SITUATION MALAWI WAUZA VALENTINO NDI YOLAM CHILUNGAMO MAI BRENDA ATAOMBELEDWA

  Рет қаралды 15,209

Malawi Trends TV

Malawi Trends TV

Күн бұрын

Пікірлер: 47
@ChristinaMdeza
@ChristinaMdeza 14 күн бұрын
A chimwene zimwe mukuyakhurazo, zoonadi chipani cha mcp, ndichoyipa, kwambiri tinawoon ife yokha, ife mene anamuphele malemu chilima, kuchikangwa kuja kupha, ngati, njoko,.mafuna kuti amuphe,mai uja, Kom Mulungu. wathu sanalole ayi,.anafuna kuwasiya poyera chocho we love you bro❤❤
@EvansEgra
@EvansEgra 13 күн бұрын
Anthu 22 aja inapha Dpp ku mzuzu sianthu? Mukungolaķhula za Chilima basi? Who is Chilima? What special of Chilima? Wosalakhulapo za anthu 22 aja,ku mzuzu
@RosePhiri-n8q
@RosePhiri-n8q 15 күн бұрын
Mukapeza wapolice ali kumbali ya mcp mumenyeni akanene kwa chikangawayo
@Staphelsavimbindhlovu
@Staphelsavimbindhlovu 12 күн бұрын
Zoona bambo anthu, mulungu akupasen moyo wautali❤❤❤❤
@NorisMlongoti-e5i
@NorisMlongoti-e5i 15 күн бұрын
1000% you're right brother!!!!!
@HerlbertKaalis
@HerlbertKaalis 11 күн бұрын
APM ndi chikuni Chosunga Moto komanso ali ndi umunthu His excellency !!!!!! Chikangawa wagwa nayo
@MikeSangano-u8m
@MikeSangano-u8m 11 күн бұрын
Well narrated my brother.Keep up bro
@AchinaKellz
@AchinaKellz 15 күн бұрын
A mcp akuti wolungama😂I don't believe ngati dziko lizakumveleni chisoni, advice kachilungamo kwa mbamva
@GstarNana
@GstarNana 14 күн бұрын
Umakwana brother Apm my vote
@AllanBiseck
@AllanBiseck 15 күн бұрын
We are tired of this ruling party
@RobertLuka-wy9cl
@RobertLuka-wy9cl 11 күн бұрын
Brother 🙏🙏🙏🙏🙏🙏
@TimothyKumwenda-z4m
@TimothyKumwenda-z4m 10 күн бұрын
Chikangawa akungopitilizabe zoipa esh
@patrickmacheso5062
@patrickmacheso5062 15 күн бұрын
Pomwe zafikapa tingoyambapo kuswana bc,,, coz MCP sikufuna Democracy ndiye nafe titha kumabwezera ngati wa MCP watiputa,,, Mfuti nafe tigula.
@DeborahNyirenda-ls1ip
@DeborahNyirenda-ls1ip 14 күн бұрын
🎉mau opanda chigamba
@JosephHill-fy1bb
@JosephHill-fy1bb 14 күн бұрын
Smartmatic nde yathudzulidwaaaaaa 😂
@WilsonFelix-j9n
@WilsonFelix-j9n 11 күн бұрын
Umachedwa kuti mfana oganiza bho? Ndakukonda aise
@JafaliAkimu-ll1bf
@JafaliAkimu-ll1bf 15 күн бұрын
ziwuzen zitsiru zigawenga za mcp chskwera pamtumbo pake
@JumaEriya
@JumaEriya 15 күн бұрын
Mopepha mutiunzire chakwera afufunze amene watengafuti ndikumuwombera mzimayi wa DPP masiku asanachuruke .ngati maremu chirima ndi athu ena aja.ngati satero timange chakwera bs😮
@ThokoMsonkho-hy4uc
@ThokoMsonkho-hy4uc 14 күн бұрын
Kodi zimene zija zikanachikira munthu wa MCP a CHIMWENDO akanapangitsa PRESS BRIEFING tsiku lomwe lija koma chifukwa ndiwa DPP akufuna atamfa kupungura mavoti. Panopa tizuke a Malawi tiphe masapota a MCP ndi apolice akangopanga mistake iliyonse NO MERCY upon ANY POLICE who is serving MCP government.
@rashidadan2533
@rashidadan2533 15 күн бұрын
Don't make another mistake this year 2025 , Omuvotela mwamudziwakale kuti ndi His exllence professor Peter muthalika The only last hope for Malawians , Ngati mukufuna Kuti mitengo yakatundu azasike ngati mwakale,,,, Ngati mukufuna kuti chitetezo chadziko chizabwele mwakale ,,,, Ngati mukufuna kuti mafuta agalimoto azapezeke ngambwi ngamhwi ,,,, Ngati mukufuna kuti ufulu wa amalawi uzapitilile ngati kale kaja,,,,, Ngati mukufuna zitukuko zakathithi,,,,, Nkhani yama passport,,,,, Nkhani yanyanja ya makawi,,,, Nkhani ya ndege kuchikangawa,,,, Zinthu zonsezi zomwe zatchulidwazi zikufunika professor , Ndati professor , sizikufunikanso nthumbidwa ngati chakwela ,
@WarriorKB-l3i
@WarriorKB-l3i 12 күн бұрын
Ndipo zoonadi asavutike kupanga kampeni chifukwa bomali lapita kale, chikangawa nthawi yatha.
@KennedyPhiri-h9h
@KennedyPhiri-h9h 14 күн бұрын
Ndipo izi izi one day azawona polekela sure
@GabbinaTengen
@GabbinaTengen 15 күн бұрын
Tisakomoke guys lyf ipitilire boma ndilomweli opposition ndiyomweyi bwelan mudzavote.
@GeorgeSydney-y1m
@GeorgeSydney-y1m 13 күн бұрын
Zoona braz
@SteveNdhlovu-r2x
@SteveNdhlovu-r2x 15 күн бұрын
Eeeetu mpaka kumenya ndi hamala chilima amene anakuikani pa mpando mmmm olo satana siwoipa choncho.
@esthermalixani2244
@esthermalixani2244 14 күн бұрын
Mawu ndipo ukunena zoonad
@isaacgmc
@isaacgmc 10 күн бұрын
Menyani apolisi mukawaona zausilu
@MichaelStaford
@MichaelStaford 15 күн бұрын
Mbava izi!!!!
@ColetteMalunga
@ColetteMalunga 15 күн бұрын
MCP should go and rest 😂
@ghettodripper
@ghettodripper 14 күн бұрын
Fact
@AchinaKellz
@AchinaKellz 15 күн бұрын
Wapolice adziwa andale zimene amachita sadzakuona kundende akazakuona dziwa kuti akupakula beans mkazi wako
@BilalihmacksonBilalih
@BilalihmacksonBilalih 14 күн бұрын
Ndiwe wamzeru
@AdyasiMaulana
@AdyasiMaulana 15 күн бұрын
Eti mpaka nyundo kutengela ku nkhalango kukamenya chilima ayi zosayenda
@WysonChilonga
@WysonChilonga 14 күн бұрын
nkhaniyo nde ndiyoona
@GeorgeBanda-x6l
@GeorgeBanda-x6l 15 күн бұрын
Brother walankhula zoonad
@AllanChabwela
@AllanChabwela 15 күн бұрын
tikufuna chilingamo mcp zotengela malamulo ku manja
@CorencPromise
@CorencPromise 15 күн бұрын
Unena zowona
@hackwellkagolo6614
@hackwellkagolo6614 14 күн бұрын
sangave chifukwa ndi mmene anaphuzilila tchito ku mcp kuti azigwira choncho basi
@Nelsonmatenda
@Nelsonmatenda 11 күн бұрын
Mcp , chakwera ayi ...
@MosesTangwe-q8o
@MosesTangwe-q8o 14 күн бұрын
Koma wapolice ameneyu tisangomusiyasiya.tilange wa police ameneyu kut ena atengelepo phunzilo
@chimwemwenkute3839
@chimwemwenkute3839 15 күн бұрын
These guys they have lost. direction indeed are forcing things
@JamesALLi-m8i
@JamesALLi-m8i 11 күн бұрын
Yes that is true mr man be strong 💪 we don't need this government again Apm is coming soon to be president of this country 😀 😉 👍 👏
@thatgirrroskrr3570
@thatgirrroskrr3570 15 күн бұрын
Anthu awa mzelu zawathela
@TitusKalea
@TitusKalea 11 күн бұрын
Bomali tatopa nalo
@FelixKChisale
@FelixKChisale 14 күн бұрын
Inu simungalimbane ndi malamulo
@AnishaMoosa-ej7yr
@AnishaMoosa-ej7yr 15 күн бұрын
boma
@EmilyKanyika
@EmilyKanyika 15 күн бұрын
Mcp machimo
Comarde Ntanyiwa Pa Limpopo Fm "Chakwera Amukaniza Kupita Ku America"
22:22
SLIDE #shortssprintbrasil
0:31
Natan por Aí
Рет қаралды 49 МЛН
진짜✅ 아님 가짜❌???
0:21
승비니 Seungbini
Рет қаралды 10 МЛН
JOSEPH NKASA WAPANGA ZA ATCHEYA BAKILI MULUZI CHAKA CHINO
8:02
Malawi News Xtra
Рет қаралды 140 М.
TALANDIRA RASHID {MWAPHA MALAWI AKUDZAYO}
4:01
VENNIX MW
Рет қаралды 19 М.
Padziko LAPANSI PALIBE CHISISI. ZAWULULIKA ZA NGOZI. NTANYIWA
31:26
FRANCIS MTAWAYA TV
Рет қаралды 60 М.
TOP 3 YA MA INTERVIEW A BRIAN BANDA OMWE ANADUMPHA MALIRE
16:35
Factory265 Media
Рет қаралды 80 М.