Bon Kalindo and Kamlepo Kalua Arrested - Mulanduwake Uti? (Is It Section 60 of Malawi Penal Code?)

  Рет қаралды 17,063

Nyasa VoiceBox

Nyasa VoiceBox

Күн бұрын

Today, we explore the arrests of Bon Kalindo and Honourable Kamlepo Kalua. As far as we know, they have been arrested for contravening cybersecurity laws related to publishing fake information regarding the Chikangawa plane crash. So, on Nyasa VoiceBox, we took the opportunity to educate our subscribers and Malawians at large on some of the laws that the government can legally use to prosecute and punish those who publish false information online.
Lero, tikufufuza za kumangidwa kwa Bon Kalindo ndi Honourable Kamlepo Kalua. Monga tikudziwira, amangidwa chifukwa chophwanya malamulo a cybersecurity okhudza kufalitsa nkhani zabodza zokhudza ngozi ya ndege ya Chikangawa. Choncho, pa Nyasa VoiceBox, tidapeza mwayi wophunzitsa anthu olembetsa komanso Amalawi kwaukulu malamulo ena omwe boma lingawagwiritse ntchito mwalamulo pozenga ndi kulanga anthu amene amafalitsa nkhani zabodza pa intaneti.
#malawi

Пікірлер: 113
@MarvGerald
@MarvGerald 2 ай бұрын
Kd malamulo amenewa ayamba liti?? Nthawi ya UDF,DPP,PP. Malamulo amenewa kunalibe or fake news kapena tiziti social media yayamba ndiusogoleri wa Chakwera omweu. Nthawi yazipani zapita zija anthu sakalankhula,mwachiziwikire boma ili likugwiritsa mphavu moputsa ndiye tosefetu atitha kutima cz maganizidwe ndiosiyana siyana km zonse ife tikuona ndipo mbiri ikusungidwa 2025 sikale.
@kenmasta
@kenmasta 2 ай бұрын
Inenso kudabwatu kuti Kodi malamulo amenewa abwera udf,dpp,ndi pp zitachoka....koma chilungamo chake mchakuti boma ili lilindimantha lathapo apa
@bwenguking3894
@bwenguking3894 2 ай бұрын
Malamulo amenewa alipo ndithu kuyambila kalekale. Vuto linalipo nthawi ya zipani zinazo ndilakuti amatayilila (lack of enforcement). Kamlepo ngati phungu wakunyumba yamalamulo akuwadziwa malamulo amenewa.
@ImanRashidi-so4oo
@ImanRashidi-so4oo 2 ай бұрын
Zopusa basi
@SteveChirwa-ne9nt
@SteveChirwa-ne9nt 2 ай бұрын
Iwenso chitsilu ukukhalira umboni MBC yako ndi Chakwera wanuyo apolisii nawonso mbuzi
@PhillspicJere
@PhillspicJere 2 ай бұрын
Kodi mukuti Chan nanu inu?
@BenBotolo
@BenBotolo 2 ай бұрын
Kamulepo played a critical role on channel Africa in early 1990s, we are all beneficiaries of his voice on channel africal
@joyahmedjoma4615
@joyahmedjoma4615 2 ай бұрын
Abwele azatitenge ife tose tikupanga ma comment aaaaaaa chakwera waziwa bwanji kuti ndinkhani za bho ndi zoona zimene amanena bon kalindo ndipo muziwe kuti sazasiya kuyankhura ok akabwera atiuza zomwe waona iweso
@Homeofpeace321
@Homeofpeace321 2 ай бұрын
Chakwela wapha chilima, anathila dala mafuta ochepa mundege kuti igwe. Zonsezo tikuzidziwa
@joyahmedjoma4615
@joyahmedjoma4615 2 ай бұрын
Kukuyu ndi budzi yamunthu afiti wose
@SheenahMwalabu-iz3pr
@SheenahMwalabu-iz3pr 2 ай бұрын
Komatu nthawi ya Peter Muntharika anthu tinkamunena kuti akupha ma albino koma Chisale ndi dpp simamangako anthu even Peter yo ankanyozedwa, kuvinitsidwa ngati cartoon koma sanamange omuseweretsa cz amadziwa kuti ndi democracy. A Chakwera ndi tonse alliance anatilonjeza kuthetsa njala, nkhaza, kuphedwa etc. Koma palibe zinasinthako ever since analowera mboma, mavuto ndendiadeile, kuphedwa, kumangidwa, kukwera kwazinthu eishhh Chilima RIP we are hoping Usi, Manganya to take mcp down cz we only believe and trust in you ndi mulungu 😢
@eliffagondewe8214
@eliffagondewe8214 2 ай бұрын
Ndipo zoona angofuna ku tseka anthu pakamwa basi asamayankhule anthu oipa awa..
@eliffagondewe8214
@eliffagondewe8214 2 ай бұрын
Kodi nanuso ndi anthu angati amene sakuyankha za kuphedwa kwa chilima bwanji onsewo sanamangidwe, zinazi so mudziwopa mulungu please..
@aliwilson7705
@aliwilson7705 2 ай бұрын
Inu chakwera ndi wakumpa
@hanifahmponda8711
@hanifahmponda8711 2 ай бұрын
Chakwela wakupha basi mwananga mutsamange a MCP bwanji chakwelayi kale kaja amanena kuti ndikhetsa mwadzi umenewo nde mulanthu DPP imangokutsiya lelo a MCP wina kunena mawu ngati omwewo mumva mabgeni CHIMENE MUNGADZIWE MCP BOMALI AMENE ANAKUPANGITSANI KUTI MUKHALE BOMA NDI UYU MWAMUPHA NDENO 2025 MUCHOKA PAMENEPO ZONUNKHA MUKUPANGA ANTHU ATOPA NADZO loko mukutsanga mwana wa John tembo kukhala wakulu oyang'anila chitsankho CHAKWELA IWE GALU KWABASI UCHOKABE 20225 MIDZIMU YAKUYA KULAMULA DZIKO NGATI UKULAMULA NYAWU KUMANDA dzikoli silachipani chimodzi wabwela mudzipha anthu ngati 1960 anthu otsayankhulapo 2025 MUDZALIMVA DZIKO KUWAWA INU MULUNGU ACHITE NANU
@MasterBlack-r2n
@MasterBlack-r2n 2 ай бұрын
zisilu Za anthu mu boma ili.. Koma it's over... bon kalindo amalankhula chilungamo komaso anthu tikulankhula chilungamo kut, boma ili ndiyakupha,kuba,kuwopseza komaso kuwononga. nde chifukwa chot bon kalindo sanyengelera amaswa kuswa nchifukwa chake amamva naye kutentha. God almighty chitanipo kanthu chonde takupokeleran😭😭🧎🏾
@maybingoma8247
@maybingoma8247 2 ай бұрын
muthandizeni imwe banthu bon kalindo osati mungokamba kamba yayi
@user-oq5rg5mz7q
@user-oq5rg5mz7q 2 ай бұрын
Ndiye Onamawo apezeka awili okhawo, Ngati ndicho chakwela nayeso akamtape, Ndiye oyamba kwanamiza aMalawi muzambili , komaso malamulowo chifukwa China Sama gwila ntchito nthawi ya DPP, UDF & PP aya kwawgilitsa nthito pan boma lolephela ndichocho malo mobweletsa chitukuko Kumango manga anthu
@MasterBlack-r2n
@MasterBlack-r2n 2 ай бұрын
zisilu Za anthu izi... bon kalindo adalankhula chilungamo. that's why boma limamva naye kutentha
@KondwaniMunthali-vf1ws
@KondwaniMunthali-vf1ws 2 ай бұрын
Malawi is a member of UN and it has signed a charter,, section 17 where by Treedom of Expression is a birth right of all
@actuarialscience2283
@actuarialscience2283 2 ай бұрын
Chakwera must go
@ChikondiChauma-ib9pg
@ChikondiChauma-ib9pg 2 ай бұрын
Akungotengera khaza chabe
@MasterBlack-r2n
@MasterBlack-r2n 2 ай бұрын
Wina adanenapo kut amene akuikira kumbuyo boma ili...ndi mmene anthu tikuvutikira mdziko lathu lomwe, ameneyo ndi mfiti,komaso ndi wasatanic. ndavomelezadi. nonse amene mukuti boma ili lilibwino kunena kwake mukumati MCP 2025 boma,,, ndinu asatana. chimene mukufuna nchakut , dziko lizatsale bwinja tonse mutatipha. Mulungu akanthe nonse kuyambila kumtundako
@SamuelLiphava-p4u
@SamuelLiphava-p4u 2 ай бұрын
Km Ku Malawiko mavuto alipo,Apa anthu ndye muthera kundende
@CHAKAKACHAKA-MANMW
@CHAKAKACHAKA-MANMW 2 ай бұрын
Kkkk boza ndilija mumatiwuza zaku CHIKANGAWA akulu akulu 😂😂😂
@Yanjanani
@Yanjanani 2 ай бұрын
Kd Malamulo amakhuza Kalindo yekha Nanga anja amat ndenge yasowa pamene itagwa aja sazengedwa mlandu wabodza?
@LahimuKamwendo-hj9ct
@LahimuKamwendo-hj9ct 2 ай бұрын
Rest peace chakwela
@Robertmkango
@Robertmkango 2 ай бұрын
MBC ndi chakwerayo padyapawo osewo awiliwo siworakwa akuyakhula chilugamo chakwerawo ndiwakumpha iyeyo ndamene akufunika kumagidwa Dpp and udf, fomo, utm chitanipo kanthu awiliwo akumagidwa kambar kayinu akufera chilungamo ??
@MussaNgoma-r2k
@MussaNgoma-r2k 2 ай бұрын
Well done guys ❤❤❤
@CaptainNyenga
@CaptainNyenga 2 ай бұрын
zapantumbo akupangazo konzani Kaye dziko kenako muzipanga za DC vuto mumadana ndi chilungamo kutiyambadala kumeneko Amusiye Born kalindo
@duncanimajidu5893
@duncanimajidu5893 2 ай бұрын
Galu iwe kwambili akutuma a MCP?
@GeorgePhiri-ub2of
@GeorgePhiri-ub2of 2 ай бұрын
Akulu akulu dziko lililonse limakhala ndimalamulo ndiye mukamangopeka khaki ndicholinga kuti akutameni akumangani ndithu
@MasterBlack-r2n
@MasterBlack-r2n 2 ай бұрын
muli mbali it? cos mmalamulo mulibe kut munthu atha kumangidwa chifukwa chobweresa nkhani pa media.
@IshumeilHaroon
@IshumeilHaroon 2 ай бұрын
Malamulo amenewo ndi opusa kwambiri malamulo omangomutenga kalindo ndi kamlepo kaluwa ndichifukwa chani malamulo amenewo samangwila ntchito kwa athu amene akuba ndalamawo zachambatu zimenezo atuluseni athuwo muwamangile Zina osati zimene akunenazo zawusilu basi
@JamesAnusa-vd6hh
@JamesAnusa-vd6hh 2 ай бұрын
It's to much people is talking about that u know that
@actuarialscience2283
@actuarialscience2283 2 ай бұрын
Popeza a Kumkuyu akuopseza anthu ndiye pa Malamulowa a Kimkuyu wo sakulakwitsa?
@CaptainNyenga
@CaptainNyenga 2 ай бұрын
Kodi maramulowo azingogwila ntchito Kwa anthu osauka ndianthu angati amalakwila malamulo koma osamangidwa muzamale DC osamuphaso muziona
@MiddayDeleza
@MiddayDeleza 2 ай бұрын
Nanga boni kalindo yu amanama ngati? Kamulepo kaluwawonso alakwa chani? Mmayesa amanena Zowona? Zoopsya kwabasi Malawi yohhhhhh mhh
@MemoryKaunda-js9qv
@MemoryKaunda-js9qv 2 ай бұрын
Nzokhuta zokha zokha malamulo anu ayanbira pa athu awiliriwa or bwanji mumanga malawi yensetu ndiye
@Moses51
@Moses51 2 ай бұрын
Kukunyu wakupha adapa witika
@fredgabrielnyangulu
@fredgabrielnyangulu 2 ай бұрын
That means inuyo ndi amene mukudziwa malamuwo kuposa a Mr Kamlepo Kaluwa omwe anali kupanga nawo constitution ya dziko lathu ndipo iwenso mwina kulibe
@HalimaMoosa-vb1lh
@HalimaMoosa-vb1lh 2 ай бұрын
Chakwela galu wa muthu ndipo ndiwakupha, ayenela achoke pampando 🎉
@ImanRashidi-so4oo
@ImanRashidi-so4oo 2 ай бұрын
Tiyamba mademotu mukapanda kumumasula DC zopusa ife a Malawi 🇲🇼 ai
@Trancy-xt4py
@Trancy-xt4py 2 ай бұрын
Ndinu oputsa dziko la democracy iri sikuzimbabwet kumalawi komaso si 1964 ino tili ndiufulu olakhula , chilima amupha ndi chakwera chilungamo chake akuchidziwa tili ndiumfulu olakhula zikasithe chifukwa cha mcp ? Chilimat wachita kuphedwa amalawi tikudziwa asazibise apha tikuona mafuso alipo ambili omwe zikuoneserat kuti angomupotokola ndiy musamaopseze antju olo kumanga anthu mudziko la democracy yomwe ena adaimvutikira anthu ena chakwerayo kulibeko olo zikhaleyo kulibekoso musamalet mupita naye chilima dzuwa likuswa mtengo tionesana inuyo
@MathewsChitsulo
@MathewsChitsulo 2 ай бұрын
Kodi a police amene anakamutenga bon kalindo analipo angati , nanga anatenga ma ola angati kuti akwanitse kumugwira Bon Kalindo? Nanga a police mudziko lamalawi alimo angati a army pamodzi ndi a nave alipo angati? Ndichifukwa chiyani anatenga ma ola ma kumi awiri ndi mphamvu zinayi kuti akapedze ndege imene anakwera wachiwiri kwa mtsogoleri wa dziko lamalawi imene inagwera mziko la Malawi? Ndichifukwa chiyani mukufuna mudziteka anthu pakamwe kapena kuletsa wanthu kukamba za dzuwa limene likuwala aliyense ndi kumawona? Bon Kalindo komaso Kamulepo Kaluwa akunena zinthu zomwe munthu wozadzidwa ndi misodzi maso mwake pa imfa ya munthe yemwe chidali chiyembekedzo Cha wina aliyense analinacho mu dziko lathu LA ufulu omwe makolo athu anafela kuti ifeyo tidzakhale nawo. Chifukwa chiyana mukuwazunza pamene mukudZiwa choona
@HalimaMoosa-vb1lh
@HalimaMoosa-vb1lh 2 ай бұрын
A bon kalindo akulankhula chilungamo, ndyeno pajatu musaiwale kuti, munthu kumuuza chilungamo amaona ngati mwano, ndyeno kachakwelaka,,,,,? Kaya
@maulidjames8542
@maulidjames8542 18 күн бұрын
Kodi iwe malamulowo abwela chifukwa chaboma lamanyili usatiya nkhulitse pantchile ukadadziwa mkwiyo wamalawi sibwezi mukuyankhula zimenezo
@Moses51
@Moses51 2 ай бұрын
Nawe iweyo ndigalu kwabasi 👺👹☠️👹👹
@FionaKhoma
@FionaKhoma 2 ай бұрын
Kod powamanga athuwo mukufuna kubisa chan? Asapezeke atasitidwa ndi iron athuwo ndiye munyera muona machende
@charlessulumba2521
@charlessulumba2521 2 ай бұрын
Komaso iweyo usazapangeso post za Bon kalindo, becoz ukuonesera mbali imene uli
@babranzima8120
@babranzima8120 2 ай бұрын
Komaso kukuyu anapha witika akusiyiranji kumumanga ndiye bon kalindo wakulakwirani chani mlandu ukhale waodio nanga wakuphamuthu mkumusiya komachoti muziwe mwaluzakale achakwera
@BlessingsLuclus
@BlessingsLuclus 2 ай бұрын
Iwe nthawi ya Peter ndi chakwela yemweyo amanena kuti peter akumapha anthu achalubino anamanga ndani chamwe nchitho amadziwa ndiye kupha ndi kumba bas uku anthu kumavutika
@COLLYAnusah
@COLLYAnusah 2 ай бұрын
Sunu kanyoko uyasijoyela kabi wena
@ibrahimalfred6539
@ibrahimalfred6539 2 ай бұрын
Awamangira chifukwa chandale mcp ndichocho
@0wenNkhambule
@0wenNkhambule 2 ай бұрын
Chakwela you mast go Why mumalo anthu amalila way sawamanga Chakwela ni galu
@ZungeniBanet
@ZungeniBanet 2 ай бұрын
Iwe ukuyiwala thawi ya Peter mutalika tinamunena mbwaji
@stevovosalimu5443
@stevovosalimu5443 2 ай бұрын
Bundle langa ndimavela zazelu osat galu iwe tisiya kukamba bon kalindo akatuluka
@InnocentSomanje
@InnocentSomanje 2 ай бұрын
Choka iwe akutuma unawona kuti mapresdent ena omwe alamula mbuyomu anthu akuzuzika chochi wakutuma uyu Ali ndimayina ambilimbiliyu namandenge
@MartinKapanga-q6m
@MartinKapanga-q6m 2 ай бұрын
kodi tiope chifukwa cha anthu ayipo analowa boma kodi kumalawi anthu amenewa apanga chani chakwela munthu oyipa kwambili anthu akugona ndi jala azingokhalila kumanga anthu muganize bwino
@JimmyAbdul-uv4xc
@JimmyAbdul-uv4xc 2 ай бұрын
Bwanji malamulowo nthawi ya dpp pamene a msp anali otsutsa samagwila ntchito, osamangomangana zilizonse aonjeza
@PreciousElias-lx2pz
@PreciousElias-lx2pz 2 ай бұрын
Aaaaaaaaaaa mwina ine ndimalakwa daily kusaziwa malamulo mundigayileko
@InnocentSomanje
@InnocentSomanje 2 ай бұрын
Boma lomwe tilinalo lelo la MCP loyipa naweso khala chete
@omarrasheed5568
@omarrasheed5568 2 ай бұрын
Watumidwa ndi achisilu a beni longwe
@babranzima8120
@babranzima8120 2 ай бұрын
Chisiru chamuthu iwe sukuonakutizomwe zikuchitika mmalawi galu iwe manyiako
@ZungeniBanet
@ZungeniBanet 2 ай бұрын
Chakwel ndiwakupha iwe nawe chisilu kwabasi
@piliranimalama6090
@piliranimalama6090 2 ай бұрын
Paja amati ali ndi umboni ndiye umboni ali nawowo ngati ali ma facts ndizimene zikawapulumutse
@SaidiMustafa-y3q
@SaidiMustafa-y3q 2 ай бұрын
Kodi mamulo amenewo ndi adamokalaazi kaphena awni phathe sithim
@CathyKanthiti
@CathyKanthiti 2 ай бұрын
Galu iwe wasowa zokamba eti???? Akaluwa ndi mwana kuti akanene umboni wabodza????? Akutumawo akupepeletsa2
@BetherNkhoswe
@BetherNkhoswe 2 ай бұрын
Kkkk
@BizweckFred
@BizweckFred 2 ай бұрын
Ambuye kd mukulolelanji izi dziko lanthu lino 😭😭😭
@LovelyBlini-cu3iu
@LovelyBlini-cu3iu 2 ай бұрын
Ili ndi dziko adzalira ndi nthawi yawo tikupempha mlungu kut awafungatire anthuwa
@amosnyirenda-pl1ss
@amosnyirenda-pl1ss 2 ай бұрын
anyanya ma bonza tatopa nawo akhale koko apuzile khalindwe
@CharityChikomo-hl1gz
@CharityChikomo-hl1gz 2 ай бұрын
Za ziiiiiiiiiiiiiii ammasuletu ameneyu amanga angatiiii coz anthu ambiri akuyakhula zosiyanasiyana so amange anthu onsewaaa Kaye mxieeee
@Jasper-xk9iv
@Jasper-xk9iv 2 ай бұрын
Komatu chakwera uziona nawexo ufa ulibe thawi
@LynessobertyPemba
@LynessobertyPemba 2 ай бұрын
Galu iwe chisilu chamunthu wakupasa ndilama gwape wakoyo
@KassimIssa-bn3od
@KassimIssa-bn3od 2 ай бұрын
Kd inusotu musatinyase ndikutulukatu nkhale mwana sakuziwa kut chilima waphedwa
@GeorgePhiri-ub2of
@GeorgePhiri-ub2of 2 ай бұрын
Enanu mulibe kalikonse koma bze kulakhula khani zopanda umboni samalani
@HakeemJossam
@HakeemJossam 2 ай бұрын
bozaso aziyankhula wandalama eti?
@GeorgeKapito-um2wl
@GeorgeKapito-um2wl 2 ай бұрын
Bakili wakhala akunena poyera kuti kamuzu wakhala akupha anthu kuphatikizapo a achina Dick matenje Kodi anamangidwapo.iwe galu usatiphere democracy yathu.
@FionaKhoma
@FionaKhoma 2 ай бұрын
Ukauze nkazi wako ndiana ako manyiakowo namachende iwe galu
@user-je8jm5uy1q
@user-je8jm5uy1q 2 ай бұрын
Za ziiiiiiiiii zeni zeni asachoke boma adzakhale moyo wawo wonse
@LynessobertyPemba
@LynessobertyPemba 2 ай бұрын
Km iwe ndi chakwera machende Yako zikukusangalasani kuti azanu azifwa foseki nyani iwe
@AishaDaud-lq4vd
@AishaDaud-lq4vd 2 ай бұрын
Nde malawi yonsetu
@FionaKhoma
@FionaKhoma 2 ай бұрын
Machende ako iwe galu umangoikira umbon wamanyiiwe m b c itsekedwe manyiwo
@meeksonmkhala
@meeksonmkhala 2 ай бұрын
Nde inu mwapeza kuti ndizabodza??
@nyasavoicebox
@nyasavoicebox 2 ай бұрын
Zimenezo oweluza si ife Koma bwalo la milandu 🙂
@AliHamis-mh3uq
@AliHamis-mh3uq 2 ай бұрын
Dikila Kaye kukubwela kuno anthu achakwela atadzayamba kugwililila ana ako ndipamene uzazindikile kuti anthu ndiwoyina. Koma idzakhala thawi yatha ayse
@MartinKapanga-q6m
@MartinKapanga-q6m 2 ай бұрын
chakwela iwe ufumu wakumwamba ulinawo kutali
@user-ko2yv4gi5y
@user-ko2yv4gi5y 2 ай бұрын
Ndiwenso munthu wamatha kagwele uko zachamba
@HarrisonMahaso
@HarrisonMahaso 2 ай бұрын
Aaaaaaah ankavula anthu zija ndiye zabwno koma izi ndiye zikuoneka ngati munthu akuukila tionana nthaw yama vote
@user-rn7wv8ze3v
@user-rn7wv8ze3v 2 ай бұрын
Ndindale zachipani chimozi chankhaza
@AyaAyanda-rg6iy
@AyaAyanda-rg6iy 2 ай бұрын
Palibe chanzeru chomwe wayankhulapo iwe,,,zaziii
@COLLYAnusah
@COLLYAnusah 2 ай бұрын
Foseck mbukulu
@EliasPhiri-yv8gv
@EliasPhiri-yv8gv 2 ай бұрын
😅😅😅
@AdamuRumbili
@AdamuRumbili 2 ай бұрын
Chakwela wapa chilima😢
@MussaHassani-zg1hm
@MussaHassani-zg1hm 2 ай бұрын
Ase iwe chipani ichi chakupha zachamba
@GeoffreyChimera-ec5kh
@GeoffreyChimera-ec5kh 2 ай бұрын
Zayamba lit??
@ShavielSiment
@ShavielSiment 2 ай бұрын
iweyo ndi chakwerayo ndinu mbuzi
@SaidiMustafa-y3q
@SaidiMustafa-y3q 2 ай бұрын
Kodi kukheza mwazi ndichani Mr chakwela
@stevovosalimu5443
@stevovosalimu5443 2 ай бұрын
Galu iwe walandila
@e.r.mchanel1460
@e.r.mchanel1460 2 ай бұрын
Boma la uchikape ili
@HarrisonMahaso
@HarrisonMahaso 2 ай бұрын
Aaaa maboza amenewo zimenezo ndiye ziti
@nyasavoicebox
@nyasavoicebox 2 ай бұрын
Malawi Penal Code 🙂
@KennethMpininga-iz2ie
@KennethMpininga-iz2ie 2 ай бұрын
Chakwera achoke pusi
@YasinMusa-ym8lp
@YasinMusa-ym8lp 2 ай бұрын
Chakwera machende
@gomezthera535
@gomezthera535 2 ай бұрын
Zowona anthu ziko akulitengela pamugongo
@ChikumbutsoJohn-rs4tt
@ChikumbutsoJohn-rs4tt 2 ай бұрын
You're crazy
@MphasoMago
@MphasoMago 2 ай бұрын
😅😅😅😅😅usilu
@BrightMkandawire-zw5dw
@BrightMkandawire-zw5dw 2 ай бұрын
Alomino aja amapha a dpp aja anthu amanena anamangidwa ndani
@LynessobertyPemba
@LynessobertyPemba 2 ай бұрын
Galu iwe chisilu chamunthu wakupasa ndilama gwape wakoyo
@LynessobertyPemba
@LynessobertyPemba 2 ай бұрын
Galu iwe chisilu chamunthu wakupasa ndilama gwape wakoyo
Ndege Inagwa Chifukwa Cha Ndale - Samuel Lwara
20:31
Nyasa VoiceBox
Рет қаралды 10 М.
SCHOOLBOY. Мама флексит 🫣👩🏻
00:41
⚡️КАН АНДРЕЙ⚡️
Рет қаралды 7 МЛН
哈莉奎因怎么变骷髅了#小丑 #shorts
00:19
好人小丑
Рет қаралды 40 МЛН
HAH Chaos in the Bathroom 🚽✨ Smart Tools for the Throne 😜
00:49
123 GO! Kevin
Рет қаралды 10 МЛН
A Chakwera 2025 Ufumu Wanu Mulungu Waukana  -- Jaffa Mussa
14:30
Nyasa VoiceBox
Рет қаралды 4 М.
Jomo wamukana Bon Kalindo
4:20
Nkhalango Multimedia
Рет қаралды 67 М.
Zomwe Zinachitika Kut Ndege Isowe
5:19
Sam Malvitha
Рет қаралды 258 М.
Times Exclusive featuring Bon Kalindo - 6 January 2024
1:03:20
Times 360 Malawi
Рет қаралды 252 М.
Chakwera wayamba nkhondo yolimbana ndi social media
7:45
Bakili Muluzi TV
Рет қаралды 91 М.
SCHOOLBOY. Мама флексит 🫣👩🏻
00:41
⚡️КАН АНДРЕЙ⚡️
Рет қаралды 7 МЛН