TONDE WADULA EPISODE 42

  Рет қаралды 20,611

Nkhalango Multimedia

Nkhalango Multimedia

Күн бұрын

Пікірлер: 82
@EstherZintambira-sq3yy
@EstherZintambira-sq3yy Жыл бұрын
Timafuna kulumikiza nkhani tipemphe iziyambila yathelapo tonde gags sanachenjele bwino😊
@dominicmphepo-jk8lk
@dominicmphepo-jk8lk Жыл бұрын
Zione and mudelanji are good examples of good girls in our society. I salute you since you don't defeated so easy.
@MisheckAselo
@MisheckAselo Жыл бұрын
Kkkk koma chiphwanya nice one 👍💪
@allanbanda4388
@allanbanda4388 Жыл бұрын
More fire guys ikankhilenibe kwakuya game chiphwanya and zio munasowat kwatsala mude and Mrs chiphwanya abweleleso thanks god bless you monseee
@georginakanyumbu7458
@georginakanyumbu7458 Жыл бұрын
Tonde sanayenera kuoneka kaye unless azaoneke ali kwa dola ngati mukupitiriza otherwise zakuvutuni kwambiri ulendo uno😮
@RazzackGwape
@RazzackGwape Жыл бұрын
😂😂😂😂😂😂. Ine ndimaganiza ngati iyayimbira paja tonde akamuudza mwana wa apongodzi ake kuti pakirani tizipita
@Gometunez
@Gometunez Жыл бұрын
ayambira polakwika nkhani sikusatirikanso😢
@ChisomoKapanda-jg2uf
@ChisomoKapanda-jg2uf Жыл бұрын
Eya alakwitsa atisokoneza
@Nadeon-y2k
@Nadeon-y2k 2 ай бұрын
Eti eti amalakwitsa posalumikiza nkhani
@Nadeon-y2k
@Nadeon-y2k 2 ай бұрын
​@@Gometunezeti eti
@anniewhite3497
@anniewhite3497 Жыл бұрын
Chibiliti baibulo mulibe😂😂😂😂😂
@OusmanDavie
@OusmanDavie Жыл бұрын
Kma anyamata a jozz nkhani yonama kwa akazi akapita ku malawi kmaso kunyenga eeeee alibe size 😂😂😂😂
@kelvinkhudze6241
@kelvinkhudze6241 Жыл бұрын
Kupwahiwa kkkkkk😂😂😂😂😂 watheba wathilidwa fumbi😂😂😂😂😂😂
@GOEMENGONDWE
@GOEMENGONDWE Жыл бұрын
Guys episode iyi congulatulations. Anthu nonse serious acting yanu made me feel like in real situation. Komano ndadabwa lero ine mpakana kugwesa misozi mmene zione anapanpila acting yakeyo 😢😢 . Guys mukutivesa kukoma 🎉🎉🎉🎉🎉
@dhaoudhiabedinegomaseko2363
@dhaoudhiabedinegomaseko2363 Жыл бұрын
Ziwo mwamulakwila kwabasi anakana amuna ochuluka ine ndi mboni sure achina Morey. Ndayiwala chilomwe cha achibiliti chija
@ChisomoKapanda-jg2uf
@ChisomoKapanda-jg2uf Жыл бұрын
Zio my favourite iweyo umatha
@KimChisola-gm7yw
@KimChisola-gm7yw Жыл бұрын
Amowe akuziziwa kumuzi kkkkkkk koma Tondeee
@estherkamwendo7971
@estherkamwendo7971 Жыл бұрын
Timadikila kuti tinve za tonde ndi Dola, zilikuti nanga
@RexChipolo
@RexChipolo Жыл бұрын
Ana a Theba aise 😊😊😊😊😊😊
@CidrickCosmas
@CidrickCosmas Жыл бұрын
Proud of you Zio...
@AndewDanger-ug1ol
@AndewDanger-ug1ol Жыл бұрын
Kod kwa tonde zinatha bwnj aaaaaa abaleeee ndy winawe kusia mkaz okhulupilika zioo Kkkk ndipasen mbali mzangokwatilamo zio bas wandimvesa chison eish
@AbdullahBullah-jj6bm
@AbdullahBullah-jj6bm Жыл бұрын
Apa mwatisokoneza bwanji simunayambile pomwe munasila anyway keep up the good work
@DennisKweza
@DennisKweza Жыл бұрын
Ndinachalira tonde zitha bwanji ndi dola
@Fanzo-h2l
@Fanzo-h2l Жыл бұрын
Anyamata wochokera ku Joni kulakwa mukuwazunza atsikana kusoya zione kukatenga second hand Cecilia mmm kulakwa keep it up Achibiliti Anagumbo akukuzelezetsani mimba ndi ya Tonse mumandimvetsa kukoma guys from Pretoria
@OusmanDavie
@OusmanDavie Жыл бұрын
Abazolowers kunyenga nkhalama zaku Zimbabwe ma oversize kuno ndiye chiyamba cha akilu aku chimalowa
@landwelchisambi4670
@landwelchisambi4670 Жыл бұрын
Zikukoma ndithu koma muziyambila pamene yathera tikudikira nkhan ya Tonde ndi Dora
@ibratime
@ibratime Жыл бұрын
Akuti zopwanyiwa ukusunga za tonde koma achipwanya
@KentKhomba-c9g
@KentKhomba-c9g Жыл бұрын
Zione ndi 1❤
@peternashyo9850
@peternashyo9850 Жыл бұрын
Zione is one of the best example in a society, she deserves a credit.
@MuhaMuhammad-n9k
@MuhaMuhammad-n9k Жыл бұрын
Akumuyenda mwakatumba kkkkkkkll
@humairamalombe295
@humairamalombe295 Жыл бұрын
Kod kunyumba ya azinveka zinatha bwanj ndi Tonde pajatu munatisiya m'malele kumenekuja
@AndersonKabaghe
@AndersonKabaghe Жыл бұрын
Muziyambira pomwe yathera koma, simuona momwe amapangira mfumukazi kapena mdyangu
@aishaStaubi-oo8tr
@aishaStaubi-oo8tr Жыл бұрын
Zoonadi akutisokoneza timuone tonde kt Ana tenga dolla
@giftblack7690
@giftblack7690 Жыл бұрын
😂😂😂😂😂😂 Nazombe wafikatu ndimoto akugwedeza heavy theba sinama😂😂😂😂😂 osatiyiwalila nkhani yatonde ndi mwana wazimveka simunayimalize kkkkkkk more fire guys mumatha
@dicksonmlera2777
@dicksonmlera2777 Жыл бұрын
Chihwanya kummasula mzake Chibiliti kuti sazala kalingonda
@JamesKeneth-c8c
@JamesKeneth-c8c Жыл бұрын
Apa ndie sinaione bwino guys mwasewera yobela tonde kotenga zovara zake amafunanso kukatenga mwana kwa zimveka kod zinathako bwanji?
@GeoffreyDan-p3d
@GeoffreyDan-p3d Жыл бұрын
Please idziyambila pomwe inathela coz ife timakozekela kut tione kut tonde zitha bwanji😢😢😢
@OusmanDavie
@OusmanDavie Жыл бұрын
Yah ndipo zoonadi sewero iliyonse imayenera kutero
@imransamson5308
@imransamson5308 Жыл бұрын
Eti kungopanga zopoila basi
@MuniruHassan-d7y
@MuniruHassan-d7y Жыл бұрын
Mmakwana chimphwanya, everywhere U go
@OusmanDavie
@OusmanDavie Жыл бұрын
Tonde anawuza mwana wapongozi ake kuti tiye tizipita last week, ife lero timati lyambira pamene paja kaa
@NdaonaMalata-vv6zw
@NdaonaMalata-vv6zw 11 ай бұрын
Zione is the best actress keep it up more love ❤️🥰
@vatineseduwin
@vatineseduwin Жыл бұрын
program timaikonda koma osasokoneza muziyambila pomwe mwathela plz
@AleksaWilliams-qc6cn
@AleksaWilliams-qc6cn Жыл бұрын
Tonde ndi Dola zatha bwanji?
@GOEMENGONDWE
@GOEMENGONDWE Жыл бұрын
Chiphwa yankha bwino wati nkazi Ali kuti😂😂😂😂😂. Your acting pafusolo it's of great deal
@OusmanDavie
@OusmanDavie Жыл бұрын
Chiphwanya anakoza shaaaa kumuza cholungamo kuti inu simumabeleka ayi kkk
@MalitaBanda
@MalitaBanda Жыл бұрын
Enafe tinachaila ya tonde ndi dora yathela pat😊😊
@kho7676
@kho7676 Жыл бұрын
Pomwe inathela sipomwe payambila zofunika muzizikoza bhobho
@MuniruHassan-d7y
@MuniruHassan-d7y Жыл бұрын
Nanga chifunilo ndi mole zinatha bwanji after kumugwira
@thomaschipinda6952
@thomaschipinda6952 Жыл бұрын
Mumaziyendetsa bwanji zinthu zi?
@franciscoduartie5762
@franciscoduartie5762 Жыл бұрын
Mnyamata waku Joni wafika ndi phumatu
@ididimussa
@ididimussa Жыл бұрын
Muzayambile powe yathera please mukutisokoneza
@tadalapatrick5914
@tadalapatrick5914 Жыл бұрын
Zione she is the best always
@elizabethkasambala9628
@elizabethkasambala9628 Жыл бұрын
Watching from USA 🇺🇸
@ZyduUmar-yw9nb
@ZyduUmar-yw9nb Жыл бұрын
Kupwahiwa 😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂
@phunzirozilinde8530
@phunzirozilinde8530 Жыл бұрын
"Am not the man that someone can play with"😂😂😂koma chiphwanya
@MwizaChinula
@MwizaChinula Жыл бұрын
Gaga kuzichemerera zokuba 😅😅😅
@RodgersKanyasko-dh3cy
@RodgersKanyasko-dh3cy Жыл бұрын
Kkkkkk vopwahiwa Chiphwanya ndi Chibiriti kkkkkk
@IsaacMpindo-ff4qi
@IsaacMpindo-ff4qi Жыл бұрын
Zione amuswera mtima km, amunanu sizoona ay
@inessmsiyambiri8517
@inessmsiyambiri8517 Жыл бұрын
Ooo yes
@chimwemwesolomon
@chimwemwesolomon Жыл бұрын
Mofayaaaa Koma muzipitilizila pamene munasiyila timakhala tikukutsatilan mwachidwi timayenela tive kut tonde why akufuna kumutenga mwana waziveka
@limbanigivinala3210
@limbanigivinala3210 Жыл бұрын
Joz timakhala busy.....
@ZyduUmar-yw9nb
@ZyduUmar-yw9nb Жыл бұрын
vuto mumayambila Pena Mesa Ronde amayitanitsa Dola aaaa
@patrickmkhalipa-my4en
@patrickmkhalipa-my4en Жыл бұрын
Fodya azisuta bwino
@Cooliodaxymw
@Cooliodaxymw Жыл бұрын
Zopwahiwa😂😂
@matembanevermind-po3me
@matembanevermind-po3me Жыл бұрын
Amachedwa pati achina made?
@emmanuelkamala8238
@emmanuelkamala8238 Жыл бұрын
Voohwahiwa vovilikana😂😂😂😂😂
@mickarison7488
@mickarison7488 Жыл бұрын
Kkkkkkkkl koma chiphwanya ayi zikomo 😂😂😂😂
@JamesMalango
@JamesMalango Жыл бұрын
Nazombe wapatheba watanganidwa tsopano 😅😅
@ClementWanja-l2l
@ClementWanja-l2l Жыл бұрын
JHB mwaveka a Chifuniro
@ronaldgowelo3865
@ronaldgowelo3865 Жыл бұрын
Zione wandinvetsa chisoni mmmm
@EmmanuelPensulo-q4t
@EmmanuelPensulo-q4t Жыл бұрын
Kumpahiwa komweko
@mafukenimasangwi5487
@mafukenimasangwi5487 Жыл бұрын
Tayikonzani program yanuyi iziyambila pamene ima thela please
@JuniorMphula-yw5jm
@JuniorMphula-yw5jm Жыл бұрын
Big up
@jrculdickson6629
@jrculdickson6629 Жыл бұрын
I love u zione I love u more serious not jokes
@mphatsojuliostandy4918
@mphatsojuliostandy4918 Жыл бұрын
Kod nkhani ya Dola inatha bwanj
@BrianB858
@BrianB858 Жыл бұрын
Komano Zione alikuti sitikumuona
@SuraChafu
@SuraChafu Жыл бұрын
𝙉𝙚𝙭 𝙚𝙥 𝙥𝙡𝙨 😮
@KenedyJolamu
@KenedyJolamu Жыл бұрын
😂😂😂😂😂😂😂❤❤❤❤
@edgarmax-pi1bx
@edgarmax-pi1bx Жыл бұрын
Mwafika basi madoro
@EmmanuelPensulo-q4t
@EmmanuelPensulo-q4t Жыл бұрын
Km chiphwanya anakoza
@shupikayintuwaluwa-5899
@shupikayintuwaluwa-5899 Жыл бұрын
Kkkkkkk
TONDE WADULA EPISODE 43
27:18
Nkhalango Multimedia
Рет қаралды 16 М.
TONDE WADULA EPISODE 44
28:09
Nkhalango Multimedia
Рет қаралды 17 М.
Will A Basketball Boat Hold My Weight?
00:30
MrBeast
Рет қаралды 109 МЛН
Это было очень близко...
00:10
Аришнев
Рет қаралды 6 МЛН
Jane apange bundle ya mowa
5:37
Jimmy & Jane TV
Рет қаралды 1,3 М.
DANIEL CHAPO É NOVO PRESIDENTE DE MOÇAMBIQUE ???
Moz na diáspora
Рет қаралды 1,5 М.
Mafunyeta memorial show
3:42
Dotolo
Рет қаралды 6 М.
H.E Lazarus McCarthy Chakwera's call to action for the African Risk Capacity (ARC)
0:42
African Risk Capacity Group
Рет қаралды 27 М.
Family planning and gender equality
6:54
Forum za enakopraven razvoj - FER / Forum for Equitable Development
Рет қаралды 52
NTV Uganda Live Stream
NTVUganda
Рет қаралды 1,1 М.
Fupa Lokakamiza Episode 13 - In cobweb of dating and lies
20:03
TONDE WADULA DRAMA SERIES EPISODE 125
27:37
Nkhalango Multimedia
Рет қаралды 15 М.
Em directo
Televisão de Moçambique - TVM
Рет қаралды 287