Wazithoyo wapanga chani manyi ako a Humfrey Mvura nanuso ndinu chitsiru
@isaihmagani56972 ай бұрын
Munena zoona, koma inuso mulankhuranu nanu mwakula mukadasiyira achi nyamata poonesa chisanzo pa zomwe munenazo
@EmmanuelNgamuti2 ай бұрын
That's the MBC we wanted very independent, not partisan or favouring the gvmnt of the day.
@Littlefair72 ай бұрын
Zipani za kumalawi zilibe ma policy abwino, DPP inayenera kupereka mpata wa SKC mmbuyomo, imayeneranso kupereka mpata kwa Nankhumwa amene chipanichi chamusula koma achina Chaponda akuononga chipani komanso ndale zathu and we expect kuti dziko litukuka? Ku Burkina Faso mnyamata walifikitsa pa world's fastest growing economy ndi ma resources omwe ali kale mdzikomo, amalawi tisiye kulekerera zopusa.
@harrisbanda58912 ай бұрын
Chikangawa is fresh for you , kwaife nditselekwete, wakupha , wankhanza komanso ndosakonda amalawi
@HestingsZiba-d6k2 ай бұрын
Awa ndi a chikangawa party adiyeni zigawenga isi ndithu
@Rometcma2 ай бұрын
Mukakhuta musamayankhule zopusa Ku MBCko 😂😂😂
@comradegondwe33112 ай бұрын
Kasakula is very objective and intelligent. I totally agree with him. Why should APM go back to state house. He does not have any unfinished job at state house.
@FrancisNyayi2 ай бұрын
Aliyese ndi support yake Inu amcp ine wachipani cha yesu
@JohnsonMaulana2 ай бұрын
Ofunika kuchita resign nd chakwela musiyen Muthalika amalizise term yake ife tikumufuna.😊
@BokhoMoses2 ай бұрын
Inuyo zanu zili pa bwino koma tonse tagwiliza kuti next year tikusitha zithu basi. Kaya wakulu kaya watani koma ife tanena tanena wathu APM . DO YOU THINK ALIPOYI ATENGASO MMMM FORGET ABOUT THAT MY MEN. AP.M MY VOTE ☑️
@DONNEXKhama-bk1gy2 ай бұрын
Imeneyo sigwilai 😂😂😂pezan njila Ina kkkkk APM ❤❤
@ubs70302 ай бұрын
I am mbuna kaliton. My comment is that peter is too old to serve malawi, he has to rest: what else does he want?
@PatrickMailos2 ай бұрын
Musiyeni Peter muthalika aphule zikoli pamoto
@LesediChanache2 ай бұрын
The republic of Malawi has it's rules and regulations,so don't compare with the American states.Leave Peter muthalika alone he will win.....
@robertkalima8742 ай бұрын
Ndiye nzodabwitsa kuti nkhalamba APM ingatipindulire a Malawi? A DPP ganizani bwino
@eliaskhofielias81522 ай бұрын
Choka iwe wa mcp ukumuopa chani?ngat mulindustamina musiyeni mesa mukut mudzawina bwanji oaamuaiya ngat mukudziwa kut mudzawina?mantha bwaaa mbutumanu za MCP?musiyeni alindi ufulu wake adzagwa yekha kusonyeza kut anthu sakumufuna akalamba.
@DalitsoMatope2 ай бұрын
Muwawuze akutumaniyo achepa even pa Bright nsaka sangamake chakwera
@lyiemax2 ай бұрын
It's better to choose nkhalamba than anyamata okuba anuwo and you can't divert our minds apapa, everyone has the right to contest and citizens will choose according to their choice
@thesocietynews31812 ай бұрын
Munganene bwanji Koma a Malawi tonse tagwirizana kuti tonse from Nsanje to Chitipa and Nkhotakota to Mchinji tidzavotera APM yemweyo kuti aliphule dziko lathu pamoto. APM woyeee DPP WOYEEE. Tatopa ndi umphawi, kupha, matangale ndi nhkanza za Chakwera ndi MCP ndi Tonse Alliance ndipo tikufuna APM alamulire basi. A MALAWI TOOONSE TIKAVOTERA APM NDI CHIPANI CHAKE CHA DPP.
@SilvesterZimba2 ай бұрын
.Mutharika sakudziganizira za moyo wake.Ntchito ya up resident nthawi ino ya democracy simasewera.
@ubs70302 ай бұрын
Vuto la chipani cha banja ndi limeneli: udf, aford, dpp, etc mavutooo a zipanizi ndi succession.
@FungulanReuben2 ай бұрын
APM my vote, come 2025
@JohnBanda-ux9fy2 ай бұрын
Mbuzi za anthu .. amalawi tikuvutuka NDI chikangawa panoso mukuti chani ..nosenu mwakula chokani pa menepo ana anu azagwire ntchito tione ngati simufa NDI njala MBC idatha mbanva nokha nokha
@harrisbanda58912 ай бұрын
Ndeiweyo bwanji iweyo siukusila ana poti nawenso ndiwe nkhalamba ?
Tilekeni tivotele emwe tamufuna osatiuza chochita pano maso ndimitu yathu tinatsekula tikuona bwino zochitika, nanu a MBC mudziwe kuti Peter tikumufuna ndiife osati malo oulutsira mawu ayi, koma tikufuna iyeyo adzayesepo kutukula dzikoli.
@MsondaBanda2 ай бұрын
I don't think wachikulire can defeat wachinyamata never
@MalitaKapesi2 ай бұрын
Voti ndichinsisi chamunthu kufuna kwake, ndiye inuyo mukati Peter wakula bwanji uyu akulephelayu ameneyu ndinkhalamba?
@ubs70302 ай бұрын
Kasakula is right
@GiftJulius-ro9ev2 ай бұрын
Simukunama anthu omwe amuzungulila ndi amene akumunamiza ....
@Littlefair72 ай бұрын
Chifukwa cha umbuli wathu ena akanena kuti APM wakula tikuona ngati akudana ndi DPP, koma APM si DPP, panopa ku DPP ndi madala team yokha yokha, zina ndi mbava zokuba chimanga, ku UTM mugwirizane ndipo mutenge boma ndipo MCP ndi DPP asadzalowenso m'boma. Biden, Trump, APM, Museveni, etc need to step aside for a better world.
@LovenessLester2 ай бұрын
Mutharika akaimiranso DPP lingokhala dyera lake uyo Ku DPP kulibe anyamata Kodi?????? Hiyaaaaa
@phillipphiri21192 ай бұрын
Amvula akula achoke nawo amagona. Kasakula is a hypocrite,he is only defending and speaking to appease his employer.If he were at Times he would have a different narrative.Coward
@harrisbanda58912 ай бұрын
This's y i dont like listen to mbc
@DadTshepo2 ай бұрын
Nde bola nkhalambayotu nanga OPHA CHILIMA WO AKUCHITANJI NANU MUKUNGOFUNA MPUNGA WANYAMA MAPWALA ANU
@HenryManda-m9h2 ай бұрын
Akatsakula,a Mvula ndi anzanuwo ,zimene zachitika ku America sizikigwirizana ndi zimene mukunena inuyo apopo,nkhani ya kuchita withdraw kwa Biden sikuti ndiya age limit musapomboneze anthu iyayi lero m' Malawi wina aliyense akudziwa m'mene zinthu zikuyendera nkhani yimene yamuvuta Joe Biden ndiya mpikisano wamukulira sanakawina ndi DonaldTrump ndichifukwa chake achipani cha Democrat awona kuti sangazaphule kanthu kwa Donald Trump so inuyo a mbc musatelepo mwayi wokhala ngati kuti watula pansi chifukwa cha age limit ayi osapusisa ,kapena kunamiza anthu pa mbc yanuyo yaboza ayi nenani chilungamo inu aMvula munayitha stage coach yonse pyitiii
@GoodsonLindani-gf8pn2 ай бұрын
Machende any nooonse ,koma zoona momwe tikuvutikila a Malawi mungatiuze zochita? nanuso pali inupo ndi khalamba kale. Ndie chifukwa chake MBC sitimaivela utsilu wake umeneo. Mutu ngat mbatata.
@lifayohbenson19942 ай бұрын
Bwana kasakula ndimaona ngati program iyi
@AusmanJohn-in6bi2 ай бұрын
Ndi Anthu a Mcp amenewo apasidwa ndalama ndi chakwela mbuzi za Anthu
@GoodsonLindani-gf8pn2 ай бұрын
A Mvula kuyambila kale mumadana ndi DPP pamutu panupo sipamaenda.KO'd othamanga magaziwo apanga chain.kapena mukunena kuthamanga ndi ndalama zamisonkho yathu. Panyo
@JimmyIsaac-xd4ef2 ай бұрын
Musalimbane ndi APM chifukwa Kuti ndi wachikulile,bwanji amene akuoneka Ngati wa chinyamata wakanika kuyendetsa dziko?
@manuelchima-d1s2 ай бұрын
mukuona ngati Ku mbc kuli munthu wazeru ndichifukwa anthu tinasiya kuonera mbc
@ubs70302 ай бұрын
Hunger, poverty, name it, are things that have been there even before many of us who are living today were born, they are part of life, everywhere under the sun. I am kaliton mbuna commenting.
@ShillahChisi2 ай бұрын
Akuziwa kt Gogo wanthu awalanda udindo
@marryphili54192 ай бұрын
Za ziiiii ife tikufuna DPP kukura sivuto borani zeru zamunthu womwe zawakanikawa ndi wokaramba
If he failed to develop malawi during his time as the country's president when he was still strong, can he do it now when he is too old? That is nonstarter. He cannot be talking of ending hunger now or poverty now when he failed then, no, that is not true. It is wickedness at its worst.
@chifundocharles23482 ай бұрын
Kodi iwowo ndi joe Biden, kalikose tiziongoona America?😂😂 DPP ❤❤❤😂 mutsekula mimba
@LamieTiger2 ай бұрын
Ziko sila mbc muudzane ziko ndilamulungu mufune musafune zomwe mulungu wamanga zikhala zomwezo kaya ndi chakwera tivotela kaya Peter tivotela makonda makonda
@PatrickMtira2 ай бұрын
Ok amawanena aja kuti alandira ndalama ndi awa eti lipopo FM moto kuti buuuuu
@HappyAbyssinianCat-xt2bm2 ай бұрын
Ine inu ndinakutsikani simakuveran inuyo munakwera chakwera nonse ndinu dzitsiru chakwera ndi ndaniso muzingodya ndalama zathu za amalawizo akukupatsan chakwera wa magaziyo chikangawa ife tikufuna peter yemweyo
@Macnovas-dp7pj2 ай бұрын
Mwina ndikolelela nkhalamba ku mbc kooooo muchoke
@harrisbanda58912 ай бұрын
Inu achikangawa munatenga nawo gawo lopha chilima pa 10 June 2024, ng'azi zopanda ntchito inuu
@Patgregorymanyumba2 ай бұрын
Kagweleni uko zinsiru za anthu ku Makanjira palibe nseu wapangidwa, mukukanika inu kuchita retire bwanji
@LawrenceBelson2 ай бұрын
Nde wanuyo chikangawa party wanuyo osasiya uprezidet bwanji nanuso popeza mwakula
@RaphealKwelani2 ай бұрын
Akut wakula ndani mensa anyamat akuba kd
@PatrickChakwana-og6ok2 ай бұрын
Ine ndiye mbc ndnasiya kuonera pano Pali mbola
@Namphuno2 ай бұрын
Kodi mmene mwakula mimbamo mukuona ngati mungayankhule chamzeru kuti musinthe amalawi,, munthu aliyense akudziwa zomwe mukudziwazo komanso zomwe mukunenazo, ndipo tikudziwa chochita, ngati simukufuna peter as your president samukani mupite dziko lina
@patrickthomsonАй бұрын
Kunali amzanu ku MBC komko pano anakhwefulidwa
@harrisbanda58912 ай бұрын
Mapwala anu nonse amene muli pa mbc'po and chomwe mungadziwe ang'azi inuu ndichoti chikangawa party inatha kale pa 10 june 2024 kwasala mkukangoyikwilila basi
@SymonNamalomba-sh3fu2 ай бұрын
Kukoma kwache Tsiku lomwe ndege idagwa Ulamuliro wa chakwera udatha
@salimmkumakumakitombi-yc7pw2 ай бұрын
Muli pachintchito ndi APM ndithu.kodi inuyo akukuretsani ndani kuima
@Macnovas-dp7pj2 ай бұрын
Mwakulanso nanu ogwila ntchito ku MBC muchoke kulowe anyamata😂😂 ndi social media imeneyo we need make up guys on social media mwakula muchoke kumeneko ku MBC
@FelleCasim2 ай бұрын
Kavotelani wamng'onoyo ife tivotela APM basi kati zikakuwawani ndizanu
@BenBanda-q9j2 ай бұрын
Inu munayamba liti kuchita zofanana ndi za anthu a kwamerica, inuyo simungasiyanise mphamvu zimene zili ndi peter ndi biden
@JohnBanda-ux9fy2 ай бұрын
Biden ku America sakumufuna coz akukorezera nkhondo kupha anthu osalakwa.. komaso mphavu zake sizingafane ndi apm ..chimene mungaziwe anthu tili mmitundu mitundu zimachitika munthu wa zaka 60 kumaoneka ngati wa 90 ..waza 90 kumaoneka wa 60 .. kagwereni uku nonse a ABC
@BenBanda-q9j2 ай бұрын
Nonsenu ndi mbuzi mitu ngati chakwera mulibe nzeru nonsenu, musiyeni peter akumufunatu ndi mamillion a amalawi
@BenBanda-q9j2 ай бұрын
Wosasangalasidwa ndi peter aone kopita muzabwelera akazalowapo amene mukumufuna
@HarrisonSupadayudah-nz9er2 ай бұрын
Aliyese pamalo pake musatisakhire
@FrancisKamoto-yg2qr2 ай бұрын
Kod Peter ali kosutsa boma mukulimbana naye watani musiyen inu mulimbane ndi mr chikangawa bs ndiamene akulamulira
@BenBanda-q9j2 ай бұрын
Iwe mdala iwe ukukamba za usiru musiyeni peter awombole amalawi, kusogolo azaona kuti azamusankha ndani woti amusiire
@NaduMbewe-zz6iw2 ай бұрын
Mugabe ndi Potala mam kuli ndani
@AlexisJailos2 ай бұрын
Ide tikufuna Peter yemweyo.mcp yakoyo ipite uko.kapasula ukuopa Kuti ntchito yako izatha . a Malawi akuziwa Kuti Uli pa MBC chifukwa cha MCP.kapasula osamunyoza munthu .mulungu akumva
@BenBanda-q9j2 ай бұрын
Peter ndi wolimba, ayenera kutipulumusa ku mavuto tikukumana nawowa
Inu mbc tikuziwa kuti ndinu mcp ndie sizomachuluka mzeru apa mwamva ma chende anu nonsenu mbc tinasiya kuisata kalekale misamazivute inu ana akhandwe. Musamazinamizeso kuti America ndi yaphamvu ziko lonse lapasi boza inu musamawanamize anthu inu America ilibe mphamvu fusani akamati super power si America yokha muli maiko okwanila 10 ndiposo America zida za khondo kulibeko mwamva ndiposo America khondo samaiziwa muzikhala mukuziwa 😂😂😂🎉
@DanielZitande-y1d2 ай бұрын
Inu a kasakula ndi a anu moyo wa ufiti ai Peter ndi munthu ngati iwe ndipo dziko ndi anthu ndiye anthu ngati akufuna Peter iwe ndiwe ndani, asiyeni anthu asankhe zomwe akufuna
Munthu amene sakuyenelela kuimaso ndi Chakwela, mufune musafune
@jonathanmbewe42462 ай бұрын
😂😂😂 so Humphreys Mvula akugonasotu aaaaa
@JuaryMbisa2 ай бұрын
Please you hear what has happened,kodi school yanu mins phunzira kuti? Konamio MBC musamale ngati mwayamba ndale anthu atatunu inu nenani chifukwa mwasiya ntchito yanu
@harrisbanda58912 ай бұрын
Anamachende apa mbc 😂😂😂
@harrisbanda58912 ай бұрын
Zitsiru inu mwalandira ndalama zamisonkho yathu mkuona mukutamiliza chikangawa wanuyo, nde mchiyani chimene wachita wa active wanuyo ?, nde sibolanso nkhalambayo zinthu zinalibwino mmalawi muno.
@MebleKalitsilo2 ай бұрын
Za ziiii zopanda nzeru
@AsimaSimama2 ай бұрын
Inu nonse mbolo Zamanu musiyeni APM ayime
@MacDonaldkachala-cm5gc2 ай бұрын
He will do Biden style just wait,
@kingssalema33642 ай бұрын
Mutumbwiletu ku MBC ko. Boma lanuli likamapita mupitila limodziiiii.
@TrizaGeorge-q8w2 ай бұрын
Kodi anyamatao ndiye akutani akutumani kuteloko ndi chiopyezo cha chikangawa party komanotu mukamakhuta mukamasangalala dzuwani kuti athu ali pamavuto azaoneni ziko lino chilichose chinaima ndi chikangawa party
@WisdomGavu2 ай бұрын
Akasakula mwafikapa pamenepo?
@DavieKumbanga2 ай бұрын
Akasakula timkakudalilanitu MBC tinasiya kumvela kalekale