Albert zayambikaso uku mnyumba muja,☺️☺️ nde wakumana ndi Ng,aluli Edo eishiiii ii, bad influence😂😂 kkkkkkkkk akuti mwaziwa bwanji nanga iziso ndanena ndine😁😁
@HelbertKalumbiАй бұрын
😂😂😂 ng'aluli😂😂😂
@HesekiahChungaАй бұрын
Edoooo mmm too much trick questions 😂😂😂😂
@EMM_KAY_KIMАй бұрын
Gani pamsana pake ndithu😂😂🙌🏽
@ChikuBulamboАй бұрын
Koma abusa ngokhomelera eee🙌🙌
@kherereluckson4343Ай бұрын
Ati ndigula bwanji zinthu zoti ndilinazo 😂😂😂
@izahakageorge9573Ай бұрын
Kmano amuna Hyphen aaaah atayatu Yesu awa ooohooohaaa #MUCH LOVE GUYS
@llewellynkhungwa4712Ай бұрын
Kuyamba banja mu banja 😂😂😂😂😂 koma Gani kkkkkkkk
@chitchohistorical1036Ай бұрын
Albert ndi more vibes😂🤣✨🔥🔥🔥
@LeticiaNgaiyayeАй бұрын
Koma barman Edo amakonda mabodza mmmmh kkkkkk amakonda azimva mabodza a mmakomo mwa anthu zimankomela😂😂😂😂
@LexMpini8 күн бұрын
Live wamabodza Edo
@reinamlongoti9286Ай бұрын
Ati vuto lake ndikatenga chicken ikafunika rice🤣🤣🤣