Joab ndifunsile funso ili,,ndinamva kuti Asprin amapanga kuchokera ku ubongo wamunthu yemwe wachita ngozi,,,in short onse omwalira pangozi amawachotsa ubongo for asprin
@pempheromulepa928128 күн бұрын
Not true. Pharmacognosy ya aspirin is from reactions that's chemistry. It's through combination of elements to make acid. That's why aspirin in chemistry is called ASA. ASA is acid form
@HamiltonwaNamuwahАй бұрын
Ishii koma Joab
@BlessingsTembenuАй бұрын
Kkkkk Koma Joab iweyo ayise,katundu tigawana ikani nkhosi njoka😂😂😂
@PatrickZinenanie24 күн бұрын
Joab uzafera zaeni
@jameslweya-eo1ujАй бұрын
Joab , kugwira njoka
@HenryMikithayoАй бұрын
Mmmm guys koma nowadays internet itionetsa zinthu zosaoneka ndithu mpaka kumakadula ubongo wamunthu iiiii nawe chakhaza interview inayi ayi ndithu