Professor Peter Mutharika Speech Mjamba Rally (19 December 2021)

  Рет қаралды 20,118

Bakili Muluzi TV

Bakili Muluzi TV

2 жыл бұрын

Professor Arthur Peter Mutharika kulankhula pa mjamba rally mu mzinda wa Blantyre lero la mulungu pa 19 December 2021.

Пікірлер: 63
@rashidstamburi2705
@rashidstamburi2705 2 жыл бұрын
President wathu koma uyu osat nyama zili panozi zachina chakwela Peter muthalika 2025 boma basi vote yanga 💙💙💙💙 I miss you adadi 🇲🇼🇲🇼🤦🏻‍♂️🤦🏻‍♂️🤦🏻‍♂️🤦🏻‍♂️🤦🏻‍♂️
@patrickmauwa1957
@patrickmauwa1957 Жыл бұрын
Umakwana izi ndimbava asatana mumaonekedwe angero
@patrickmauwa1957
@patrickmauwa1957 Жыл бұрын
We miss you adad chimandisangalasa sakonda kuyankha zopusa my only president PETER MUTHALIKA
@ismailmalawi2697
@ismailmalawi2697 2 жыл бұрын
Adadi mwakhulurukile mayi anga popongela vote kwa ng'ona kwatale ameneyi
@patrickmauwa1957
@patrickmauwa1957 Жыл бұрын
My bloved president tinachitanso rural electrification musaiware
@wyclifsymon5105
@wyclifsymon5105 2 жыл бұрын
More fire 🔥🔥 Mr president wanthu 🔥🔥🔥
@lukainnocent5380
@lukainnocent5380 2 жыл бұрын
Singapore yija yilikuti
@williamdaisithom5913
@williamdaisithom5913 2 жыл бұрын
Excellent Adad DPP and UDF together is one; well done, will not make mistake again please. 🕊📖.............✍
@lukainnocent5380
@lukainnocent5380 2 жыл бұрын
Ine palibe ndikutengapo chazeru nyasi zokhazokha
@dumisanilubisi3471
@dumisanilubisi3471 Жыл бұрын
Lowan ndindare zanu agogo
@Razarusmbavachakwera
@Razarusmbavachakwera 2 жыл бұрын
Nyasi ziwilizi ziyenera kuchosedwa mwachangu
@mwayikaunde8868
@mwayikaunde8868 2 жыл бұрын
Mwayipatsa moto adadi
@user-le9su3mt7r
@user-le9su3mt7r 3 ай бұрын
Chilima bomaaa
@chikumbutsotsalangu5511
@chikumbutsotsalangu5511 2 жыл бұрын
Mbambande. Mr president
@user-le9su3mt7r
@user-le9su3mt7r 3 ай бұрын
Apitala amumeni mwachekulaa
@user-nd4gh1fi5q
@user-nd4gh1fi5q 4 ай бұрын
🎉
@lazarusnamakhwa6184
@lazarusnamakhwa6184 2 жыл бұрын
DPP boma
@user-cy5ko2qw5d
@user-cy5ko2qw5d 3 ай бұрын
ADADl tipulumutseni
@wysonmpatama4393
@wysonmpatama4393 2 жыл бұрын
Zoona ndi ng'oma nkhaza kwambili
@yusufujbinali8934
@yusufujbinali8934 2 жыл бұрын
100% bro
@mikerrr7552
@mikerrr7552 2 жыл бұрын
Big man we miss you
@alephangoma2158
@alephangoma2158 Жыл бұрын
Zinthu zakwera ndi chakwera
@hopeskafumbiphiri6011
@hopeskafumbiphiri6011 2 жыл бұрын
salute father you are the best
@esnartnkosi3419
@esnartnkosi3419 2 жыл бұрын
Better Dpp than MCP
@user-le9su3mt7r
@user-le9su3mt7r 3 ай бұрын
Pitala mbava kwambili waba kwambili
@lewisbonongwe8518
@lewisbonongwe8518 Жыл бұрын
It's only these two parties DPP and UDF
@frankkamunde4575
@frankkamunde4575 Жыл бұрын
Kulira samaletsana tamalirani ndi nthawino yanu anzanu analira mokweza dzaka 26 ali kunja Kwa boma tsono inu dzaka dziwili dzomwezi simunati mulira zeni zeni
@user-le9su3mt7r
@user-le9su3mt7r 3 ай бұрын
Pitala una zanga mithundu
@selemannyirongo1994
@selemannyirongo1994 2 жыл бұрын
Yankhulani zomveka nanunso.samati ndimakugonani kwambiri
@patrickmauwa1957
@patrickmauwa1957 Жыл бұрын
Ikudula mwana wasatana iwe
@patrickmauwa1957
@patrickmauwa1957 Жыл бұрын
Chakwera simunthu wamulungu ndimwana wasatana,i like malemia's speech that chakwera is a great fool
@patrickmauwa1957
@patrickmauwa1957 Жыл бұрын
Men of integrity (my President Author Muthalika professor
@patrickmauwa1957
@patrickmauwa1957 Жыл бұрын
Please don't reverse your mind of competing again am listening your speech here in southAfrica n 2025 we r coming to vote for u my dear President.
@sheilabanda7935
@sheilabanda7935 2 жыл бұрын
Nanu munationjeza koma nanga mpaka chimulirenji kukhala vice🤠
@user-le9su3mt7r
@user-le9su3mt7r 3 ай бұрын
Pitala usanga mituthu hiwee
@chesterphiri7523
@chesterphiri7523 2 жыл бұрын
Indeed inutu simunamange anthu koma kuwotcha anthu mu nyumba.
@shukranphiri2109
@shukranphiri2109 2 жыл бұрын
Kkkkkkk man mwatani kodi
@chesterphiri7523
@chesterphiri7523 2 жыл бұрын
@@shukranphiri2109 Aaaaaa Bwana azitiwuza zawozo lero yet we lost the Tambala family ndi moto. It was useless leadership of Peter Mutharika that brought us Chakwera. If it were that APM was doing his job properly pano a Chakwera a Leader of Opposition koma incompetence ya Madalawa lero anyhu akulira ndi Chakwera
@claramaonga4678
@claramaonga4678 2 жыл бұрын
Timadziwa kale kuti chakwera yake ndi ya ubusa osati kuyendetsa dziko pano athu akumwalira ndi njala iyeyo akudya kumeneko
@bestonjoseph2193
@bestonjoseph2193 2 жыл бұрын
Koma abale munthu mukumuvutitsa Chifukwa chani, osamusiya azipuma bwanji
@lughanomwakibinga7944
@lughanomwakibinga7944 2 жыл бұрын
ndimaona ngati nkuluyi anayankhulako zanzerutu..... still living in the past and trying to manipulate innocent minds to his own selfish desires....once ur hooked by it mpamene ukumati ADADI ADADI... stupidity of lazy people who always waste their time and energy on politicians....instead of focusing their own future..
@akamchachakamchacha429
@akamchachakamchacha429 2 жыл бұрын
Unaba kalekale ndalama zathu zamsonkho gologolo iwe
@stephenkbanda598
@stephenkbanda598 2 жыл бұрын
Amalawi sitichedwa kuiwala,munthu ameneyu anawononga zinthu ali muboma pano tikuti anali bwino🤣🤣 thus why sitizatukuka,we will always be one of the poorest countries 😭😭
@user-le9su3mt7r
@user-le9su3mt7r 3 ай бұрын
Is true pilata mbavaaa
@paulnkhama3621
@paulnkhama3621 2 жыл бұрын
Kapumene mwakalamba
@nellikkmwenda7087
@nellikkmwenda7087 2 жыл бұрын
Boza achakwela ndichilima
@actuarialscience2283
@actuarialscience2283 2 жыл бұрын
Never again
@alephangoma2158
@alephangoma2158 Жыл бұрын
Not chichinji
@akamchachakamchacha429
@akamchachakamchacha429 2 жыл бұрын
Aaaaa ndalama unaba nchifukwa chake achakwela boma sizuenda bwino coz of u alaaaaa kagwere uko
@alexjuah8831
@alexjuah8831 2 жыл бұрын
Nkhalambayi ikagwele uko waba yiba ndalama wayambilaso kunamiza a Malawi ogona
@luciascharles4345
@luciascharles4345 2 жыл бұрын
Anyamata ndi awa akutinamiza, kutibela, komaso kutikwezela zinthu
@mikerrr7552
@mikerrr7552 2 жыл бұрын
True mcp nonsense
@user-ix4yp5lp8m
@user-ix4yp5lp8m 9 ай бұрын
Koma inetu fundo zina za AMALAWINU MUMAKHALA Ngati mbuli zokhazokha ...Amalawi chinthu chomwe mumachifuna simumachidziwa m Chifukwa chake MUKHAULA Lelo NDI Chakwela wanuyo ..Inu mungamati Adadi Alibe fundo ndiyeno Muli m fundo ndinuyo???? Haaaaaa kuvetsa chisoni Amalawi KUCHITSA MANYAZI
@talimilejosephmakawa4967
@talimilejosephmakawa4967 2 жыл бұрын
Hahahahha iwe ndiiwe mbuzi kwabasi mcp yalephera pati poti nthawi yawo siidathe tizaweruza ikazatha term yawo
@alexjuah8831
@alexjuah8831 2 жыл бұрын
Tikukumbukilabe ndalama zathu za msonkho iwe ndi nzakoyo zipani za banja
@luciascharles4345
@luciascharles4345 2 жыл бұрын
Ndiye uyo zidali boo amakubelani koma mokuganizilani,,,, lero mukubeledwa, kukukwezelani zinthu, ndikumakunamizaniso popo
@alexjuah8831
@alexjuah8831 2 жыл бұрын
@@luciascharles4345 YENDA ULENDO MAYIKO ENA UPEZE YANKHO
@luciascharles4345
@luciascharles4345 2 жыл бұрын
@@alexjuah8831 palibe aise ine ndaenda ndipo ndikuyendabe koma zikuchitikazi siboo
@lukainnocent5380
@lukainnocent5380 2 жыл бұрын
Mbuzi yamunthu stil far gys amalawi ife. Ndife azisiru kwambiri aaaaà dpp ndiudf zipani zausiru malo mokoza dziko akulimbana ndizazii fundo mlibe agogo
@Littlefair7
@Littlefair7 2 жыл бұрын
Kupanda manyazi madala 🤣🤣🤣🤣
@user-le9su3mt7r
@user-le9su3mt7r 3 ай бұрын
Chilima bomaaa
@user-le9su3mt7r
@user-le9su3mt7r 3 ай бұрын
Pitala mbava kwambili waba kwambili
Izindaba zesiZulu @19H00 | 03 June 2024
19:39
SABC Izindaba
Рет қаралды 10 М.
Tonse alliance yatha; Chakwera akhale President wamuyaya.
10:18
Bakili Muluzi TV
Рет қаралды 37 М.
Indian sharing by Secret Vlog #shorts
00:13
Secret Vlog
Рет қаралды 57 МЛН
Do you have a friend like this? 🤣#shorts
00:12
dednahype
Рет қаралды 49 МЛН
Pray For Palestine 😢🇵🇸|
00:23
Ak Ultra
Рет қаралды 33 МЛН
2024 Elections | 'I have accepted the results'| Maimane
15:40
SABC News
Рет қаралды 103 М.
Watondeka; Chitukuko kulibe ku Malawi; Fetereza wadura kwambiri
15:19
Bakili Muluzi TV
Рет қаралды 20 М.
The Times Malawi Report: CCPF Impresses South African Officials
2:51
Galu Wamenyedwa Mbuyache Wadziwika  - Bon Kalindo (Nyasa VoiceBox Edit)
22:32
Indian sharing by Secret Vlog #shorts
00:13
Secret Vlog
Рет қаралды 57 МЛН