ZOMWE ZILI KU NTCHEU

  Рет қаралды 14,698

HOT 265

HOT 265

Күн бұрын

Пікірлер: 62
@BerthiaChikopa
@BerthiaChikopa 3 сағат бұрын
True palibedi angavale shoes ya my beloved father in heaven ❤
@Homeofpeace321
@Homeofpeace321 39 минут бұрын
Chakwela akamaona nkhope Yachilima amakhala ndichimwemwe kwambili kuti wakwanitsa kupha amene amamupinga 2025. I pray nzimu wachilima uuke umukanthe Chakwela ndi banja lake
@paulbanda9638
@paulbanda9638 Сағат бұрын
Mangqnya achosedwe pliz pliz
@Fatima-db8ut
@Fatima-db8ut 4 сағат бұрын
Thr best president Malawi never had 👍
@ZioneMkwanda-y6i
@ZioneMkwanda-y6i 24 минут бұрын
Manganya yu nda amene akusokoneza ku UTM chonsecho chinapha Chilima mogwirizana ndi a MCP aaa galu manganya mulungu azakulanga iwe. RIP SKC😭😭
@OmegaChingamuka
@OmegaChingamuka Сағат бұрын
Manganya nfiti ya munthu
@JoefreyGongoni
@JoefreyGongoni 59 минут бұрын
Usi asakhale ngati ndiwe vachifundo mulungu akukhanda
@chimwemwechiundira6002
@chimwemwechiundira6002 6 сағат бұрын
His shoes were too big for anyone to fit in. RIP Biyeni. Lahla kahle Ngwenyama😭😭
@ShymanJamaicasingini
@ShymanJamaicasingini Сағат бұрын
Exactly
@OmarManjawira-up3ns
@OmarManjawira-up3ns 2 сағат бұрын
Ine izi zomati " I don't see any other president who can fit his shoes," sindimagwirizana nazo maguy we had Bingu the real Mafia tonse timalira ndi Imfa ya SKC koma stop kuwononga mbiri yawo pochemelera molakwika
@UlemuBaldwin
@UlemuBaldwin 5 сағат бұрын
Mr alankhulatu bwino zed,mau mau opanda chigamba
@abwinoamatani4921
@abwinoamatani4921 3 сағат бұрын
Wadyera ndi Michael Usi
@JoefreyGongoni
@JoefreyGongoni Сағат бұрын
Khunda sizingauluke choonadi chisanadziwe😢 chonde maBishop mwambo uyu mudzauchiteso kachikena chonde, muzimu vaChilima ulipadziko pano
@MariamJohn-dg4em
@MariamJohn-dg4em 2 сағат бұрын
SKC Rip, we wil never forget u Biyeni
@ChimwemweMathyola
@ChimwemweMathyola 28 минут бұрын
Mukuyangula koma ukupha alipopo
@spargomw
@spargomw 5 сағат бұрын
Manganya atachita kuvalira malaya a Gwanda😂😂😂😂😂 zilikotu ziliko manga😂😂😂. RIP bwana Chilima
@AlfredNazombe-me2ly
@AlfredNazombe-me2ly 4 сағат бұрын
Akufuna chani sikonoyo osamushwako bwanji
@ZioneMkwanda-y6i
@ZioneMkwanda-y6i 27 минут бұрын
Bonnie Kalindo adafunsa funso lomweli kwa A UTM kuti? Kodi Chilima akanakhala moyo inu a UTM bwenzi mukupanga izi muchitazi ? Koma anthu amati Kalindo ndi wamadrama lero ndiizi akubanjanso akunena, mautu a Bonnie Kalindo sapita pachabe, wamisala adaona nkhondo tisaiwale. Apa Bonnie Kalindo akukhala ngati akulongolora zomwe a MEC ndi NRB akubela ma lD nambala,apa zikuoneka ngati zopanda mzeru koma mawa tizaliranso , Kodi amalawi tizadzuka liti ?? Mmm kugona 2 much
@abwinoamatani4921
@abwinoamatani4921 3 сағат бұрын
Musatichitse manyazi angoni kulandira ziphuphu zochokera kwa Chakwera
@stevenmwamadi3035
@stevenmwamadi3035 5 сағат бұрын
Manganya ndiye ayi mumuchose kwambili ndi muthu oyipa kwambili anamupereka ameneyo
@AchinaKellz
@AchinaKellz 5 сағат бұрын
Manganya ayi akufuna aphe legacy ya abiyeni
@abwinoamatani4921
@abwinoamatani4921 3 сағат бұрын
Vice president kuvala ngati mukukawedza mbululu. Nkhope ikuchita kuoneka ufiti
@eliffagondewe8214
@eliffagondewe8214 2 сағат бұрын
😂😂😂
@OmexMainala
@OmexMainala 53 минут бұрын
Ndizoona palibedi angakwanise kuvaladi nsapato yachilima never
@PhilominaAustin
@PhilominaAustin 4 сағат бұрын
Ndipo usi ndikakuona sindikupuma nawebwino
@abwinoamatani4921
@abwinoamatani4921 3 сағат бұрын
Iwe bola, ine ndikamuona ameneyu ndimafuna nditasanza
@RosePhiri-n8q
@RosePhiri-n8q 4 сағат бұрын
Manganya alibe vumbulutso la moyo wake kaliat woyeeeeeee
@stevenmwamadi3035
@stevenmwamadi3035 5 сағат бұрын
Asakupepereseni manganyayo ndi muthu oyipa kwambili ameneyo akufuna achitenge chipani cha utm kupita nacho ku mcp musamare angoni ndithu
@giftbanda7690
@giftbanda7690 3 сағат бұрын
Wa Camera mumuuze kuti siku Lina azakhale ndi Starnd
@abwinoamatani4921
@abwinoamatani4921 3 сағат бұрын
Akubweretsa dyera ndi Chakwera
@DauglasBowa
@DauglasBowa 3 сағат бұрын
Manganya kanyama kameneka ndikoipa kwambiri
@muhamadizaidiphiri4449
@muhamadizaidiphiri4449 3 сағат бұрын
USI or ndalama kupeleka zoona
@JafaliAkimu-ll1bf
@JafaliAkimu-ll1bf 6 сағат бұрын
yudasi anamupereka chilima ali pompo udiyo
@muhamadizaidiphiri4449
@muhamadizaidiphiri4449 3 сағат бұрын
Koma izi kungopanga mukutilisa Ife abale chilima ndi machine
@DavieChiwale
@DavieChiwale 3 сағат бұрын
Kodi akuluakulu manganya akukakamira Ku UTM chifukwa chiyani achoke achoke sakufunika achoke
@BiliatMzungudala
@BiliatMzungudala 4 сағат бұрын
Manganya Rip 😂😂😂
@millionsenenje5010
@millionsenenje5010 5 сағат бұрын
Mawu amphamvu homie simeon salambula
@marthaphiri3600
@marthaphiri3600 5 сағат бұрын
I wish all leaders who want to stand for presidency in UTM should think twice to these words said by chilima's relative. Ine I said it in the last comment. Musaculuke ofuna u president chifuwa mudzagawana zisankho. Pick two only were I suggested manganya should lose the elections chifuwa adzagulitsa cipani. Kodi mwamvatu lero?
@FlynessWinga
@FlynessWinga 5 сағат бұрын
Manganya manyazi bwaaa
@abwinoamatani4921
@abwinoamatani4921 3 сағат бұрын
Usi chita manyazi
@AnusaNkhoma
@AnusaNkhoma 6 сағат бұрын
Manganyayo ndamene anampeleka
@JoyceZimba-pc4du
@JoyceZimba-pc4du 5 сағат бұрын
Good point my brother
@TonyMhone
@TonyMhone 5 сағат бұрын
Manganya ndikamamuona sindikuinapo za chisoni mwa iye. Mpaka ndakhala jenkha. Osabvalakp ndi shirt ya UTM eeeeeeeh!!! Kulimba mtima wotani Usi. Ndachita mantha kwambiri
@CardoJustin-l7m
@CardoJustin-l7m 4 сағат бұрын
Mnyamata uyu wandiyankhulira bwino kwambiri
@AginesWailes
@AginesWailes 6 сағат бұрын
Ndipotu tiziwe tikhutire bas 😭😭😭😭😭😭😭😭😭
@georgekamanyuzi108
@georgekamanyuzi108 6 сағат бұрын
Will never forget he was for everyone rip SKC
@yusufsadic2930
@yusufsadic2930 5 сағат бұрын
Ukanena kt wina sadzaonek nhat chilim ukunam Mulungu simunth mot iweyo ufuna kt uwauz Anthu kt Mulung sangapang munth ofanan ndichilim Paineyo sindingakhulupirir kt chilim adal wabwino kupona aliyens kumalawi ukunam
@BeatriceSaulosi
@BeatriceSaulosi 3 сағат бұрын
Munangodana naye ndiye ubwino wake simungsuone
@FysonKashon
@FysonKashon 6 сағат бұрын
❤❤❤❤❤❤
@FlynessWinga
@FlynessWinga 5 сағат бұрын
For sure no one can fit the shoes of Dr saulos chilima
@YamikaniWitness-vw3jl
@YamikaniWitness-vw3jl 3 сағат бұрын
Rest In Peace Mr Biyeni
@eliasgondwe
@eliasgondwe 5 сағат бұрын
Anthu tilibe pabwino Dr Usi adakalephela kupezeka kumwambo umeneu tikadampezaso zifukwa, lero wapezeka walakwitsaso iiii! Ambuye ndinu oyela basi
@GeofreyBandah
@GeofreyBandah 3 сағат бұрын
Ndipo zikanachita bwino kwambiri why to day yet walephera kupezeka muma occasion ambiri
@GeofreyBandah
@GeofreyBandah 3 сағат бұрын
Ndipo ine sizinandisangalatse
@JameRast
@JameRast 5 сағат бұрын
Yes his shoes were too big, , , ,
@Randy-er2xo
@Randy-er2xo 6 сағат бұрын
Mau mau
@mishecksipolo7153
@mishecksipolo7153 6 сағат бұрын
Bayeeeeeeeeeethe,
@EthelKubalasa
@EthelKubalasa 2 сағат бұрын
Ussi osamukhulupilila ku UTM ko
@AdamJames-x7x
@AdamJames-x7x 5 сағат бұрын
iwe manganya wazimvera wekhatu apa, akuti palibe yemwe angafanane ndi malemu skc ku utm ko, and chilungamo chake ndi chimenecho basi kkkkk kungoing'alula basi .
@JosephIsaac-s1c
@JosephIsaac-s1c 6 сағат бұрын
Alibe manyazi kukapezeka mwambo wa Eni Malawi anapenya aseeee this is not 1960
@AchinaKellz
@AchinaKellz 5 сағат бұрын
Ndipo inu
@BeatriceSaulosi
@BeatriceSaulosi 3 сағат бұрын
​@@AchinaKellzmposoo
BOBI WINE'S SPEECH TO BODA PEOPLE WHO HAVE ESCORTED HIM TO MAGERE
8:17
Shalom Television Uganda
Рет қаралды 1,4 М.
Random Emoji Beatbox Challenge #beatbox #tiktok
00:47
BeatboxJCOP
Рет қаралды 45 МЛН
Smart Sigma Kid #funny #sigma
00:14
CRAZY GREAPA
Рет қаралды 92 МЛН
MY HEIGHT vs MrBEAST CREW 🙈📏
00:22
Celine Dept
Рет қаралды 101 МЛН
Миллионер | 2 - серия
16:04
Million Show
Рет қаралды 1,9 МЛН
KWAGWANJI YA LERO 🔥 🔥 🔥 31 October 2024
36:39
HOT 265
Рет қаралды 20 М.
mdyangu comedy new 🔥
27:58
Malawi comedy 🔥🔥
Рет қаралды 1 М.
CHAKWERA ASAMALEEEEEE
4:26
Umatha Daily
Рет қаралды 10 М.
Kwambuka pugwe pugwe ku chipani cha UTM  aphana uku
4:03
RAHIL KAY TV
Рет қаралды 2,6 М.
A SULEMAN ndi ACHISALE KUYANKHULANA MOSAOPA
21:24
HOT 265
Рет қаралды 28 М.
RUSAPE NGOZI.........CHII CHINOITIKA KUMUNHU KANA AFA  [PART 3]
28:32
Drewmas Media
Рет қаралды 1,1 М.
NTHAWI YOCHOTSA CHIPANI CHOKUPHA CHA MCP YAKWANA - COMRADE CLIF CHINYAMA
10:07
NKHANI ZIKULU ZIKULU ZOMWE ZACHITIKA LERO
19:05
HOT 265
Рет қаралды 6 М.
Random Emoji Beatbox Challenge #beatbox #tiktok
00:47
BeatboxJCOP
Рет қаралды 45 МЛН