*(TINA Lyrics)* Artists: Phyzix, Ace Jizzy & Beejay Beatmaker: BFB Engineer: BFB *(Intro)* Yeah Very Good/ Very Good Yeah Exklusive/ It’s Only Entertainment *(Hook: Beejay, Phyzix, Ace Jizzy & BFB)* NDILI NDI MKAZI WANGA wina dzina lake TINA Ndimamuuza Phwanga dzuka iwe Yamba kuvina Ukapanda kupanga choncho ndipeza nkazi wina Mangodabwa Nkazi uja Wayamba kuvina (Molalo) Tina Tina Tina Tina (Molalo) Tina Tina Tina (koma tiaKazi) Tina Tina tina (Molalo) Tina Tina Tina Tina *(Verse 1: Ace Jizzy)* Anabadwa nthawi ya Bakili IVON // nthawi ya UDF... ndi Yellow BORN // koma apa ndili ntiakazi TINA M'TINA // tufanana maina....TINA, M'TINA // uyuyutu aise uyu aise ndi NKAZI WABWINO // izi or kale lija ndiNKAZIWA BWINO // komano utilore nkazi ifeyo tili BHO!! // ma ex aMATILIRA ngati uLIMBO // suli ngati tiakazi ta ITI // tovala TIGHT // hehehe NAH ITI // toyenda NIGHT // akazi enawa paiweyo SAMAFIKA // sangaimbeso dancehall koma attention ama SEEKER (Masicka) *(Hook: Beejay, Phyzix, Ace Jizzy & BFB)* NDILI NDI MKAZI WANGA wina dzina lake TINA Ndimamuuza Phwanga dzuka iwe Yamba kuvina Ukapanda kupanga choncho ndipeza nkazi wina Mangodabwa Nkazi uja Wayamba kuvina (Molalo) Tina Tina Tina Tina (Molalo) Tina Tina Tina (koma tiaKazi) Tina Tina tina (Molalo) Tina Tina Tina Tina *(Verse 2: Phyzix)* Verse pa beat/ maliro Sneaker kuphazi mpaliro/ ndikatenga bebi yako ndekuti ndi mpaliro/ am top of the table doyilo/ Tha! Tha! Tha! boyilo/ mfana wofewa bondo elbow/ mwadzadza ma oil/ China nchina mkazi yemwe ndimafira m'Tina/ umadziwa akazi okongola amaswa mitima/ ntchito za mum'dima usathamange taima/ ikamandimenya stress ndimapita kokathima/ ineyo ndi wina/ sine loser ndine winner/ ndimamenya zi ma hit komanso ndili ndi dzina Zomwe ndimapanga ndili khethe khethe ndi udolo/ ineyo ndi ma hit ma hit/ tili ngati khutu ndi ndolo *(Hook: Beejay, Phyzix, Ace Jizzy & BFB)* NDILI NDI MKAZI WANGA wina dzina lake TINA Ndimamuuza Phwanga dzuka iwe Yamba kuvina Ukapanda kupanga choncho ndipeza nkazi wina Mangodabwa Nkazi uja Wayamba kuvina (Molalo) Tina Tina Tina Tina (Molalo) Tina Tina Tina (koma tiaKazi) Tina Tina tina (Molalo) Tina Tina Tina Tina *(Verse 3: Beejay)* Koma ase tinayo akangodzuka Cha Usiku/ Udziwe kuti Wez Day imeneyo silake tsiku/ Ndupanga za Tina .. Ndamukweza Coach afike ku Dinner/ koma Sikuti iye ama cheater ndi Kinnah/ Ndine mfana Wamamuna phwanga sinditha kuima/ Ndimathamanga Bee AKA Khrishna/ Amavina ngati Mphepo Hiroshima..sungamudye phwanga Ukuziwa kuti Sinsima/ China ndi china Man / ichi ndikumanani Tina akafika Amakumanani/ Phuma nanu .. Kuuma nanu Ase uli ndi Mkazi wako ..Koma ineyo.. *(Hook: Beejay, Phyzix, Ace Jizzy & BFB)* NDILI NDI MKAZI WANGA wina dzina lake TINA Ndimamuuza Phwanga dzuka iwe Yamba kuvina Ukapanda kupanga choncho ndipeza nkazi wina Mangodabwa Nkazi uja Wayamba kuvina (Molalo) Tina Tina Tina Tina (Molalo) Tina Tina Tina (koma tiaKazi) Tina Tina tina (Molalo) Tina Tina Tina Tina
@emilynakoma9417 Жыл бұрын
Mutu wa Physics nawo uyimba liti 😜😜😜
@manuelchamadenga9084 Жыл бұрын
Fire 🔥🔥🔥
@madbwoy2975 Жыл бұрын
Eeee komatu ma guy's munayi pweteka... Keep fine burning 🔥🔥🔥🇿🇦🇻🇨
@rajabdaud1883 Жыл бұрын
That Bee jay's energy 💪
@Phyzix Жыл бұрын
TINA VIDEO OUT NOW 🔥🔥🔥 Official Video: kzbin.info/www/bejne/pnK8n2Sbe9B6gbc Lyrics Video: kzbin.info/www/bejne/pqqvXqKQbdZjjJY Spotify: open.spotify.com/track/3mCC9kfQvQ6EwJFxWKuFL4?si=znUl05VqSYeOH6JryZLcdw Apple Music: music.apple.com/mw/album/tina-feat-bee-jay-ace-jizzy/1663605026?i=1663605027 Malawi Music Dot Com: www.malawi-music.com/P/25-phyzix/13629-tina/20082-tina-ft-beejay-and-ace-jizzy Mikozi: mikozinet.com/id/tina-explicit-ft-beejay-ace-jizzy-prod-bfb/
@apeliuskamugisha4560 Жыл бұрын
Wimbo mzuri or good song by apelius kamugisha from Bukoba Tanzania
@EffieMuhama Жыл бұрын
Tina , mulalotina❤❤❤❤
@toptaker1357 Жыл бұрын
Uncle ❤️🇲🇼
@baxxymw Жыл бұрын
Yaaaaaahhhh 🔥🔥🔥dope video for the bangerrrr!!! Team work really makes the dream work.
@Phyzix Жыл бұрын
Energy ⚡️
@isaacchambwinjajr4984 Жыл бұрын
That fire of Bee Jay ayaya
@Zenith4kt Жыл бұрын
Ace jizzy 🙌🔥
@EffieMuhama Жыл бұрын
This,guy has,came,whit,fire
@misheckmzumala7894 Жыл бұрын
I like the video and very simplistic.
@khanyesoko5589 Жыл бұрын
Nice song, great video
@mukeyachirwa5453 Жыл бұрын
Great video concept...
@Wetcha116 Жыл бұрын
Ace Jizzy’s word play is top notch 🔥🔥🔥
@nyengoavalo3162 Жыл бұрын
Vele good Vele good
@charlesmakumba4215 Жыл бұрын
Big baaaaad video guys Eeeeh 😀😀😀 keep it lit🔥🔥
@johnstonmalivasi5291 Жыл бұрын
The true definition of thinking outside the box🙌 The video is legit 🔥🔥
@smartchitimbe2450 Жыл бұрын
Tina❤
@tafadzwabonongwe8147 Жыл бұрын
Tina💙💙💙
@stevensalambula8293 Жыл бұрын
Phyzix umabwera ndima concept abho and umatha kusankha ma artist oika munyimbo💥💥💥