Hi!!! My name is Joseph from Mangochi, actualy i'm here in MOZAMBIQUE, panopa anthu omwalira chifukwa cha má demostretion akukwana 350 Anthu omwe abvulala modetsa mkhawa, moti ena sazayendanso chifukwa cha ulumari 1035 Anthu omwe ali m'chitokotsi chifukwa cholimbana ndi boma ndi 4250 Update 28/12/2024
@AlicePaweni14 күн бұрын
😅é😊
@KOLOMITICHITUPE11 күн бұрын
Zovut kw
@kennymwanyongo816520 күн бұрын
Titengelepo punzilo pa zomwe zikuchitika ku Mozambique. Anthufe sitikuyifuna SMARTIMATIC yomwe MEC ndi MCP akulimbikila. Mpoto yake ndiyimeneyi tikuonela limodzi ku Mozambique. Manual ndi yokayo yodalilika. A Kachale, chonde, lowelelani pa nkhaniyi monga Judge yemwe anayendesa bwino previous credible Chisankho. Zikomo kwambili....❤
@GiftMusorola-l2o15 күн бұрын
Inuyo mukukanika ziwonesero iweyo umbuli ndiwumene wakuvuta a police akumalawi simungachite kanthu Iweyo usalimbane Ndi Mozambique
@ThaboKhanye-wp9pm3 күн бұрын
we are ready
@AlexKaunda-w7l20 күн бұрын
Mozambique south African Bukina faso and Nigeria ndi maiko awanthu ochenjela osati malawi dziko la anthu opusa dzoona kuopa chimwendo Banda 😂😂
@NASP-g7h17 күн бұрын
South Africa nde ayi amwene... Uziwa kut sa kuli dela loti athu okuda sangafikeko kom president wakuda nayeso safikako komaso sa rizevu banki ya sa ili manja wazungu akunja
@SaraDomingo-n9i13 күн бұрын
Mozambique amwene yafika pena ndipo wachipani chotsutsa alamula pa 15 mwezi uno tikulumbilitsa
@AliSmartMposa20 күн бұрын
Good job brother
@LeyvanSamuel-pe5tc21 күн бұрын
Aaaaaa Kuno sizngatheke a Malawi Ife ndi amatha timaopa police 😢
@JamesCheed17 күн бұрын
Leka Bale wanga anthu amatopa
@IsacMassielea12 күн бұрын
zitero ndithu😮😮😮
@MchachaGoodson21 күн бұрын
Amalawi tipezepotu phunzilo osati MEC ndi Anabell mkazi wa John tembo azitipusisa.
More fire Apule atsopano anthu atopa basi Malawi tili m'mbuyomo kunoso anthu adatopa pano zafika Poti azibusa auchifwamba akumachemerela Boma
@AchinaKellz21 күн бұрын
Big Up amalawi aziwe kuyipa kwa smartmatic, tikhare osakha moyenera kuopa zimenezo tikapusa kuvuta, ndie dzakoyo akufuna kubwera kuno ife pamene tikufuna kubwera komko kusiyana kufa ndinjara, big up tikapusa next ndikuona
@HONORIOMATEUS-w7m9 күн бұрын
Muzissiye zikubweletselani mavuto a Malawi MOZAMBIQUE siyamasewela ndikuzani KUTI VENACIO akadzafika zaka 20 NDI mwayi FRELIMO imapha
@GiftMusorola-l2o15 күн бұрын
Palibe chomwe mutazachite aMalawi iye sangazaziyike pa U president ndiwe osusa usalimbane Ndi Boma
@Chikwawa21 күн бұрын
M“busa ameneyu akapusa adzatha moipa kwambiri
@lucasalmocodivaissone73716 күн бұрын
Bigman Kunoko kwavutadi ..ine ndimakhala ku Mozambique Kuno
@SymonSandram-l8d14 күн бұрын
Akulu mukabweretsa nkhani osakhala ndi mbali or against government mwava
@rabecachiutsi665715 күн бұрын
Inenso ndili kuno ku mozambique, zoona adaberedwa mavote, moti venancio mondlane pa 15 akhala president wa Mozambique, moti tayamba kale kusitha flag komanso pa 6 ndi pa 7 january kukhala kusanga mafumu etc
@GiftMusorola-l2o15 күн бұрын
Sangakhale president ngati waluza azapanga Boma la gwirizano
@GiftMusorola-l2o15 күн бұрын
Kukemya zinachitikanso lelo olamula akupitirizabw Africa mtchito yawo ndiyimeneyo palibe chomwe chingasinthe Malawi Mbuli zoopa ma Demo 5 years yatha mwapangapo chani osusa
@MercyKazembe-q9w21 күн бұрын
Ndizowona lne ndilikonkuno ku Mozambique kwavutilatu simasewela ayi anthu akwiya
@isahogrijob34611 күн бұрын
Aaa zovesa cisoni mabwana
@falliotphiri68820 күн бұрын
Amalawi sakonda nkhondo,,, Malawi ndi yosiyana ndi Moshiko...Atolankhani a social Media , muzisamala malankhulidwe
@FranciscobulandeBulande16 күн бұрын
Aise kuno silibwino komabe Venancio alamulila basi
@IsacMassielea12 күн бұрын
ineyo ndine wakuno ku mozambique ndi zoonadi zavutadi ndithu
@BenChitando16 күн бұрын
Not Mec, CNE, Comoção nacional das eleições. meaning: National Commission of Elections.
Zowonadi tiyenera kusintha system ya smart Matic chifukwa tizawona zomwe Zikuchitika Ku Mozambique
@Mahamudu-q6b21 күн бұрын
Yes❤
@LazaroSinerioSineiro20 күн бұрын
Ineso ndi malawi ndiri komkuno. A bomawa anabadi
@WilliousNyirongo12 күн бұрын
Sanawine koma njala yofuna undinfo aluphetsa nayo anthu . Makala amoto ali pa mutu wake. Imfa ndi gahena zikumuitana. Osavomereza bwanja? Ndalama ndikufuna kutvhuka zinamugula uyu ,tangomupatsani miyezi yochepa chabe alipila.
@GiftMusorola-l2o15 күн бұрын
Iweyonso mtolankhani ukunena zokomera Dpp osati ndale Mozambique Ndi ziko la nkhondo sngagane Ndi mbuzi za kumalawi Iweyo ukukomemesera nkhani
@MosesNyalugwe-ll8hh14 күн бұрын
Atchulapo Dpp apa?
@ClifordyAlfredo16 күн бұрын
Teagas wAtha kuno
@ClifordyAlfredo16 күн бұрын
Panopa kulibe police kuno bg
@Masekoliche16 күн бұрын
😢
@ClifordyAlfredo16 күн бұрын
Kuno zavutako man akufa anthu asalakwa moti a police ndi amene aku malitza anthu kuno
@StaffordblairFuleza16 күн бұрын
Ndizoonadi pakufuni kupewera Natalie nkhani imenei .kuyambira pa 09/10/2025 m'paka lero pa 30/12/2024. Akuluakulu a chipani cholamura adathawa .onse akupezekera ku songo tete caboraBassa..ine ndine modzi one nkhani ikuchitika ndi masoanga awiri. Kukati kwada tikumagomana make nkhutu alipanja.
@ChiccuElijah17 күн бұрын
Kma mwati ku Malawi mu 2025 sitiziona Kwa2 kuno????
Mcp singawina zimenezi or mwana akudziwa ife tisanayambe kuotcha chaboma choyambirila tizakaotcha anabelo John tembo ntalimanja chifukwa ndiamene sakufuna kumva chenjezo anabelo ngati pali amene akumulimbitsa mtima atengele chitsazo za ku Mozambique one day is one day