nkhalango multimedia you did it 🙌mwatsitsa mitima ya anthu tonse timawakonda a chibiriti 💔
@mercykhembo60473 ай бұрын
This episode portrayed our culture in times of sorrow very well, so far my favourite episode was the one Chisomo fought Makwale and Zakhwima, now i have added this one to my favourite list. Thank you for the entertainment while reminding us of our culture, koma Tonde ali kuti? 👏👏👏
@jamejoeljere01492 ай бұрын
Congratulations guys nice acting and this is what actually happens in now days during funeral of somebody aliyense amakamba zambiri
@AgriwhatMW3 ай бұрын
😂😂😂😂i cant keep calm when gaga is in action akuti achibiliti chita kukhwimilidwa 😂😂😂😂
@jameschiziwa3 ай бұрын
Adzukulu amalemu chibiliti 😂😂 mu mantha. Mwamupezerera chiphwanya. Nchicho chifukwa enawotso akuti zikuoneka kuti akhwimira nyumba 😂😂😂
@GiftJulius-gx2kb3 ай бұрын
Nthawi imeneyo pa saint kizito tikupanga masewelo limodzi pa assembly.ndi manuel ndomondo.ndimakhala dyelatu big up amanzy dalickeni alikuti
@ChitaniJoseph3 ай бұрын
Watching from cape town, I salute you guys. Great mindset ❤
@nkhalangomultimedia3 ай бұрын
Thank you 🙌
@Unknown-n9w4y3 ай бұрын
Mmm kom zankhwim ndimzake sangamapange maganyu kom bas kukhalila mmm anyamata obowa kkk
@MandingoJack-p6o3 ай бұрын
Malume wa Muthinda ati malemu adawapondesapo kasipa kkkkk
@DanielGanizani3 ай бұрын
😂😂😂😂😂 koma zakwima ndi nzakoyo mumakwana gayes🎉
@MandingoJack-p6o3 ай бұрын
Zakhwima ndi makwale sazatheka yooooo,,,RIP MR CHIBILITI😢
My saul of ret Vincent Rester ( Chibiliti) continue restin in peace We love you but God loves you more. Big up to Tonde wadula drama series for showing us all what happened and now we know exactly that Mr Chibiliti is really no more. Since that time we knew but the country was covered with black cloud. Thanks so much to management.
@LameckManuel-f3q3 ай бұрын
Kod iyiyi inali live man?
@giftmatemba31943 ай бұрын
🔥🔥 kept up always mumandimvetsa kukoma
@ashankagwa6683 ай бұрын
Tonde comedy my favorite, you are real guys 🔥
@FaheemChipojola3 ай бұрын
Kkkkkkkk koma achina zamkhwima musandikomole 😂
@VictorChinulaachebe3 ай бұрын
well managed, directed and organised zakhwima action yozunguzayi 😎mmmh🫰wadya nayo one
@AllanMwakalenga-wn5ib3 ай бұрын
I started following Tonde Wadula after an award ya entertainers of the year...these guys are the best
@nkhalangomultimedia3 ай бұрын
Thanks so much
@HenryMalikebu-i4g3 ай бұрын
Kkkkk Gaga bwinotubusaloze Chala Munthu makani ati iye skuziwa
@AbelMchema3 ай бұрын
Nkhalango multimedia mwakunga iyi,,,,Rest well legend Chibiliti😢
@ChrisDanielkuchondeАй бұрын
Ndiye kukhutatu mpka pamenepo maliro nkhan yake yosaka ndalama iyaa
@WilliamBauren3 ай бұрын
I have been following this series long time up to now, I'm glad today waiting you guys big up, but where is real Tonde never see him almost 7 episodes now?
@Foster-y5z3 ай бұрын
ndipo apa mutithandize
@AllanMwakalenga-wn5ib3 ай бұрын
Even pa maliro Tonde osaonekapo,alikutiko
@tonykapito28993 ай бұрын
Is Mr chibiliti dea in a real life ?
@DollahChombo-hw9ow3 ай бұрын
Yes@@tonykapito2899
@Georgeabudulrateef3 ай бұрын
Yes@@tonykapito2899
@CrispineBetha2 ай бұрын
😂😂😂Big up guys
@richardfalite67693 ай бұрын
I enjoy this drama watching from Zim 🎉🎉🎉
@AbdulhakeemMushushu-f4n3 ай бұрын
Ntchito mukugwira bwino respect ❤
@SleepyHarmonica-rg4ic3 ай бұрын
Paka kuyitanisa katundu wa ambuye awo kkkkk koma anyamata amenewa alibe ulemu kwabasi
@shupikayintuwaluwa-58993 ай бұрын
Ya zinguuuu kkkkk sapano mwati ya Agodern muliyeee
@BridgetGunde-w9c3 ай бұрын
Koma achina zakhwima,kuchititsa manyazi mayi anu aaa😂
@frankcholimbirapo2623 ай бұрын
Zakhwima waba ndalama za maliro😂😂😂
@patrickzembani43153 ай бұрын
Zakhwima mpaka kuba ndalama za mbale iiiiiiiii ayi 🙌🙌