Boma losakhidwa ndi Mulungu wamoyo ilo....chilungamo,chitetezo,chitukuko
@WaysoLufas58 минут бұрын
Tukusyanitsa ulamliro wa cakwera tibwelere mbuyo dad omwei alind pokomera pake pangono
@thatgirrroskrr35702 сағат бұрын
Mungulu ndamene anatipasa adadi
@Amina-gg5grСағат бұрын
Peter Mutharika amalemekeza msufulu aanthu, achakwera koma kupha. Mmene anangopha chilima Muja wamenyera campaign dpp iyenda ndimapazi wa ku state house
@Amina-gg5grСағат бұрын
All we pray for adad long life , chakwera amwalira pompano amulondola chilima anamupha uja akusiyani mukulamilanso boma li
@JeanBanda-zy6wu2 сағат бұрын
A MCP mpake sakugona kuganiza zobela zisankho sangamake apa olo pang'ono
@bonwelllinyenga87114 минут бұрын
Umboni ukuwoneka wokha ndiye winaye uzati chipani cha wina ndi mcp uzaona maloza
@chimzywyson284211 минут бұрын
Katundu wa boma ❤❤❤❤
@ELLENZAPS51 минут бұрын
Anayamba ntsinje wakhalidwe
@PatumaCassim12 секунд бұрын
Chipani chosusa chimenechi 😅😅😅😅 ai fenkis ndithu komatu achakwera anapita pa ludzu pompo kukapanga nsokhano chimwendo akati kwacha anthu kut ziiiiiiiiiiiiii😂😂😂 nde wina aziti boma ndilomweli sitikusitha aaaaa 😅
@LacksonChimwazaСағат бұрын
Mmm koma yaa amenewa anthu ngati final ya world cup