I like this sewero koma zakhwima ndi the brother apole moto otherwise ationongera ana
@user-Mamie46110 ай бұрын
I wasn't expecting this,, I'm so happy ndigona bwino I love this comedy ❤🎉
@isaacsalamba605610 ай бұрын
Mpoonsooo
@RoyalThai-rn2nu10 ай бұрын
❤
@SquareBoma-vl2rj10 ай бұрын
Mbambandeeee Tinder wadula ndi 1. Proud of you guys
@KondwanStolo10 ай бұрын
I love you guys mumatha muzangosowa
@Matabwah56 ай бұрын
Ching'aning'ani ndi 1😂 Chibiliti yu ndi dolo naye...need much effurt kuti akhale wabho
@johnmahata10 ай бұрын
Congratulations guys i love ur work specially makwale and dzakwhima ana awa sadxatheka mumatichosa tulo apa I'll sleep but not now😂😂 akanakumalizan kumene 😅😅😅chibilit
@simeonkhamwaha852910 ай бұрын
😂😂😂😂😂ndipo ana amenewa avuta eeeeee maka makwale eeeee mwana ovuta fodya amapweteka 😅😅
@Mpungwe12310 ай бұрын
Umu muli captain Gaga eish😂😂😂 Komatu simunationetse exit ya ex wife wa Ching'aning'ani
@AndrewHamiton-er8wn10 ай бұрын
Watching from mvera support dowa
@AfredKaponda10 ай бұрын
koma Chifunilo kod mwa Muthinda unaonamo chani😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂
@georgelungu246510 ай бұрын
Nice one at the end make a full movie if it's 1 to 3 it's ok
@LloydPitros-iu7wp10 ай бұрын
Much appreciated
@KunyengaMoyo10 ай бұрын
Ndipo mukamachedwa kutumiza ma episodes anu sindmamva bwino, zikukoma izi
@anoldluke-rl6pe10 ай бұрын
Mumatimvetsa kukoma kuno ku Nairobi
@GoodsonGeleta9 ай бұрын
I salute chisomo doesn't tolerate nonsense from zakhwima and makwale
@EsterLusale10 ай бұрын
Chisomo koma ndikamtima.uzakwatiwa koma ukaliri umenewo😂😂
@MussaBwayi10 ай бұрын
Mumakwana zakwima 😂😂😂😂😂
@justinenambazo685510 ай бұрын
Muthinda zikuvuta pati kuyankha foni? Mwati bwa? 😅😅😅😅😅😅
@violetnkhoma853510 ай бұрын
Nice one
@chibambarichard229 ай бұрын
CHISOMO YOU ARE A LIONESS 🦁 ❤️❤️💓💛✌️✌️
@johnmahata10 ай бұрын
Chibilit iwe wapeleka mimba ndikakusumira kumabunge ndiwe oukira ndilembera text ku uneco akumange😂😂😂 ndimakonda kuchedxa osanditengera
@danielantoniomsutu873610 ай бұрын
I was waiting for this, after watching I can take a sleep now 😢😢
@matiasnjewa10 ай бұрын
makhwala ndi zakhwima akuononga aphuzitsa ana zoipa
@rosemarymponda27410 ай бұрын
ndipo sewero lonseli limaonongeka ndi amenewa ali ndi khalidwe loipa
@jolowalenkhonde10 ай бұрын
Welcome ndimadila ndigona after ndikamaliza kuwonela
@SamMasese-ok5on10 ай бұрын
Muthinda pamenepo palibe kuzemba kkkk
@elizabethkasambala962810 ай бұрын
Watching from USA 🇺🇸 can't miss Tonde
@simeonkhamwaha852910 ай бұрын
😂😂😂😂😂eeee chee!!muthinda zamuonekela ndiye chifuniloyo eeee amuva madxi paja ndi zodiak tu anurse kuno 🗣️🤣🤣
@RenasMoyo10 ай бұрын
Achingangani 🎉🎉
@GOEMENGONDWE10 ай бұрын
Mothindwa kuvuta iwe 😅😅😅
@jaffasaidi115810 ай бұрын
Keep it up 🎉
@WillySitambuli10 ай бұрын
Gaga wasala madzi amodzi
@patrickzembani431510 ай бұрын
Chisomo ndi makanimakani kkkk
@husseinmoffatt10 ай бұрын
I like you guys 💕💕 serious
@TigwiLilongwe10 ай бұрын
Achipwanya ndi tondo 😅😅 amatha wakwatila iye nkaxi woyela avutatu kkkkkkkkk
@moffatthomas477610 ай бұрын
Keep it up guys am proud of you always ❤❤❤
@SHAHIDAHUSSEIN-y2y10 ай бұрын
Good one
@SamMasese-ok5on10 ай бұрын
Chisomo very strong and courageous I love her actions
@violetnkhoma85358 ай бұрын
And she really knows how to act
@williamlamick613010 ай бұрын
Never sleep 😴 waiting dis
@matembanevermind-po3me10 ай бұрын
Still following
@anniewhite349710 ай бұрын
More🔥 timakunyadirani nonse😂
@ChisomoyoungstoneMwinjiro10 ай бұрын
Ka xmas surprise...mmakwana fam
@giftblack769010 ай бұрын
😂😂😂😂😂 koma chibwenzi chimanzunzatu muthinda kulephela kuyankha foni iyi izathela ma penalty
@PromiseKhenzo10 ай бұрын
ZIMVEKA umakwana 😅😂😊
@GOEMENGONDWE10 ай бұрын
Ndili ndi question mark 🎉🎉🎉🎉🎉🎉kkkkkk koma
@mbwindinga10 ай бұрын
Nice
@MathewsCharles-mh8yg10 ай бұрын
Keep it up 💪🏽
@SamuelNkhoma-v8w10 ай бұрын
Chisomo❤
@shupikayintuwaluwa-589910 ай бұрын
Kkkkk amfumu osaziwa za maliro
@kelvinkhudze624110 ай бұрын
Muthinda akatundu 😂😂😂😂😂😂😂
@madalitsoyakobe212310 ай бұрын
😂😂😂muthinda
@EsterLusale10 ай бұрын
Muthinda big man 😂😂😂
@inessmsiyambiri851710 ай бұрын
Muthindaaaaa
@GloriaSuply-zn5uo9 ай бұрын
❤❤❤
@MaliyaDaiton10 ай бұрын
Tonde wadura ndi 1mumativesa kukoma mix simuchedwesa timakunyadira guyz
@georgeamosi993110 ай бұрын
Koma Zankhwima,,Bar ilipo ya opposition
@GeorgeGeorge-bu6cy10 ай бұрын
Mumakwana guys
@HalimTalim10 ай бұрын
Keep it up my people 💯
@sayidimisessa10 ай бұрын
Ineso sewero iri ndimalikonda
@fatsanibanda86910 ай бұрын
Muthinda wachitika pakala pakala
@siskanyirenda10 ай бұрын
Koma malita akolola panopa koma
@TigwiLilongwe10 ай бұрын
🎉🎉❤😅😅😅 koma makwale
@Tawina010110 ай бұрын
Tonde wamdula ,,,umakwana
@inessmsiyambiri851710 ай бұрын
Senior gaga
@GOEMENGONDWE10 ай бұрын
Guys iyi ili boh mwstivesa kukoma . Happy Christmas to u all
@MussaBwayi10 ай бұрын
❤❤❤😂😂
@ClementWanja-l2l10 ай бұрын
Gaga ndi machine kuyendesa ufumu afumu alipo 21:11
@Tawina010110 ай бұрын
Senior Chief
@susantembo20769 ай бұрын
I love everything shown but the Makwale and Zakhwima part in the way they treat elderly people including their own uncle. I am not sure about the impact it has on young fans.
@susantembo20769 ай бұрын
Watching from US of A
@violetnkhoma85358 ай бұрын
Sizimandiwazanso,,, It's too immature
@RobertLuka-wy9cl10 ай бұрын
Athamangiseni 😅😅😅
@kondwanimwamba690710 ай бұрын
Free range system
@MalizinaCodo10 ай бұрын
Muthinda alindi chiwanda chá uhule
@PromiseKhenzo10 ай бұрын
Chemuthinda yankhani 4n kkkkkkkkkkk 😊😅
@SamukLungu-zg7fl10 ай бұрын
Timakunyadirani guys
@kingsleyseda687310 ай бұрын
Mwatizunzatu mkudikila
@ClementWanja-l2l10 ай бұрын
18:47 Chibiliti mantha
@yesayabongwe423410 ай бұрын
Zamkwima and Makwale😂😂
@rosemarymponda27410 ай бұрын
I like this sewero koma zakhwima ndi the brother apole moto otherwise ationongera ana