Sorry, koma n'gono was Tonde akuchulukisa drama - its just a comment. Koma ma Guys onse amene mnalimo kale kale m dramayi mwapuluva guys and you act mwa real guys. 🎉🎉🎉 Achina zankhwima ndi azake eti " kuwasamalila katundu instead of hatsulling 😂😂😂😂" ya ndizimene zima beba thus to bring in new tongue . Mkubeba guys
@cassimyusuf6683 Жыл бұрын
Anakhumbo mimba ya tonde kwapachika achibilitu, tondeyo ndiwamaluziso ngati uyo akuthandizani chani😂😂 i like chisomo mu sewero imeneyi she's so serious
@GOEMENGONDWE Жыл бұрын
Ndingosoka ma Bala awiri aaaa Tonde koma🎉🎉🎉
@shupikayintuwaluwa-5899 Жыл бұрын
Keep it up guys. Zkuťheka kkkkkkkkk ma deal eshiiii. Nae falao shiiii
@markbanda7434 Жыл бұрын
Ukayezesa DNA mwina ikangokwana 2kg basi😂😂😂😂 koma tonde undisamale kkkkkkkkk
Muli boo Guys koma siwone Ali kut am from cape town
@ibratime Жыл бұрын
Mawulemu anu nose amu comedy ya tonde wadula mulandile nose
@Maria-nv8ev Жыл бұрын
Koma Molly mkz uja 2 hr pano kuphwanya zimbe kkk
@keita9875 Жыл бұрын
Typical of village life. Amfumu atuma mkulu wa ma thieves. Mai Phiri mwatiflashatu mbali yakuno. Chisomo nd supper star. Zimveka tikufunira zabwino usafe plz. Nagumbo masam ako sakuthandiza
@BridgetGunde-w9c Жыл бұрын
ati mma show anthu kuwathandiza kusamala phone😂
@MathiasNyilili Жыл бұрын
Ndimakunyadirani guys Koma chiphwanya wasowatu ndi mkazi wake kkkkkkk
@MussahYahaya Жыл бұрын
Timakunyadirani guys koma chipwamya wasowa ndi mkazi wake 😂😂😂
@sayidimisessa Жыл бұрын
Kkkkkk komaya nde muli okuba 😊 18:37
@phunzirozilinde8530 Жыл бұрын
Ati ukubooker mateyala😂😂😂
@AndrewHamiton-er8wn Жыл бұрын
Mmakwana guys Mukutisangalatsa kwambiri Kkkkkkk
@ibratime Жыл бұрын
Moleni akuti abig atumidwa ndi afumu mukugulatu ma teyala inu musowa m'mudzi muno
Kodi seweroli limachitikila kuti coz eeee kumatchulidwa kwambiri mbiri tu
@TheLeezo Жыл бұрын
If u know BT very well,it's set in Bangwe and most Bangwe settlers are originally from Mulanje and Thyolo,so midzi akutchulayo ndiya ku Mulanje n some parts of Thyolo
@thomaschipinda6952 Жыл бұрын
@TheLeezo they said amapangila kwa William which is chaku lunzu uku if I'm not wrong.
@gracekwapata Жыл бұрын
Zilibwino
@asiyatujuma5507 Жыл бұрын
Kkkkkk ❤❤❤❤
@ChifundoSikelo Жыл бұрын
Kalambo njee
@ChifundoSikelo Жыл бұрын
Tonde umakwana
@ibrahimdyman4356 Жыл бұрын
Sewero labwino
@RexChipolo Жыл бұрын
Mumatha daily
@georgeamosi9931 Жыл бұрын
Nice nice nice
@KenedyJolamu Жыл бұрын
❤❤❤❤❤❤❤😂😂😂
@SprianoAndrew-kf7gd Жыл бұрын
Mumakwana
@RajabMwhite Жыл бұрын
😂😂Farao
@jaffargeorge3477 Жыл бұрын
😊
@tzshoppers4471 Жыл бұрын
Amfumu amusewelo ili he act ndithu exactly amfumu eni eni ndithu