Nde a mcp akuzivutiranji kupereka ma ID kulilingwe kokha kkkkkkk
@PhalesNotta2 күн бұрын
Komatu koma DPP yanyamuka bas satana walephera😮😮
@MustapherLino2 күн бұрын
Dpp woyeeeee Peter mutharika woyeeeee
@TheresaNtodwa2 күн бұрын
Mcp condem!!!!! ❤❤❤❤. Dpp bomaaaaaa
@alexsumani68232 күн бұрын
msonkhano opanda oimba uwuu
@RobertLuka-wy9cl2 күн бұрын
Dpp my vote ❤❤❤❤❤
@JoefreyGongoni2 күн бұрын
Mukhale cheru ana asatana atsikira komweko
@RiteRoderick2 күн бұрын
Komaa guys ku Lilongwe konko 😂😂😂😂😂 opandanso kugawa ma 2 pin😂😂😂😂😂😂
@brainsmkumbwa62672 күн бұрын
Kochedwanso kuti ndi kwao kwa Chakwera
@RiteRoderick2 күн бұрын
@@brainsmkumbwa6267 Ndipo boss mmmmmm🤣🤣 Boma iloooooooooooooooo 🤣🤣🤣🤣🤣💪🏿💪🏿
@HenryPhiri-d2s2 күн бұрын
Omega banda ufune usafune dpp boma
@robertkalima8742 күн бұрын
A Dad omwedyo
@MosesChazima2 күн бұрын
My voti❤
@SamuelChaibu2 күн бұрын
Dpp boma
@ThandieChris2 күн бұрын
Nyanja nyanja siine koma Brian banda
@JamesLongwe-qz9fd2 күн бұрын
Kkkkkkkk
@SamisonLevison-z5p2 күн бұрын
Nsonkhano koma umenewi,osati Kuma dance kuja
@IdahMphaya2 күн бұрын
Boma iloooooo
@LucyMachine2 күн бұрын
❤❤❤❤❤
@PatriciaAlomwe-oz8wc2 күн бұрын
Kubwela anthu mwa nyooooooo
@MercymithiMithi2 күн бұрын
Zikuchta kubeba
@EsetaGerate2 күн бұрын
💙💙💙💙
@DynaMzumara2 күн бұрын
Zilibwino
@NdaonaSandifolo2 күн бұрын
I love 💕 mcp boma sitisntha
@MzadziWanga2 күн бұрын
Sitinasinthepo boma timangosintha utsogoleri boma linalipo n lidzakhalapo mpak kale adindo ndiomwe timasintha😅
@AdamSaizi-k2q2 күн бұрын
Zabwino zonse blue Army
@ShamimuBisani2 күн бұрын
Wachikangawa wakutuma ndani kuti ubwere apa manyazi bwanji ndi ufulu wako kuvotera zmwe ukufunazo koma usabwere apa ndi manyi akowooo DPP ipatse motsooooooooo ufa mudengu osati chitedze mbale DPP
@AubreyWilson-j8w2 күн бұрын
Ayi zikomo wina ngati anyere
@felixsaidi67152 күн бұрын
Musiyanitse pakati pa show ya Dun lu. Ndi msonkhano wachipani. APM. Boma
@FatimaAdam-r5y2 күн бұрын
My vote ❤❤❤❤❤❤❤❤❤❤❤❤❤❤❤❤❤❤❤❤❤❤❤❤❤❤❤❤❤❤❤❤❤❤❤❤❤❤❤❤❤❤❤❤❤❤❤❤
So mwano mmanena uja kuti a mcp aziotchedwa kumwera, uku wakuotchani ndani? Anthu atsankho inu.
@DONNEXKhama-bk1gy2 күн бұрын
Without 2pin
@GeoffreyMaulana-rh5rx2 күн бұрын
Chipani chafuko
@tasmania5272 күн бұрын
Chipani cha Alomwe kkkkkk. Brothers' party, not so?
@MzadziWanga2 күн бұрын
@@tasmania527chikanakhala Cha alomwe anthu akwa mgona sakanatuluka bwezi Ali mmanyumba mwao,ine ndi nchewa from nkhotakota sindisapota chipani chifukwa chodziwana devaluation yake imenei mzikasapota zamanyi
@RiteRoderick2 күн бұрын
Koma eeeeee DPP ndi chipani chadziko zedi mmmmmm APM my vote ❤❤❤❤❤❤