрын
Bravo ntanyiwa
@idahntchito
@idahntchito Сағат бұрын
Amtanyiwa #1
@EmilyBanda-xx8gd
@EmilyBanda-xx8gd 3 күн бұрын
Munasowatu timaopa kuti akupezani kodi your welcome Mr
@FrancismbeweChitsotso
@FrancismbeweChitsotso 2 сағат бұрын
Pitilizaniiiiiii comrade Mtanyiwaaaa
@HajjAmadu-e1u
@HajjAmadu-e1u 3 күн бұрын
Koma phiriwa kuipa kwake kwa nkhopeko akungoyeneradi kupha munthu
@DalitsoMatope
@DalitsoMatope 3 күн бұрын
Kumposa kadzidzi
@RemitterFlik1130
@RemitterFlik1130 3 күн бұрын
Ndipo amenewa Ali pabanja abambo amenewa or amati mamuna amakongola nthumba koma awaso eeee ayi ndithu
@kasimmussa-c5v
@kasimmussa-c5v 3 күн бұрын
Mr Tanyiwa Tinakusowan ❤❤❤
@MosesChazima
@MosesChazima 3 күн бұрын
Fayaa mabomba iweyo mtanyiwa
@MariamJaffali
@MariamJaffali 3 күн бұрын
❤❤❤❤❤🔥🔥🔥🔥🔥
@Stewartchikoja
@Stewartchikoja 3 күн бұрын
Ntima wapwa ntayiwa tamva mau
@GIFTPAUL-c9s
@GIFTPAUL-c9s 4 сағат бұрын
Ukunamatu iwe umango lubwalubwa kuchikamwa konyasako garu wacha bwechabwe iwe
@TameeraInglis
@TameeraInglis 3 күн бұрын
Chilichonse. Chikangobwela poyela. Basitu zimakhala zasuluka
@moureenmolesi
@moureenmolesi 17 сағат бұрын
ndipo zowona
@TameeraInglis
@TameeraInglis 3 күн бұрын
Tsonotu nkhope. Ya avalentonowo ndi asing'anga. Kale paokha.
@anicakandiado
@anicakandiado 3 күн бұрын
,😂😂😂😂
@chesterphiri7523
@chesterphiri7523 50 минут бұрын
Iiii inutu muli ndi nsambi 🙈 chani????😂
@samanthamuller7643
@samanthamuller7643 3 күн бұрын
Tanyiwa ndakatundu awa
@Laurent-h9u
@Laurent-h9u 2 күн бұрын
❤❤❤😢😢😢
@georgemalola4507
@georgemalola4507 Күн бұрын
😅😊
@NelsonBanda-j1f
@NelsonBanda-j1f 2 күн бұрын
Mtanyiwa umatha
@RachealPongolani
@RachealPongolani 3 күн бұрын
😂😂😂😂kom Mtanyiwa kuseka kokha utha kugwa nd BP 😂😂🙌
@jameskachulu8141
@jameskachulu8141 3 күн бұрын
Bushiri 😂😂😂😂😂
@ChikhuMasanjala
@ChikhuMasanjala 2 күн бұрын
tiuzen''zambili'
@ulemunkhoma2867
@ulemunkhoma2867 3 күн бұрын
Tinaku sowana
@ulemunkhoma2867
@ulemunkhoma2867 3 күн бұрын
Tinaku sowani Mr
@StellaCharmer
@StellaCharmer 4 сағат бұрын
Grace uja anali mwana wamulungu weniweni
@zimmekapachika6784
@zimmekapachika6784 3 күн бұрын
Anya nayo sanati,angolubwa lubwa game yawo sikuyenda😅😅😅😅😅😂😂😂yomweyo Chikangawa Silimangeni 😅😅😅😂😂😂😂
@RodrickPhiri-j8e
@RodrickPhiri-j8e 3 күн бұрын
Mr comrade Mulungu akuze malire achitetezo chanu komanso kukupasani moyo wautali
@AdamJohn-z9u
@AdamJohn-z9u Күн бұрын
Koma ayaluka
@LameckNgwangwa
@LameckNgwangwa 3 күн бұрын
Ndipo live
@MISHECKBANDAH-m3h
@MISHECKBANDAH-m3h 3 күн бұрын
My role model mtanyiwa almighty GOD protect u.
@ZikaniJere
@ZikaniJere 2 күн бұрын
Long live mtanyiwa. By the way I need those tracks there's content in there
@DavidJackson-ox4xm
@DavidJackson-ox4xm 3 күн бұрын
I support Limpopo FM with Comrade Mtanyiwa
@WarriorKB-u3k
@WarriorKB-u3k 14 сағат бұрын
Gyz ma church onse a bushiri tikuenela tiwawotche chisilu chimenechi chikutionongela dziko, walowetsa satanic mmalawi tiyamba kuotcha ma church ake pomaliza pati pakumane nae ife bushiri timuotchela pompo ana opanda amawo alibe ntchito
@ChimwemweSauka
@ChimwemweSauka 3 күн бұрын
Welcome my brother ntanyiwa
@HarryMakwale
@HarryMakwale 3 күн бұрын
You are number one mr
@arafatMtyala-bo8ev
@arafatMtyala-bo8ev 3 күн бұрын
We love you brother ntanyiwa
IMFA YA CHILIMA ENA AKUDYERERA - COMRADE NTANYIWA PA LIMPOPO FM.
27:43
Mpungwe-Pungwe mw
Рет қаралды 15 М.
NKHANI YADZIDZIDZI - COMRADE NTANYIWA PA LIMPOPO FM
19:11
Mpungwe-Pungwe mw
Рет қаралды 15 М.
GIANT Gummy Worm Pt.6 #shorts
00:46
Mr DegrEE
Рет қаралды 107 МЛН
ОТОМСТИЛ МАМЕ ЗА ЧИПСЫ🤯#shorts
00:44
INNA SERG
Рет қаралды 4,8 МЛН
Israel strikes Houthi rebels in Yemen | LiveNOW from FOX
10:35
LiveNOW from FOX
Рет қаралды 666 М.