*MADA Remix Lyrics* Produced by Sameface Beats & Cuff-B *INTRO - Phyzix* Yeah/ It's Only Entertainment/ Cuff-B Production/ Sameface on the Beats Mumakwana a Mada/ mwabhebha mwabhebha Mwaipatsa moto a Mada/ mwatentha mwatentha *VERSE 1 - K Banton* Woozzah Akakhosomola ndekuti afuna pizza // Amadaliso nthumba mwawo sachedwa ku pisa // Issa mpaka namupangisila Viza // Nkazi oti nangokumana naye pa Insta Gram// Pano ndi mlamu // Mmhu am so dam // Ine nkangofuna kudya Buble gum hmmm// Murder Murder Murder Murder hmm satha kumvetaa // Pena Gena.. zomwe imapanga the other gender // Pakakhala Dollar imangobenda Yeah // Malo mopala moto undipalimulisa // Mabomba a rasha ndizindikila nda phulitsa // Katundu wanuyo ndikuziwa mumagulisa // Mdulidwe wazimayi kulibe nde osadulisa// Iiih aMada *CHORUS - Phyzix* Mwanakazi Mwanakazi Undipalamulitsa Mwanakazi Mwanakazi Undipalamulitsa Iyiyi nde ndi Murder Case/ Murder Case/ Murder Case Iyiyi nde ndi Murder Case/ Murder Case/ Murder Case *VERSE 2 - JEG Tellem* Zofuna za Mada ase / Zikangolowa ku madance eti / Kugula Gin Wawa Castel / Aphula sin akangotell Mhuu Uyu singagwire mwa easy Kundipasa chance singasinze Ngati chux ndi maplan ndili busy Kuti ukhale mula wa Jizzy Nkazi wachi body chonyadisa nde sinzakubisa anthu akudziwe Pa Facebook insta ndi Twitter ndikasintha picture pakakhala iwe Koma MADA doesn't care / Ena ATI ndika wash and wear / ndimamufuna kuposa mpweya / Mundilangiza ine, Osamvera aaah *CHORUS - Phyzix* Mwanakazi Mwanakazi Undipalamulitsa Mwanakazi Mwanakazi Undipalamulitsa Iyiyi nde ndi Murder Case/ Murder Case/ Murder Case Iyiyi nde ndi Murder Case/ Murder Case/ Murder Case *VERSE 3 - Mellz Kumpanje* Ukumachita kundigwedezera matako mada, ine si charisma pa Tuno//aaah FADA (alipo samafuna kudya) (mada) ine ndiofewa mchiuno//atandimanga sangamve zokuti umachita kundipeza wekha kwathu kuno//nde panopa,sukumavalamo mwado (mada) ukumangongoyenda buno buno//ndikati easy--- umati NO..umaipatsa moto (ipondeni fadah)//umaiwala zoti amanjata (Gwii).........ufuna ndikalowe ndi Mada//?? Why you gotta do me like this mada// Ukufuna kuti ndipange commit mada// Ukupanga chani madalitso ufuna khoba izawatenge fada// *CHORUS - Phyzix* Mwanakazi Mwanakazi Undipalamulitsa Mwanakazi Mwanakazi Undipalamulitsa Iyiyi nde ndi Murder Case/ Murder Case/ Murder Case Iyiyi nde ndi Murder Case/ Murder Case/ Murder Case *VERSE 4 - Jolasto* Mpaka ndiphula ma sin kamba ka iwe Mada Wina ndimuNYIKA ndimadana ndizaFANTA Ndakumvela kuwawa kuti ufike apapa Ndipo muwuzane wina ndimuchotsa mphafa Unaponya status ukumenya nip Sikuti ndikuku kumba ndangowona ma pic Kuyiwala kwanu unapanga mistake Ati Blantyre sinodi? Zawu wayilesi Madaaa kaya unafa kwambiri Nane ndi mfumu ndikudyesa ma tick Ukuwonjeza my queen Nane town ndiyanga ngati maskin Eti uli blues? Ukumwa manica? Ukuspendar dollar Ulindima niga? Eti zafika poti boys ikukugwila? Ati uli ready akufunayo aika? *VERSE 5 - Guntolah* Mada mbuyo monsemu sinakhale case Mwina ndili mwana kusewelesa zikhesi Koma anthu akwathu akati napangidwa curse Akazi ndinkagwila ngat Shammah no reverse Nkaz opanda mbuyo, kumandibwenza mmbuyo Sinaphake naye life ati Anali smoke, sinatchaye olo life Ati Samva Maloza, chifukwa chan anaonapo maloza Ati x wake sankapanga cholozeka Asing'anga agwila ntchito ine ndekha ndolozeka Koma inalipo nthawi, yosowa chochitika Ma Beat mangonyika Asilamu akudanda ati sindipanganika Kubwera mada, kuwelama Kuzasikana kenako kukwerana Ndichi red sign nkona tikufilana. MADA *CHORUS - Phyzix* Mwanakazi Mwanakazi Undipalamulitsa Mwanakazi Mwanakazi Undipalamulitsa Iyiyi nde ndi Murder Case/ Murder Case/ Murder Case Iyiyi nde ndi Murder Case/ Murder Case/ Murder Case *VERSE 6 - Beejay* Mwana kazi undipweteka Unditakasa Undipepeta Ndikagona Ndiku Mbrupahur hvd Ndiku bwebweta! Upange zomwe wanena Ndipo ndizione zikuthekeka Ngati wati cheke Cheke apa! Ndikuone ukuchekeka iiiyh MADAm mada .ukalola Ine Wadya!! MADA undimadalits Iii taonani undibalalitsa! Azimayi Nthungululu pamenepa! Amanena kuti love Is blind Ine kuno khungu Nde yandipweteka Sindikuona komaso sindikubona undivetse *VERSE 7 - Ace Jizzy* Dzina ndani? Madalitso Ndiwe okongola ngati ku paradizo Tabwera kuno....mdzataniso? Tiime pachulu ngati bwana Mbizzo Ana okuposa palibetu Or nkhalamba paliJETU Gaire ndalama....pa Easy'tu Dollar yaine sungamalizetu Ine ndi mponda matik Ndimamenya ...mponda ma kick Nkonda ma gig nkonda ma chick Mada usanditole tola ma pic Umulore MADA gangster Honey moon ndiku MADA gascar Ndamva zoti wakana chi namtindi Iwe ndiine love Mwantinti *CHORUS - Phyzix* Mwanakazi Mwanakazi Undipalamulitsa Mwanakazi Mwanakazi Undipalamulitsa Iyiyi nde ndi Murder Case/ Murder Case/ Murder Case Iyiyi nde ndi Murder Case/ Murder Case/ Murder Case *VERSE 8 - Che Kalonda* Mfana ophulitsa life ngati Makombola Kuthamanga kwambiri kuposa Corolla Kumuuza Kuti tiye amangolola Chilichonse atha kupanga nabola Dolla Nde Ali Ndi chi figure Ngati Masamu Dzimatatoo Mbwee Mmatakomu.. Wapengetsa Ma Bwana Ntaunimu Koma Chonde Usadye Ndi Halamu Nde Mwati iyeyu ndi Ndani (KAYA) Wabwera Ndi Ndani, Akumwa Chani (KAYA) Mwina Kapena Ndimupatse Plan.. Mmmmh Dadda Uyu Akuchedwetsani *VERSE 9 - Waxy Kay* Akazi akalowa mu boy zone//olimbana nao amwa poison//Bambo anga paza kuden zima weapon//Wina azakushoshe azalira Ring tone.. Iwe Uzangomva ngiri ngiri//Wina azanditenge kuchigwiri gwiri//amuna anga alusiratu kuno dada//amuna anga atha kupalamula mada *CHORUS - Phyzix* Mwanakazi Mwanakazi Undipalamulitsa Mwanakazi Mwanakazi Undipalamulitsa Iyiyi nde ndi Murder Case/ Murder Case/ Murder Case Iyiyi nde ndi Murder Case/ Murder Case/ Murder Case
@sheilakankhwangwa75248 ай бұрын
This is really nice
@PoshaPhiri7 ай бұрын
No🎉😅 2:00 😢😮🎉😅😮😅😢🎉😢l
@PoshaPhiri7 ай бұрын
No🎉😅 2:00 😢😮🎉😅😮😅😢🎉😢l
@Tabie1028 ай бұрын
Ace Jizzy ndi Bee Jay ndi anthu owopsyatu 💥🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥
@focusrica-dq6ii8 ай бұрын
Jolasto fans let's gather here 🎉
@GabadCaster8 ай бұрын
Dolo ndi jolasto 💪
@Motionmedianow8 ай бұрын
Shasha uyu
@FaipPhiri-sz6rh8 ай бұрын
Jizzy ndikatundu wambiri eee🙌
@C1_Eddie8 ай бұрын
Mellz fans gather here aphwetekatu kuno gist ija..umatha breda
@Motionmedianow8 ай бұрын
Fada awa🔥
@muhammadanussa67828 ай бұрын
Remix iyiyi palibe number 1, nonse mwawina maguy👊💪💪
@PreciousStephano-h5w8 ай бұрын
Team of Young King Waxy Kay lets come here verse wapha bwino kwambiri katundu Waxy Kay ukali wanu fadah 🔥🔥🔥🙌
@TrynessChima8 ай бұрын
Guntolah and kbanton
@matiasselepa58778 ай бұрын
BEE JAY top funny let's gather here😂😂😂
@Motionmedianow8 ай бұрын
🔥😂
@KelvMwanga6018 ай бұрын
Mellz, Bee jay eeee mwaipweteka guyz ...... Big up
@ernestjuniormbanga33708 ай бұрын
Mada on repeat iyiyi ndie ndi Mada😊 all fans of mada lets gather here
@jamesvwelekete44008 ай бұрын
Well done guys iyi mwaika a phyzo ngati panokha simukwanisa kubebesa nyimbo kumaitana azanu moyo ndi lende
@keazalinthwane57877 ай бұрын
Guntola wabwela iweyo❤
@ManuelMateyu-m5b8 ай бұрын
Ace jizzy uja osazaphwekesa osaiwala k banton💥🔥🔥
@frankchitala11648 ай бұрын
Ma verse awawa samayenera hook ndi beat ngat iyi, Phyzix aaah do chi hit kuposa legends
@CedrikChikuti8 ай бұрын
Nyimbo yomvela pa repeat ija nde ndiimeneyi✊🏿big up
I hated the song but this remix phyzix big up u jxt take it too far I love this ❤❤❤❤ remix
@AubreyDesilva8 ай бұрын
Ace jizzy no mistake, deliverance on point
@DavieSaidi8 ай бұрын
❤ Guntolah 1, ace jizzy 2 for me 😊😊😊😊Mellz 3,Banton 4 content and styles kwinako mumaliza .... Collaboration of the year hip pop
@gadamaaaron7868 ай бұрын
K banton big imavuta uyuu listen ma headset abho bho u will see fact! , koma Mellaz wapweteka onse
@MosesPhiri-bu9fs8 ай бұрын
Young King siwamaswera, koma mellz uja osadzamuphweketsa
@giftscot84905 ай бұрын
Ndiwe wachibwana. Usamasewere ndi ace jizzy ndi bee
@Motionmedianow8 ай бұрын
🔥🔥🙌eeeh boiz inasiya kucheza
@kondwanisimkondaJue8 ай бұрын
Ace Jizzy mofaya🔥💫
@chantobmw8 ай бұрын
Nyimbo Mwaipanga mada iyii ❤
@IvyMaureeenMhango5 ай бұрын
Mellz Kumpanje ndi dholo ada🔥🔥❤️
@preciousbulambo-o5g8 ай бұрын
Guntolah1, Ace Jeezy2, Mellz3,Waxy 4. Nice coraboration guys. Yabeba. Apa pa repeat basi
@giovannilmataya54398 ай бұрын
Mellz n Waxy 🔥
@sydneyharawa95808 ай бұрын
Che Kalonda- usadye ndi halam🏃🏃
@enocksasani45088 ай бұрын
😂😂😂 wapha 🔥🔥🔥
@Motionmedianow8 ай бұрын
Chilombo ichi
@chrismasula8 ай бұрын
Chi nyimbo on repeat 🥳🔥😩
@pboysucre-MILM8 ай бұрын
Nyimboyi yangokhala ngat cypher 🔥🔥😂
@ajdamawaya53428 ай бұрын
Ace jizzy waidya 🔥🔥🔥🔥
@ZaynabYusuf-dj1lm7 ай бұрын
❤❤❤ nice guys za srs pamalo
@Molly-ij1yr8 ай бұрын
Osafera zinazo jolasto waika power
@ishmaelthomasndipange8 ай бұрын
Ace jeezy, iyeyu kaya bwanj... Bax titola ma pic... Guntolah nanu mwakhazika bata enao...🎉🎉🎉 Young king lero simunatitengetu tinakonzekera inuyo komabe👍