NKHANI ZAKE MPAKA KUFUNA KUMUZEMBETSA MWANA WA MAYI KULI KUTSEKA CHILUNGAMO

  Рет қаралды 8,354

Malawi Trends TV

Malawi Trends TV

Күн бұрын

Пікірлер: 40
@FelixMachika
@FelixMachika 2 күн бұрын
Udziyankha, usangoti mutu ngati choswera malambe apa. 😊😊😊😊😊😊😊😊😊😊😊😁😁😁😁😁😆😆😆😆😆😀😀😀😀😀☺️☺️☺️☺️☺️😄
@Homeofpeace321
@Homeofpeace321 2 күн бұрын
Zakuphedwa kwa chilima ngati mukutenga zachibwana a MCP tiphanapo, Tikulila tsiku ndi tsiku kumulila Chilima, don't joke with that death ku MCP enough is enough.
@jamessheki4293
@jamessheki4293 Күн бұрын
Ankayesa atitha
@MarthaMbewe-uk5nn
@MarthaMbewe-uk5nn Күн бұрын
TACHIONENI CHI RICHARD CHIMWENDOCHO DANZI NGATI KUTSOGOLO KWA JOMBO
@JeffreyKambwemba-zs7wy
@JeffreyKambwemba-zs7wy Күн бұрын
😂😂😂😂 mmayi iwe apa nde walasa eti kkkkk
@CathreenKadwala
@CathreenKadwala 17 сағат бұрын
Abale musatisekese chonde mimbamu mulibemo kanthu😅😅
@kasimmussa-c5v
@kasimmussa-c5v 2 күн бұрын
Ndagalu amenewo mbuzi zawantha
@misoMoyo
@misoMoyo 2 күн бұрын
Eeeeeh zafika pamenepo kmatu sizithekai chifukwa chill Chonse chinachitike Kwa Mary akhala a Chikangawa zoopsatu kwambiri
@zimmekapachika6784
@zimmekapachika6784 Күн бұрын
Ayelekeze kumosowetsa ndipomwe atawadziwe amalawi
@AgnessKalindo
@AgnessKalindo Күн бұрын
Tili konko osaopa,osafooka kmaso osatopa more fire mary . Ife timamva kuwawa kwambiri nanga iwe? Anyani amenewa tidzawaonesa tidzaloreraso kufa.
@AuphieBannet
@AuphieBannet Күн бұрын
More 🔥 fire Mr KANGAWUDEE❤
@babranzima8120
@babranzima8120 Күн бұрын
Tilinanu limodzi mayi mary chilima, South Africa
@StarchJonas
@StarchJonas Күн бұрын
Kkkkk koma mametedwe ama minister aku Malawi,,,, kkkkk golira chani?????
@ElizabethMulinde
@ElizabethMulinde Күн бұрын
Pushubekitu😂😂😂😂😂
@ElizabethMulinde
@ElizabethMulinde Күн бұрын
Apenga misalatu anthu awawa sure chomwe akupanga sakuchidziwa
@AlidihGanie
@AlidihGanie Күн бұрын
Mbambande
@Halima-i4x
@Halima-i4x Күн бұрын
Kkkkk😂😂😂😂😂😂😂😂 koma kuli anthu amalangula eeeeee chikangawa unaziyamba wekha kunyasa kwangophe ndi mtima omwe kkkkkkkkkk fiti zisowa ngophe??????
@MariamJaffali
@MariamJaffali Күн бұрын
Tili limozi mayi chilima osaopa osafooka osapopa malawi ndiwanthu uyu siwachakwera ayi
@BeckhamDavid-v6c
@BeckhamDavid-v6c Күн бұрын
Zafika pochimwitsana anthuwa akufuna kupha amalawi ose
@ephraimphalawala4720
@ephraimphalawala4720 Күн бұрын
Eish
@DauglasBowa
@DauglasBowa Күн бұрын
Tiyeni pasewu akutionelera akanganya amenewa
@HaroonAbdulrazackKazembe
@HaroonAbdulrazackKazembe Күн бұрын
Kamajekete nde ali khope ina ina2😂😂😂
@IsaqueFernandoAntônioAntônio
@IsaqueFernandoAntônioAntônio Күн бұрын
Mulungu pulumutsani anthu anu kumalawi
@OssmanAbubaker-w3x
@OssmanAbubaker-w3x Күн бұрын
Ulemu wanu brother
@OssmanAbubaker-w3x
@OssmanAbubaker-w3x Күн бұрын
Osaopa osafooka osatopa
@VanessaAlinafe
@VanessaAlinafe 16 сағат бұрын
Kodi inu anthu akumalawife timulephera kupazamphavu kukhoza Malawi wathu chifukwa chanthu wosachepa ndi 10 safika zoona koma ,ndiposo nkhani ya Chilima zikuziwika kuti bomalo ndilomwe linapha Chilima koma Amalawi tikulephera kupanga chigamulo zoona ai pamenepa ndipomwe tikudziwikilathu kuti Amalawife umphawi unakatikakamilabe chifukwa chamantha
@AndrewjemesJemes
@AndrewjemesJemes 21 сағат бұрын
Chiweluze chiliko Chaka chamawa mu September CA mcp kungopanganso mistake uvota pa mbari malawi watha
@FrancisDominic-w1s
@FrancisDominic-w1s Күн бұрын
Dziko muno mulipo anthu below 20 million kod atapasa wina aliyese 1 million banja lilirose dziko silingatukuke?
@mabvutomichaelpanagona1949
@mabvutomichaelpanagona1949 Күн бұрын
Kodi amene amakhala ndi maganizo nthawi zonse omanga anthuyu kweni kweni ndindani dyabulosiyo?
@LoutChionda
@LoutChionda Күн бұрын
Akuti zikhale ng'oma 🥺 ng'oma zimenezo mukayimbira Ku ndende🙄🥺
@JeffreyKambwemba-zs7wy
@JeffreyKambwemba-zs7wy Күн бұрын
Adali ndii ntima woti a chilima ndi u handsome wawo uja u President ukadawakhala kwambili kuipa kwa ntundu wanji achakwela ndi mai akunyumba kwanu nonse kuipa nkhope ngati sinu akumalawi
@DanielMjasten
@DanielMjasten Күн бұрын
Komatu malawi
@Faida-v7m
@Faida-v7m 38 минут бұрын
Ambuye akuyendeleni achakwela ndiathu anu
@MchachaGoodson
@MchachaGoodson Күн бұрын
Chakwela is cawrd he must come back home there's nothing he is doing on his Trip all bad things happen when is here.Abusa abusa omwe sindinawamvepo akutchulapo zachikodi pa misokhana yawo eve mentioned one word from the bible.
@AtupeleChitenje
@AtupeleChitenje 20 сағат бұрын
Uyu wamutu ngati chigumu chopelewela sodayu chimwendo
@Faida-v7m
@Faida-v7m 39 минут бұрын
Iiiiiiiiiii km mumava chitsomo inu, komatso kupanda chilima simukanawina mwava.
@AnnieKalipo
@AnnieKalipo Күн бұрын
Zoona osaopa ,Osatopa ,Osafooka ,
@ednanamboyachilambe6901
@ednanamboyachilambe6901 Күн бұрын
Mulungu alowelelepo
@Lunnah-b1t
@Lunnah-b1t 17 сағат бұрын
Awuzeni zenizeni ,masatanic,akumidima
@WisikiBlack-gj4gu
@WisikiBlack-gj4gu Күн бұрын
Mai chilima chonde more 🔥 🔥 ife amalawi ifa ya chilima imatiwawa kwambili tikaganiza tchito yomwe anagwilila amunanu mmmmm ayi zosathekha
Миллионер | 1 - серия
34:31
Million Show
Рет қаралды 2,2 МЛН
А ВЫ ЛЮБИТЕ ШКОЛУ?? #shorts
00:20
Паша Осадчий
Рет қаралды 9 МЛН
Mfumukazi - 2 October 2024
29:00
Times 360 Malawi
Рет қаралды 1,6 М.
Israel keeps up bombardment in Lebanon
7:57
SABC News
Рет қаралды 9 М.
Миллионер | 1 - серия
34:31
Million Show
Рет қаралды 2,2 МЛН