A very good reference to Malawi. Let SKC be Moses but our Joshua is not here yet neither what we are remaining with. MAY THE SOUL OF Dr SKC KEEP RESTING IN ENDLESS PEACE 😭😭😭
@kelvinchola73928 күн бұрын
Listening you from Zambia 🇿🇲, May God protect you more Man of God Kambili
@patrickndojime1632Ай бұрын
Abusa akambwiri Mulungu adzikudalisani ma unthenga anu onse munthawi zonse ❤❤❤❤❤❤❤❤❤ Amen
@LinesiKanzota-fw7sjАй бұрын
Amen pastor kambiri mwatilimbikitsa ulemu NDI matamando zipite Kwa iye wamwambayo
@user-ks2fq6ep4tАй бұрын
Pastor kambiri you are a blessing to us, we mourn with u here in Zambia.
@LuskaMoses7 күн бұрын
😢😢😢poti simulakwitsa ambuye munaxhitira dala kuti tione akapuku kudxiko kuno kuti ndani ndipo tikwaonadi eish ambuye chitani monga mufunira😢😢😢
Eish achakwsra akuoneka ngati mkangotu, tawawoneni pa chithudzipa
@devlinebhema272924 күн бұрын
Anamulakwila munthuyi😢
@HawahJamesАй бұрын
Men
@jtm7233Ай бұрын
Usiku opweteka osowa choyankhula
@jtm723317 күн бұрын
Abusa zikomo kwambiri chifukwa cha uthenga wotilimbikitsa , Zoona ndi Mulungu yekha amene Ali ndi mayankho a zonse. Mizimi ya abale athu kuphatikiza a Vice President iuse mumtendere