Coka kumkuyu Kodi black box ija ilikuti umkakamba ija.
@BenardKalilaniКүн бұрын
We need black box iwe kunkuyu history is the best teacher
@TonyMhoneКүн бұрын
Iwenso Chayima ukunena maganidzo AKO futseki. Tiopa mpaka liti galu iwe
@DiveliousNyirenda2 күн бұрын
Munthu wa straight sangalimvetsedi lipoti lija poti mafuso ambiri sanayankhidwe for example apangidwa bwanj kafukufuku opada black box, komwe kuli black box sakutiuza chosecho anduna ananena mwaveveve kut yilipo ndipo akusunga bwino......
@TonyMhoneКүн бұрын
Zonsedzi dzidzatha black box itatulutsidwa timve zili mmenemo ndipamene ineyo ndikhulupilira ziti Ngozi ija ndi ya natural come out Chikangawa iwe. Tiudze zoona
@Eqrah-hj2nuКүн бұрын
Chilingamo chidziwika after 2025 elections
@BrightPhiri-c6hКүн бұрын
Anthuwa akungo kutinamiza za report ya ndenge. Those guys akufuna kubela ma vote coz akuthawa report la Chilima. Guys tiyeni tisinthe Bomali. Kenako tinzamva zenezeni za Ngozi ya Chilima
@abwinoamatani4921Күн бұрын
Atsogoleri achinyengo analandira ma envelope asanayambe kafuku-fuku
@AnyelwisyeSikwese2 күн бұрын
Mayankho abwera Chaka cha mawa pa 16/09/24.Tizachotsa chikangawa
@StevenMasamba-y1p2 күн бұрын
Zoopyezana ai akunena chirungamo
@UPCChisomoChoirКүн бұрын
Commisssion of inquiry yanuyo munali a mipingo omwe analandira ndalama mesa munawalipira ,mxweeee mitu youmayo
Abishopu akatolika akuti sakukhutitsidwa chifukwa choyamba adati ndikunkhalango yoopsa (thick forast is it so
@gibsonkhumalo6649Күн бұрын
Akulankhula molimba mtima ameneyo ndikuwona ngati akudxiwa bwino bwino za ngozi ya VIC president pafuka utsi ndiye kuti Pali moto eeetu
@TamandaniMaseyaКүн бұрын
Iwe chaima kuli mulungu
@WisikiBlack-gj4guКүн бұрын
Kukhuyu palibe chomwe angatiuze kodi muesa a malawi 🇲🇼 fe ndiopusa kkkkkk munamatu akukuyu
@MosesTangwe-q8o2 күн бұрын
Simungawanamize anthu chilungamo tikuchidziwa. sangapange kafukufuku opanda black box.black ilikuti?
@ChimwemweKondowe-nj4lx2 күн бұрын
Nkhani yithe poti anafa aja si abale ako. Iyitu siyitha
@wacksoniron2 күн бұрын
Achayima inuso mukuzidziwa
@chitanibenito1109Күн бұрын
Where is black box?? How can I bring out a report without mentioning the issue of blackbox???? Maboza basi anthu mukudana ndi kuuzidwa chilungamo bwanji????
@JOHNOlesmasCosmasКүн бұрын
Nkhaniyi sikutha pokha pokha okuphayo nayeso ataphedwa ife a Malawi tidzakondwa ndipo tidzaiwara mpaka kale
@YamkelaDamba-x5fКүн бұрын
Chakwera must tell the country the truth
@FrancisNyayiКүн бұрын
Mpomwe aziwa ku usi sufuka popanda moto eee kwasala akubanja😢
Koma oliwoza boma akusowa kuti atulutse black box yomwe anatinamiza kuti ilipo,,,afufuza bwanji za ngozi ya ndege popanda Black Box??? This is rubish
@WilsonMbendelaКүн бұрын
Kodi iwe chaima umati chani matako ako
@TachikoMwanamanga2 күн бұрын
Ndipo khani imeneyi anthu mudzayakha. Itha bwanji anthu mukupanga research mobisa kumangotinamiza. Timaona ma research amaiko ena different with our country
@DjshukulanGift2 күн бұрын
Pokut chakwera ndi mulungu koman zizatha
@FelixKChisale2 күн бұрын
Iwe ndiwe opusa kwambiri iweyo sungakhale mtsomgole
@Alexanderdzungu-i5o2 күн бұрын
A kunja ndi abodza koma akuti ma bishop ndiwo amadziwa kaya zanu izo
@TamUs-u2hКүн бұрын
Kodi za Imfa ya Isa Njaunjo why you bishops munakhala chete?
@JuniorAllan-n1t2 күн бұрын
We need black box that's all
@ConradccjSokoSokoКүн бұрын
Chindere, sikuti ukakhala opanda mkazi, Wana sikuti sufuna mtendere, Mtendere ndiofunika kwa aliyense dziko lonse Lino Mmali mobweretsa uthenga wa chiyanjano, mtendere, chiyembekezo iyeyo akupereka uthenga wopasula, wa mkwiyo. Iyeyo ndi Mulungu? Akufuna lipoti lolembedwa ndi Mulungu?
@rabisonpias5131Күн бұрын
Mwauze ACHAIMAWO mutu wawo udapenga. Tidzingomvomereza ndi za bodza zonse?. Where is a black box?. Who ordered searching isiyidwe.? Who told CHAKWERA zoti ndege idakafika ku MZUZU. Amene adamuwuza CHIMWENDO zoti malo mu ndege athamo, yet he/she knows zoti padali only 9 passengers. What was their intentions?