Am going to husband yomweyoooo kuno... Mude wasanduka husband
@JosephSenzani5 ай бұрын
Gaga ndi zimveka madolo anthuwa😅😅
@CeciliaMaliwa5 ай бұрын
Gaga wayamba kuzigulila malo sopano 'eee amfumunso awliiam amalusaso etiii
@PromiseChristianGregory-g5i5 ай бұрын
Gaga amatha
@JussabRobert5 ай бұрын
Koma Gaga e muli fundotu 😅😅
@anniewhite34975 ай бұрын
Mai phiri ndi wododoloka😂😂😂
@MpachikaChitani5 ай бұрын
Gaga the big machine wazigulira Malo zayamba kumvana ndi mulamu wake 😂😂😂
@amoschataika74405 ай бұрын
Zakhwima 😂😂😂kuyesa mwayi
@RhodaMwanza-o5b5 ай бұрын
Kkkkk azaveka bwanji ndimwanatu uyo
@e.r.mchanel14605 ай бұрын
❤😂😂😂 Big up Nkhalango Multimedia
@MathewsBanda-s4s5 ай бұрын
Gagayo❤❤❤❤🎉🎉
@madalomachira77665 ай бұрын
Zankhwima ayi zikomo 😂😂😂😂
@elizachimaliza63615 ай бұрын
You are the best guys mumati Vesa kukoma. Apa tonde uja wayamba di kudula kkkkkkkk zaululika yemwe anapha chifuniro Watsara tidzanve mwini wa mimba ya Chisomo 😅😂😂
@user-mw-tv5 ай бұрын
Gaga ufiti alinawo 😂 komanso akhoza kukhala munthu wakuba real life
@kaylagerezala5 ай бұрын
😂😂😂😂😂 zoonadi
@AfickDaud5 ай бұрын
Kkkkk zimveka adha eeeesh nd kawawa❤
@AnnieMatias-j5f5 ай бұрын
Ati my husband Mude😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂
@PrinceThom-pe6ie5 ай бұрын
Mwezi Uno WA June tataya ANTHU wofunika kwambiri Ku malawi😢😢.Achilima, Lucius Band ,achibiliti mmmm
@OsmanKachule5 ай бұрын
Ndizimene timafuna ituluke ifa ya chifuniro
@DONNEXKhama-bk1gy5 ай бұрын
Gaga anakonza kkkkkkkk waing'alura uku
@milinalakamkota82185 ай бұрын
😂😂 ines I love you ❤😂😂😂
@GOEMENGONDWE5 ай бұрын
Zankwima 😅😅😅😅😅
@NditajiMaxwell-cz8ir5 ай бұрын
Km zakhwima mn😅😅😅😅
@lucianogeoffrey42755 ай бұрын
Wow! Mwabwela mu nthawi take guys🎉
@EsteryHassan5 ай бұрын
Afumu mumatha ❤❤ kkkkkk kma zakhwima I Am going to husband kkkk😂😂
@MavutoJackson-j3v5 ай бұрын
Talowan Mr.zinveka
@ClementJoabe-tg3wx5 ай бұрын
Gaga diwa waing'alura😂😂😂😂😂
@godfreyguwa58055 ай бұрын
Zimveka ndi munthu oti sungamumvetse mbali imene amadyera...😂😂😂
@Maxwell-e2d5 ай бұрын
😂😂😂😂😂😂😂😂😂 Koma amfumu wa ndinkawaona Ngati samalusatu 😂😂😂😂